KANGAUDE---29/10/2023...ku mulanje anthu okwiya aika mtembo pakhomo la munthu...on @mibawatv

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 2 окт 2024

Комментарии • 91

  • @AronLuka-ue5hl
    @AronLuka-ue5hl 11 месяцев назад +4

    Nkhani ndayimvesela bwino bwino apa olakwa ndi Group ndi TA anthu awo palibe chimene alakwa

  • @pioireneuvictorpio1391
    @pioireneuvictorpio1391 11 месяцев назад +3

    Akulu akuluwo ndiwolakwitsa chifukwa sanawauzei koti akayike maliro ndipo athuwo ndiwosalakwai pakutengera ndimene akufotokozeramo,

  • @PikeypapucildeRamilo
    @PikeypapucildeRamilo 11 месяцев назад +1

    Malawi on flre

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 11 месяцев назад +3

    😅😅😅😅😂😂koma anthu akuyenda okwiyatu

  • @JohnChibalo-wf8gr
    @JohnChibalo-wf8gr 11 месяцев назад +5

    Kuyambira aTA ndi mafumu enawo ndi achinyengo manda sazaza amadula minda yomwe yadzungulira mandawo pang'ono pang'ono ndiponso nkhati ndalama inasonkhedwa ndikukagula munda chirungamo chinachitika koma kwanako anakana mukukana kwawo amafuna chichitike chani ? Zomwe anakafuna ndizomwe zachitikadzo asamusepo nyumbayo akamange kumandako akunkha panyo mayiro ndiyosalakwa ndipo ndianthu abwino .😂😂😂😂😂😂

  • @MtenjeHassan
    @MtenjeHassan 11 месяцев назад +3

    Umwa chani Abel Zulanga ❤❤ iweyo ndi one asy

  • @EusencioBernardoAchione
    @EusencioBernardoAchione 11 месяцев назад +1

    Por favor boa noite meus caros irmãos do programa kangaude simplesmente eu respondo pelo nome de Eusencio sidadao mosambicano.venho por esta:agradecer a Deus nos vossos programas.por favor pesso o vosso contacto eu quero conversar convosco me ajudem

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 11 месяцев назад +2

    Eeeee amfumu a mayero ndi nkhani Zina ndi ufumu zosagwilizana eeeee phuma 2 much

  • @jacquelinewasili-eh3uv
    @jacquelinewasili-eh3uv 11 месяцев назад +2

    Mukuyesetsa Mibawa creativity that dazzles indeed.keep it up kutibweretsera nkhani zodabwitsazi.

  • @khadjahmustafa8273
    @khadjahmustafa8273 11 месяцев назад +1

    Nchifukwa chaketu ife tinaukana ufumuwo nkungoupatsa kea ena asaaaa kuphetsa izi. Nzachibwana aaaaaa

  • @HopePhiri-r7q
    @HopePhiri-r7q 11 месяцев назад +1

    Kumalawi adha

  • @AubreyRoxinal
    @AubreyRoxinal 11 месяцев назад +4

    Malaw ngti atafike December ndakaika

  • @NeneHassan-l3r
    @NeneHassan-l3r 11 месяцев назад +2

    Komat kufotokoza Kuli apa pa mfumu a mayelo eshi zovuta kunvesesat.

  • @blandinabonaventure
    @blandinabonaventure 11 месяцев назад +4

    Khani ya maliro ndiovuta llibe bwana kma mamfumu ndiolakwa apa utsogoleri wavuta apa

  • @marymuhahara791
    @marymuhahara791 11 месяцев назад

    Next interview kwa a group a Dzenje plz tiwaone

  • @lillahnmahuzahshabah5883
    @lillahnmahuzahshabah5883 11 месяцев назад +1

    Mafumu akumalawi kudyera 😂

  • @AlexKaunda-x3p
    @AlexKaunda-x3p 11 месяцев назад +1

    In Malawi know good leadership sense all of them theyre dogs😂😂

  • @gladyschisomo4324
    @gladyschisomo4324 10 месяцев назад

    Unakumanana nazotu Abel kugugudidwa pachifuwa anatsala pang'ono kukumenya 😂😂😂😂😂

  • @vatineseduwin
    @vatineseduwin 11 месяцев назад

    kulakwa anyamataw sanalakwe kanthu olakwa ndi mafum

  • @mustafahaji2599
    @mustafahaji2599 11 месяцев назад +2

    Amayero akuyakhura ndiphuma

  • @AlexKaunda-x3p
    @AlexKaunda-x3p 11 месяцев назад +1

    Tizingo otchana izo zimatha malo

  • @SamsonChitezi
    @SamsonChitezi 11 месяцев назад +1

    Paribe fundo achose mariro pakho mkutitukwanisa alomwefe

  • @Maria-x4x5l
    @Maria-x4x5l 11 месяцев назад

    Dyela rakulapo apa chinyengo amalawi nawoso police mulibe chilungamo bwanji kod?

