TIMVETSE | 7 JANUARY 2025

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 22 янв 2025

Комментарии • 107

  • @JoelKacheche-x6i
    @JoelKacheche-x6i 15 дней назад +6

    Ine choyambilira ndiyamikire MBC Chifukwa choyambisa program yapamwambayi ya TIMVESE.No wonder you are the mother of all Channels in malawi.Zikomo Amalawi ambiri taseguka kumaso pankhani zambiri zamaboza zomwe zipani zosusa zakhala zikulegeza pa social media kunyozesa boma lilipoli kuti silikuyendesa bwino chikhalireni opposition ndiyomwe yiliyosokoneza chuma cha ziko lathu la malawi.Akulu akulu a program ya Timvese ulemu wanu Mr Kasakula,Mr mvula, Mr mpikasambo,Blessings kanache.Pitilizani ntchito yabwino mukugwirayi.Mulungu wakuyikani pamenepo ndi cholinga,keep the fire burning guys, there will always be a great price from God to those who sacrifice their lives for justice and truth on behalf of the voiceless Malawians.Honestry God is pleased with you guys❤❤❤❤.We Malawians we cannot vote for dpp or any other opposition party back in government.Our votes are given to president Dr Lazarus maccarthy chakwera and Malawi congress party ❤❤❤❤❤❤❤

    • @WarriorKB-l3i
      @WarriorKB-l3i 15 дней назад

      Masiku ano si malawi broadcasting corparation ai, koma manyaka broadcasting coparation. Mawu ambiri ndilibe ndngoti nonse a mbc kuphatikizapo cikangawa panyoo panu nonse muwuzane💙💙💙💙💙💙💙💙💙 caka cino boma

    • @JoelKacheche-x6i
      @JoelKacheche-x6i 15 дней назад +1

      Munthu mumalo moyankhula mfundo zomveka kungokhalira kutukwana basi.Sitikudabwa kwenikweni munayamwira kwa gogo wanu uja mthalika,ulendo uno ndiye akunama gogo wanu kutalitali sanga wine chisankho chikubwerachi,chakwera akuwinanso chisankho mwankokomo.

  • @Enock-gu5ff
    @Enock-gu5ff 15 дней назад +3

    Amene angakunveseni inu ndani anthu onvesa cisoni ngati inu

  • @JamesMatupi
    @JamesMatupi 15 дней назад

    I like these gentlemen

  • @RakulMtambalika
    @RakulMtambalika 11 дней назад

    mwadya ma banz ochulukatu

  • @MaryMlongoti
    @MaryMlongoti 15 дней назад +2

    M c p my vote

    • @WarriorKB-l3i
      @WarriorKB-l3i 15 дней назад

      Panyoo pako ndi mcp yako yomweyo mukumanga oposition pamene mwaona kuti tayandikila kudzisankho muwuzane imenei sigwiila mufune,musafune caka cino iwe ndi mbc kuphatikizapo chikangawa wanuyo wakukasiya 💙💙💙💙💙💙💙

  • @chighogha
    @chighogha 15 дней назад

    We need more Kossams in the country

  • @hermeschapola3583
    @hermeschapola3583 14 дней назад

    A Mvula ndi Kasakula ndi zitsilu ...

  • @Wangisa
    @Wangisa 15 дней назад +2

    Akasakula tikuwasowa ku times TV Hot Current . Amati mvesa kukoma.

  • @MzikaPhiri
    @MzikaPhiri 15 дней назад

    Anthu pa MBC mumaoneka momvesa chisoni why😊

  • @AgnesNjikho
    @AgnesNjikho 15 дней назад +2

    Dzikomo Avula tiuzeni tivesese ena basitu angosusa chilichose auzeni ndithu

  • @abangaabanga4677
    @abangaabanga4677 12 дней назад

    Komatu penampena though I am not affiliated to any political party, you gents are starting to make sense in my head, I see your case.......!

  • @GodwillTegha-n1u
    @GodwillTegha-n1u 15 дней назад +1

  • @AlicksonMakata
    @AlicksonMakata 15 дней назад +2

    Lamulo ligwire ntchito ndithu asatuluke ku ndendeko.

