Musamvele Chisoni APM Mumvele Chisoni M’Malawi Amene Akuvutika D Phiri

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 3 фев 2025

Комментарии • 10

  • @ReadsonChisaga
    @ReadsonChisaga 9 дней назад

    Hule iwe Jessie Kabwila, chimutu ngati mamuna.

  • @isaacbandah3617
    @isaacbandah3617 9 дней назад

    Wayankhula bwino m'bale moluzanisa anthu pamodzi ndakunyadirani, tisamalimbaneso tokhatokha osusa sizabwino ayi tiyeni tibwele pamodzi kuti timenye nkhondoyi

  • @AminaKambulire
    @AminaKambulire 9 дней назад

    Nkhanitu ya aLongwe ndiyosavuta chomwe a ALongwe akanachita ndikupepesa kwa ntundu wa a Malawi ndikutiuza kuti tisamuope sanatumidwe ndi munthu koma wabwelera kuzalila limodzi ndi a malawi ndikutiuza ife kuti champangisa kusintha maganizo ndi chiyani asanayambe kuyanhula pa bwalopa

  • @MarySinjirani
    @MarySinjirani 9 дней назад

    Musiyeni hule wamkuluyo aka sume chitsiru cha mzimayi

  • @AcctyhBuno
    @AcctyhBuno 9 дней назад

    Jese osadanda naye and wachita kupepetulidwa mudikile masiku akubwelawa mumva kuti wavula wayamba kuyenda bwanuswe

  • @StewartGoma
    @StewartGoma 9 дней назад

    Apm akufuna kuwatchosa Amalawi mmanja mwa phraroh ndikuwayika thandwa lolimba

  • @PhilemonLloydGalawanda-tz2zb
    @PhilemonLloydGalawanda-tz2zb 9 дней назад

    Zamanyazi kwambiri apite akasume ku ICC ndipo akuchedwa kodi kwawoko kulibe okalamba ? Who is forcing APM to stand as a Presidential candidate? Do you have any sufficient evidence? What is your problem with APM? Ndi bambo ako? Pali ubale wanji pakati pa APM ndi Mcp? Don't think Malawians are so stupid like yourself. Go to hospitals and see how patients are suffering....ukadandaule za APM kuti ndi okalamba ndi a bambo ako? Welcome back Ben Longwe on board..I support you brother Phiri...

  • @ChikoMasapula
    @ChikoMasapula 9 дней назад

    Chakwera (satana) kwake ndikupha, kuba ndi kuononga.

  • @RoseThindwa
    @RoseThindwa 9 дней назад

    Zoona boma ili Malo mopanga fix zinthu Ali busy kulimbana Na nzao yet Ali boma