LIMPOPO FM WITH COMRADE NTANYIWA

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 29 сен 2024

Комментарии • 199

  • @LekkttarKhembo-or1tx
    @LekkttarKhembo-or1tx 3 месяца назад +4

    Mumakwana brother ntanyiwa mlomwe salora zithu zopusa zizichitika maso mwake

  • @AlinafeChimtengo
    @AlinafeChimtengo 3 месяца назад

    Zoonad

  • @originalblack100
    @originalblack100 3 месяца назад +2

    The best part of the show is the chant" Ndakuchokerani dziko lanu lopusalo" Ndakusiyirani dziko lanu lofoiralo, dziko la chamba, lokanika ku pusha, lopondereza osauka, kumangokangana zopusa". 🤣🤣🤣🤣. On a serious note Comrade, praying for your safety, ndi ana omwe, ndi onse omwe amathandiza kuti tidziwe zomwe zikuchitika. Show iyi ndi yofunika. It is everyone's fundamental God given right to speak their mind, even if we might not agree with the thoughts. Mulungu akudalitseni boss.

  • @collennyadile8179
    @collennyadile8179 3 месяца назад +3

    mcp ndi ankhanza ndikumbukila 1992 tili anyamata tikapita kuzochitika timalephela ndi kusokomora ngakhale kuyankhulana akuti mukufuna kuwukira boma sizinali zamasewela mcp yinali ndi achinyamata ake madela onse mu Malawi or ine wina akamati kwachaa! lero ndimangoti aaaaa ufiti anthu timayenda khumakhuma

  • @ellahmwams831
    @ellahmwams831 3 месяца назад +2

    Malo moti ndalamazo azigura mankhwara muzipatalamu koma dziko ili mulungu atichitile chifundo

  • @ruzuwanmoyenda23
    @ruzuwanmoyenda23 3 месяца назад +3

    First comment

  • @YasmeenYalabi-b2c
    @YasmeenYalabi-b2c 3 месяца назад +2

    ALimpopo FM ndi Comrade Ntanyiwa munabwera kudzakhala

  • @TressLuka
    @TressLuka 3 месяца назад +2

    King of the radio 😢😅

  • @JamesChiphwanya-m4v
    @JamesChiphwanya-m4v 3 месяца назад +2

    Ipondeni tanyuwa yomweyo galu iwe amene mukudana ndi tanyuwa muzamfa mukunyinyilika kkkkkk

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 3 месяца назад +2

    😢😢😢😢😢😢 chilima anafa ifa yowawa chakwera ndi gulu lako 😢😢😢panya pa agogo anu nyini za akazi anu😢😢😢😢😢😢😢😢

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 3 месяца назад +2

    Ntanyiwa ndinu one osaopa ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @AlexManuelMisomali-sv1vn
    @AlexManuelMisomali-sv1vn 3 месяца назад +2

    We support 10 July demonstrations in Malawi 💪💪

  • @ProspaMitumba
    @ProspaMitumba 3 месяца назад +2

    Ntanyiwa ndikatundu more fire limpopo ndi no: 1

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 3 месяца назад +1

    Ndiponso inu nsapato Trauser koma anthu Ali ndi nsambi mwamva Rip Achilima ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @Lazarus-qo1sl
    @Lazarus-qo1sl 3 месяца назад +2

    Salute Limpopo

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 3 месяца назад +1

    Palibe zomveranso zamisala zolamkhula zamisala za munlo, kachaso anamumaliza kale amene uja😂😂😂, akuti suit yake ndiyodula kuposa ya ng'ona chakwera 😂😂

  • @ChimwemweKondowe-nj4lx
    @ChimwemweKondowe-nj4lx 3 месяца назад +1

    Tet them try to kidnap your kids, they will see end of the their lives including their families.
    Tikawaotchera nyumba zawo eni wake Ali nkati

  • @HevenChiwaya
    @HevenChiwaya 3 месяца назад +1

    Akuona ngati akubanja ndi opusa sakuziwa kuti akuganiza mozama mwakuya wina azamva kuwawa

  • @AliKalima-p6d
    @AliKalima-p6d 3 месяца назад +1

    Antanyiwa ndinu original tea wamu honny!!!

