Kamangira your a great man, God sender to know the truth may the almighty God continue to protect and engulf you wherever you shall go in the mighty name of jesus❤❤❤
powerful message "its better to be alone but with God than like chakwera having chimwendo chithyola kunkuyu ken nsonda jessy all police officers and zikwanje boys but without God" kuyankhula mwanzeru
Kamangila ukamupezeso jaji wa court la kusalima ndipo palichinyengo osati masewela anthu akuzuzika maka azimai mkadakhala ndi mwai mkadawavumbulutsa ine
Good development comrade Kamangira!!! That's what SKC wanted to do. Keep it up bro we're with you actually in prayers.
Watching from SA Durban KZN
Watching from Johannesburg viva loya wagulu kamangila
God be with u pray for protection Mulungu akumenyelani nkhondo muli chete anthu akukupemphelerani
Kamangira your a great man, God sender to know the truth may the almighty God continue to protect and engulf you wherever you shall go in the mighty name of jesus❤❤❤
Ambuye akutsogolereni,Mr kamangira poyima pachilungamo💞💞💞💞💞
Kamangila keep it up May the Almighty God be with you.Amen
The fear of God is the beginning of wisdom
Okha asuma kukhoti...okha agamula kale kuti akufuna 250 million...ndiye kubako kumeneko....
You was created for purpose. God bless you
Well done brother may God protect you always
Pray for kangira to be protected by almighty lord bravo
powerful message
"its better to be alone but with God than like chakwera having chimwendo chithyola kunkuyu ken nsonda jessy all police officers and zikwanje boys but without God"
kuyankhula mwanzeru
This Man is a real Malawi freedom fighter ✊️
We pray for God to use you more n more
Watching from boksburg north SA 🇿🇦❤
God sent you to open up our eyes..viva kamamga
You are the true son of Malawi, may God protect you
Mmalawi wa chilungamo ali pambuyo pako.... Onga iwe ngosowa...Ulinawo mwai opanganso ziphuphu koma yatsankha chilungamo...Keep up this noble task..
Bravo. Brother....osaopa...osatopa. Osafooka 💪
Thanks for that God will bless you every time
May the almighty God protect you where ever you go
Kamangila ,Chizuma, chilima and Mr Mupaka they were need to put our nation on a better level
Powerful massage, brove
God be with you Mr Kamangira
Respect mr continue your work
Watching from Capetown {SA}I follow you god protect you
God be with you always
Thanks for the good and great job you are doing God bless you
We're busy to pray for you kamangira may our almighty God be with you and protect you always never give up 💪
Ndizikupemphelera mpaka nditamaliza School tizathandizane Nkhondo imeneyi
Job well done kamangila ❤❤❤❤❤
Ndiwe heavenly sent ayise
The spirit of God is where ever you be bravo comrade ❤❤❤ 🔥 🔥 🔥.
God bless you and protect you comrade.
Abwana, we need change in Malawi. Things are not ticking in our country. Kumangopusisana
I pray for you kamangila God will protect you, just worry will president is not supporting you there is suspicious
Tili nanu kulikose bro
Aing,alule ameneyo tizipephelera iyeyo tonse mpaka dziko lisinthe anthuwa anajaira kwambir Malawi
Mulungu akutetezeni::musakumane ndi za Chilima
Majajiwa amatasa kwambili.amachita kuwonesa kut ndi achinyengo kwabas
Mulungu adzikudalitsani tuyenere a Malawi
God of Isaac , Abraham and Jacob be with Kamangira
God of daniel shadreck and abdinago
Kodi oduka mkono amanena wa Bakili muluzi tv uja.. ali mgulu la anthu chinyengo?
Mulungu akutetezele pamene ukutimenyela nkhondo imeneyi
Mulungu akudaliseni❤
Agwire pakhosi!! Umathaa!
Mulungu ndiwamkulu akhala kumbali yako kt oipayo akhale pambalambanda
Mumumva kuwawa eeee! Mumumva kupweteka! Mukamalimbana naye KAMANGILA yo, mumumva kuwawa eeeee! Nthawi yakwana, anthu amenewa Mulungu awayike pa mbalambanda basi. Kip de 🔥 burning
Nzikamanda ngati umphawi wamupweteka apita akakolope nyanja
Freedom fighter kamangila
Agalu amenewa akungikhalira kugona azimai omwe akipita ku ma court Kuti milandu yao iyende bwino
Soldiers , mphungu wa amphawi, inu mutakhala president wa dziko la Malawi titha kuona kusintha dzikoli
Kamangira mulungu akutetezereni ndipo anthu oipa awa alangidwe ndithu
Malada kamangira keep it up
Bwana muike platform anthu adzinena milandu yawo momwe inapindikila.
Anthu awa akupanga zachabe
Km iweyo ndiweniweni olankhula chilungamo umakwana
Dpp utm afford must hire this innocent lawyer ( special soul )
God bless you my bro
God b with you 🙏 and us
Tinakusowanitu❤❤
Ambuye azikutetezani
Komatumwene ndinu achilungamo komasono mikangoyakeimeneyi sokumezani amoyo ? Inendilindinkhawa ufausanadyelele
We pray for u
Mumanena zoonaboss mulungu azikudalitsani
Khang'a wina ndameneyu
Malawi is suffering because of them
Maitha
Koma chakwela osamusiya ndi nzake chimwendo
Koma nde mupalasra mchenga mu mpunga wa gulu2 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
A Malawi ife ndiovesa chisonikwabili timagoziwa kuchemelelabasi komano kuchita a shown sitimatha komano misechebasi mulugu azikudalisani man
very true a Malawife nkhani kuombera mmanja kwa anthu opusa ati Boma lomweli
Kamangila ukamupezeso jaji wa court la kusalima ndipo palichinyengo osati masewela anthu akuzuzika maka azimai mkadakhala ndi mwai mkadawavumbulutsa ine
Kani yabwino