If it is true.... I blame the Malawi defense force..... We have the weak defense system in our country..... And it's unfortunate that the military just watching when the country is captured by cartel of elite eliterate politicians.
Koma yaaa! Ndizoona mene ndavera ine, chiwembu chinachita kukozedwa 😭😭😭, koma asaiwale kutu kuja kuno kuli MULUNGU ngakhale saoneka ndi maso koma amapanga zithu zobisika kunkhala poyera, aonatu zimene zizichitika, mizimu ya athu onse anafera mu dege iwunse mtendere.
Zoana pastor shumba boma lokupha anthu lichoke tidanena ife kuti MCP singasinthe wamagazi ndiiwamagazi ameneyo ndi chikangawa basi osati chakwera koma chikangawa apa nde zimuvuta
Politics is good and social media is good too, we are free to talk anything we have in mind but my fellow malawians, Am so scared some opinions we are sharing to each other have possibilities of being accurate or not, therefore bare in mind beloved friends in Christ, mans of God,who ever you're or what position you carry in this world, God is there still watching over everything we are doing, meaning if its right God will add a blessing if not you'll go for hell whether men of God or not. So be careful of what you share we are may watching and hearing, i would be glad that any view on this add to our grace to be in heaven and recieve eternal life.❤❤
That could be true.... Chilima could have been killed on trip coming from Korea. But they new that some members of MCP were on board. That is why the the plane that carried Chilima to attend the funeral were only UTM and military security for the president that's give us another question mark.
Kodi Pastor shumba anthu omwe anali pa Airpot analibe mayina? Pastor shumba ndinutu aboza heavy chifukwa simukutchula mwasatane tsatena za anthu omwe anali pa airport mukudana ndii mcp chomwe mungaziwe ndi choti nonse mukudana ndi mcp kuti inatengapo gawo pangozi ija muziwe kuti mukupeleka mdaliso ochuluka kwambiri kwa mc
Ndiposo awachule mai iweo suunayambepo wapanga zinthu ndikunena kuti ineo km osakandichulako khaniyo kuuzidwa km ndikunene kuti osakanchula zina langa iwe phwala lako wakupha iwe
Abusa inu mukufuna kubera ndani Kodi, ngati utumiki wakuvutani tiyeni tikalime ku munda basi. Report la chipatala silingawonetse momwe ndege idayendela abusa.( Mapping and logistics, ikawoneke ku chipatala ). Eish koma sukulu ndi yofunikadi ndithu😢
Nde mbuzi zimenezi zikabwera kwanu mkumazisekerela Amalawi timaganiza bwanji koma?? Likanakhala dziko Lina state house itasesedwa yonse once ngozi ija itangochitika, koma poti kumalawi umva tionana 2025,kugona Basi.
Amen pastor God bless and protect because of your truth
Amen Pastor Shumba pamozi ndiinu nose mukudziwa chilungamo bwelani pammbalambanda Heaven will reward you
Pastor Shumba is right, and anthuwa adachita kuphedwa
Usawaphetse a shumba usamatchule maina
@@ThokozaniMaulana-oi5hz sangawaphe mesa akut sakuopa
If it is true.... I blame the Malawi defense force..... We have the weak defense system in our country..... And it's unfortunate that the military just watching when the country is captured by cartel of elite eliterate politicians.
Right thing for the incident.. God protect you Pastor Shumba
Amen pastor of god auzeni kut paziko lapasi palibe chitsisi chikauluka chimatera apa chikutera
Timadikira report Ili osati la ku German ...ulemu wanu pitilizani kutipatsira zoonazo.....kumupha mzake moteromo tionana mu September 2025
Koma yaaa! Ndizoona mene ndavera ine, chiwembu chinachita kukozedwa 😭😭😭, koma asaiwale kutu kuja kuno kuli MULUNGU ngakhale saoneka ndi maso koma amapanga zithu zobisika kunkhala poyera, aonatu zimene zizichitika, mizimu ya athu onse anafera mu dege iwunse mtendere.
AMEN my Pastor Shumba May the Good Lord BLESS you and keep you safe from these Killers
Amen akumususa pastor shumba ndi mfiti
Amen abusa otsutsa azitsutsa koma chilungamo ndichomwecho
Akangotuluka mboma zonse tidzanva bwino sure ...
