MDYANGU 27 DECEMBER 2024

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 3 янв 2025

Комментарии • 82

  • @BashilDaud
    @BashilDaud 7 дней назад +2

    Chuma watimalidzira bwino chakachi mu mdyangumu kkkkk taseka simasewera❤

  • @EsteryHassan
    @EsteryHassan 7 дней назад +2

    Kkkkkkk kma tifane uyamba zosakhala bwino sopano nvuto ndiloti ukakhala pabanja kumadalila azimbambo sibwino zimazachitika izi zamuchitikila tufane ndi ndazionazi tikakhala mmabanja tiziyesako kupanga tima Business kuchitila nyengo iyi ikatipedza tisavutike ndi ana taonai apa tifane akunvutika ndazionaso akunvutika mpaka akupepha ndalama kwa amuna ayiniwake sizabwino izi kumakhala ozidalila wekha osati mamuna nanga apa atamwalila azimunawa azimayiwa siakayamba kupita ku bara chonde amene timaonela masewelo awa sikuti tizingotha kuseka koma tiziphunzilamo zithu zina zake Ilove you guys ❤❤❤❤

  • @mussaganeti
    @mussaganeti 7 дней назад +2

    My favorite comedy

  • @MoffatBinali-pp8hi
    @MoffatBinali-pp8hi 6 дней назад +1

    Wakumanazo mercy tsopano akuti apeze Malo ndi nthawi achapanepo kkkk

  • @abdulsalammkwepu3321
    @abdulsalammkwepu3321 7 дней назад +4

    Chuma chibwibwi chimenechi mphamvu zoimbira ka muluzu ukuzitengaso kuti?😀😀😀

  • @bornfacewilliams
    @bornfacewilliams 7 дней назад +2

    Shock shock usamale akazako ayidziwa Kuti wapana ,,kk

  • @TendaiBamusi
    @TendaiBamusi 7 дней назад +1

    chuma waibebesa 😀😀😀😀😀 chibwibwi wachifasila

  • @lovemorenaluso8965
    @lovemorenaluso8965 7 дней назад +4

    Chuma how can you stammer even for singing apa nde wanamatu😂😂😂

  • @elizabethnyamathanga4906
    @elizabethnyamathanga4906 7 дней назад +1

    Queen ndi lucky woman😅😅😅

  • @HaarithMilesmandanda
    @HaarithMilesmandanda 6 дней назад +1

    😂😂😂Chuma ndi machine guys

  • @AchiwaShakira
    @AchiwaShakira 7 дней назад +2

    Big up 🥰🥰🥰

  • @sosureup5745
    @sosureup5745 7 дней назад +1

    Kugona sivuto 😂😂😂😂
    Keep fire 🔥 🔥🔥

  • @danieleneya808
    @danieleneya808 7 дней назад +2

    Yake ija mwadza 🎉

  • @PeterJay-cn9sf
    @PeterJay-cn9sf 7 дней назад +3

    Koma ine mkazi wa sasokayu amandiwaza ,,

  • @AchiwaShakira
    @AchiwaShakira 7 дней назад +1

    Big up 🥰🥰🥰🥰

  • @blessingsmimu5236
    @blessingsmimu5236 7 дней назад +1

    😂😂😂mercy wakomana nazo

  • @YohaneThomson
    @YohaneThomson 7 дней назад +1

    Nice movie guys❤❤❤❤

  • @TsuzenThomas
    @TsuzenThomas 7 дней назад +1

    Koma Chuma nd nkhan zina 😂😂😂😂

  • @abbasjutasi909
    @abbasjutasi909 7 дней назад +1

    😂😂😂😂😂😂😂😂😂 Koma Chuma waseka

  • @MarySoko-d5d
    @MarySoko-d5d 7 дней назад +1

    Nic movie guys❤

  • @JoiceIsmael
    @JoiceIsmael 6 дней назад +1

    Kkkkkkkk koma chuma ndiye kusekatu

  • @MercyMjima-tv5py
    @MercyMjima-tv5py 7 дней назад +1

    Koma chiphwanya ndi sasoka atuluseni ku ndendeko tawasowa

  • @IsaacChisambi
    @IsaacChisambi 6 дней назад +1

    ❤❤❤❤❤❤

  • @KELVINGezakanjan
    @KELVINGezakanjan 7 дней назад +1

    Ashokoshoko 😂😂😂 akwatilatu mkumbuyo komwe

  • @PenjanBwanaisa
    @PenjanBwanaisa 5 дней назад

    Chuma ndiwe katakwe 😂😂😂😂😂

  • @PeterBendeka
    @PeterBendeka 6 дней назад

    Mmakwana guys kkkkkk Mbabane pa nswanz pompa

  • @FladielMwase
    @FladielMwase 6 дней назад +1

    Umakwana chuma 😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @FraserNamaona
    @FraserNamaona 7 дней назад +2

    Poison sopano school mate pa Luchenza secondary xul

  • @hansyorknyundo2970
    @hansyorknyundo2970 7 дней назад +1

    Chuma adha😂😂😂

  • @RodwellKumwenda-l1i
    @RodwellKumwenda-l1i 7 дней назад +1

    😂😂😂😂 bg up

  • @MoffatBinali-pp8hi
    @MoffatBinali-pp8hi 6 дней назад +1

    Munyanyiwa amathanso

  • @DavidPhiri-o6w
    @DavidPhiri-o6w 6 дней назад +1

    Koma chokochoko wapeza bomba la mukazi ndiwokongola

  • @graceLufan
    @graceLufan 6 дней назад +1

    Tili pano chifukwa cha yonu azimayi nda zi bambo

  • @christinaibbu4339
    @christinaibbu4339 6 дней назад +1

    ❤❤❤🎉😂

  • @RhodaMwanza-o5b
    @RhodaMwanza-o5b 6 дней назад +1

    Sasoka ndi chiphwanya abwere

  • @MoffatBinali-pp8hi
    @MoffatBinali-pp8hi 6 дней назад +1

    Wabwera chuma basi kkkkkk

  • @ShalifuKachigwe
    @ShalifuKachigwe 6 дней назад +1

    Chama ndiwe dolo katatu

  • @GraceKhupala
    @GraceKhupala 6 дней назад +1

    Chuma😂

  • @EsnartMittochi
    @EsnartMittochi 3 дня назад

    ❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @felistarmgemezulu5823
    @felistarmgemezulu5823 7 дней назад +1