  • @MisheckAselo
    @MisheckAselo 15 дней назад +1

    Mmmm zakanika a chikangawa inu mubwabwasa basi 😂😂😂

  • @JacksonMwase-j1g
    @JacksonMwase-j1g 15 дней назад

    Kasakula anafika pamenepa

  • @jumawasi9038
    @jumawasi9038 15 дней назад

    DPP my vote

  • @RichardMpakani
    @RichardMpakani 15 дней назад +3

    Dpp mbuzi

  • @FrankAbraham-e9o
    @FrankAbraham-e9o 15 дней назад +1

    A DPP asadzabwereso ndi Anthu Ankhaza kwambiri.

  • @LindiweMoloi-wn5qo
    @LindiweMoloi-wn5qo 15 дней назад +1

    Anthu onama inu, okondela mbali imozi

  • @NikolasNanawe
    @NikolasNanawe 15 дней назад

    Amandana MBC ndifiti kwambir 😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @petertengani
    @petertengani 15 дней назад

    We mustn't cheat one another here, there's others who gonna always be above the law up until to the grave.
    Mamuluzana ojiya.
    😆😆🙏🏾❤️.

  • @YahyaUmari-t5t
    @YahyaUmari-t5t 14 дней назад

    Andale onse ngakuba akuluakula amvula anaba mopanda chisoni mpakana company ya Shire bus lines kutha anthu onsewa ndimbamva zopanda chisoni

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 15 дней назад

    Masiku ano si malawi broadcasting coparation ai koma manyaka broadcasting coparation.kasakula ndi mbc yako yonse panyoo panu kuphatikizapo chikangawayo bwanji mukungomanga oposition yokha! Mcp sikuba; sikupha inu zisilu kwambir💙💙💙💙💙💙💙 voti yathu nyau inu tatopa nanu.

  • @WonganiPhiri-j9j
    @WonganiPhiri-j9j 15 дней назад

    Anthu nde kumangadi Koma black box nde kusowa..😢ayi zikomo boma Ndi lomweli

  • @EdenBrigadia
    @EdenBrigadia 15 дней назад +3

    DDP ndi chipani cha Kuba amene amaganiza bwino sanga votere DDP aba ndalama zambiri

    • @FannyWadson-zg4oj
      @FannyWadson-zg4oj 13 дней назад

      Kkkkkkkk iwe mbole Yamato ndithu wanva chakwela wakoyonso pa nyapake

  • @ShakiraJackson-x8w
    @ShakiraJackson-x8w 15 дней назад +2

    Kasakula wakhala pheetu relo unamwali uja unamveka

  • @ziyamporoma377
    @ziyamporoma377 15 дней назад +3

    Zikomo kwambiri azibambo inu potibweletsera zenizeni kuti timvetse chifwa kunjaku kuli awash with fake news

  • @CharlesFeston-r1v
    @CharlesFeston-r1v 15 дней назад +1

    Ndiye dpp imagulisa chani kt ipeze forex

  • @MzikaPhiri
    @MzikaPhiri 15 дней назад

    Nanga fuel akusowayu akupita kuti makape inu

  • @BillyBentryMunthali
    @BillyBentryMunthali 15 дней назад

    Osawasiyira panjira amenewa

  • @saviacafe
    @saviacafe 15 дней назад

    Truth be told, politics aside but if 400 Billion was routed those people must surely be prosecuted. Full stop

  • @AlicksonMakata
    @AlicksonMakata 15 дней назад +1

    Ndipo nthawi yomwe mbuzi za dpp zinapita kupolisi unali mwai omva chilungamo choti agwidwa chifukwa cha kuba anaba sugar.

  • @mikenjunga4758
    @mikenjunga4758 15 дней назад

    Tivetsetse your nonses?

  • @AlicksonMakata
    @AlicksonMakata 15 дней назад +1

    Ndipo dpp ndiyokupha ambiri afa chifukwa kuba Ambuye asawalore kulowa m'boma.