Abusa God be with you
History is a best teacher
Tingokonzapo Poti airport imatsekedwa . Apo mpaboza ndege zina zimafika usiku ndithu. Ndangofuna kukonza apapa pokha
Palibe ndege imabwela madzidzi ogwira tchito ku airport osadziwa... Naneso ndingokoza pamenepo... Anthu amadziwa kuti usiku walero palibe ndege imeneyi ikubwela then amatha kutseka airport
Ndiposo kunoko ndege usiku sizingabwele iviniso ma boda imasekedwa 6pm imazasegulidwaso 6am
Ambuye akutetedzeni Abusa mmmmh ❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️
inutu ndiye mukulankhula zoona ambuye akudalitseni
Pastor shumba ,
Plz komwe muliko musamukeko, chifukwa chakwela ndi ndunazake watuma ma lsrael kuti akuphulitseni ndi bomba
Kkkkkkkk
Kikikikikiki
God bless you pastor shumba
Pepho kwa asilikali a mdf udindo wanu ndi oteteza anthu osat munthu ndie wina asamakulamuleni ngat udindo wanu sumuuziwa, wandale sangakuuzeni zochita chifukwa iye ali pamenepo m'mawa azachokapo , inu muzakhalabe msilikali don't fear anyone,koma muziwe udindo wanu😢
Zoana pastor shumba boma lokupha anthu lichoke tidanena ife kuti MCP singasinthe wamagazi ndiiwamagazi ameneyo ndi chikangawa basi osati chakwera koma chikangawa apa nde zimuvuta
❤❤ history it's best teacher azawona polekela agalu amenewa a mcp mfiti zazikulu
100% said that's true chakwera kwake ndikupha basi😢😢😢😢
Politics is good and social media is good too, we are free to talk anything we have in mind but my fellow malawians, Am so scared some opinions we are sharing to each other have possibilities of being accurate or not, therefore bare in mind beloved friends in Christ, mans of God,who ever you're or what position you carry in this world, God is there still watching over everything we are doing, meaning if its right God will add a blessing if not you'll go for hell whether men of God or not. So be careful of what you share we are may watching and hearing, i would be glad that any view on this add to our grace to be in heaven and recieve eternal life.❤❤
History is a good teacher
kaya ndizoona Kaya ndizabodza inebe chakwera wanuyo vote yanga sazayiona
Kulibe wamuyaya dadie naonso ka nkhasu kakafupi kaja kakuwadikilira💔💔
Izi ndizoona palibeso umboni wophosa yapha ,Ankaka ,a Richard Chimwendo and all the Chikangawa crue Afiti ophempera
A Shumba ndiumbuli ukukuyankhulitsani zabodza ngati izi. Zonse mukunena ndi mphekesera chabe. Umbuli ndi matenda ndithu.
Mwagundikatu zikuthandizani chani😂😂
Wekha wekhatu
You're right pastor Shumba
Amen pastor
Pastor wakuti ameneyi ngati akufuna kuntchuka ndinkhani iyiiiinndithu aziwona pakuti pachilichonse chizifunika umboniwabwino .ndi airport yakuti imene imetsekedwayo pamtumbopakosobwanji shimba pamodzindi adakutumawo
Kma izi muzipindula nazo chan? Ndi phindu lanji lomwe mungalipeze? Kumangochedwa nazo malo momapanga Zanu Kuti zikuyenderen pakhomo panu , mungochedwa nazo iziii!
Mukudya kwanu eti
zIkomo kwambili mtumiki wa mulungu AMEN
Anthu amenewa awakhululukire ndi mulungu yekha koma ife sitingawakhululukile kupangira pa mawa angazabwelezeso
True, these killers r just trying to be clever but History is the best teacher
Akulu, report lakucipatala ndi la ku Germany ndilimenelo lokhuza asilikari acilendowo, zabodza basi😂
Ndibodza bwanji ayankhula kuti ngozi mkati mwamawu awowo a shumbawo? Ngati adachita kuphedwa kuti singozi anayenera kumati chiwembu. Ifa imeneyi adayilowetsa ndale
Sizoona angofuna kutigawa ndipo akufuna anthu amenewa
Achilima mdzimu wao uwutse muntendele
Airport simatsekedwa bwana. Izi ndi zizindikilo zakuti nkhaniyi ndi yopeka chifukwa chongodana ndi mcp. Anthu oipa inu ongofuna kusokoneza mtendere wa dziko.
Ndipo nkhani zake zopeka zokha zokha ndipo samadabwa kuti samayankhidwa
Bwerani ku khoti akulu
Yesu anati fera kale
Akulu airport idayamba yatsekedwapo?
Go dipper man of God
Chakwera anapha chilima akane akane koma ndi dziko ili palibe chisisi.
That could be true.... Chilima could have been killed on trip coming from Korea. But they new that some members of MCP were on board. That is why the the plane that carried Chilima to attend the funeral were only UTM and military security for the president that's give us another question mark.
Mulungu akudalitseni paster 🙏🙏🙏
Atate kumwambako yankhulani,,tikulephera kukhala cete ife
Kodi Pastor shumba anthu omwe anali pa Airpot analibe mayina? Pastor shumba ndinutu aboza heavy chifukwa simukutchula mwasatane tsatena za anthu omwe anali pa airport mukudana ndii mcp chomwe mungaziwe ndi choti nonse mukudana ndi mcp kuti inatengapo gawo pangozi ija muziwe kuti mukupeleka mdaliso ochuluka kwambiri kwa mc
Mbolo
Ndiposo awachule mai iweo suunayambepo wapanga zinthu ndikunena kuti ineo km osakandichulako khaniyo kuuzidwa km ndikunene kuti osakanchula zina langa iwe phwala lako wakupha iwe
@@AndersonBishop-i2t mmangolota kutukwana basi
Bishop ochititsa manyazii
OK
Abusa inu mukufuna kubera ndani Kodi, ngati utumiki wakuvutani tiyeni tikalime ku munda basi.
