ZOMWE ZACHITIKA KUMENE A MICHAEL USI AYANKHULANSO29 July 2024

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 18 окт 2024

Комментарии • 246

  • @Prianka567
    @Prianka567 2 месяца назад +8

    May God give you more wisdom Manganya our Vice president, Dont be shaken lots of people are pharisees

  • @GoodsonSame
    @GoodsonSame 2 месяца назад +11

    Iyi inali apayi ndi Group la odyazake alibe mulandu,,palibe wa utm apa.

  • @SolokingChimzy-yt7dj
    @SolokingChimzy-yt7dj 2 месяца назад +14

    Ndichifukwa chake Yesu Khristu atabwela sanalimbane ndi ufumu wa Dziko la pansi iye anangobwela kuzapulumutsa chotaikacho bas...He k ew kut ufumu wa Dziko la pansi ngwa oipayo

  • @InnocentMtafya
    @InnocentMtafya 2 месяца назад

    Utsogoleri wabwino ulimo umu ,, bwana VP, you got it✊✊✊✊✊✌️✌️✌️✌️

  • @KondananiNjakwa
    @KondananiNjakwa 2 месяца назад

    The guy is so wise. Now I know why even President Chakwera did not hesitate appointing him

  • @smallAsima
    @smallAsima 2 месяца назад +3

    Muzithako kupanga zanu komaso kuvomeleza zinthu zikachitika aliyese azamwalila nde musapake ena imfa ya munthu azamwalila nthawi inakwana bas iyi ndinthawi ya Usi mufune musafune

  • @Nya-Jeka
    @Nya-Jeka 2 месяца назад +3

    Osadabwa kuti all this time he never wore UTM uniform….. all of a sudden wakayipeza. Shupiti zako Manganya

  • @JosiahKachali
    @JosiahKachali 2 месяца назад

    Manganya the best man. Keep the vibe

  • @MarvinChilombo.flourish
    @MarvinChilombo.flourish 2 месяца назад +1

    1.kusayankha ma diss it's fearing kut abwera ambiri
    2. Ati nthawi yoyankha alibe koma aziganiza ngongole, kodi akuona ngati wafikapo eti. Apanga mpaka liti?
    5. Lero ndie anaganiza zovala party cloth? Ndie wu betrayer umenewo

  • @CharityMhone-uk9ym
    @CharityMhone-uk9ym 2 месяца назад +5

    Suka kamunthu kakupha aka...kamwana ka chikangawa aka😮😮

  • @MemoryMbepula
    @MemoryMbepula 2 месяца назад

    Don't let enermy scatter us. Viva UTM

  • @GraceZumazuma
    @GraceZumazuma 2 месяца назад +3

    Wagwa nayo Usi dziko lakutulukira kale kuti ndiwe wa mcp osokoneza iwe ukuganiza ukawina ku convention

  • @StarchJonas
    @StarchJonas 2 месяца назад

    Tikuferanji at the best level, za drama zenizeni, nanunso oyimba ng'oma kumavina apa mumavinirapo zichani?

  • @PreviousStanley
    @PreviousStanley 2 месяца назад +7

    Chifukwa chani chirima anamunkhulupirila manganya nanga ndichifukwa chani manganya sanachosedwe unduna maulendo onse omwe ankhala akusintha maunduna manganya hi was a trusted person to chirima

  • @BrightZionga
    @BrightZionga 2 месяца назад +1

    Kodi mukamati chakwera akumakukumbutsa kuti chilima ankati tipangechani kkkkkk seriously manganya bwanji sankamugwilitsa ntchito ngati mmene akupangila iwemo 😢😢😢😢 manganya sudachenjele bwino

    • @lacksonsiyadi943
      @lacksonsiyadi943 2 месяца назад

      Eti eti chilima amangonyozedwa lero zatani manganya bzy bzy chonch chadza ndiyani