  • @CharlesFeston-r1v
    @CharlesFeston-r1v 15 дней назад

    Fertilizer ndalama zili kt Cash gate ya sata ili kt nduna zalemela ndalama azitenga kt magesi mwakoza kt machende anu azibambo Inu mulibe umunthu osakamba mene zinthu zikuyendela panopamu coz inuyo mukudyerera

  • @khwimaBanda-s3u
    @khwimaBanda-s3u 15 дней назад +1

    ndidanena kut palibe boma libwino mwanzimva izz lelo ndiye ndalama zosezi kuononga pali ubwino apa

  • @lucianogeoffrey4275
    @lucianogeoffrey4275 14 дней назад

    Nyopanu nonse kumtundako mwavaa? Azibambo opusaaaa

  • @johnchikoti2552
    @johnchikoti2552 15 дней назад

    MBC imanditaitsa nthawi yanga

    • @WarriorKB-l3i
      @WarriorKB-l3i 15 дней назад

      Sinu nonkha ife a malawi okonda dziko lathu imangotitayitsa nthawi masiku ano tikumavela history is a best teacher mwayidziwa eti? Kkkk

  • @FloridaPhiri-rt6vx
    @FloridaPhiri-rt6vx 15 дней назад

    Boma likusintha ili chikangawa akupita sureman azakhala minister of police muzavutika

  • @MzikaPhiri
    @MzikaPhiri 15 дней назад

    Ndinu abodza ine salima sugar nayamba kumuona kalekale msatinamize

  • @YoungMwacho
    @YoungMwacho 15 дней назад

    Mvula ndi nzake Kasakula mbuzi ngati Chakwela

  • @JacksonMwase-j1g
    @JacksonMwase-j1g 14 дней назад

    Kusauka sizinthu kumapangitsa kuti chilungamo ucizembe

  • @Chifuniro-i8d
    @Chifuniro-i8d 15 дней назад +1

    Chilungamo kuwawa

  • @IBRAHIMCHIPASULA
    @IBRAHIMCHIPASULA 15 дней назад

    Anthu opusa inu. Mumangoononga misonkho ya a Malawi. Forsek

  • @GiftZuze-ge1ne
    @GiftZuze-ge1ne 15 дней назад

    Ntchungayo tawi imene ija timagura ndalama zingati inuyo zozezo ay inuyo chimene mukuyendasa bweno ndichn

  • @mabvutochimkondenji910
    @mabvutochimkondenji910 14 дней назад

    Boma lomweri basi

  • @NoelGondwe-x7r
    @NoelGondwe-x7r 15 дней назад

    Tizitsilu taanthu

  • @RodgersBanda-l6j
    @RodgersBanda-l6j 15 дней назад

    Anyapapi inu ntchito yanu ikutha mu September Muno, badyani chibanzi Cho

  • @NickMalika
    @NickMalika 15 дней назад

    Agalu mbuzi za anthu inu

  • @DysonMuwata
    @DysonMuwata 10 дней назад

    Zazii

  • @ShakiraJackson-x8w
    @ShakiraJackson-x8w 15 дней назад +1

    Amati kukula mutu si dzeru ndaonera wanthu yawa

  • @LameckChinomba
    @LameckChinomba 15 дней назад

    Inu munganene kuti chani, poti mukulipidwa ndi mitsonkho ya malawi

  • @EdgarBuleya
    @EdgarBuleya 15 дней назад

    Nothing can share us

  • @MaxwellMilanzi-w5k
    @MaxwellMilanzi-w5k 15 дней назад

    Hmmmmmm inu!

  • @DanielChinula
    @DanielChinula 15 дней назад

    Amangidwa bas amenewo

  • @AgnesNjikho
    @AgnesNjikho 15 дней назад

    Ngati lero mukutukwana Chochi nanga mukazaluza zizatha bwa poti simuvera fundu yikulankhulidwa nchito kutukwana polani moto amalawi osatukwana Chochi ndimene likhalila dziko mawa muzalamula ndinu muzava bwanji munthu azatukwane musogoleli wanu

  • @GiftZuze-ge1ne
    @GiftZuze-ge1ne 15 дней назад

    Chimwendo simuna mangetu bwanji

  • @khwimaBanda-s3u
    @khwimaBanda-s3u 15 дней назад

    indedi matractor adalowela ku sizavotelaso dpp nawoso adawonongaso kwambili nawoso ndiokupha kupha sikuposa pamenepa azanu amakuziwani kut ndinu okuba nanuso ndinu mbuz zimene akulankhula apa atimvese ndizoona

  • @johnmbira6422
    @johnmbira6422 15 дней назад

    Why is this issue being brought panopa, 4 years has passed without any arrest

    • @apatsaphanga9252
      @apatsaphanga9252 15 дней назад

      Kafukufuku wandalama over 4 billion simungapange chaka chimozi ndalamazo zimawabisa achina macholowe apite ameneo

  • @jumbradoone4164
    @jumbradoone4164 15 дней назад

    Mwangokuka Mitu eti? Anyapala achabechabe inu.