  • @augustinechibbalazi8897
    @augustinechibbalazi8897 3 месяца назад +1

    All authorities are devoid of Christ love hence money minded...grossly cupidity oriented

  • @Sabina-hw4js
    @Sabina-hw4js 3 месяца назад +1

    When I saw the picture of the late I lfirst asked myself where are the clothes!!!!!!!!!!

  • @EsetaGerate
    @EsetaGerate 3 месяца назад +2

    Auze ntanyiwa agaru amenewo

  • @ShiraKasekaNyirenda
    @ShiraKasekaNyirenda 3 месяца назад +1

    Ndimadwala ngati tsindinamvele Limpopo

  • @JuuuKomba
    @JuuuKomba 3 месяца назад +1

    Kodi asilikali aku malawi kwathu kuno amqgwila tchito yanji ndiziwe nawo a police nde ndimaziwa amagwila opezeka ndi pagolini ,chamba atavala uniform yosuluka akuyenda pasi Mr ntanyiwa ndipelekeleni moni kwa amalawi ose

  • @LilianKachala-yz2xf
    @LilianKachala-yz2xf 3 месяца назад +1

    Amayenela kupepesedwa ndi Mai Chilima

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 3 месяца назад +1

    Benlongwe ufiti chani akazi onsewa,kapena anakutuma anzakowo okuphawo kuti ulemera 😅😅😅😅😂😂😂😂

  • @KunyengaMoyo
    @KunyengaMoyo 3 месяца назад +1

    Maka msilikari uja miyendo kukhapidwa chonchija idali ndege yomweyo???

  • @HowardTchauya
    @HowardTchauya 3 месяца назад +1

    Let's do it again

  • @FloridaMakwinja-eq2ek
    @FloridaMakwinja-eq2ek 3 месяца назад +1

    Kodi comrade Ntanyiwa
    Kuti tikutumizireni ma audio omwe anzanrhu a maiko ena akulankhura tongakutumizireni bwanji

  • @MeliaMichael
    @MeliaMichael 3 месяца назад +1

    I will join you on fasting

  • @Musa1828-l5d
    @Musa1828-l5d 3 месяца назад +1

    Boma la MCP ndidzitsiru dzose dzinapha Chilima

  • @MuhammadBAKILI-kl2mj
    @MuhammadBAKILI-kl2mj 3 месяца назад +1

    Limpopo fm best radio

  • @Yabwata
    @Yabwata 3 месяца назад

    Please avoid chi music ichoo chikutayisa thawi iyaaz chinyimbo gwaa why imwe yooyaninge waka while the background music is going on like muluzi tv not kuyooya nakulekaso kuzakhula kusiyaso aaa ulikasi malungo chani

  • @BlessingsChitekwe-k5z
    @BlessingsChitekwe-k5z 3 месяца назад +1

    Limpopo FM radio station 🚉⛽⛽ Massive heart ❤️❤️❤️❤️❤️

  • @cynthiakananji1608
    @cynthiakananji1608 3 месяца назад +1

    Anthanyiwa kholo ndi kholo, chilima tinamva kut makolo ake anamwalira kale kale, kholo silingalore ndalama kugulisa ndi moyo wamwana wake. Tiyen tivomereze chilima anali mwana amasiye, akanakhalapo Mai ake akanalankhula mau oti dziko likanagwedezeka chifukwa cha imfa yoopsa ija. And kholo silingalore ndalama. Koma mzimu wa achilima ukuwasowesa mtendere chakwera, that's why akungogawa ndalama kuyesa kut anthu aiwale imfa ya chilima. Koma ndakaika ngat anthu angaiwale. Ndalama azilandila koma anthu sadzaiwala.

    • @VeronicaChirwa-ct4os
      @VeronicaChirwa-ct4os 3 месяца назад +1

      Mwina ndi Abale a makolo awo ndi amene alipo. Ndi amene akutengedwa kuti ndi makolo awo

  • @HiltonMalambo-tm8sg
    @HiltonMalambo-tm8sg 3 месяца назад +1

    Limpopo fm massive go go go more fire

  • @chimwemwechilongozi9013
    @chimwemwechilongozi9013 3 месяца назад +1

    Comrade more fire.