    A chuma wachibwibwi amayimba bwino bwino.not kuimba muchibwibwi😂😂😂

  • @HaniffMatola
    @HaniffMatola 6 дней назад +1

    Mumatha maguyz

  • @ElubeHenley
    @ElubeHenley 7 дней назад +1

    😂😂😂😂 koma

  • @NathanKamanga-w6i
    @NathanKamanga-w6i 6 дней назад

    😂 chuma adakonza 😅😂

  • @ChrissyScot
    @ChrissyScot 6 дней назад +1

    Kkkkkkkkkk Koma Chuma

  • @daviekamanga1417
    @daviekamanga1417 7 дней назад +1

    🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉

  • @MdalaTobiasi
    @MdalaTobiasi 7 дней назад +1

  • @JoannaNAMA
    @JoannaNAMA 6 дней назад

    Koma Mercy sazatheka 😂😂

  • @EliaMartin-w5c
    @EliaMartin-w5c 7 дней назад +1

    Koma achuma😂😂

  • @luciapita
    @luciapita 4 дня назад

    Koma team iyiyi imandivetsa kukoma😂

  • @victoriachilala9995
    @victoriachilala9995 7 дней назад +2

    Achuma Ayi zikomo😂😂😂😂😂,

  • @jeffmkhomo5690
    @jeffmkhomo5690 7 дней назад +1

    Mumatha gys

  • @PeterJay-cn9sf
    @PeterJay-cn9sf 7 дней назад +1

    Koma chuma asadazafe kkkkk

  • @EricCanada-ig9xe
    @EricCanada-ig9xe 6 дней назад +1

    Mbambande

  • @BobickVbobick
    @BobickVbobick 7 дней назад +1

    Tifani yambani geni basi

  • @DMCARTSTHEATRE
    @DMCARTSTHEATRE 7 дней назад +1

    Mwayamba kuchedwesa kupanga upload 😪😫😫

  • @MoffatBinali-pp8hi
    @MoffatBinali-pp8hi 6 дней назад +1

    Chuma mkatundu amandiwaza

  • @AlieSalimu-c4c
    @AlieSalimu-c4c 6 дней назад +1

    Chuma mukutitela time

    • @FloridaOssy19
      @FloridaOssy19 6 дней назад

      Eti inuyo aaaaa inetu Sakundisangalasa chuma yo lol 😂

  • @DjshukulanGift
    @DjshukulanGift 7 дней назад +1

    Chuma kuyakhula paka kuzikhesa magaz wekha? Kkk

  • @DaveiRichard-y4g
    @DaveiRichard-y4g 7 дней назад +1

    Sasoka wasowatu gays achipwanya kulibe

  • @PeterBendeka
    @PeterBendeka 6 дней назад

    Amercy mundidijile ndidzajukwatira Kona undiuze Kaye mimba inapitakuti

  • @CollinsLingu
    @CollinsLingu 4 дня назад

    Kkk Kodi a chuma ife atumbuka ndamene timamwa tea kukatentha ? 😂

    • @IyahMohyoh
      @IyahMohyoh 20 часов назад

      Kweni atonga imwe amatemwa chai nyengo yonse

  • @EnelesKanyerere
    @EnelesKanyerere 6 дней назад

    Zachumazo nde zikumabowa

  • @ChikuChatenga
    @ChikuChatenga 5 дней назад

    😅😅😅😅😅

  • @LeniaSauzande
    @LeniaSauzande 6 дней назад +1

    Koma achuma aaaa chibwibwi too much mudzitolere

  • @HaziwellKambelembele
    @HaziwellKambelembele 7 дней назад +1

    Km shokoshoko sadzatheka guys

  • @PeterBendeka
    @PeterBendeka 6 дней назад

    Komano queen dejkhani

  • @TravourZhinga-p2v
    @TravourZhinga-p2v 6 дней назад

    😂😂😂𝐚𝐭𝐢 𝐦𝐮𝐧𝐭𝐡𝐮 𝐚𝐥𝐢 𝐦𝐭𝐢𝐤𝐚

  • @HarrisonDinala-r9p
    @HarrisonDinala-r9p 4 дня назад

    apa chaka timaliza bwino

  • @StevenhoChikaondah
    @StevenhoChikaondah 5 дней назад

    Chuma umatha iweyo

  • @jackbello2170
    @jackbello2170 4 дня назад

    Mwatiyimilira

  • @LegoElton
    @LegoElton 6 дней назад

    Chima ndi dolo oposa madoloyo palibeso

  • @OwenDevaleous-xs1ut
    @OwenDevaleous-xs1ut 7 дней назад +1

    Mativetsa kukoma guys big up

  • @DavidPhiri-o6w
    @DavidPhiri-o6w 6 дней назад +1

    Koma chokochoko wapeza bomba la mukazi ndiwokongola

  • @SalaryHassame
    @SalaryHassame 5 дней назад

    Big up 🥰🥰🥰

  • @MalumboMndala
    @MalumboMndala 6 дней назад

    Chuma😂

  • @VertusKauteka
    @VertusKauteka 3 дня назад

    ❤❤❤❤❤❤❤