NKHANGA ZAONA MANGANYA WATUMIDWA NDI MCP KUTI ATHETSE UTM WALANDILA NDALAMA KUTI AGULE MA VOTI

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 12 сен 2024

Комментарии • 196

  • @user-cd4df3vg4y
    @user-cd4df3vg4y 17 дней назад +9

    Ulemu wanu Comrade Ntanyiwa. Kodi Chakwera chomwe akufuna ndichani anapha SKC lero akulimbana ndi chipani UTM. Munthu akupitilizabe kudana naye munthu alikumanda.Manganya ndi Yudasi ndipo a mcp amachitadi kulakhura SKC alipommwepo. Mulungu atimenyere nkhondo ndithu.

  • @AdamYas-ec9oc
    @AdamYas-ec9oc 18 дней назад +16

    Amene anayera kwapangira mademo ndi chakwerayo mumakwena mtanyiwa mafuso a bwino

  • @user-wl7xn3or6d
    @user-wl7xn3or6d 17 дней назад +5

    Mangadya ndi mfiti akusokoneza chipani chikangawa palibe wachita ana ngo bwela kudzaba kuononga ndi kupha Satana weni weni

  • @TonykalicheloKalichelo
    @TonykalicheloKalichelo 18 дней назад +8

    Palibe chifukwa chomulolera manganya ku covetion

  • @gmxplayboy6559
    @gmxplayboy6559 18 дней назад +18

    Akamawapatsa nsalu za UTM anthu a MCP ndi cholinga choti aziwoneka ngati a UTM alipo ochuluka omwe ali pambuyo pa MCP, akuzinamiza wokha. Akuzipanga okha chinyengo, ndipo posachedwapa ndikutha kuwona Manganya akusowa kolowera

  • @CassimMbalaka
    @CassimMbalaka 18 дней назад +10

    Borani muthalika kusiyana ndi mfitiyi

  • @CassimMbalaka
    @CassimMbalaka 18 дней назад +6

    Mulungu salakwitsa kalikose adziwa pomuyika aliyese wokhudxiwa ndi ifa ya chilima

  • @user-ss9bj5eh6b
    @user-ss9bj5eh6b 17 дней назад +3

    Limpopo fm with comrade ntanyiwa machine bambo

  • @Malume2024
    @Malume2024 18 дней назад +7

    Watumidwa usi ndi mbuzi ya munthu koma utm singathe ayi

  • @blessingsnyalo-rp9ko
    @blessingsnyalo-rp9ko 18 дней назад +6

    Apano ndigone chifukwa nkhanga zomwe ndimadikira zafika 🎉🎉🎉🎉

  • @Rose-wu5ef
    @Rose-wu5ef 18 дней назад +6

    Chakwela wapha chilima, ndi chakwela

  • @SamukLungu-zg7fl
    @SamukLungu-zg7fl 18 дней назад +4

    Kodi conversion siyingakapangikire ku tcheu

  • @AdamAhamad-k2i
    @AdamAhamad-k2i 17 дней назад +2

    Michael usi ndigalu akathera ku convention ya UTM

  • @user-ly4xw3gf3e
    @user-ly4xw3gf3e 15 дней назад +1

    Chilima mmmmh 😢😢 kufa imfa yosadziwika bwino, chipani chake nkumachilondanso akufuna chani kwenikweni a MCP wa?????