  • @TriciaSeleman
    @TriciaSeleman 3 месяца назад +1

    Limpopo FM best radio ever...

  • @etomansailes4932
    @etomansailes4932 3 месяца назад +1

    Ben longwe alibe nzeru uja wangoyenera kungwiririra mwana😂😂

  • @AliAli.aliheassim
    @AliAli.aliheassim 3 месяца назад +1

    ❤❤❤ more fire Ntanyiwa

  • @StanleyDama
    @StanleyDama 3 месяца назад

    Zazi

  • @FloridaMakwinja-eq2ek
    @FloridaMakwinja-eq2ek 3 месяца назад

    Ndipo comrade akakutengera Ana ako dziko liwotchedwa

  • @MosesShaibu-ee8hn
    @MosesShaibu-ee8hn 3 месяца назад +1

    Nthawi yakwana chobisika chi woneke pa white page

  • @Sabina-hw4js
    @Sabina-hw4js 3 месяца назад +1

    Asoka chonena

  • @HevenChiwaya
    @HevenChiwaya 3 месяца назад

    Comrade Mtanyiwa ndi boma loima paloka osamalimbananaye kkkk

  • @AhronMchini
    @AhronMchini 3 месяца назад

    Kutenga Ana a Mr mtanyiwa ndiye aputa mabvu pachisa kusonyeza kulepherako kumeneko

  • @ZionekaMember
    @ZionekaMember 3 месяца назад +1

    Tili ndi Radio imoz yodalilika komanso TV imoz yodalilika
    Bakili Muluzi TV
    Lipompo FM
    Ma station okhao amene sanadye chibaz amene akutumikila a Malawi

    • @JoyceBanda-k8t
      @JoyceBanda-k8t 3 месяца назад +1

      Ndipo zoona

    • @ZionekaMember
      @ZionekaMember 3 месяца назад

      Ma station awa azayalusa wina nthawi ya zisankho

  • @StanleyDama
    @StanleyDama 3 месяца назад

    Zazi uli ndi nkazi?

  • @chesterkumwenda
    @chesterkumwenda 3 месяца назад +1

    No1limpopo fm

  • @AlinafeChimtengo
    @AlinafeChimtengo 3 месяца назад +1

    Zoona

  • @FrancnsWilliamdambe
    @FrancnsWilliamdambe 3 месяца назад

    Ine ndiwakumwanzako kom aaaaa mulo sangawiene

  • @Judah-zb6sl
    @Judah-zb6sl 2 месяца назад

    🎉🎉🎉🎉🎉🎉

  • @AndrewWilliammvula
    @AndrewWilliammvula 3 месяца назад +1

    Limpopo ndi one

  • @Sabina-hw4js
    @Sabina-hw4js 3 месяца назад

    Where does the president get money he's giving out to bishops and chiefs?Not his sweat of course.If he is a good president he would have considered the hungry people first in villages and townships!!!!!!!!!This is v evil and selfish

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm 3 месяца назад

    I support Limpopo FM with Comrade Mtanyiwa God bless you all the time.

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 3 месяца назад

    Palibe kupha longwee, alimchani kamfamsiyanji ngati amene uja, anagwilira mwana wake kuno 😂😂😂😂, apolisi aku South Africa akumufunanso amaba magalimoto poopseza ndimfuti 😂😂😂😂

  • @ClementMushele
    @ClementMushele 3 месяца назад

    Timamva nanu kukoma A tanyiwa

  • @AiameAdamo-su1nt
    @AiameAdamo-su1nt 3 месяца назад

    Limpopo fm Best Radio. Very clear and loud from Mozambique.