  • @MarvellousTech-kz6no
    @MarvellousTech-kz6no 2 месяца назад

    Thank you Mr vice

  • @tblon7441
    @tblon7441 2 месяца назад +3

    VP ndi more fireeee
    Image moto Boma ilo

  • @IshumaerWazakile-u5d
    @IshumaerWazakile-u5d 2 месяца назад

    ndikufuna chisot ndi maglass ndipitilize kupanga masewelo ndi nyimbo ya winiko umandisewelesa

  • @kingsleymsampha2260
    @kingsleymsampha2260 2 месяца назад +1

    Dr. Chilima had no intentions to quit the alliance? Chilima spent more time in courts with powerless position.... Malawians, learn to use your heads properly in reaction to everything which enters into your heads. God shouldn't be mentioned everywhere brethren because a day is coming. Stay blessed.

  • @JemesMalawa
    @JemesMalawa 2 месяца назад +1

    Palibeso zoti tingakambilane nanu athu okupha inu ngati mukulephela kupeleka ma information yangozi ndiye mukuganiza kuti tingakusekeleleni afiti osekelela 😢😢😢😢😢😢

  • @ayaanchaudhry9370
    @ayaanchaudhry9370 2 месяца назад

    More fire mr vp l love u more , hel

  • @cassimyusuf6683
    @cassimyusuf6683 2 месяца назад +6

    Zopanda nzeru zomwe akulankhula awa, ngongole kodi aliyese angalandile ? Azimayi mumangoziwa kuyimbira zilizonse ndizopusa zomwe.

    • @ThomasShuga
      @ThomasShuga 2 месяца назад

      Kupusa amalawi eeeeesh 😢😢😢

  • @GladysBanda-h2w
    @GladysBanda-h2w 2 месяца назад

    akutukanani eya mwaonjeza inu aaaaa

  • @DanielPhiri-u5x
    @DanielPhiri-u5x 2 месяца назад

    Yaaaaa coma vice president uyuuu anakonzaa zowonaa

  • @PrinceKachimanga
    @PrinceKachimanga 2 месяца назад +1

    michael USI ALIBE MFUNDO...NDIPO NDIMA DRAMA ENIENI...PALIBE UTSOGOLERI APA

  • @MzadziWanga
    @MzadziWanga 2 месяца назад +9

    Utm pitani ku conversion zosezo zitha 😢

  • @ChanceGondwe
    @ChanceGondwe 2 месяца назад +1

    Manganya ndi khuluku. Posachedwapa mulungu si James. Zomwe Iye amafuna zachitika. Betrayer

    • @GiftKumbweza
      @GiftKumbweza 2 месяца назад

      Anthu ongoyankhula zopanda umboni.Personal opinion kumaipanga present ngati fact

  • @StevenGJohn
    @StevenGJohn 2 месяца назад +1

    Chisiru ichi chopanda mfundo akukakamira ku MCP coz Cha u vice president ukuonangati a MCP akukuonera kukondwa?

    • @GiftKumbweza
      @GiftKumbweza 2 месяца назад

      Malemu Chilima anatuluka mu Alliance asanamwalire paja?

  • @francistonysanena5349
    @francistonysanena5349 2 месяца назад

    Ku off camera anagawa ma bwa?😅

  • @LACKSONJULIUS
    @LACKSONJULIUS 2 месяца назад +1

    Mukhale pa nthuzi mulandire kanganyanse

  • @MPHATSOKALUWA-lm2uy
    @MPHATSOKALUWA-lm2uy 2 месяца назад

    Only azimayiii km abale tiziona

  • @RaphaelKweve-u5s
    @RaphaelKweve-u5s 2 месяца назад

    Bwana Vp chimwalireni Sck munakumanapo ndi Nec yanu ya Utm ngati mtsogoleri,,,muyenda bwanji ndi alliance kutengera kuti amene anasaina wamwalira?

