Malawi Ndi Dziko Lomvesta Chisoni

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 1 окт 2024

Комментарии • 81

  • @Phill-nh8ru
    @Phill-nh8ru 7 месяцев назад +1

    Olo apasidwe ndalamazo sangawinebe .DPP ikakanidwa mojority sizavota. Mcp izazivotela yokha

  • @jomochirwa
    @jomochirwa 7 месяцев назад +1

    Koma inuyo mmene mukuwonela ndichipani kapena munthu uti amene angakoze dziko lamalawi kuti tisavutike chifukwa dpp idatizunza lelo mcp.ikutizunzaso.

  • @StevenAjusugama
    @StevenAjusugama 7 месяцев назад +1

    Ya mwalankhula bwino kwambiri koma chimodzi mwaiwala ndikuoona ngatiso A DDP amphunzile kulemekeza NDi kutopa anthu omwe amawasankha chifukwaso amakhala NDi kusimbwa kwambiri kunenna zoona NDi amene anayamba kuliponya dziko la Malawi pamoto

  • @lyiemax
    @lyiemax 7 месяцев назад +3

    Powerful talking that's real, keep it up thank you so much Biggy 🔥🔥🔥🔥

  • @VictoriaKumwenda-k6o
    @VictoriaKumwenda-k6o 7 месяцев назад +1

    Nannuso adpp mwatengela inuyo mmene mnalandila boma ku udf basi mkuonaso ngat mcp alanda boma kwa inu daily alomwe zokamba kamba si ufumu ayi ili ndi dziko

  • @Abdul-xk8dq
    @Abdul-xk8dq 7 месяцев назад +2

    Ndine oyamba akulu mukunena zoona thawi ya piter anthu ambili amabwebwetuka amabungwe amipingo koma lelo kùli zii Ali ndi mbali yawo

    • @LinessDzimbiri
      @LinessDzimbiri 7 месяцев назад +1

      Akuona Ngati akhala muyaya pampandopo

    • @Pangolinimw
      @Pangolinimw 7 месяцев назад

      Indee

    • @eliffagondewe8214
      @eliffagondewe8214 7 месяцев назад +1

      Ndipo times radio ndiyomwe so amathandizaso kumenya campaign lero it's your turn walakwa Jim Brian musiyeni nthawi ya Dpp anali ndi kasakula kusambwadza Dpp a atseka radio ndindani asiye matola nkhani osamwopseza ayi

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole 7 месяцев назад +1

    And all departments have captured including some judges

  • @MatildaTatos
    @MatildaTatos 7 месяцев назад +1

    Tathokoza chifukwa chachilimbikitso chanu kwa chipani cha DPP pamodzi ndi a Malawi onse. Komanso mwayankhula mosonyeza kulikonda dziko lanu . Kuwalilira a Malawi pamaso pa Mulungu Namalenga

  • @isaaczidana2914
    @isaaczidana2914 7 месяцев назад

    Mwalankhula chilungamo chokha_ chokha ndipo Ambuye atipulumutse , atichotsele boma lankhaza limeneli

  • @TrizaGeorge-q8w
    @TrizaGeorge-q8w 7 месяцев назад +1

    Ndipo zovetsa chisoni kwambili kutengela ndimene dzikoli athu ife tikuvutikila 😢😢 ndipo mulungu akuona adzalipila misozi yose mmm chosadziwa ndipo tikanadziwa sitikanavotela m,busa chakwela

  • @mashallahleonard2793
    @mashallahleonard2793 7 месяцев назад +1

    Allah ndye yakho, sachedwa en safulumira.

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg 7 месяцев назад

    True Son of Malawi, MCP has captured even judiciary just as Zuneth satter did with Malawi Government. How can a court injuction be greater than constution.?!

  • @ZackThozan
    @ZackThozan 7 месяцев назад +1

    Aaaa kutemberera mupita ndinu kumasano

  • @dyachetewills
    @dyachetewills 7 месяцев назад

    mavuto aku chipani chanu asatikhudze. a Malawi mwawafuna lero, muli m'boma munkava za munthu? si aja mumagula zikwanje kuwapatsa anyamata aziwopsyeza otsutsa boma?

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 7 месяцев назад

    Dzikoli ligulitsidwe tigawanepo ndalama aliyense aziona kwake kolowela, Atsogoli azipani ambili mitu mwawo muli manyi.
    MCP ndiyankhaza kwambili

  • @StevenMuliza
    @StevenMuliza 7 месяцев назад

    Big mukuyankhula momveka pitilizani kutiimilira akusowa ofotokoza chilungamo ngati inu

  • @owenmajoni-d3n
    @owenmajoni-d3n 7 месяцев назад

    Komatu mukuliladi akulu. Dpp inatizuzatu inu munali kuti. Lero inuyo ndi anzeru kkkkkkkkk. Zomwe mwalankhulazi ndi zofuna za mtima wanu ndipo muchedwa nazo.

