Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
Up coming president of Malawi you are welcome Mr President love you from Zambia ❤❤we voted for you
You are smart and the Best. Wishing you All the Best Dr Kabambe the UTM President 🎉❤
Thank you very much
@@Malawitoday265Always.. Mumatha inuyo.. keep the fire burning 🔥 🔥
Congratulations to Dr kabambe economic
Uyu ndi Muthu wankulu basi but asawayiwale akaliati
Maso patsogolo lets support him moro kuti buui
Kunena zoona panopa munthu yemwe akufuna usogoleli wa malawi azikhala wa zeru woziwa mavuto amalawi komaso kuyendesa chuma zoti ndinali mubusa zatha
Nkhani ndiyakuti tikufuna munthu yemwe angatengele Malawi patsogolo, osati kungokhala mtsogoleri chabe ayi
Coming President 2025
Usi agwe nayo anaikisana muziwauza amutumnuka ndi akaliyat
Kugula ma delegates🎉
Kumavetsetsa atsogo uyu ndi Chunga not Wonder😂
Hahaha thanks for correcting us
I love Fredo
Kodi Nankhumwa alipo? Koma ndale kkkkkkk
Tidziwenso zomwe zalepheretsa ena
Kaliat matama basi
Koma nkulu uyu
😂wabwera mwachabetu
Usi musamukhuze nenani za kaliyati kkkkkk
Usi wagwa nayo kkkkkk
ndiwe wabodza kwambiri
Usi akumva bwanji kumeneko amawona ndiyekha
Usi wayenera kukondwa chifukwa ankhala kale amene amazimva kuti ndi eni chipani amene amadana naye ndiomwe alephera 😅
Bola asapitise chipani ku Dpp monga mene anthu akuganizira
Ndikomwe UTM idachokeratu paja
Don't kuyankhula za usi , musiyeni munthu wasogolo labwino, mbuzi ndi njawala kaliati kambala agulitsa chipani. This is stupid of utm sogolo
Hehe yudas ngati uja abwino wake uli Pati ana anjoka inu kagwere ndi yudas wakoyo