The truth about it is that Dr Bakili Muluzi is a clever guy that always looks into every situation and think that what is it there for me??? The thought behind his thinking is that UDF should partner with MCP so that his son should become the Vice President?
We need someone who is capable and competent enough to lead our country Useless chakwera has failed us he must go back to amayi anvano izi zikufunika anthu ochangamuka amzeru to bring back our country together
😂😂😂😂 Brain Banda funso la mtopola. UDF sichipani cha nkhaza a Tcheya alibe tsankho. Akanakhala oipa mtima bwenzi atadana ndi DPP koma ai a DAD ATHU AWA😂
Mr brian zipani zing'ono zing'ono zisapusitsike ndi kuphatikizana ndi dpp kapena mcp .mupusa nazo .dpp sidzakukumbukani inu mudzanong'oneza bondo .dpp ikuchita kuwonetselatu kuti ndi ya tsankho ngatiso mcp yomweyo.ithink gud idea idali yakuti for the first time mcp iyende yokha,dpp iyende yokhaso koma mgwilizano ukhalepo pakati pa udf,utm,afford pp ndi zipani zina .ok after election ngat onse atalephela 50 plus 1 then ndipamene utadzapangike mgwilizano wa bwino with gud mandate.
Brain Ali ndi dyera akumunamiza pitala Kuti azapita Ku state house Koma azakhumudwa Ku dpp kuli anthu oipa achina chisale sadzamutenga brain adzakhala akulilaso
Ine interview ya Atupele sinandigwire mtima seems is not ready to lead UDF the way he conducted from those simple questions. Guess what what fellow Malawians should believe in him probably 2025 kuli zinthu ndithu 🔥🔥🔥
President of democracy❤❤
UDF inatha kumakhomo kwaoko our daddy says that and i totally agree with that ❤
Udf siingawinitse Mcp,,tiyeni tiwasiye awa
Bakili was approachable, democratic and he use to answer the concern of citizens without hesitation.
A Chair woyee! You will always be my favourite president
Atcheya mumatha auzeni adaku belani boma aja za Democracy mdziko. Osatikugawanitsa anthu mitundu mdzikomuno ayi. Atcheya ndinu omanga dziko pamodzi Mulungu akudalitseni ndimoyo wautali .❤❤❤
Awa akupita ku MCP
Zaonekeratu
True
Zili mmalamulo aboma akuenera kutero
Love this old guy ❤
Basitu tifunilanji umboni wina alandila kale ndalama ku MCP
Apm ndi dolo apa tiyeni tonse ku DPP ndi omwe angatiombole
Kasaundi mumaika mkati mwa conversation ka muchotse kamasokomeza kwambiri
Ndipo kwambrinso kwake
Kkk,exchange rent.Iyeyu 2002 atamufunsa kuti bwanji zinthu zikungokwela anasowa chonena anayankha kuti alibe shop,bwanji sanatenge uphungu wa otsutsa?.
Bakili ndi chi machine atupere saziwa kuyankha mafunso atupere still young to lead the country
Alibe utsogoleri atupere
Kwa inuyo mtsogoleri wabwino ndi oyankha mafunso bwino?,odziwa kulankhula osati odziwa ma plan otukulira dziko?.
Anthuwa ali mitundutu iwiri,pali a ndale ndiye pali odziwa ntchito,ophunzira.Wa ndale kawiri kawiri ndi amene amakondedwa ndi anthu osazindikila bodza lake,pamene odziwa ntchito satha kulankhula,satha ndale ndiye amaoneka ngati opanda ntchito pamene deal ndi iyeyo.
Bingu sitikanamupeza pachipanda Bakili chifukwa Bingu,ngakhale anayambitsa chipani chake,ndale sankatha, kulankhula sankatha,iye anali ongodziwa ntchito,ophunzira nchifukwa anasinthadi zinthu.Ndiye olankhula kwambiriyo ndiye kambele mbele abodza,ongofuna kukaba m'boma,ikani m'boma anthu a serious ndi kukweza dziko osati chifukwa amatha kapena satha kuyankha mafunso,izo ndizobwezela dziko m'mbuyo chifukwa tizisankha nazo mbava zokha zokha.Tichangamuke andale ndi ma crooks.
Zipani zinazi mtima ukukana koma DPP mtima ukukhutisidwa ndikuona Ambuye ali kutisonyeza ku DPP ❤
oh yes ..!!+Afford&Utm featuring
The truth about it is that Dr Bakili Muluzi is a clever guy that always looks into every situation and think that what is it there for me???
The thought behind his thinking is that UDF should partner with MCP so that his son should become the Vice President?