  • @HaroonSaidi-jv3ek
    @HaroonSaidi-jv3ek 7 месяцев назад

    CHISIYENI CHILUNGAMO CHIYENDE NGATI IMFA COZ IMFA IKAFUNA KUTENGA MUMTHU SIIONA KUTI PALI ADOTOLO ,ASIN'GANGA,WA CHITETEZO WAMFUTI AYI IYO IMAYENDERA LAMULO LA AKALIMAUTI

  • @LastoneBottomane
    @LastoneBottomane 7 месяцев назад +1

    Kulankhula kwanzeru kosonyezq kt munthu alindi unongo

  • @FrancisSangwa-c6r
    @FrancisSangwa-c6r 7 месяцев назад

    Ndiye ukulankhulazi ukufuna ife titanii ingopita ku Parliament ukalankhule kumeneko

  • @praisekafulatira4361
    @praisekafulatira4361 7 месяцев назад

    Koma nthawi nkachutsiludi. DPP kulira Lero?

  • @AhmadumkomaTambala-lr9gp
    @AhmadumkomaTambala-lr9gp 7 месяцев назад

    Ndpo malemla uja Mene amavutila kupaliament eeeeee Koma lazalo. Watienjeza asaaa Maka chinankhumwa

  • @greychizaka4088
    @greychizaka4088 7 месяцев назад

    just like the way people stoped tuning to mbc, zodiak they will also stop tuning to times

  • @FrancisSangwa-c6r
    @FrancisSangwa-c6r 7 месяцев назад

    Apm ndi boma liti inu ndinu a bolzano eti dpp its a family
    Party kulibe democracy kuja

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 7 месяцев назад

    Ndi a mcp amenewo si adpp akanakhala adpp akanatulukanawoso zimene ndi mbuzi za mcp

  • @olivechikwindi9126
    @olivechikwindi9126 7 месяцев назад +1

    Eishhh may the good LORD Bless you Brother, Mulungu amenye yekha nkhondoyi anthu akuzunzika kwambiri

  • @FrankRabson-q6j
    @FrankRabson-q6j 7 месяцев назад

    Koma afumu mumatha kulankhula ndinu Number one

  • @JohnChapanda
    @JohnChapanda 7 месяцев назад

    Ndikupemphe mbale wanga kuti upitilze osamva akhale choncho ambuye azikudalisa you are very strong i support you

  • @ChristopherKalikiliki
    @ChristopherKalikiliki 7 месяцев назад

    Uko nkulila kwa cadet

  • @sparkdymon3429
    @sparkdymon3429 7 месяцев назад +1

    Mwana wazeru iwe God bless you

  • @KondwaniMadeya
    @KondwaniMadeya 7 месяцев назад +1

    May God bless you my brother

  • @arafatMtyala-bo8ev
    @arafatMtyala-bo8ev 7 месяцев назад

    Koma nkulu uyu ndiye walatsa ntchende garutu, zonse zomwe wanyakhula apapa sananyike ayi mbari zonse zonse

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 7 месяцев назад

    So touched, MCP ndi ma coward awa boma anachita chooanda ili Kuba komwe sitinawonepo kuwononga dzikoli kodi alamuli 10yrs basi dziko latha po sure.. Anthu awa a choke before it's 2 late anthu kusamva mwaziona tsopano zipatso🙌🙌🙌

  • @juniornkhata2518
    @juniornkhata2518 7 месяцев назад

    Brian banda should just open his own Radio. A chunga kaya enawo nanga zimene akukapamba ndizomveka..

  • @AlefaKazembe
    @AlefaKazembe 7 месяцев назад

    Kulibe chanzelu chomwe ukunena iwe zinayamba lelo zimenezo ungofuna ndalama galu iwe khala chete Malawi niotembeleledwa bwasi

  • @BwanaGD
    @BwanaGD 7 месяцев назад

    Amalawi nthawi zose timakoza zinthu zitafika posauzana ndipodi ndipo mulungu akupenyelera zosezi kubuula kwanthu ndikunkhulupira kukuveka kwa mulungu ndipo anthandizana nafe

  • @GeorgeTembo-v6i
    @GeorgeTembo-v6i 7 месяцев назад

    Komatu a chakwera inuyo mukudziwa anthu akulira misozi yamagazi kamba kainu? Ndithu mulungu womoyo akukathe Amen

  • @marthansaliwa7732
    @marthansaliwa7732 7 месяцев назад

    So so so very true sir God Bless you for this revelation. Chomwe munthu amadzala ndi chomwe amakolola. There's no forever money, richness, and flavored life. Time will tell. They think they are in Heaven with poor peoples money but they living in hell.. Yes time will indeed tell. Busy pleasing lucifer but lucifer has his own time. People are having sleepless nights praying. We are praying every poor person is praying. Mulungu amakhala chete. Very soon they will see. God will rise for us. MCP ndiyodzadza ndi mbava, akhupha ndi afiti.

