Tonse alliance ndiyolephera even chakwera ndi olephera....blame game za ziii.....chakwera muja amayendera kunja muja kukakambila NDA Zungu zimapindula zachi.... MCP inapita ndi mwina wake kamuzu
Definitely yes. It was the best ever. Kungotitu zonse zinachitika post 2019 polls zija inali kale plan. If you don't know mtambo was intercepted talking to a certain politician kuti APM akadzangoti wawina kudzakhala ziwawa zoti boma lidzakhale ungovernable mpaka boma lidzalandidwe and it was exactly what happened. Chitsankho chimene chija a UN auditors anali ntcheru kuonetsetsa kuti pasaberedwe. Majaji ajatu ankayenda chewu chewu mpaka ankayenda pa heavy military escort wokaweruza milandu. Zinyaeu nazo zinavuta mu LLs.
Chiliichose chili ndinthawi. Kulibe wa muyaya. It's time for those ruling to rule. Nothing is wrong.. Ife mu nthawi ya Kamuzu sugar timagula K50. Accept change.
The journalist lacks skill of questioning.sensitive questions:1.did you share tippex? 2.your successor used same resources and workforce but there was no tippex used,why? 3.why you didn't report to police for kukhetsa mwazi intimidation? If you go to bank to collect money,all the details and figures are correct but there is tippex, will they allow you to get money,why? There was no cheating at all at examination centre and police were there but a student used a red pen instead of a black pen.will Maneb mark that paper?4.As a referee,why did you attend swearing ceremony while your successor never attended the swearing in ceremony? 5.Do you that mp elections only affect one area.for example tippex used on mp vote in Luchenza will only affect that outcomes of Luchenza but not of Karonga Nyungwe or Migowi but tippex used on president vote in Mzimba for example can affect the outcomes of the whole country?
So tippex used on MPs and councillors was ok cos only affected mma constituencies? Maganizidwe a chinyengotu awa 🤣 Thought the MPs were elected in the same manner as the president ? You don’t pick and choose when you talk about justice, that is a corrupt mindset, kufuna zofuna zako zokha zichitike
Mcp machende mwanu nonse ndi galu chakwera
Mulungu tilore akhale mulungu ndi amene akudziwa chilichonse amen
Thanks mibawa for hosting mama Jane Ansah, well explained mama....
🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
May Allah bless you we always love mom
Big up my Lady
Ubwino wake wadziulula wekha zoti ndiwe wa DPP si mesa ukukaimila DPP pa u Mp
We did not know that we were making a big mistake by demonstrating over you.... But forgive us... forgive the entire Nation... We love u mum
Salute
Don't say we as if takutuma
we you n who?,
Mai ndinu munthu oipa komaso wabodza nokha mukuti simunathawe koma munathawa momwe mwalakhulira apamu and simumkafuna kutsazika Kwa mabwana Anu...mukutiso mumanena kuti asagule tipex nde tipex anapezekapo pamenepo ngati judge simukuona kuti sizinayende bwino poti inuyo ngati munauza Anthu Anu kuti asagwiritse ntchito tipex monga zisakho zinazonse zimakhalira mbuyomu nde mumafuna kuti Anthu asadabwe mesa Inu njira imeneyo munaikana chifukwa ndi yomwe amabelera chisankho a DPP Mai wachabe osakonda dziko lino munapita ku UK kukakhomelera kuti IMF isapeleke zithandizo cholinga Tonse alliance government ioneke yolephera
Tonse alliance ndiyolephera even chakwera ndi olephera....blame game za ziii.....chakwera muja amayendera kunja muja kukakambila NDA Zungu zimapindula zachi.... MCP inapita ndi mwina wake kamuzu
A Jane nenane zoona Yesu akubwera posachedwe munathawa. boza ndi ntchimo mukudziwatso zimenezo
Ngati anathawa mulandu pano akulamulira ndindani?
Mama you did your part
Mmai Okonda dziko lake
Mum you really loved malawi
Chilungamo akuchidziwa iwo ndi Mulungu wawo
ndikuyankhilen fuso may kunali km kuthawa😂😂😂😂😂😂
Satana akomako ndithu
The woman who genuinely loves this country. Mum please forgive us for what we did . We were really crazy tinalozedwa
Satana wamkulu galu ameneyu alibe chilunga ndipo asanyase Malawi sitimufunaso. Ndipo ndizodandaulitsa kuti imfa ikutenga anthu ofunikira kumasiya satana ngati ameneyu zodandaulitsa kwambiri
Kuyankhura kopusa uku
Back to Sender ungayambe kumwalira Ndi Iweyo Kapena Azibale Ako Galu iwe😠😠😠😠
Satan mesa ndi chakwera wakoy
Cod knows kuti Mai ameneyu ndi Mai oyipa nkhope ndi mtima omwe. Chilungamo tiyeni tizinena, anali ndi mtima oti anthu pafupifupi 20 million iyeyo akane zigawo zawo ndikuti atipangile chiganizo chopambanitsa DPP pamene anthu tinavotera ena. Zagalu wako usamapatse ine wamva? Iwe ukuchita kumva yekha akuti akuma polling center anawawuza kuti azingonkwatcha nzere, chinavuta ndichani kuwauzaso aku tally center kuwauzaso choncho poti onse amayendetsa chisankho chimodzi chomwecho? Ndi ugalu wakowo sungaone kuti panali chinyengo?
Iwe ndiye mbuzu yamunthu , nyau yachabechabe
You are a strong woman Jane
May God continue to bless Jane Ansah ....
