Kunte inu mukulimba ndi iwe iwe wie akubawo adikire zimenezo 😅😅😅😅😅😅 ulemu wanu..... Boss yooo next azakhare serious coz he cud be furious when he saw zithu zabedwa nde akusekasooo Koma zimayamba 1212 next time i hope he gonna show us good things Thanks guys
Commedy sili mwala kweni kweni, content sikusangalatsa, kunte wapeza ntchito yaulonda after orientation akuba abwera amumenya aba katundu, abwana amupeza kunte atakomoka. Not that good as we expected
Iyi nde mwapala, muzi actor adha omwe aja
Mesa umadelera thana nawo amenewo😂😂😂😂osamayesa zida kunteeee😂😂😂
Abwana akewo eish Sali serious 😂😂km kunte NDI dolo atakhalamo yekha😂😅
The boss would have done much better than this. Otherwise kunte ndiwe dolo kwambiri 😂😂😂
Koma kunte asiye agogo anga a Queen Elizabeth 👸 ✨️ ♥️
The voice recording was much perfect for me I love it💯🤣🤣🤣🤣 I like you ase acting yabwino kwmabiri only the boss sanali serious
Big man simumatichitisa manyazi😂😂😂
Kunte inu mukulimba ndi iwe iwe wie akubawo adikire zimenezo 😅😅😅😅😅😅 ulemu wanu.....
Boss yooo next azakhare serious coz he cud be furious when he saw zithu zabedwa nde akusekasooo
Koma zimayamba 1212 next time i hope he gonna show us good things
Thanks guys
Koma ndaseka😂😂😂😂
Kunte iwe ndi one aise😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
nice acting from the boss, its natural
Kkkkkkkkk bro mkufuna touch
Umatimvesa kukoma kunteeeee
Kodi leader of gang ndiwe et? 😆😆😆
Kunte sazatheka kma uyuyu nd dolo...
Brazi yaine
Koma gunte ❤❤❤❤❤
😂😂😂😂 km inu Akatundu kd ulipobe ndimaganiza kut munadziya
😂😂😂😂😂😂😂😂
Nice
The boss is not serious
Mwala
Kunte wapeza ntchito after freddy
😢
😂😂😂
Nkute kkkkkkkkk
The boss acting simbali yake try achina molegeni yomwe aja amatha
🤣🤣🤣
Next time never work with these guys the boss and gang members there not serious in terms of acting
Kunte ulemu wako
Kkkkkkkk
fire kunte
master kunte
kkkkk
Kunte Band
Commedy sili mwala kweni kweni, content sikusangalatsa, kunte wapeza ntchito yaulonda after orientation akuba abwera amumenya aba katundu, abwana amupeza kunte atakomoka. Not that good as we expected
Please do better next tim
Worst comedy from Kunte,,iyi mwanyika Man
Ongolerani pamene pakufunika kut apange improve ,,, don't discourage lunso
😂😂😂