  • @SabitSamohgruva
    @SabitSamohgruva 2 месяца назад

    Mutifusileko kut Kodi iwowo ngt mtsogoleli wa UTM anayitanitsa ana awo ngt akambilane nawo? Zakutulukako nanga ndizoti UTM ndiyomwe idzakhale patsogolo mu 2025 ngt mwagwilizano wawo?

  • @MikeKanyaza-bm5tp
    @MikeKanyaza-bm5tp 2 месяца назад +2

    Tinalodzedwa ndithu,VP kukhala manganya ,munthu waku Zimbabwe😮😮😮😮😮

  • @PachaloInvestment
    @PachaloInvestment 2 месяца назад

    Come to mcp my friend

  • @francistonysanena5349
    @francistonysanena5349 2 месяца назад +1

    Lero nde mwavala za SKC?😅

  • @Geraldmkwewu
    @Geraldmkwewu 2 месяца назад +1

    Nose muli kumeneko ndi bambo asikono Mr yudasi tiye uko osakamba za madam mery akulira mwamuna wawo fisi lwe ndi chikangawa anthu okupha analakwachani skc 😢😢😢 manganya lweyo

    • @mwaleronald8325
      @mwaleronald8325 2 месяца назад

      Komatu

    • @SigereAckren
      @SigereAckren 2 месяца назад

      Chikuwalimbikitsa nchiyani kulimbana ndi ngongole mmalo mongogawa ndalamazo akufuna kuwabelanso amphawi

  • @DixonChimanya
    @DixonChimanya 2 месяца назад +2

    Bwanji zomwe ukupanga Bwanji sakamulora chilima kumatero ndi chifukwa utm yeniyeni ukukwiya nawe

  • @YOMALO.
    @YOMALO. 2 месяца назад

    The VP is wise 🎉

  • @Masina515
    @Masina515 2 месяца назад +1

    Awaaa koma? Azimai kutengeka😮

  • @ChrisjuZiyaya
    @ChrisjuZiyaya 2 месяца назад +1

    Ngati alidi mtsogoleri wa utm bwanji sakupanga push za report ya ngozi ya ndege kuchikangawa kuja ???????????

  • @AboudujanahMawulidi
    @AboudujanahMawulidi 2 месяца назад

    Mzimayi ndiwoyimitsa mutu kwabasi amangoyimbila m'manja zilizotse

  • @edsonphangula5817
    @edsonphangula5817 2 месяца назад +1

    Good speach ndale Zapa internet no good zipani Zina kulemba anthu Kuti aziwapatsa malipilo nchito yake kutukwana mulunga sangakuwiniseni muluzaso

  • @kondwanivyalema9449
    @kondwanivyalema9449 2 месяца назад

    Kamthila kuwiri aka kamunthu kowumila aka kayambise Chipani chake kazafa ngati galu aka

  • @TecksonKaima-dr6er
    @TecksonKaima-dr6er 2 месяца назад

    Wamfupiyu mzeru alibe uyu ndiye bambo asikono galu kumtumbo kwako

  • @doublekaizale7903
    @doublekaizale7903 2 месяца назад +1

    Only fools can trust this short man
    Kambelembele uyu

  • @KondwaniMunthali-vf1ws
    @KondwaniMunthali-vf1ws 2 месяца назад +1

    Mwasoketsa kit ya UTM,,,, KKKKKKK,,, HEEEEDEEEEEE😂😂,,, OCTOBER IS NEAR,,,

  • @swintonchirwa1897
    @swintonchirwa1897 2 месяца назад

    Akufuse ngati ndani? Just wait for convention

  • @NEBERTMVULA
    @NEBERTMVULA 2 месяца назад

    think carefully about this I dont think Saulosi would still be in MCP by this day today

  • @GiftCharlesMuhapala
    @GiftCharlesMuhapala 2 месяца назад +4

    Dr Manga palibe cha nzeru mukunena apa

  • @sandersonmayuni7557
    @sandersonmayuni7557 2 месяца назад +2

    Micheal Usi is a unifying leader regardless of political divide.

