Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
Mofaa Billy Kaunda,,iwe ndiwe chitsanzo cha oyimba otsaopa zithu zikamalakwika ndimakonda kwambili nyimbo zako mr billy kaunda.
Good speech mr BK
Billy Kaunda anadalitsidwa ndi nzeru, kuyankhula kwa nzeru honorable Billy.
Koma za chitukuko alibe
@@WorriedNdhlovuZoona?
Kod akadalibe mp iwowa@@WorriedNdhlovu
RIP ,his songs motivated me during my childhood
Peter Thomas from port Elizabeth Thank you Billy kawunda chifukwa chamawuAmenewa
Umakwana ❤❤❤❤❤
Title of the background music please
Mumakwama wakulu a Billy 😂😅 1998 production 🤔 Mwapindulanji? from your first album 🙏🏼 to God must be Glory
Rip sir sodier Lucius banda Zikomo 🙏🙏sir Billy kaunda chifukwa Cha mawu achilimbikitso.
Nyimbo mukuimba pansizo zikutisokoneza
Zoonadi editing ikumuvutilapo doloyu si video yokhayi almost all of them😢
anyamata ogwila pa lisani omwewa
rest in peace 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
Rest In Peace our Legend
Osalotsa ndale pls
Uchuluka zelu pamalilo sikwabwino
Rip Lucius Banda
Who sang the song on the background?
Black Jack
❤
That music in the background is really annoying 😊
What kind camera 📷 u use is not looking nice for us
Ndipo camera 📸 imeneyi bola Samsung Galaxy s24 ultra
Live sioneka bwino,, even yaku American is vivid
Osapita camera yako bwanji?
@@BlessingsNkhambule-x4q iwe ndichoke ku u k chifwakwa chakamela ndiwe opusa
Bwanji ankasa sakupezeka mumaliro?
Samagwirizana komwe mbenjere nayeso sanaoneke nawo kumaliroku
Amapezeka koma amakhala Malo obisika
Ndikunva ngati dzira likukana nkhuku kuti anango ndifungatira nku gogomola mwana piye koma sindinachoke ku nkhuku
Akunena chilungamo koma
He is saying the truth. You promote what is already there, while to mentor is to bring out something hidden in someone
The background sound is so loud and it's msking the video so boring.
Inenso zanikhudza kwabasi Gift Zambia
Rest in peace soja
RIP well soldier
A Billy Kaunda palibe chimene anachita ku constituency yake, misewo yoipa kwambiri, ndipo kumanvetsa chisoni ku Kafukule kwawo. Asaname apo.
Imwe ndimwe wazeleza Billy Kaunda akukhuza za maliro ndikulomgosola za moyo wa Lucius Banda, Inu basi mwaipeza campgain kuyamba kunena za mseu , zikugwirizana pati? Ndinu achitsiru kwabasi
Eti mpha nyifwa. Zaku consistency vya kwinu uko. Respect is needed. Kwakula ni sanje
Zikugwilizana ndi zazitukuko why people you don't use your brain you talk nonsense xmx
Sono zikulowanq pati
6:28 @@memorymselemu
RIP
Nyimbo ikuveka pasipo ikusokoneza. Is making noise
Zomwe this zomwe that is boring as a fuck🤕
Rip soldier
Rip
Mofaa Billy Kaunda,,iwe ndiwe chitsanzo cha oyimba otsaopa zithu zikamalakwika ndimakonda kwambili nyimbo zako mr billy kaunda.
Good speech mr BK
Billy Kaunda anadalitsidwa ndi nzeru, kuyankhula kwa nzeru honorable Billy.
Koma za chitukuko alibe
@@WorriedNdhlovu
Zoona?
Kod akadalibe mp iwowa@@WorriedNdhlovu
RIP ,his songs motivated me during my childhood
Peter Thomas from port Elizabeth Thank you Billy kawunda chifukwa chamawu
Amenewa