Olakwa ndine pogula data yanga chabwino😢 SKC may your saul rest in peace, ine Manganya andichimwisa uyu, tazingopangani zokupha anthuzo ku mcp kwanuko, dzina la Chakwera lakolo ife usanatiuze
Bwana Usi when did u know kuti Malawians tikuvutika? You have been in Govt for 4 years tsono za NEEF mukutithira nalo bodza Lero ? Please note that it's not you who grants the loans . Pali bungwe lake so don't politisice this . By the way ,are you UTm or odya zake alibe mlandu please leave the UTM alone musamaichule coz Ife eni ake a UTm tinadziwa mbali yanu three years ago
Nsonkhano wa UTM azikakharira kukamba za Chakwera nde zichani zimenezo uyu asatipusitse ife a UTM apite ku MCP kwakeko Sitikufuna tizimva dzina la Chakwera ku nsonkhano wa UTM
Stupid politics in Malawi, this is time utm yatha ..ngati you think that you are the owner of utm ... Give everyone freedom to participate into party without fear or jealous.. some members of utm big problem you have is about greedy you think you best than anyone.. believe me utm gonna end like UDF believe me
Olakwa ndine pogula data yanga chabwino😢 SKC may your saul rest in peace, ine Manganya andichimwisa uyu, tazingopangani zokupha anthuzo ku mcp kwanuko, dzina la Chakwera lakolo ife usanatiuze
Mbewa zikatha anona ndi aswiswiri ndithu tigulitsapo malawiyu basi tigawane ma share aliyense awone kulowera
Olakwa ndiwe pegula data kkkkk
Sindinamve
@@user-oh9cp6zw9r ndithu olakwa ndine 😓
Usi uchisilu
Ukakamila za chakwera u vp'wo untha chaka chamawa
Zabodza zimenezo chakwera akuwina
@@user-bd5kw8oq1r😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@@user-bd5kw8oq1rchakwera sangawine pamtumbo pako iwe galu fiti munapha chilima inu
Amene wamva andiuze,, ineyo palibe chomwe ndkumvapo
Alibe mfundo awa koma tikufelanji
Ndipo zazii zenizeni
Kkkkk km
Mbuzi ya munthu
I still can't believe why this guy was chosen 😠 to be a VP. he has nothing to offer to my poor country Malawi. Even fundo zake doesn't make sense.
Wamisala iwe! bwanji sadatipatse chilima alipo?unkadikira uphe chilima kaye?usatichimwitse.
Zinayamba liti zimenezo za ngongolezo,mwaona lero kuti anthu kafuna chimanga mulungu akuona
Fundoless Mr vp
Comedy iyi ndiye ilibwino mugulisatu tikudikira ma asikono atiyakhure I like vc comedy
Anthu omvetsa chisoni kuwombera m'manja chidude cha mcp ngati chimenecho
Asowa kolowera asowa chochita uyu
Uyu nde phala
Thank you Mr usi , keep it up
Chilichonse “achakwera andituma”? Are you serious? 😭💔
What's wrong with that? He is vice president of Malawi second to the president. Amatumidwa kumene. Muzisiyanisa ndale ndi ntchito.
Uyu ndiye mfundo alibe ngati ambuyake achakwera aaa
Or chilima analibe mfundo koma kunama basi
Uyu wayankhulazo parbe chomwe ndatolapo ai.
@@Y0hanelLyson ndani usi
Zoti ndi wa UTM uyu ndakayika iiiiii .
Mbwelera zenizeni... udasi scaliot anamize anthuwo
Brilliant our vp
Powerful speech from the. Vice president, opeka nkhani zamabodza ndiye alipodi koma manyazi awagwira
Four years diwn the line adzikamba za NEEF lero?
Where was that money past years
Anthu amasiyana zochita leave him atha kupanga iyeyo mogwilizana ndi udindo wake
Zako izooo,, Tiye ku Convention
Za kumachende manganya za ziii Mr Chikangawa Party
Yelekeza kubwera kuno ku Mangochi,uza pita kwanu machende Ali mmanja kuno ku Mangochi sitigawatu masweet paja ngati izii ,
Manganya akufuna kusokoneza utm
Osokoneza simukuona kuti ndi apatricia Kaliati
Ife tinamutuluka Manganya wa Chikangawa part, UTM next year tipanga zathu
Unamutuluka wekha uziti ineyo ndinamutuluka😅😅😅
Wow! So powerful! Odumpha mumpoto dumphani iye athyakula nsima mpaka anthu adye cheteeee!
Most welcome Mr usi
Malawi anatilozayo iye ndi mtundu wakwao sadzapedza mtendere 😢😢
Aaah uyu akapitilize masewelo ake aja azidya ma like a bho koma izizi nde ayi osamkhulupililai chisilu cha munthu
Mawu abwino ndipo achilimbikitso Dr Usi
Langidzo langa ku UTM please remove usi from UTM party serious mulowetsa mphepo yachabe ndipo kwake mkusokoneza
Aaahhh khani singongole ayi km zithu zisike asusen achakwela khanza kwa amphawi nchenga laisesi mpaka katundu kudula misonkho mwaonjeza thawi yonseyi mukambe lero za ngongole cz chisankho chawandika no
Aaaaaa uyuyu sadzabwereranso ku utm
Mr Yes bwana awa ....angoti Chakwera this Chakwera that
Ofuna kulumphayo alumphe 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Umakwana Usi
Thank you
Keep it up mr Usi , salute
Ine ndekha ndakana zokuthandiza kudabwazo wava Manganya
Rest in peace SCK 😭😭😭😭😭
Manganya osatinyasepo apa wava 😊
AMALAWI ndife anthu wochitisa manyazi..