  • @YoungMwacho
    @YoungMwacho 11 месяцев назад +2

    All this is because of poor leadership in Malawi starting from the President. This was a very simple problem.

    • @Clyne_Phiri_265
      @Clyne_Phiri_265 11 месяцев назад +1

      Would you make a connection between the two?

    • @victorbanda9039
      @victorbanda9039 11 месяцев назад +1

      Ndale mwafika nazo pauchitsiru zikugwirizana bwanji ndi poor leadership

    • @gesinasutherland9241
      @gesinasutherland9241 11 месяцев назад

      kufuna kuwoneka anzeru😂😂😂boma ndi Maliro zikufana chani?busy kunyoza boma pa ziiii...mburi za Ku Malawi..😂😂 penzani chonyezela boma...si za ndale iziii..more fire kangaude..

    • @YoungMwacho
      @YoungMwacho 11 месяцев назад

      @@victorbanda9039 you will understand when you go back to school.

  • @blandinabonaventure
    @blandinabonaventure 11 месяцев назад +2

    Amayiro samayenera kukhala mfumu nda mphuma

    • @miccah81
      @miccah81 11 месяцев назад

      Kwabasi, muli phuma la nyooooo

  • @khadjahmustafa8273
    @khadjahmustafa8273 11 месяцев назад +1

    Nchifukwa chaketu ife tinaukana ufumuwo nkungoupatsa kea ena asaaaa kuphetsa izi. Nzachibwana aaaaaa

  • @wallezysmooth4169
    @wallezysmooth4169 21 день назад

    Abel koma umazionera yhooo ai taaa keep it up good work

  • @khadjahmustafa8273
    @khadjahmustafa8273 11 месяцев назад +1

    Nchifukwa chaketu ife tinaukana ufumuwo nkungoupatsa kea ena asaaaa kuphetsa izi. Nzachibwana aaaaaa

  • @egreymkumba-tj5ji
    @egreymkumba-tj5ji 10 месяцев назад +1

    Amfumu a mayelo mutu wanu sumagwila

  • @miccah81
    @miccah81 11 месяцев назад +1

    Anthuwa ndiolusadi komaso phuma 🙌😅😂

  • @TriciaDeborah
    @TriciaDeborah 2 месяца назад

    Mwakumana nazotu bwino mungamenyedwe

  • @austinvincent1264
    @austinvincent1264 11 месяцев назад +1

    Mfumu mayero zikuoneka kut ali ndukali mpake kufotokoza

  • @mtisungegondwe2043
    @mtisungegondwe2043 5 месяцев назад

    Anthu si anthu😂😂😂

  • @AlexKaunda-x3p
    @AlexKaunda-x3p 11 месяцев назад +1

    Dyela amalawi kafuneni ntchito iya

  • @JuuuKomba
    @JuuuKomba 4 месяца назад

    Awaso ufumu wawo okanika za mowa bas

  • @Ruth-y5q9n
    @Ruth-y5q9n 11 месяцев назад +2

    Kkkkk mbado wachakwela tiona zovuta kwabasi ngati pulezidenti akupanga chinyengo ndiye bwanji mfumu

  • @semusiliva4106
    @semusiliva4106 11 месяцев назад +1

    Khaniyi njayikuludi .

  • @khadjahmustafa8273
    @khadjahmustafa8273 11 месяцев назад +1

    Kkkkkkkkk koma iwe wamibawq iweee adzakukanganirana ndithu kkkkkkkkk koma ndaseka mpaka ntola nkhani kusowa omumvera

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj 11 месяцев назад +1

    Alomwe ndi makape

  • @raytavares2256
    @raytavares2256 11 месяцев назад

    But in Ghana, Angola, South Africa and Botswana there are other cultures which bury their beloved ones within their yards some in Ghana bury a person in a house and the bedroom a person died from. The bedroom used which the corpse has passed that's where they dig a hole to bury the person including the children of the person if the bedroom has been big enough and every year they put wreath as well as marble stone where the grave is after a year, i think even some Nigerian cultures like the Philippines. Ghana they can keep the body of their beloved ones inparticular for more than two to three years depending on the agreement of the children of the dead person.