  • @JohnFrank-cg1yh
    @JohnFrank-cg1yh 2 месяца назад

    Kodi Dr manganya Inu ngat msogoleri wachipani Cha Utm mwachitapo Chani kut athu azigwirizana kuchipani Chanu, chifukwa zikuoneka kut mukuyenda nokhatu kuchipaniko akuluakulu onse akukukayikilani mutani,kut athu ayanjane komanso chipani Cha Utm chikhale chaphavu

  • @mkhokholasamuzonda5094
    @mkhokholasamuzonda5094 2 месяца назад

    UYUTU MBOLIYA MAKE AKUPUSITSAI GALU YU

  • @TrustMangando
    @TrustMangando 2 месяца назад

    Aaaaaaaa....iwe sungatputsitse ase......apa pokha wanama bacccccc....Awa wangoveka za UTM...aaaaaaaa ahaaaa!!!!

  • @IshumaerWazakile-u5d
    @IshumaerWazakile-u5d 2 месяца назад

    thiko wa mapoto awir utm and MCP unapha chilima nthiko

  • @AllanChikoti
    @AllanChikoti 2 месяца назад +2

    Kkkkkkkk
    Ndikamamvera awa ndumasowa chonena zumangondiseketsa

  • @GoodsonSame
    @GoodsonSame 2 месяца назад +1

    Awa si a utm,awa ndi a group yake ijayi amati odyazake alimbe milandu lija 😅

  • @RuthBinali-b8c
    @RuthBinali-b8c 2 месяца назад

    Za dyera basi olo inu mukuyankha pasi pasi muganiza ngati gwilizano amauthesa mwini wake malemu koma a malawi muzachangamuka liti ndindale akufuna kukakamila gwilizano cholinga simukudziwa shame

  • @ChrissySalimu
    @ChrissySalimu 2 месяца назад +3

    Choka okupha munamupha Zanu kut mutenge mpando wake Ausi Muli ndimulandu ndimulungu sure

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg 2 месяца назад +1

    Mukuyankhula zonsezo chifukwa inuyo zanu zikuyenda, mukuwauza anthu kut tonse ndi amodzi. Funso ngat tili amodzi ndichifukwa chiyani a President akungolemba ntchito abale awo komanso azinzawo??? Kodi umenewo ndi umodzi? Bwanji simudzuzula kusankhana kumeneko.

  • @BertharrySecurity
    @BertharrySecurity 2 месяца назад

    Akulu awa akufuna agulise chipani cha UTM.chakwela msamale nayo.or iweyo usi usamale akutafuna

  • @giftnyirongo-ey3qy
    @giftnyirongo-ey3qy 2 месяца назад

    Why today?

  • @victorauwana7258
    @victorauwana7258 2 месяца назад +3

    Mayi Chilima,,,, tiziwapemphelela chifukwa munawaphela amunao

    • @wisdom20mkango49
      @wisdom20mkango49 2 месяца назад +1

      So many plane crushes in the world achimwene sizinayambe kumalawi

  • @LawrenceBelson
    @LawrenceBelson 2 месяца назад +1

    Oro utani naweso uzafa waphesa chilima iwe mwachidule ndiwe yudasi iskariot ndipo pa exclusive unanena kut umapita kwa achakwera komaso kwa chilima zomwe zikuonesa kuti ndiwe waphesa chilima

  • @stalickkafera3454
    @stalickkafera3454 2 месяца назад +4

    Wa chisokoneza chipani cha UTM

  • @Mtalimanja1
    @Mtalimanja1 2 месяца назад

    Uyu ali ndi fundo zogwira mtima

  • @chippakaribafox2865
    @chippakaribafox2865 2 месяца назад +12

    This shortman cant be trusted....