Ndipo simasewera😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
Vuto si Michael kma vuto ndi a Usi
Division of utm ,down fall of utm
very powerful
Za ziii
Wa ziiii ndiwe opanda mchere
Zithileni sugar dad zikome
Kungoyakhula ..change cant come within days
Kkkkk takuvani, osafuna UTM atuluke koma inu ndi mutueti!😂
😂😂😂lero zimenezo??? Ai zikomo, zioneka zokha chaka cha mawa atsogoleri
Manganya ndi wa MCP kuchuka kale
2025 my vote for chakwera, kut buuuuuuuu!!!!!!!!
Akunama uyu ndi mwana akuti cholinga mumusapote😢
🔥 fire fire uli bho😅
😂😂😂 Bwererani ku tikuferanji.
Ur Agud team ndi winiko the DC
Rally and voting for you is two different things
Wabalalika
Bwana Usi when did u know kuti Malawians tikuvutika? You have been in Govt for 4 years tsono za NEEF mukutithira nalo bodza Lero ? Please note that it's not you who grants the loans . Pali bungwe lake so don't politisice this . By the way ,are you UTm or odya zake alibe mlandu please leave the UTM alone musamaichule coz Ife eni ake a UTm tinadziwa mbali yanu three years ago
Why is he not in UTM colors. Anyway, rest in peace my president SKC
Thimitse data Yanga ndigone
Akuti chani inu aws 😂😂😂 aaaaa alibe mfumdo
Wa Mcp uyu galu
Miyambi two much manganya😊😊
Ife a UTM tikudikira convention
Aka akatafuna posachedwapa 😢ngat chilima aliku Manda aka nkandani umhuuuu
,
😂😂😂😂😂😂😂😂eeee ndaseka
Bwana,anthu akufuna National ID panopa osati neef,neef angaladile ñdi ochepa,koma ID ikufunika kwambiri kuti munthu akavote.
Uyu ndee zeriooo
Uyu andichimwisa aaaaaah ! Inetu ndiopemphera
RIP SKC
Nsonkhano wa UTM azikakharira kukamba za Chakwera nde zichani zimenezo
uyu asatipusitse ife a UTM apite ku MCP kwakeko
Sitikufuna tizimva dzina la Chakwera ku nsonkhano wa UTM
Zimunapha nzakho matchende akho iwe
Pathako pinuuu , na panyinamweeee shupitiiii
Zausiiru mukukanika kukwanilisa zanu zija nde mukufuna kukwanilisa zawina ywe
Koma uyu ayi zikomo 🙌💔
Nice vs p
Usamutukwae mudu wanena yeka timudikirire kkkkk
Rest in Peace Impi Bhiyeni
Kodi lero mwapha Chilima nde muzipanga msokhano Manganya simumapezeka pa msokhano uliose wa UTM lero takhalaso bwanji?
You😢😢😢😢😢🏹🏹🏹
Ineyo ndimadabwa kuti anthu aku UTM samaona okha kuti Michael Usi ndiwa MCP?
Uku nde kuyankhula kwabwanjinso zongokwiitsa palibe cha nzeru chikuyankhulidwapo apa
Manganta Sickomede mwasunta
Manganya ndamene anapha chilima anakonza chiwembu ndi iyeyo amawugula wu vis president
Usationongere chipani ,, moyoooo ine where are you SVK
Uyu ndiye ali ndi mfundo ngati chilima. RIP SKC😭
Osapeleka zaulele bwanji ngongole ya Chani ndalamazanuzo ife ayi timasaka tokha
Ndiwe wa MCP kuyambila kale asakudziwa ndani Yudasi iwe
Zochimwitsana izi😭😭😭
Stupid politics in Malawi, this is time utm yatha ..ngati you think that you are the owner of utm ... Give everyone freedom to participate into party without fear or jealous.. some members of utm big problem you have is about greedy you think you best than anyone.. believe me utm gonna end like UDF believe me
Matongo akenso ameneyu😢
❤❤❤
Undilankhulitsa udyo iwe wanva 😊
Speach ya akulu awa mmmmm sindimaivesesa😂😂vice wa dziko
Mulungu wake utiyo galiwe iyaa
Hahahahahaha mwana wa anthu osauka ake atiiiii?
Akufuna kusokoneza UTM
Iwe Manganya ukamatchula dzina la Chakwera wakoyo likumandichititsa nselu
Second devil 😈😈
Kulankhula kwa munthu wankulu komanso kwanzeru komanso kowona tsogolo.
Zaziii kulibe sapoti wa utm apo atenga ma tishert ndikupatsa anthu a, mcp zau galu basi ,,,mgwilizano unatha ndani anga vale makaka amenewo zamanyazi
Banzi ilimkamwa akulephera kulankhula chenicheni, akanangonena zot ndalowa mcp
Ngati walephera phulezdent ndiwe ndani
Uyuuu ndi galu kwabasi akutiza za ngongole after 4 years titanamizidwa zaziiii zenizeni shatapu