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 3 месяца назад

    Ovomeleza ndichitsiru Malata your days are numbered, fool doctors and idiots government wait your will see soon what happened in Kenya, boma lambuli mpaka ku admarc

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 3 месяца назад

    longweyo azikapanga supply mbeu kwa admarc for wat?, akagwililira mbewuzotu 😂😂😂😂

  • @chrisboyce2
    @chrisboyce2 3 месяца назад

    Ntanyiwa ndi akamuna zoonadi ndipo nthawi zonse amayima pachilungamo OSAOPA Comrade 💪

  • @cynthiataulo5211
    @cynthiataulo5211 3 месяца назад

    May God continue to protect you and your family from all harm Mr Limpopo

  • @chadreckchibwithala1493
    @chadreckchibwithala1493 3 месяца назад

    za report kafutseni abanja bcz ndiwo analemba Doctor ameneyo. nde osatsutsana ndi banja mkhale inu aaaa or ku school simunapite.

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 3 месяца назад

    Judas iscariot anampereka yesu chifukwa cha 3 tambala koma mapeto ake anakadzimangillira yekha chifukwa cha chikumbumtima. Wina adzimangiliradi Chaka chake ndi Chino chikumbu mtima chikuphani

  • @lyiemax
    @lyiemax 3 месяца назад

    Proud of you our trusted journalist, the real professional journalist 🔥🔥🔥🔥

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 3 месяца назад

    Ana alakwa chiyani mukufuna kukapanga kidnap?, usatana nde ndumenewo, tithana nanu one by one achina longwe, munro , chimwendo, kumkuyu, zikhale,yolamu, howa milk mkaka, etc

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 3 месяца назад

    Pa 10 pano agule nonse mukubwelera kumanda muzikazola matope mkumayenda maliseche 😂😂😂

  • @BMDMasulani
    @BMDMasulani 3 месяца назад

    Munlo ndichitsilu palibe chimene angapange olo kumwanza tilibenaye ntchito ndaphunzilanako kuthambani kachabechabe or kuyimila mp akaimila pati?

  • @OssmanAbubaker-st7pu
    @OssmanAbubaker-st7pu 3 месяца назад

    Ulemu wanu big ifeyotu mumatiimilira .panopaifeyotu kuno ku South Africa mumzinda wa Johannesburg tagula Kaletu mfuti ndipotikufuna Chakwerayo ndi Ndunazakezo antumize anthu kuno ndipo tikuwadikila tiwaphela komwekuno ndiposabwerela ndimoyo tatopa Ndi MCP

  • @Extratremendouszeus
    @Extratremendouszeus 3 месяца назад

    Chakwera wapepetulidwa ndipo azingopanga zobalalika mpaka,adzslowa mmanda.matembelero ali pa iye kuyambira tsiku lomwe adabadwa,tsiku lomwe adzalowe mmanda mpaka tsiku louka kwakufa...mbuzi yachabechabe

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 3 месяца назад

    Pa 10 pano agule nonse muzipita kwachamanu muzikakhala kumanda mulimbuu uku mukuyenda maliseche 😂😂😂😂

  • @dysonmasiye5736
    @dysonmasiye5736 3 месяца назад

    Ndiye mwatinso kunapita ampesa ku state house? Achina ndani amenewo? Ndiye mukuti nawonso alandirako chani? Koma nzoona izi? 🤔

  • @jamiajafali6619
    @jamiajafali6619 3 месяца назад

    Brother Ntanyiwa how are you feeling today?get well brother

  • @RachealHarawa-xc9gs
    @RachealHarawa-xc9gs 3 месяца назад

    Tsiku losala kudyalo tuzeni tisale nao chifukwa ena Mulungu amatiyankha pompompo mapemphero athu

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 3 месяца назад

    Osadandaula mtanyiwa, ana athu sangapangidwe kidnap, ingondipatsa maina aasatana omwe akukonza chiwembu chimenechi ndithana nawo

  • @Sabina-hw4js
    @Sabina-hw4js 3 месяца назад

    It's been prophecised all over about this death.Do not tell us lies

  • @priscillamangata4023
    @priscillamangata4023 3 месяца назад

    Sono chotengela Ana a comredy athu ndichani atenge azaone chomwe chinameta khanga mpala

  • @elizasingano
    @elizasingano 3 месяца назад

    Masamba aliwonse kuno aliko timadya chomwe tikuchifuna hahaha ......
    Ngat akulimbana nawe mulungu awakantha amenewo ..