  • @talandilabenedicto
    @talandilabenedicto 15 дней назад

    Azibambo omvetsa chisoni mkaganizidwe

  • @patrickbacknet3127
    @patrickbacknet3127 15 дней назад

    MBC is always party radio any regime. It talks favour on government. Are you talking truth?

  • @khwimaBanda-s3u
    @khwimaBanda-s3u 15 дней назад

    and inu a dpp mumangosusa zilizose nanuso ndinu mbuz ngat m'mene mukuwanenela anthuwa ndimaona ngat inu mumakonda chilungamo koma nanuso mumadana ndi chilungamo

  • @StoneckJali-s3n
    @StoneckJali-s3n 14 дней назад

    Chonde abale osanyozana lankhulani fundo zomveka

  • @felixjoseph8161
    @felixjoseph8161 15 дней назад

    Kasakula kunyini Kwa Mai ake nkhope ngati kunyini Kwa Mai chakwera

    • @JackMvura
      @JackMvura 15 дней назад

      Akuyendeleni yesu mwapadera akulu ndiye zemenezo or mfiti imaopa inu mwaposa mfiti

    • @masianobrighton
      @masianobrighton 15 дней назад

      Anthu osakonda ziko lawo kwao kutukwana basi andale onse amaononga Malawi ndi kuba kopanda chisoni

  • @WedieKaseka
    @WedieKaseka 15 дней назад

    Mbuzi zokhazokha

  • @CharlesJames-f1w
    @CharlesJames-f1w 15 дней назад

    M.bc.ose.ndiagalu

  • @JohnSoweso
    @JohnSoweso 15 дней назад

    The useless heads of old guys
    Join active politics
    Why are you there?
    Mvula is sleeping, you can see even his eyes
    How much is he receiving?
    Is it a salary or allowance?
    What role kasakula is playing in modern politics?
    We all know,he is MCP guro
    MBC is partisan
    Conflict of national interest is the order of the day
    Chase these guys
    These are law brokers
    Eating taxpayers money for nothing

  • @henryhenry6632
    @henryhenry6632 15 дней назад

    Mbava za dpp zimangodwe, asatana

  • @IshmaelNesta-rb8dx
    @IshmaelNesta-rb8dx 15 дней назад

    Za ziiii🚮

  • @Jafari-s3c
    @Jafari-s3c 15 дней назад +1

    Mfiti zakumana so lero

    • @henryhenry6632
      @henryhenry6632 15 дней назад

      Iwe ndiwe opusa kwambiri pathako pamako, ana anjoka peter mathanyula mboli zanu

    • @Jafari-s3c
      @Jafari-s3c 15 дней назад

      @henryhenry6632 chikangawa anthu ake mumadziwika ndi ndikuwola mkamwa

    • @Jafari-s3c
      @Jafari-s3c 15 дней назад

      Ngati kuli aomwe amakuopa ndi omwewo ineyo ndiye sindimaopatu opsyezani opusa omwewo iweyo ndine titengetsanatu

    • @henryhenry6632
      @henryhenry6632 14 дней назад

      @ iwe panyelo pamako, mwana wa refugees

    • @henryhenry6632
      @henryhenry6632 14 дней назад

      @ chikangawa mkumato kwa mayi ako , dzitsilu anthu aku Mozambique

  • @ShakiraJackson-x8w
    @ShakiraJackson-x8w 15 дней назад

    Amalawi anavotela mcp for a change soo stop comparing that dpp an this mcp anthu akanakhala kuti samafuna kusintha dziko sakanavotela mcp

  • @MOSESCHAZEMBA
    @MOSESCHAZEMBA 14 дней назад

    Mmmmmm ndinu anthu oipitsitsa pa dziko lapasi chokani apa fiti anthu adyera ndi ndalama mwakulilamo aaaa shame on you 🫣

  • @innocentkapachika6591
    @innocentkapachika6591 15 дней назад

    Delete. Mbuzi za anthu inu..

  • @MaulidiAtibu
    @MaulidiAtibu 15 дней назад

    Achisakula tachulani black box mwasinga kuti?