My mama God be with u forever
Mayi ankalifunira dziko zabwino uyu koma ife kusamva pano ndi izi ndikuona nyekhwe amalira ndipo tilira zeni zeni 😂😂😂😂😂😂sinditha
Ine ndlibe nanu mlandu nsaname
😂😂😂😂😂😂ma comment
Amai inuyo ndi mmai obheba kwambili ,pano tikuvutika zoziyamba tokha a malawi ,mum konda you
The only best woman Malawi ever hard
The great Mama
Amay ochenjera kwambili inu mabodza kumwamba kuri mulungu
Mai mbambande,mulungu nthaw yina amagwiritsa ntchito satana kut Zina zikhale bwino
Tippex pa headline wabwera bwanji
I have bad memories about this woman
The great woman Malawi ever had🎉🎉
Mayi madando mkukamba zabodza izi inu munathawa basi
Inde mdzko muno zinthu sizikuyenda bwino koma pachilungamo maiwa adalakwitsa ndthu,, ndpo yankho ndilakut adathawa mademo 😂😂😂
Mai ambuye azikudalitsani kwambiri
Zisakho sizinayende bwino kuvomereza ndikwabwino
Kapenatu name umagwira ku MEC
M'manjamo mwa mayi Jen kuti phwa phwa phwa ulemu wanu amayi .
Koma Dziko la Malawi!
Ananena za mwazi anali lazalo
Nkhani ndiyoti mumava bwanji kuti chisakho chomwe mumayendesa aku court nachikana? Ndipo ati chinalakwika chibwerere
Amamva bwino chifukwa pano dziko likuyenda bwino ndipo aMalawi akusangalala😂😂😂😂
Mai oipitstsa uyu .
Inuo olungama
We love you mum
kkk nde ati ndi chisakho choyamba kuyenda bwino kkk
Definitely yes. It was the best ever. Kungotitu zonse zinachitika post 2019 polls zija inali kale plan. If you don't know mtambo was intercepted talking to a certain politician kuti APM akadzangoti wawina kudzakhala ziwawa zoti boma lidzakhale ungovernable mpaka boma lidzalandidwe and it was exactly what happened. Chitsankho chimene chija a UN auditors anali ntcheru kuonetsetsa kuti pasaberedwe. Majaji ajatu ankayenda chewu chewu mpaka ankayenda pa heavy military escort wokaweruza milandu. Zinyaeu nazo zinavuta mu LLs.
@@isaacpelani andare amwene iiiii
@@successm-vt3dxndimamafia and anthu azithokoza kuti APM ndi munthu ofatsa and sanafune kutsatira nkhuli yautsogoleri inadzala mmitima mwa anthu analuza 2019 aja.
@@successm-vt3dxndimamafia and anthu azithokoza kuti APM ndi munthu ofatsa and sanafune kutsatira nkhuli yautsogoleri inadzala mmitima mwa anthu analuza 2019 aja.
Satana anatinyenga , you were genuine mum
Mai wautsiru uyu
Mai oipa inu
🎉😊
Sorry my lady, you were right during your era
Jane Ansah ngwabodza ndalama za deal saperekera pagulu
Koma nde aondatu
Mulungu Akutsongoleni mama munagwira nchito ya bwino
BIG STORIES
Aaaaa she's was corrupt by using tipex as jugde
Kkkkkkkk anthu amajama za Mai uyu.Koma iyeyo ankafuna kuti sugar asafike pa K4,500
Chiliichose chili ndinthawi. Kulibe wa muyaya. It's time for those ruling to rule. Nothing is wrong.. Ife mu nthawi ya Kamuzu sugar timagula K50.
Accept change.
Nthawi ya Kamuzu sugar timagula K50. What are you talking about. Accept change. 4500 yomweyo
Amalawi kunzunzana wokha wokha.a immigration masende anu nonse
Kkkkk
I don't trust this one
Kod munthu akakhala paudindo sakuyenela kukhala mfulu wachipan
CHOMWE NDINGANENE MAI SIBWINO KUKAKAMILA PA MPNDO INE NDILI KUNONSO KU MANGALANDE TIKHOZA KUTENGAKO CHITSAZO KUCHOKELA KUNOKO
Pansana pako iwe
Forgive Malawi Mai Malawi...
Mastn sopano mukuwalatu
Mbava izi
Galu uyu wabodza
sattha kufusa mafus.
Ndiye mwati amai awawa anali a judge ndithu mmhhh?
Akuti tipex anatani? Mai uyu eeeee
Atani kusakhala judge?
Mrs T ipex my good mum
Satana akomako ndithu
chakuba icho
I told them
Kodi akutichan
The journalist lacks skill of questioning.sensitive questions:1.did you share tippex? 2.your successor used same resources and workforce but there was no tippex used,why? 3.why you didn't report to police for kukhetsa mwazi intimidation? If you go to bank to collect money,all the details and figures are correct but there is tippex, will they allow you to get money,why? There was no cheating at all at examination centre and police were there but a student used a red pen instead of a black pen.will Maneb mark that paper?4.As a referee,why did you attend swearing ceremony while your successor never attended the swearing in ceremony? 5.Do you that mp elections only affect one area.for example tippex used on mp vote in Luchenza will only affect that outcomes of Luchenza but not of Karonga Nyungwe or Migowi but tippex used on president vote in Mzimba for example can affect the outcomes of the whole country?
So tippex used on MPs and councillors was ok cos only affected mma constituencies? Maganizidwe a chinyengotu awa 🤣
Thought the MPs were elected in the same manner as the president ? You don’t pick and choose when you talk about justice, that is a corrupt mindset, kufuna zofuna zako zokha zichitike
Amateur journalist