  • @SydneyMwale-u9w
    @SydneyMwale-u9w 3 месяца назад

    Akufanadi anthu awa kulibe uchitira mwina.
    Koma mtanyiwa sadzatengako mbali biii.

  • @RodgersNtambalika
    @RodgersNtambalika 3 месяца назад

    Ntanyiwa ine agaru amenewa andidesa kukhosi oferedwa ndi akubanja la achilima ndi akazi awo si afitiwa ayi komanso azipembezo anthuwa ndi adyera

  • @HestingsZiba-d6k
    @HestingsZiba-d6k 3 месяца назад

    Ben longwe chisilu chamunthu chija kukulamutu basi ndani angavele Ben longwe chisilu

  • @liz9425
    @liz9425 3 месяца назад

    Mawa fasting guys ya 5 days let’s gooooooo

  • @pellinamphande3045
    @pellinamphande3045 3 месяца назад

    Limpopo fm, you are the best.more fire brother ntonyiwa

  • @ImraanSambani
    @ImraanSambani 3 месяца назад

    Kungoti chilungamo chimawawa mpake zikumakhala ngat zonena za Mr Ntanyiwa zimakhala zopeka.

  • @HestingsZiba-d6k
    @HestingsZiba-d6k 3 месяца назад

    Mafumu nawoso awa akumapita ku state House ngadyela, kwambili zisilu kwambili

  • @JafaliAkimu-ll1bf
    @JafaliAkimu-ll1bf 3 месяца назад

    inu boma ili alipo ali ndi nzeru zitsuru zokha zokha zigawenga mizimu ya anthu anaphedwa iwazunze asatana amenewa chakwera mapwala agigo ake ndithu

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 3 месяца назад

    Ndipo ena mwa anyamata mwatchulawa thupi lawo losamva mafuta ngati amakhalira kusamba mankhwala (mizu😂😂)

  • @RuthMoto
    @RuthMoto 3 месяца назад

    More fire mtanyiwa agaru amenewa atinva mmadzi pa 10 choyamba tiwaonesa kuti timatha

  • @chadreckchibwithala1493
    @chadreckchibwithala1493 3 месяца назад

    VUTO KULANKHULA DAIRY PA GROUND ZERO AA NTANYIWA NDIWE KAPE AAA .

  • @CiprianoBindissone
    @CiprianoBindissone 3 месяца назад

    Nafenso kumozambique timayikonda limpopo

  • @ChifundoJohn-w3t
    @ChifundoJohn-w3t 3 месяца назад

    Awuzeni chilungamo chiziwike chakwela ndi mfiti kwabasi

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 3 месяца назад

    Chakwera wayaluka galu mfiti okupha 😅😅😅😂😂😂😂😂😂yomweyo galu iwe

  • @HakikaWiskes-yb6zq
    @HakikaWiskes-yb6zq 3 месяца назад

    Apapo tafika poti tikayankhula azitisaka achepa kwambiri pano tili ndi ufulu oyankhula za kukhosi

  • @FloridaMakwinja-eq2ek
    @FloridaMakwinja-eq2ek 3 месяца назад

    Kodi MCP akuwatenga anthu aku Malawi ngati zitsiru

  • @TrizaGeorge-q8w
    @TrizaGeorge-q8w 3 месяца назад

    Komatu zafika povutatu m, pakana kupanga ana kidney up ndiye athu akamati ndinu athu akupha mudzikana mmmm

  • @GraceLimani-zw7dx
    @GraceLimani-zw7dx 3 месяца назад

    Ben longwe ndi reds on munlo tinataya azingopampetsa ku mcp

  • @AlexManuelMisomali-sv1vn
    @AlexManuelMisomali-sv1vn 3 месяца назад

    Anachita kukong'ontha anthu aja ankafuna Chilima koma anaphanso ena 8

  • @JafaliAkimu-ll1bf
    @JafaliAkimu-ll1bf 3 месяца назад

    chakwera wayalukatu ndiwuchgawenga okupha chilima

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp 3 месяца назад

    Chakwera wapa chilima palibeso kubisanaso apa

  • @YasinMmadi
    @YasinMmadi 3 месяца назад

    Comrade mtanyuwa keep it up osaopa osafooka diso pasogolo