'AMANDIYAMWISA MALISECHE DAILY '- MMWENYE AWUZA WA NTCHITO ADZIMUYAMWA MALISECHE

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 19 окт 2024
  • MMWENYE AWUMIRIZA WA NTCHITO KUTI AZIMUSEWERETSA MALISECHE
    Kupeza ntchito ndi chinthu chokoma kwambiri kwa munthu aliyense makamaka uyo amene wakhala nthawi yayitali akuyisakasaka ndipo ali ndi anthu amene amadalira iyeyo monga makolo, ana komanso mkazi. Pamene munthu wapeza ntchito ndiye kuti amakhala ali ndi chiyembekezo chachikulu kuti zinthu zake zisintha ndipo amene amamudalirawa ayamba nawo kukondwa. Komatu zimenezi sizili motero kwa mkulu wina wochokera mu mzinda wa Lilongwe. Mkuluyu amene dzina lake sitilitchula anapeza ntchito yophika kwa mmwenye wina a Jayesh Kumar Dalwad amene anali wothandizira ntchito za mkulu wa kampani ya Shayona Cement Corporation ku Kanengo analibe malingaliro akuti chimwemwe chake chakuti wapeza ntchito chitha posachedwa ndikuyamba kukhala moyo wa mavuto.
    Atakhala kwa nthawi yayitali asanapeze ntchito, mkuluyu amene amakhala kwa Mtsiriza mu mzindawu anali akukanika kusamalira ana ake atatu, koma mu mwezi wa January 2023, iye anapeza ntchito ngati wophika ku nyumba ya bwanayu imene ili ku malo amene kuli ma office a kampani ya Shayona yi ku Kanengo. Atangogwira ntchitoyo kwa mwezi umodzi, mwezi wotsatira wake umene ndi wa February zinthu zinayamba kusintha ndipo akuti abwana ake aja anayamba kumamawuza kuti adziwasisita bondo lawo.

Комментарии • 53

  • @KassimRasheed
    @KassimRasheed 4 месяца назад +1

    Aaaa zanchamba bass
    Iyeyoso anagwirizana nazo bwanjibosangosiya nchitoyo bwanji nonse machende anu 😂😂😂😂😂😂😂

  • @FysonMkuzura
    @FysonMkuzura 4 месяца назад +7

    Mumabweretsa nkhani zofunikira koma musinthe speed yamalankhulidwee

    • @Sharoshining247
      @Sharoshining247 4 месяца назад

      Ndipodi ife kuti tinve bwino bwino palitu ntchito 😂😂😂🤣🤗🤗

    • @AleksaWilliams-qc6cn
      @AleksaWilliams-qc6cn 4 месяца назад

      Mwina ndi manyado,ineso sizimandiwaza

    • @PiscaDicksoni
      @PiscaDicksoni 3 месяца назад

      Ndipo ndie zimanyasa

  • @ChifundoNinje
    @ChifundoNinje 4 месяца назад +3

    Muthu kwanu ndimulolela kupanga zimenezo zaziii zauchisili ngati zimenezo

  • @MelissaMondey
    @MelissaMondey 4 месяца назад +2

    It's bad!!!😢😢😢 plz amalawi munthu ameneyo amangidwe

  • @user-lf6qf2tw5o
    @user-lf6qf2tw5o 4 месяца назад +3

    Km guys kwathu komwe tizilandila nkhanza zoterez amalawi ena kumavomeleza km mmm 😢

  • @IsaacMwale-hu9kg
    @IsaacMwale-hu9kg 4 месяца назад +1

    God have mercy on us

  • @mercynamangale98
    @mercynamangale98 3 месяца назад +1

    Aaaaaa zauchitsiru basi,amangidwe ameneyo basi

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj 4 месяца назад +5

    Umphawiwo wakula bwanji mpaka kuvomeleza zimenezo bwanji osawulura kapena kusiyana ntchitoyo kuyamba zochita zina

  • @giftblack7690
    @giftblack7690 4 месяца назад +2

    Hahahaha ine olo zitavuta maka sindingapange zauve ngati zimenezo

  • @AndyGama-m3u
    @AndyGama-m3u 3 месяца назад

    Ayi wachitola chikwama
    Nanga ma million onsewo pajatu ndalama zilimunyasi

  • @mercybwanali-qe3dv
    @mercybwanali-qe3dv 4 месяца назад

    Nseu wamangochi wu zikukhala bwanji?