  • @StevenMsanyama
    @StevenMsanyama 2 месяца назад

    Wisdom defeats knowledge

  • @Emmamalunga-fj4ey
    @Emmamalunga-fj4ey 2 месяца назад

    Thawi yonseyi bwanji simunkavala uniform ya utm even mwini wakeyo Ali moyo aaahhh we can't trust you bwanj wakakamila ku mcp relo mwayamba kuvala uniform ya utm chifukwa mu kuziwa kuti joka akufelani alimanja aahhh

  • @PaulvinMhango
    @PaulvinMhango 2 месяца назад

    Wayaluka pano angobwebweta

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 2 месяца назад

    Manganya akufuna kuononga chipani cha utm. Anthu amene alipo si a utm wose koma ena ndima khwangwala. Manganya ndi sweet talk. Ndichifukwa chani manganya akukakamira ku mcp pamene chilima anafa ifa yovesa chisoni. Manganya aononga utm ngati pamene nankhumwa anaonongera dpp. Manganya amalawi asakupusiseni akukuyikani mukamwa mwamukango.Akufunako chani ku mcp? Mcp yo ndiyimene yinachedwesa kufufuza ifa ya chilima. Mtsogoleri basi palipose ngongole ngongole pamene pali bungwe limene likuyendesa zangongole koma pule ndi vp busy kuyakhula ngongole munthu opusa zeru ndi amene akusangala ndingongole koma wazeru amazisakira yekha chuma ndipo akachipeza chimakhala changeiro pamaso a Mulungu.Manganya ngati ukufuna khala ku mcp ko ndi ufulu wako koma asiyire azako apange za utm

  • @TisopeMkozo
    @TisopeMkozo 2 месяца назад +2

    Anthu ali apawa palibe wa utm angovala ngati a utm

  • @GilbatChimwaza
    @GilbatChimwaza 2 месяца назад

    Manganya amatha

  • @abdu-razaqxhatiyah
    @abdu-razaqxhatiyah 2 месяца назад

    I like manganya but I smell something fishy in him

  • @MorganMwikhala
    @MorganMwikhala 2 месяца назад +2

    Azimayi muzatiphetsa

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 2 месяца назад

    Mesa umati suyankha nde ya nthikoyo ukuikambiranji aaaaaa iwe galu wakumpha

  • @ernestphiri2934
    @ernestphiri2934 2 месяца назад

    Panga chako chipani , achilima anachoka pa vice president ku dpp alimboma ndikupanga Chao chipani

  • @frankpreciousmulwa7006
    @frankpreciousmulwa7006 2 месяца назад

    I can't trust this guy now

  • @ClydeNyasulu-tk6fj
    @ClydeNyasulu-tk6fj 2 месяца назад

    Aaaa kamthira kuwiri ako shupit kopereka nzake

  • @PrinceKachimanga
    @PrinceKachimanga 2 месяца назад

    usi akuti chani kodi???UTM kufika chaka chamawa yikhala ma katani okhaokha😂😂😂😂😂

  • @MustaphaCassim
    @MustaphaCassim 2 месяца назад

    Iwe manganya usagawinitse anthu autm koma ndalama ndi satana udamupha chilima

  • @mkhulukinyata5198
    @mkhulukinyata5198 2 месяца назад

    Michael Usi usaganidze kuti an'thu ife ndiwopusa ayi , We know the all strategy that you are Playing .. Iweyo muntima mo ukudziwa kuti UTM Unatuluka chilima ali moyo , Makaka a UTM Wayamba kuvala pomwe CHILIMA wamwalirapa , Iweyo olo utapanga timapulani takoto " Koma a Malawi tikudziwa kuti Imfa yachilima iweyo unatenga nawo gawo ,Even Chilima atati Mulungu amudzutse lerolini " , Iweyo ndimunthu woyamba yemwe ungakhale m'dani wa CHILIMA . Anthu womwe alipamenepowo " We know very well kuti ndi anthu a chipani chako cha MCP , Koma apa wangowaveka makaka a UTM kuti anthufe tidziti" Ukutsatilidwa ndi anthu a UTM , Iweyo palibepo chomwe ungamatiwuze a Malawi ife ' Then nkuyiwala zachipongwe chomwe munamuchita CHILIMA ku chikangawa kuja , Chilima munamupha imfa yowawa kwambiri . Ndipo iweyo siwukuyeneranso kumakamba chilichonse chokhudza CHILIMA , MUNTHU WOYIPA , WOPANDA CHISONI , WOPANDA MANYAZI

