Mukubwela boh gyz koma please tayesani kuwonjezela ena achilendo comedy imakoma mukachulukisa zochitika monga ngat awa akupanga zama hustle ena kumapanga zama bebi enaso akupanga zandewu ena so akupanga zinazo thawi iziwoneka ngati yochepano simumabweleza kwambili muthu modzi but anyway I love you gyz mumandinvesakukoma next year muwina award komaso ndikazitolela ndikupezeleni HD camera yaboh izishuta patali Sony or cannon
Lucy being a very beautiful lady she knows how to act mostly akakumana ndi boys Keep it up Lucy
😍😍😍😍😍😍😍😍😍
Rucy ndi pweteka . 😂😂😂😂 Kumakhal zinthu akakumana kikkkkkk
Mumàkwana😂😂😂😂
Happy new year ❤ from boksburg north SA 🇿🇦
Thank you
Prophet wafika pondikwana achina Tiger anaoneka lit its too mch guys zasiya kukoma
Pepani
Lucy ndi mpweteka eeeh 😂😂😂
More fayaaaaaaa maguyz
Zikomo
Ampweteka amathadi kufunsila koma kapena kuchemelera ndalama zawo
😂😂😂
Thanks guys chak chath bwin tikudikilil next year kt mwatikozel zotan
Osadandaula we coming with fire
Koma camera guys please muguleko ina coz imeneyo ikumatimana HD simukuoneka mowara please happy New year 🎉🎉🎉🎉 guys 🎉🎉
Zamveka
@ghettorhythmstvseries ok guys
My favorite ❤️ 🥰🥰😍😍😍
Thank you
Inuyo mutenga award next year coz iyiyi nd serie ya ghetto ngakhale thawi zina mumathawa channel ya ghetto
Osadanda tikomza
We watch u gyz from Australia 🔥🔥🔥 don't gv up guys
Thank you very much😂😂
Eh prophet umazungulilatu😂😂😂😂😂😅
Eeee kwabasi
Km prophet sazatheka
😂😂😂
Massive
Thank you
Mukubwela boh gyz koma please tayesani kuwonjezela ena achilendo comedy imakoma mukachulukisa zochitika monga ngat awa akupanga zama hustle ena kumapanga zama bebi enaso akupanga zandewu ena so akupanga zinazo thawi iziwoneka ngati yochepano simumabweleza kwambili muthu modzi but anyway I love you gyz mumandinvesakukoma next year muwina award komaso ndikazitolela ndikupezeleni HD camera yaboh izishuta patali Sony or cannon
Takumvani. Ndipo mutapanga choncho zikhoza kukhala bwino
More fire guys ,koma a prophet nthawi mkuwapasa yambiri we also like to watch like a china love D. Kukanganilana atsikana 😂
Osadandaula tikukonza muona kusintha
@ghettorhythmstvseries thx koma mkugwila ntchito yabwino mumatisangalatsa
Zikomo kwambili@@CollinsLingu
Mphweteka wamushatapula lucy 😂😂😂😂 chikuti chitha kumudyetsa 1 to 30 kaya masiku enawa azikadya kwani?😂😂😂
😂😂😂😂😂😂
Koma mpwereka eeee
Wabwera ndiyokwiya
Koma noxy ndi legend kkkkkk😂😂😂
@@chansleyissah 😂😂😂😂😂
Kkkk Koma munyeliwa
Wataninso😂😂
Koma akaka Ka movie aka kamandiwaza heavy. Koma kamtande akufunikira
Zikomo kwambiri..osadandaula kantande akubwera mwa nkokomo
Munthu modz mimodzi paliponse aaaaaah gyz
Pepani khululukani🙏
😂😂abusa kuyamikila😢😢😢
😅
New year 🎊🎉
Umangoziwilatu😂
Happy new year gyz❤❤❤
Happy new year
Avoid busao palipose kupezeka 30minis abusa okhaokha basi
Zamveka
Thawi ikutichepera
Iiii abale
Koma pano munayamba kuchebwesa kutulusa why
Tmaluzi bwana
Koma apulogeti 😂😂😂😂😂
😂😂😂😂mwati bwanji dzinalo
@ghettorhythmstvseries pulofeti
Ooo ok ok kumamutchula bwino munthu wa mulungu
Anko k plz add me to your comedy group
@@MosesDicostar osadanda. Mumakhala kuti
Ineso uncle K ine ndimakhala ku Ntcheu
Improve video guys tmakufillan 😂😂😂😅
Takumvani
Happy new year 🎉🎉
Happy😂😂😂😂
😂😂
𝐀𝐛𝐮𝐬𝐚😂😂😂𝐚𝐭𝐢 𝐧𝐝𝐢 𝐦𝐚𝐥𝐞 𝐤𝐚𝐩𝐞𝐧𝐚 𝐟𝐞𝐦𝐚𝐥𝐞 😂𝐦𝐮𝐭𝐮 𝐧𝐠𝐭 𝐧𝐣𝐞𝐫𝐰𝐚 𝐳𝐚𝐤𝐮 𝐦𝐳𝐮𝐳𝐮 😅𝐚𝐧𝐲 𝐰𝐚𝐲 𝐦𝐮𝐤𝐮𝐛𝐰𝐞𝐥𝐚 𝐛𝐡𝐨
😂😂😂😂😂😂 uthenga wafika
Kumangomva zama tayilosi waste of time
Abale khululukani
poor video guys
@@franklizi2912 ok ok tikonza
Prophet salora
Ndipo avuta