I'm here on RUclips channel because you every time I'm just have been waiting you don't make mistake to stop things please please please please I love you brother thanks
Lumumba and Kwame Nkhrumah were democratically elected. Traore and Tchiame were not legitimately elected. Don't twist facts. Where is the evidence that Samora was killed? Where is the evidence that Sankara was killed by the west? Mwayamba kunama kwambiri
You are a great historian
Takunyadilani kwambiri zedi bro!! Thank you very much 🙏🙏!!
Azungu amadana ndi anthu omwe amateteza Africa. Koma soon or later, Africa will be free!!
i love the work you do
You are the best man
I'm here on RUclips channel because you every time I'm just have been waiting you don't make mistake to stop things please please please please I love you brother thanks
i love this chanel chifukwa chamkuluyu amafufusa bwino komanso amayankhula chilungamo
We have been waiting for this thanks very much baba
Thenks bro
Am with you brother man!!
For westerners, atsogoleri abwino ndi amene amawatandiza kuba mu Africa.
May God protect our Traoré and Tiani!!
Boss we love continue the good work
You stand for us all the time elder ❤
0
makwana wakuru respect
mativesa kukoma live timakusatrani
Thank for new
May our Allah protect you Traore . Big thank you for your information big up.❤
I count on you
Bakiri muruzi mumativesa kukoma keep it up the good work 👍
Go up with your talent
Tingowaikiza mmanja mwa mbuye tikufuna afrika isinthe atibela kokwanila, ambuye atetezeleni ndinu👏👏
GOD'S POWER SUPERCEDS ANY POWER THAT EXISTS ON EARTH.
Africa leader they must do something
The best historian ever
BIG 👍
We love bro❤
For once , u got this on POINT.
Best Chanel ❤
Thanks sir; iwo bwanji sangomayamba kubwela kukagulako myala ngati amalonda basi? Akawalala akulu akulu ee eee.
Timvere zimenezi bro
Never giver up
Timakuyadila kwambiri ❤❤❤❤❤❤❤
God bless Africa please
Thats why we like Russia. America kwawo ndi kupha ma africans leaders
Umakwana big...ine ulemu napeleka kale kwainu....
Inu mumatha bro keep up
Power mesa💪💪💪
Mumayankhula Chichewa chomveka bwino sir
The best hesto
Koma abale zikoli ntendere tiwupeza kt?
❤
Aphekoso chakwera
Putin akumkanika akulimbana ndi mwana uyu that's why Africa is poor because of these enemies france America ndi azawo
Russia is still there to protect my fellow African leaders and their properties ,
Ana awawa afa imfa zowawa kumene, USA sipanga phada
Mulungu odziwa kuteteza tipempha muwateteze atsigoleri amenewa
Eish America 😢😢😢
Following mwachidwi
umakwana boas❤
Good boss
Rise up Africa. Don't sit down and watch please
My Africa. Tidalile Russia basi. Otherwise USA ndi France akutilowa mkabudula. Pano atipuditsa ndi permanent seat ku UN peace chani kaya uko.
Asawaphe pls
Jelard Ford my love
Mumakwana Big pitilizani kutipatsilazina ndizina
5 minutes yokhabasi ayi zikomo
Best tv
Tili panopa braza
Word war 3🤔🤔
Apedwe
❤❤❤❤
Mumakwana big
Putin naye atumizaso ake
Iiiiii koma amereca umbavawu azasiya lit
This time Russia silola zopusa zimene France ikufuna.
Iwe ndi katundu pa history aise
😂😂😂 aphedwe
What's the plan to stop this?
🙏🙏🙏🙏
Things are are not OK
Nanga putin what he is doing to defend these leaders
Ulemu wanu big
Ndafika kale
Maiko aluyawa ndi nchocho amakonda kulowelela pa zilizonse
America ndi aluya kodi???
Inusot inu mamericans ndaluyas kd
Azungu ose machende ao 😂😂😂
America ikanakhala kut ndidolo ikanamusowemtsa put putin. Osaopa ma guy
Koma yatha mwachangu bwanji
America nd atopola
Big tatiuse saku Morocco kut sikuta bwanji kumeneko please please big
Sizabwino zomwe America ikuchita
Tidkkila zimenexi bg
Russian we Will be our side forever
Silero America ikutha bolani dongo la pachulu
Puttin is Here this time around
Wapenga Biden
Timamva kukoma tikamamva mbiri ya dziko lapansi
Lumumba and Kwame Nkhrumah were democratically elected. Traore and Tchiame were not legitimately elected. Don't twist facts. Where is the evidence that Samora was killed? Where is the evidence that Sankara was killed by the west? Mwayamba kunama kwambiri
Ulemu wanu man. Koma tadzapanganiko history ya Kwame Nkrumah
❤
❤