  • @mwanaishababes9630
    @mwanaishababes9630 11 месяцев назад

    Ku Malawi kupuma kulibe

  • @highcallingglobalministries
    @highcallingglobalministries 11 месяцев назад

    WACHIBWIBWI NAYESO KKKK

  • @mwanaishababes9630
    @mwanaishababes9630 11 месяцев назад

    Poti tamva mbali imodzi

  • @langsonmndalanga
    @langsonmndalanga 11 месяцев назад +1

    Amaudindo mmziwe mulungu 😢😢

  • @EmmanuelMassa-v7j
    @EmmanuelMassa-v7j 11 месяцев назад +2

    Malawi on fire 🔥🔥🔥🚒

  • @LizzieKazembe
    @LizzieKazembe 6 месяцев назад +1

    Abel my vote 😂

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 11 месяцев назад

    Malawi wa lero malodza eni eni aliyense akupanga zomwe akufuna🙌🙌🙌

  • @GiftChadika-he7nd
    @GiftChadika-he7nd 11 месяцев назад

    Inuyo ngati uli umphawi mmm nyamata iwe ndimaona ngat ulankhura zanzelu naweso ulibe nzeru ngat kuli kusauka yamban kugwira ntchito nanga milandu ya manda mmmmm

  • @anafiidie9058
    @anafiidie9058 11 месяцев назад

    Mafumu anji olephera kulongosola nkhani bwinobwino

  • @asiyatujuma5507
    @asiyatujuma5507 11 месяцев назад

    Kkkkkkkk

  • @MichaelKalua-mc8ty
    @MichaelKalua-mc8ty 10 месяцев назад

    Ukakhala ndi ndalama ndimavuto pa malawi ishiiiiiii

  • @josephkuseke4166
    @josephkuseke4166 11 месяцев назад

    Manda si a mmudzi manda ndi banja. Dzenje tinakupezani

  • @jamesngalande4345
    @jamesngalande4345 11 месяцев назад

    Vuto lakula apa ndi umphawi ndikusowa chochita

  • @AnnettieChimwala
    @AnnettieChimwala 6 месяцев назад

    😂😂😂😂 kumalawi nkokoma

  • @EthelNdalama-o3y
    @EthelNdalama-o3y 11 месяцев назад

    Big up abel💪

  • @austinvincent1264
    @austinvincent1264 11 месяцев назад

    Iyiy nkhani inali ya simple koma chinyengo dyela

  • @GladysChifundo
    @GladysChifundo 10 месяцев назад

    Malawi tikapuma kumwamba😂😂😂😂

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 11 месяцев назад

    Aaaaa kangaude uli bho

  • @khadibasilli4897
    @khadibasilli4897 11 месяцев назад

    Cecilia, m

  • @TraverMbewe-e6o
    @TraverMbewe-e6o 10 месяцев назад

    Akulu awa sakukwanitsa kufotokoza

  • @Mejanakwawa
    @Mejanakwawa 11 месяцев назад

    Kkkkk afumu ati ndizivomela ene kkk

  • @anniewhite3497
    @anniewhite3497 11 месяцев назад

    Gwirinzano unavuta apa😢

  • @TrizaGeorge-q8w
    @TrizaGeorge-q8w 11 месяцев назад

    Ambuye atithandize 😢😢

  • @RazzackGwape
    @RazzackGwape 11 месяцев назад

    A group zawavuta ndithu

  • @JaffaSaidi-db6ic
    @JaffaSaidi-db6ic 11 месяцев назад

    So bad

  • @aaronmakuta911
    @aaronmakuta911 11 месяцев назад +1

    Mwini nyumba akanangofukula ndiku yasa moto basi chichitike chichitike

    • @semusiliva4106
      @semusiliva4106 11 месяцев назад

      😂😂😂😂😂

    • @RazzackGwape
      @RazzackGwape 11 месяцев назад

      😂😂😂😂😂. Ineso ndikanatero

  • @VictoriaWilliam-ms2ft
    @VictoriaWilliam-ms2ft 11 месяцев назад

    A group ndi a TA onse ndi adyera

  • @PatrickMbewe-cz6tn
    @PatrickMbewe-cz6tn 6 месяцев назад

    🤝

  • @freedommuyaka8597
    @freedommuyaka8597 11 месяцев назад

    Zichitika mmasiku osiriza ndithu timva ndi kuona zinthu nthawi yakumapetoyi ndithu this is just a beginning

    • @JOHNSANGWALI-ox8mu
      @JOHNSANGWALI-ox8mu 11 месяцев назад

      Not masiku osiliza blo zikoli lilipo mpaka kalekale

  • @JimmDauda
    @JimmDauda 11 месяцев назад

    Mafumu dyera eishhh

  • @marykaunga-cm1dd
    @marykaunga-cm1dd 11 месяцев назад

    Kumalawi mkokoma😂😂

  • @alicehananiya
    @alicehananiya 11 месяцев назад

    Mfumu maelo ndi mbumba yanu mupeze Munda wanu ukhale Manda zooka malilo Minda ya anthu enazo ayi

  • @KeneMike
    @KeneMike 11 месяцев назад

    🎉😂

  • @charleskalajira380
    @charleskalajira380 11 месяцев назад +1

    Big up Abel

  • @MercyMulenga-pc3ow
    @MercyMulenga-pc3ow 4 месяца назад

    So bad

  • @ChikondiBanda-r4h
    @ChikondiBanda-r4h Месяц назад

    Banda samazaza