  • @CardoJustin
    @CardoJustin 7 месяцев назад

    Man mwayankhula monveka bwino ndithu I hope kuti Time radio yanva ndithu

  • @AlefaKazembe
    @AlefaKazembe 7 месяцев назад

    Very useless Malawi

  • @JamesMannuel
    @JamesMannuel 7 месяцев назад

    Ulibe fundo

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 7 месяцев назад

    Following bro ,

  • @Dauson-j5i
    @Dauson-j5i 7 месяцев назад

    Mawu amphamvu

  • @ConfusedAstronaut-qv6wq
    @ConfusedAstronaut-qv6wq 7 месяцев назад

    Sir ,Mulungu akutsogolereni this is a very good speech .

  • @DouglasDazuKamwendo
    @DouglasDazuKamwendo 7 месяцев назад

    True talk

  • @thereissenseinthenonsense7169
    @thereissenseinthenonsense7169 7 месяцев назад

    Glory to God,His time is coming when He shall rescue malawians

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick 7 месяцев назад

    Eishiiiiiiii brother keep it up well explained eeeeeeeeeeeee ndipo auzedi zenizeni ❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @JoyceBanda-k8t
    @JoyceBanda-k8t 7 месяцев назад

    Amcp akuopa mutharika ndi mlona akusokonedza ku dpp

  • @LilianKachala-yz2xf
    @LilianKachala-yz2xf 7 месяцев назад

    Mwalankhula bwino Ambuye Akdalitssni

  • @FredaLibamba
    @FredaLibamba 7 месяцев назад

    Ambuye timenyereni nkhondo mdziko la Malawi

  • @musaphiri317
    @musaphiri317 7 месяцев назад

    Ndizoonad bwana wanthu akulira ndimavuto 😢😢😢

  • @LembeniMtenje
    @LembeniMtenje 7 месяцев назад

    Kuyankhura mwamphamvu komanso mwanzeru ❤🎉

  • @PeterPhiri-nd6op
    @PeterPhiri-nd6op 7 месяцев назад

    Kuyakhula kwabino❤

  • @laisibukumatelesi1586
    @laisibukumatelesi1586 7 месяцев назад

    Eeeee koma lelo ndiye mwalatsadi abwana

  • @RobertTanganyika
    @RobertTanganyika 7 месяцев назад

    You are taking my Brother Very true

  • @LaynaAdam
    @LaynaAdam 7 месяцев назад

    Mwanena momveka bwino achimwene

  • @omarajibu860
    @omarajibu860 7 месяцев назад

    Hara akuchitidwa control

  • @YoungScott-p7e
    @YoungScott-p7e 7 месяцев назад

    God bless you sir, great revelation.

  • @amosChataika-e8h
    @amosChataika-e8h 7 месяцев назад

    Very Brave, big up Brother

  • @ThomasTrein
    @ThomasTrein 7 месяцев назад

    Zonazale mukulankhulà zoona

  • @ho222nussa
    @ho222nussa 7 месяцев назад

    Indee mukunenazi zoona ndithu

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete 7 месяцев назад

    Mau abwino kwambiri ❤❤❤❤❤

  • @PiusChawinga
    @PiusChawinga 7 месяцев назад

    Brian Banda amatitsegula m'maso musamupinge pinge

  • @asiyatujuma5507
    @asiyatujuma5507 7 месяцев назад

    ❤❤❤❤❤

  • @TiyaMtete
    @TiyaMtete 7 месяцев назад

    ❤❤❤❤❤

  • @georgesmart3791
    @georgesmart3791 7 месяцев назад

    Mau a mphamvu comrade

  • @estherkauyange6548
    @estherkauyange6548 7 месяцев назад

    Adzayamkhadi sure

  • @MoosaSame
    @MoosaSame 7 месяцев назад

    Powerful words bro

  • @TiyaMtete
    @TiyaMtete 7 месяцев назад

    Dpp my vote

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 7 месяцев назад +1

    Kulira kwathu mulungu akumve

    • @Pangolinimw
      @Pangolinimw 7 месяцев назад

      kumene mulungu akuona

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick 7 месяцев назад

    Atani atani APM ndi bomaaaaaa basi boss umatha kunena Chilungamo zedi❤❤❤❤

  • @IsaacOsman-w1i
    @IsaacOsman-w1i 7 месяцев назад

    Thanks for your powerful revelation Sir, 🙏

  • @francis12fombe54
    @francis12fombe54 7 месяцев назад

    Lucius banda lero akumanandi ndithu mulungu

  • @WilsLimited
    @WilsLimited 7 месяцев назад

    True man of GOD