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire 3 месяца назад

    ,,,😂😂mzimaiyo akunama amafunanso nae amagwilidzana naeso akufuna chipepetso eti 😂😂😂😂🤸🤸🤸🤸🤸

  • @e.r.mchanel1460
    @e.r.mchanel1460 4 месяца назад +2

    Eishhhhhh zosayenda bwanji

  • @IdiWilliam-uo8tw
    @IdiWilliam-uo8tw 4 месяца назад +4

    Koma ndikhani iyiyi boma lamalawi limayenera kumuitanitsa mwenye ameneyu kuonetsa kukwiya nazo

    • @RiteRoderick
      @RiteRoderick 4 месяца назад

      Boma lake litiro brother???😂😂😂😂😂

  • @HellenGondwe-d1g
    @HellenGondwe-d1g 3 месяца назад +1

    Mpaka Chaka kumalorera zimenezo mavuto ake amtundu wanji

  • @AlfredNazombe-me2ly
    @AlfredNazombe-me2ly 4 месяца назад +1

    Osamuluma nchilawakewo bwanji kkkkk ndikuluma maphwala akewo bs yesyes kkkk

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 4 месяца назад

    Mmmmmm koma abale zina ukambva yohhh kukhwima kapena?

  • @UmariBakari
    @UmariBakari 4 месяца назад

    Channel ichi ndichonama

  • @ElediaChingoma
    @ElediaChingoma 4 месяца назад +1

    Eshiiii

  • @CollinSepamatla-xk2lw
    @CollinSepamatla-xk2lw 4 месяца назад +1

    Mchitsilunso bwanji ameneyo

  • @bdbigdream9015
    @bdbigdream9015 3 месяца назад

    Amalawi akaona nkhungu lofiira eish

  • @DumisaniMhango-e4i
    @DumisaniMhango-e4i 4 месяца назад

    Amangidwe mwenyeyu

  • @EmmanuelMoyo-hy5ni
    @EmmanuelMoyo-hy5ni 4 месяца назад +3

    Umphawi ndi mavuto

  • @twavysibale4751
    @twavysibale4751 4 месяца назад

    We shouldn't Allow this in Malawi, that's not acceptable here,..

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick 4 месяца назад

    Osaiwala kuti Chakwera ndi chilima nawonso ndiodanatu ndi chilungamo ndie izi zangoyenera kumachitika basi

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick 4 месяца назад

    Boma la Tonse Alliance ndilodana ndi chilungamo nalo ndie atha kukamumanganso bambo olakwilidwayi poti

  • @RobertKwazizira
    @RobertKwazizira 4 месяца назад

    Umfiti amabungwe loweleranipo chilungamo chichidwe basi

  • @StellahChikupira
    @StellahChikupira 3 месяца назад

    Kulakwa 😢

  • @lonnythom
    @lonnythom 4 месяца назад

    Koma amwenye sazatheka 😢

  • @juniortsegula3847
    @juniortsegula3847 4 месяца назад

    Asaaaa 😂😂

  • @GidionJonas-sr4zr
    @GidionJonas-sr4zr 4 месяца назад

    Iiiiii shaaaaa!!!

  • @JosephNgona-f9v
    @JosephNgona-f9v 4 месяца назад

    Munthu ukuvutika kut ukufuna ntchito umapanga chitheka so I don't blame him ndipo iyeyo amkafuna kusamala ntchito komanso amkakukumbikila mavuto akwao koma munthuyi adangokhala oipa basi

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon 3 месяца назад

    Kupusa bwanji samakadandaula ku ma bungwe ndi opepera

  • @MilacleSankhani
    @MilacleSankhani 4 месяца назад

    Km ndye bola andicose ntcito

  • @FloridaOssy19
    @FloridaOssy19 4 месяца назад

    Mmmmmm 😢😢😢😢

  • @PetroJack
    @PetroJack 4 месяца назад

    Sad

  • @mercybwanali-qe3dv
    @mercybwanali-qe3dv 4 месяца назад

    Chanma lindimo umo😂

  • @FrankMkwala
    @FrankMkwala 4 месяца назад

    Why Malawian we allow such pple

  • @ErnestAllex
    @ErnestAllex 4 месяца назад

    Chitsiru ndiiyeyo vuto longochoka koweta ng'ombe 😒😒

  • @NgomaRaheem
    @NgomaRaheem 4 месяца назад

    Umphawi szinthu

  • @charityamos2183
    @charityamos2183 4 месяца назад

    Uchisiru bas

  • @alickkachepa3801
    @alickkachepa3801 4 месяца назад

    Mmmmmmm zotsayenda

  • @WillmotChiuimia-vr6ou
    @WillmotChiuimia-vr6ou 2 месяца назад

    Zopusa

  • @janemsiska3345
    @janemsiska3345 4 месяца назад

    Zovuta aaa

  • @clementMuyafula
    @clementMuyafula 4 месяца назад

    Amabungwe kuno changu

  • @FatimaRehemah-gi4mp
    @FatimaRehemah-gi4mp 3 месяца назад

    ma gay achimwenye🤨🤨🤨