Achair ndi one ❤❤
We need someone who is capable and competent enough to lead our country Useless chakwera has failed us he must go back to amayi anvano izi zikufunika anthu ochangamuka amzeru to bring back our country together
My vote ❤❤
😂😂😂😂 Brain Banda funso la mtopola. UDF sichipani cha nkhaza a Tcheya alibe tsankho. Akanakhala oipa mtima bwenzi atadana ndi DPP koma ai a DAD ATHU AWA😂
Kalipo kalipo acheya ndi MCP
Udf anzanga tsikani kumeneko akumenyetsa kumtengo
Achair ndi mthuzi wa malawi alingati gogo athu thanks chair
Abale mulungu watikonda UDF tiipa Moto tisapange masewera vote atupele muluzi
Mr brian zipani zing'ono zing'ono zisapusitsike ndi kuphatikizana ndi dpp kapena mcp .mupusa nazo .dpp sidzakukumbukani inu mudzanong'oneza bondo .dpp ikuchita kuwonetselatu kuti ndi ya tsankho ngatiso mcp yomweyo.ithink gud idea idali yakuti for the first time mcp iyende yokha,dpp iyende yokhaso koma mgwilizano ukhalepo pakati pa udf,utm,afford pp ndi zipani zina .ok after election ngat onse atalephela 50 plus 1 then ndipamene utadzapangike mgwilizano wa bwino with gud mandate.
Brain Ali ndi dyera akumunamiza pitala Kuti azapita Ku state house Koma azakhumudwa Ku dpp kuli anthu oipa achina chisale sadzamutenga brain adzakhala akulilaso
Chipani chabwino ndi Dpp bas chimadziwa bwino kusamalira anthu ake poosatengera mtundu
Atupele akuoneka wamantha than momwe analili m'mbuyomu
Amangwetu hiiiiiiii anali ndani kd
Akuopa milandu awa,,kulimba mtima kuja kunatha
Udf inatha kalekala akagwere uko awa mwana waoyuso ndi mbuzi yeneyeni
AChair adya bhanzi awa.
Channel chanuchi chili ndi vuto konzani
A chair akatunduu
Video ya anthu inu iimakoma ngati times
Koma a Tcheya akuti inatha kumakhomo kwaoko kkk
Komaineyo nduonakuti yawawa,kapalikalipo,wadya kenakake sured ,l can see UDF their combeneti with MCP,but the followas they don't know
Bakili muluzi anabadwa mwaumunthu osati chifiti chakunyajachi
Achair kufuna kuthokoza mcp fukwa anawathesera mlandu muyerekedze mupite ku emusipiko mukabilira komk
Adzapita after mavote coz panopa akuopa anthu awathawa🙆♀️
Ndipo ife ngati a udf tagwirizana kuti boma ndilomweri zinazi mmmmmm
Anaononga zithu awa aah amwenye kugula ma company etc
Zoona acheya kumawasilako achinyamata koma amzanutu sakukuona kukula kwawo kuti asiile achinyamata apm sakuvomeleza komatu akalamba za ziii basi
Ine interview ya Atupele sinandigwire mtima seems is not ready to lead UDF the way he conducted from those simple questions. Guess what what fellow Malawians should believe in him probably 2025 kuli zinthu ndithu 🔥🔥🔥
Ali ku mcp he is so stressed
Wachepa pa ndare even if you can hear mayankhidwe madarawa Ari power
Amalawi sitimamukonda atupele chifukwa choti sapanga ndale zonyozana komaso zamabodza. Uyu ndi tsogoleli yemwe amafunikila ziko mwanthu muno just kut a malawife tinszolowela kut andale azitikwana amzawo komaso kulonjeza za bodza like for example kutinamiza malawi atimangila ngati Dubai 😅ena fertiliser 4500, zomwe a Malawi timaziwa kut sizimgatheke ndizomwe timafuna andale azitinamiza
Bakili agulitsa chipani ku mcp
Andalewa ndi amodzi asatinamize
❤
Tiyeni tiwasiyire achinyamata atero acheya
❤❤❤
Atola nkhani away ayamba kunyasa chifukwa alandila ndrama ku dpp tsono times yayamba kubowa
Aaaa ayi
Ukunama iwe chilungamo chimawawa bwanji kodi?
Chilungamo xhakubayatu
madala madala
🎉
Mavuto anjara omwewo bwana😅😅😅😅
Democratic party yachani mukangopanga part ndi MCP ,mukhala mwaononga tsogolo la mwana wanu lot azalamulire dziko lino,hope sazalamiliraso
Mukati wadya bazi ndiye kuti aliyese wopita ku MCP wadya baziiakapita ku meneko sanadye bazi? Oooo.
Bakili muluzi wooooyeeeeee
Congratulations udf
Zikumvek
Chipani ichi chigwira ntchito ndi Mcp basi zikuveka zomwe alakhura amuluzi
Zopanda ntchito
Olo atapanga alayansi no more chikangawa
Nde mpaka chikangawa???? Nde anthatu
@@SliviaJosephy Chakuwawani ndi chani aliyese ali ndi ufulu oyakhulatu musaiwale Mcp idabwela kuzakhala ndiposo iwinaso kumbali yanga
@@DoreenBanda-hg7oe kwaiweyo
Times ndi ya DPP yayamba kunyasa
ZANU izo mukufuna aziyakhula zadpp ngat adpp ndiomwe ari ground ? Musamaonere muzikomoka amcp
Kachilungamo kamawawa 🔥🔥
Hehehe kabaya kachilungamo
UDF kotsutsa kwatikwana tipita ku mcp