  • @AnoldKonde-pd4qt
    @AnoldKonde-pd4qt 2 месяца назад

    Ngat alliance ilipo a pule abwere poyera kut ati akaime pa ballot paper nd ndan ulendo uno?

  • @RaphaelSiyeni
    @RaphaelSiyeni 2 месяца назад

    Ng'oma sound yake ndi mcp

  • @frankpreciousmulwa7006
    @frankpreciousmulwa7006 2 месяца назад

    Palibe chanzeru apa

  • @FrancisSteven-we1dj
    @FrancisSteven-we1dj 2 месяца назад

    Zikuwoneka kuti mungakhale tsogolo umu

  • @DONNEXKhama-bk1gy
    @DONNEXKhama-bk1gy 2 месяца назад +1

    Uyu ndie satana bas

  • @EthelKubalasa
    @EthelKubalasa 2 месяца назад

    kkkkk lero tavala makaka achipani koma zilko, drama sizithu. tisapusepo apa ndi ngongole, tiyeni tilembetseni zimenezo ndi ndalama zathu.

  • @MariamJohn-dg4em
    @MariamJohn-dg4em 2 месяца назад

    Rip SKC only God knows😢😢😢😢😢

  • @TorresBandala
    @TorresBandala 2 месяца назад

    Watenga a mcp okha okha apa manganya

  • @BryanJSimeon
    @BryanJSimeon 2 месяца назад

    Politics. Its something one will never understand. 😂

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 2 месяца назад

    Usi sakuwelenga bible. Munthu wazeru satumikira mabwana awiri nthawi yimozi. Ngati utm ukuyifuna tuluka ku mcp ngati sikuifuna utm khala ku mcp ko ukuganiza kuti marry chilima akusangalala nazo chimene ukuchita. Ifa ya chilima ikutipweteka amalawi munthu inde amakhala ndizifika koma kufa kwa chilima ndi azake cabinet yose yinapanga rigsin ndi president yomwe koma potimanyazi mulibe and amalawi tikuseketera zithu zoduka mutu.

  • @MPHATSOKALUWA-lm2uy
    @MPHATSOKALUWA-lm2uy 2 месяца назад

    Lero wati avaleko makaka a UTM

  • @ShearstonNyirenda
    @ShearstonNyirenda 2 месяца назад

    Otukwanawa ndi adpp

  • @GladysBanda-h2w
    @GladysBanda-h2w 2 месяца назад

    lero bola mwavalako makaka a UTM

  • @TisopeMkozo
    @TisopeMkozo 2 месяца назад +1

    Lero mpaka kuvala za utm mmm koma dzikoli

  • @Joejere-x3k
    @Joejere-x3k 2 месяца назад +2

    Utm sichipan inu ,,vote Dad

    • @AngelinaMzowa
      @AngelinaMzowa 2 месяца назад

      Kwanu konko

    • @Joejere-x3k
      @Joejere-x3k 2 месяца назад +1

      @@AngelinaMzowa napangani zoti Lero mudye bwwnj

  • @JohnConar-kq4hi
    @JohnConar-kq4hi 2 месяца назад

    Yudasi anapheleka chilima 🤔🤔

  • @ChifundoChiwanda-ru3pg
    @ChifundoChiwanda-ru3pg 2 месяца назад +1

    Mwayamba liti kumvala za UTM a manganya

  • @EmmanuelMoyo-hy5ni
    @EmmanuelMoyo-hy5ni 2 месяца назад +11

    Mwana wa Chikangawa