  • @user-ww4ei5fb7d
    @user-ww4ei5fb7d 17 дней назад +2

    Wicked world, satana ndi olephera

  • @WysonAnton
    @WysonAnton 17 дней назад +2

    Chikangawa ndiwoyenera mademo😢😢😮

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg 18 дней назад +3

    manganya ndimunthu oipa tikuonerani patsogolo uzazindikila

  • @DauglasBowa
    @DauglasBowa 18 дней назад +3

    Ntanyiwa sadzatheka pa Limpopo fm

  • @MarySelenje
    @MarySelenje 18 дней назад +1

    Waiting for the chikangawa report

  • @PreciuseMBinga
    @PreciuseMBinga 18 дней назад +3

    Palibe chobisika pansi pa thambo

  • @Lunnah-b1t
    @Lunnah-b1t 18 дней назад +3

    Sindife wokhutira ,ataaa pang,ono

  • @BatumeyoChikopa
    @BatumeyoChikopa 15 дней назад

    Voti ili mu mtima osati mu chovala cha chipani, SKC and 8 others mhsrip 😭😭😭

  • @Rose-wu5ef
    @Rose-wu5ef 18 дней назад +3

    Tafika kale Mr ntanyiwa lreland

  • @SprianoJeke
    @SprianoJeke 18 дней назад +2

    Ndikutha kuona magazi ku UTM

  • @JaneNgwira-y1x
    @JaneNgwira-y1x 15 дней назад

    Onse amayenera kumangiridwa ma demo sakukhonsa onse vuto anthu timayiwala zakumbuyo timakumbukila zanthawi yomweyo yangolakwa ndi infa tima funa kuyeza utm awiriwa alephera

  • @INNOCENTMOFOLO-io8tg
    @INNOCENTMOFOLO-io8tg 18 дней назад +3

    amalawi tinazitemberera tokha kumuchotsa Peter Mutharika ndikumuyika satana pampando lero akutipha taonani amalawi anzanga
    koma ndikuona ngat kukhuta komwe timkakhuta ndi apeter Mutharika muja

  • @MaryRasmussen-mr4zo
    @MaryRasmussen-mr4zo 18 дней назад +2

    Peter was good

  • @joempesi
    @joempesi 15 дней назад

    Ndikuupempha Mzimu wa S K chilima ukuvutitse manganya. Asagone tulo mtenderenso asaupeze mpaka imfa yake

  • @MusaPatireck
    @MusaPatireck 17 дней назад +1

    Tinazimbidwa ndikukhuta nthawi ya Peter ija lero ndizimenezi kkk

  • @AminaPhiri-pp9tw
    @AminaPhiri-pp9tw 18 дней назад +2

    Yofunika apo ndi step down achakwera atule pasi

  • @NtolelaNtimna-e3v
    @NtolelaNtimna-e3v 17 дней назад +2

    Oyenera ma dem ndi chakwera

  • @veronicagullo9373
    @veronicagullo9373 17 дней назад +1

    Amtanyiwa mudzapatsidwa u minister mu m,boma LA dpp

  • @WilsonChisoti-dz6vs
    @WilsonChisoti-dz6vs 18 дней назад +2

    Chakwera ndiye afunika ma demo

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon 15 дней назад

    Athetsa chipani chake cha odya zake alibe mlandu UTM singathe akunama kwambiri kafula ameneyu ndipo zimuonekera asowa kolowera amenewa

  • @user-fy7qk6kk5s
    @user-fy7qk6kk5s 13 дней назад

    MCP ndi makape tithana nawo manganya akudziwapodi kanthu.Mai kaliyati pachilomwe timati chonsamva anachiphikila muliponda musapite kulilongwe

  • @JoyceBanda-k8t
    @JoyceBanda-k8t 14 дней назад

    Amalawi mulungu atikhululukire chifukwa sitimadziwa comwe tikuchita chakwera anatiseka maso ndi mphavu zake wakumidima kt tisamaone ubwino wa peter mutharika koma kunena zoona chakwera alibe masophenya utsogoleri mwa iye mulibe koma mutharika abwererenso 2025 dpp woyeeeeeere chikangawa alongedze adzipita

  • @Littlefair7
    @Littlefair7 14 дней назад

    Chakwera ndi APM onse ndi olephera, dziko la malawi likufunika new blood.

  • @EagerChicken-qj6xu
    @EagerChicken-qj6xu 17 дней назад +1

    Manganya usatilakwitse chonde yendelani zanu.

