Ndipo panopa Ali busy kumaphunzisa ma part time. Kwa ana amene Ali osowa school Yao iri pa chiophyezo chifukwa mwana aliyense akumalipira 5thousand pa mwezi. Tithandizeni a Kalindo
Mwazindikira liti kuti development fund sikufunika koma alomwe mmadzitengera ngati ndinu madolo eti munaziyambitsa nokha tiyeni perekani ifeso timapereka
❤ kmad zoonad kumangoyend ndi apolice ambir kukaend bawo kukaphik.zipwete.akt avice kkkkkkkk zalowa makomedy
Go ahead DC God bless you chilungamu chokha chokha
iwe chakwela Ife alomwe watiyesa Ngati zisilu zimene kupanga tikuwona
Ndipo panopa Ali busy kumaphunzisa ma part time.
Kwa ana amene Ali osowa school Yao iri pa chiophyezo chifukwa mwana aliyense akumalipira 5thousand pa mwezi.
Tithandizeni a Kalindo
The whole vice President kumakagawa feteleza kumisika !! Paja ananena kuti iyeyo amadziwa kupempha nde akuwaphunzitsaso ena kuti akhale ndimoyo wodalira kumangolandira
Khan sialomwe Khan ndiot mcp yaipisa dziko
Anatinamiza za ma net, anatenga ma I'D anthu amenewa
eee izi ndi ma boma ambiri or kumpoto juli ma school ambiri monga awa,,kauwa,kaviwale ,lupaso,kazando,ndi ena ambiri
Ng'alula bon umakwana osaopa osafooka
Sindiwe ndi nzako ntambo sindinu munapangisa
Koma bwana Bon mumalimbana ndi Sausage 🤣🤣🤣
Abale tigaireni number ya Kalindo
Anayambadi kale kale zopusazi😮😮😮
Akalindo mukuziwa lelo ii zinayamba kale zaka zingapo pano ana athu anasiya kupita kusukulu ndalama tilibe ikazapezeka azapita kutsukulu
The DC ndimakunyadila
DC ndi katundu mcp ikufuna idzikolola ndalama paliponse ndi ma primary momwe alibe manyazi chakwera
zazii kukhara ngati mutu wazungurira manganya zimene akupanga koma marawi taziwona ndipo sazatheka ambuye tiyendereni tikuvutika ndinjara mayendedwe yooooo
Kuno ku msaka monkey bay pa siku machine awo akuzima katatu zimene zikupangitsa ulesi kulembetsa anthu ambiri
The DC
The DCCCCCCCC CCC CCC CCC booooooooooon kalindoooooooooooo mwana owopsyaaa kwambiri may God be with you always
Katundu wa boma uyu basi
Southern Africaaaaaaaa
Aboni kalindo ndi achisilu
Koma osaposa usiru wa iwe ndi president oduka mutu
Achisillu ndi inuyo kaa
Mwazindikira liti kuti development fund sikufunika koma alomwe mmadzitengera ngati ndinu madolo eti munaziyambitsa nokha tiyeni perekani ifeso timapereka
mwachenjera poti muri pamupando Koma mziwe Kuti murungu simunthu mziwe Kuti munthu arindi ufuru kusankha amene akumufuna ovoter ndi anthu
Kd iweyo ufuna uyankhul kuti chni zopereka sukul fund inayambra kale koma kale timapereka kamodzi osat kumangoitanisa nthawi iliyonse
Mulungu tipasen sogoleri oopa Mulungu atichosere satan devil jabulos Chakwera atipase sogoleri oopa Mulungu okonda anthu ake case closed