  • @ThomasMlowoka
    @ThomasMlowoka 18 дней назад +2

    Chakwera ndiye akufuna ma demo

  • @ThivadoartistDyson
    @ThivadoartistDyson 18 дней назад +1

    Tazindikula amalawi kuti manganya siwa UTM 😂😂😂😂

  • @user-lw4hw9ce4w
    @user-lw4hw9ce4w 15 дней назад

    N kape akulamulirai APM tinamulakwira

  • @user-bl2ee4zk4n
    @user-bl2ee4zk4n 14 дней назад

    Mukuchedwa palibenso zama demo boma ndilomweli la Dr Lazarus maccarthy chakwera,simunganene zoti mademo muwayamba lero,mademo mwakhala mukupanga kale inu a dpp zaka 4 zonse boma la MCP likulamulira kuzera kwa Boni kalindo,koma Amalawi ndi anthu wozindikira kuti akumatumidwa ndi dpp,mukungovutika Mcp ikutengaso boma oloko chisankho chitachitika lero.

  • @TecksonKaima-dr6er
    @TecksonKaima-dr6er 15 дней назад

    Manganya ndi wasataneki,mzeru zake zikufanana ndi kufupika kwa msinkhu wake

  • @MarkoSimon-q3b
    @MarkoSimon-q3b 15 дней назад

    Manganya. Usamale. Nthawi. Yako. Yatha. Unanpeleka. Chilima. Usamale. Kwambiri. Usadzitame

  • @ruthkundwe7448
    @ruthkundwe7448 14 дней назад

    Zonsezi God is the judge, don't worry

  • @dagaphiri1867
    @dagaphiri1867 14 дней назад

    Manganya galu chitsiru. Unafupika ndi nzeru zomwe.

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile 15 дней назад

    The answer is we don't want lomwe people to rule us anthu ozikonda kwambiri

  • @lonnexjeke6840
    @lonnexjeke6840 5 дней назад

    Ine ndimaona ngati manganya ndi Munthu wabwino koma uli Dyabulosi weniweni mwana wa Satan 😢

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 15 дней назад

    that's the fact black or white without manganya chilima ndi Raphael sadakafa, munthu oyipa kuposa hetra 😢

  • @user-le9su3mt7r
    @user-le9su3mt7r 15 дней назад

    Chakwela mbuzi yamuthu chikangawa alibe zelu zaku yendesa boma mbuzii

  • @VeronicaChirwa-ct4os
    @VeronicaChirwa-ct4os 15 дней назад

    Ka michel usi ko nkachitsiru kwambiri

  • @IssaJohn-cb8vn
    @IssaJohn-cb8vn 15 дней назад

    Antanyiwa mukumuyelekeza president muthalika ndi mbuzi iyi yilipoyi?muthalika ndakatundu osayelekeza ndi thelele lilipoli

  • @ZainabZainab-sh2qv
    @ZainabZainab-sh2qv 10 дней назад

    Comrade mmmmmmm ulind bodza 😂😂😂😂😂😂 mpaka nkhan ya degree yafika kumeneko

  • @lukathamison1984
    @lukathamison1984 17 дней назад +1

    Apa ndiye panja peni peni

  • @MarkoSimon-q3b
    @MarkoSimon-q3b 15 дней назад

    Ayi. Ife. Sitikukhutira. Uyu. Ndi. Oyipa. Kwambiri. Chakwerayu.

  • @esaMoha-dm4kj
    @esaMoha-dm4kj 18 дней назад +1

    Mr president mtanyiwwa ulemu wanuw km munkushedwa ndilipoti llandege bwanji

    • @Yoxym
      @Yoxym 18 дней назад +1

      Ndi lerotu😂😂🎉

    • @esaMoha-dm4kj
      @esaMoha-dm4kj 18 дней назад

      @@Yoxym we've been 200 in ons to withng the nganga sawona lipopo from yesterday antill now on please mtanyiwwa ☝️🙏

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile 15 дней назад

    Vuto nonse amene mumakhala ngat a utm si ndinu ,ndinu a dpp

  • @ShaibuYussufu
    @ShaibuYussufu 18 дней назад +1

    Chidule antanyiwa tipangira chakwera mademo

  • @paulpaseli6310
    @paulpaseli6310 18 дней назад +2

    Mr chikangawa ndiyemwe akuyenela kupangilidwa mademo eeee uyu watizuzatu

  • @Lunnah-b1t
    @Lunnah-b1t 18 дней назад +2

    Amane amayenera mademo amphamvu ndi chakwera

  • @ShalifuMatola
    @ShalifuMatola 18 дней назад +3

    Ausi akufuna kufa naye

  • @ZinawZinawmulu
    @ZinawZinawmulu 14 дней назад

    Amenenyu wachikangawayu ndiye akufunika mademo chikangawa

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 17 дней назад +1

    Manganya unaphesa chilima nyini yamako😢😢😢

    • @LovelyAntenna-jh8yh
      @LovelyAntenna-jh8yh 17 дней назад

      Yeni yeni😢😢😢😢😢

    • @LawrenceBelson
      @LawrenceBelson 14 дней назад

      Ndipo machende ake ozendewera pansi manganyayo ndi chikangawa party

  • @ThoccoChimbali-h6g
    @ThoccoChimbali-h6g 17 дней назад

    Vuto a malawi munaika chitsilu pa mpando, munthu kumtola chipiku mpaka pulezidenti?a malawi sitinali serious ngati dziko

  • @CorneliusSande
    @CorneliusSande 15 дней назад

    Wonse palibe wabwino wonse wali ndi mavuto ofanana.

  • @ChikumbaLenzo
    @ChikumbaLenzo 12 дней назад

    umakwana comred auzeni anthuwo

  • @HassanMillion
    @HassanMillion 17 дней назад

    Ngati akub madigili anthu ena mosiyeni naye afa ngati chilima tili popano ndithu

  • @MaxwellMbesa
    @MaxwellMbesa 17 дней назад +1

    Tiuze zoona MTANYIWA

  • @user-fy7qk6kk5s
    @user-fy7qk6kk5s 13 дней назад

    Comrade palibe cha mzeru chilichonse wachitapo chikangawa ndi amene akufunika mademo a dziko lonse lapansi,peter ndi mtunda 2025 akubwerera osati manyakawa, dzisilu dza MCP ana a satanic

  • @PhiriVictor-e9l
    @PhiriVictor-e9l 23 часа назад

    Tinataya nthawi.2020 .kupanga.masankho

  • @IssaJohn-cb8vn
    @IssaJohn-cb8vn 15 дней назад

    Mayiko usi mutu mwake mulibe dzelu mumayenda mazi okhaokha

  • @OdettaLowrence
    @OdettaLowrence 14 дней назад

    Kma chikangawa sunzatheka iweo👉👉

  • @user-wl7xn3or6d
    @user-wl7xn3or6d 17 дней назад

    Lusiyasi ujaso ana chita kumupha kuti ti iwale ifa ya chilima Abanda ana chila

  • @StewartGoma
    @StewartGoma 17 дней назад

    True he knows how Chilima killed manganya Utsi he failed to go n visit n see where Chilima n 8 others killed shame

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile 15 дней назад

    Alomwe mwayamba liti kumukonda chilima anthu oyipa inu

  • @MussaChilembwe
    @MussaChilembwe 18 дней назад +1

    Manganya ndi mbuzi ndikufupika kwake Kuja galu amene uja

  • @S-rr1eu
    @S-rr1eu 12 дней назад

    Akazafa chakwela ndi manganya ndizasangarala

  • @JboyrashiiKatundu
    @JboyrashiiKatundu 18 дней назад +2

    Chifwamba ndi usi

  • @EvanceRazaki
    @EvanceRazaki 15 дней назад

    Peter muthalika ndiyamen tingamenyele khond

  • @LilianKachala-yz2xf
    @LilianKachala-yz2xf 18 дней назад +1

    APM Sadayenele kuchitsedwa pa mpando pano tikuvutika Zedi.

  • @yunuschiutula
    @yunuschiutula 13 дней назад

    Palibe cha nzeru chachitika katundu wakwera mitengo ma business tinaduka

  • @Shelifibraheem
    @Shelifibraheem 17 дней назад

    Can't wait kumva report Mr mtanyiwa.

  • @ThomasBlessings-j8k
    @ThomasBlessings-j8k 15 дней назад

    Tingakondwele ndi munthu opha anthu chingawa ife ayi

  • @PeterBendeka
    @PeterBendeka 18 дней назад +1

    Oyenera ndi chikangawa Peter inali nsanje chabe

  • @user-lw4hw9ce4w
    @user-lw4hw9ce4w 15 дней назад

    APM tinamulakwira mfumu

  • @Blessingskanyinji-x7s
    @Blessingskanyinji-x7s 17 дней назад

    Waiting for report ku fm ntanyiwa🔥🔥🔥

  • @JamiluSunday
    @JamiluSunday 12 дней назад

    Chikangawa watikwana kwambiri

  • @GregoryMatambo-m6y
    @GregoryMatambo-m6y 15 дней назад

    Basi busy kuipitsa mbiri ya anthu mupindulanji

  • @FreddieNkhoma
    @FreddieNkhoma 18 дней назад

    Kodi ndani asakuziwa kuti UTM inachoka mumgwirizano,
    Ndichifukwa chiyani akugwilisa nsalu za UTM

  • @MandalaChaona
    @MandalaChaona 17 дней назад

    Michael Usi usamalise ndi unthira kuwiri wakowo, omweo ukudya nawo iwe mkumasangalala adzakupha.
    Devil at work 👹⚒️🔨⛏️⚒️👹

  • @YasenYasen-q9g
    @YasenYasen-q9g 15 дней назад

    Chikangawa achoke

  • @esmybanda2227
    @esmybanda2227 18 дней назад +3

    Mcp chipani chokumpha 2025 pack and goo with you manganya

  • @NancyNyelenda
    @NancyNyelenda 18 дней назад +1

    Chikangawa

  • @user-ev6bi7jr7g
    @user-ev6bi7jr7g 17 дней назад

    Usi ndi wa MCP, Chakwera achoke APM pachiongolero APM boma

  • @user-db3mh9wr9v
    @user-db3mh9wr9v 18 дней назад

    Micheal Usi akuziwapo kanthu pa imfa ya Chilima polonjezedwa kuti apasidwa u vice president

  • @VeronicaChirwa-ct4os
    @VeronicaChirwa-ct4os 15 дней назад

    Chidanti malunga ndi galunso

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon 15 дней назад

    Kumalawi anthu ndi atulo kwambiri akanakhala maiko ena chikangawa ndi NDUNA zake atathamangitsidwa kale pampando

  • @RukayaIssah-h7t
    @RukayaIssah-h7t 15 дней назад

    Usi ndi wa mcp osati utm asatiputsitse ife palibe chimene anapanga kumwalira kwa chilima

  • @CharityMhone-uk9ym
    @CharityMhone-uk9ym 15 дней назад

    Manganya si munthu ndpo zintchito zake zikuoneka kakuchita kusangalala ndikungolubwalubwa ngati gwape, osamva chison ndi ifa ya mnzako, ine ndee kamandinyasa kwabasi😮😮😮

  • @MerryWayson
    @MerryWayson 16 дней назад

    Sizitheka Manganyayo akatenge amake ndi azilongo Ake akawasiye Kuchikangawa kwakeko