Report la chipatala silingawonetse momwe ndege idayendela abusa.( Mapping and logistics, ikawoneke ku chipatala ). Eish koma sukulu ndi yofunikadi ndithu😢
Nenani kuti mwangizikinda chabe ndalama akulu limemelo ndi bodza
Ndi zimene tikuziziwa anthu aja anachitadi kuphedwa
Ndikuona umbuli mu report ili, osangokhala chete bwanji? Mutichititsa manyazi
Report la bodza, black box yitipase report basi
Zikomo koma mizimu ya anthu amenewa ikugwira ntchito
Koma chilima udachokelanji ku DPP ife amalawi kwathu ndi kulira nzimu wako use mumtenere 😭😭😭😭😭😭😭
Praise the Lord kumwamba kulemekezeke
Ndizimene timadkila Kuti adziwike Kut ndima 👹
A Malawi tose taziwa Kuti chakwera wapha anthu athu tsopano tipange bwanji??
Tiyeni tiyene tichotse nyasi mademo basi !!!
Zoona
Komatu zina pofuna ulankhula muziyamba mwaganiza, chifukwa ambili mungofuna wunjezera nkwiyo kwa a Malawi zinthu zoti sizipindula kanthu
Kasume ku court.
Nkhanitu siyiwola,iweyo ukuwona ngati izi ndi bodza koma tsiku lina uzakhulupilira koma popeza ndiwe wa chipani chakuphachi zikhale choncho
Kkkkkkkk chilungamo kuwawa asogo
So azibisa
Tiziwiseni Amen
Zikomo pastor shumba, mawu achikulu konanso omveka bwino
Report ife tinaliziwa kale angoonongapo chabe ndalama za boma apa iyaa
Bola pamenep mwachta bwino kuulula knu ndi one
Km mbiri ya chakwera ifufutika ngakhale ali moyo chonchi mbuzi ya munthu sindikuopa coz chilima enafe akutivuta kumaloto
Amen pastor netsan😂
Ngati zili zoona bwanji osatengana ndi born kalindo mupite kukhothi mukamusumile mkakayo aaaa ife mitimatu idakali yosweka
Tiuzen zoona tikuliratu ife😢😢😢
But ceme out man of God anthu awupandu aziwike magazi alimajamwawomu
Abusa inu nthawi ya usiku imene mukutchulayo inuyo ku airport mnkataniko kuti mkadziwe za a Mkaka? Abusa inu ndinu aboza opanda chilungamo. A Mkaka angayendetse zaku airport? Taphunzira kumanena zachilungamo.
Ndiabale anu kodi 😂
Munthu angamafotokoze zosezi ??? Palichinachake
Amene akuti ndi zabodza abwele apa anene mbari yake sizomanganatso apa, zisiru za anthu.
Pali Bodza pamudzi pano😢😢
Kkkkkk ndipo inu ndipo
Nde mbuzi zimenezi zikabwera kwanu mkumazisekerela Amalawi timaganiza bwanji koma?? Likanakhala dziko Lina state house itasesedwa yonse once ngozi ija itangochitika, koma poti kumalawi umva tionana 2025,kugona Basi.
Nkhani yonse yakambidwayi ndiyoona,Mulungu abweze pachimenechi kwa anthu onse oipawa Mulungu awakanthe ndi lupanga lake
Analipo nayeso mubusayo umbo Islington agitate asingoleti akuyixilayere azayakha ndiwo abusawo
Ulemu wanu Abusa chilungamo chimamasurave Eishiiiiiiii koma abale inu 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
Ndeno mwaulula chani pamenepa pastor odwala mutu
okay uthengawu ndiwonama reason yake ndiyakuti Kodi ndegeyo inakabwerekedwa kuti ? 2,nanga anthuwo amagwira ntchitoyo pa airport ndindani?3,abusa muli apapa musakhale okolezera mabala kwa anafedwafe ndiyeno anamuphayo ndi Chakwala kapena ndi mkakayo pamene timasureni tidziwetu nanga
Mbusa wonama uyu. Alibe Yesu koma osaka ndalama ku zipani potumikila zabodza.
Chilima ndi anzake anachita kuphedwa ndi chakwera
Panyo pake Chakwera 😢
Ndipo agalu awa Ishh azayankha 2025…akuona Ngati afikapo “amvekere tiyenzeka”wakumaula nonse😡💩🦧
I agree with you this is true
Komaso mcp ngakhale mutayifunila zoyipabwanji koma sikutuluka mmboma muchita manyazi machende Anu nonse odanandi mcp
History is best teacher😂😅😊❤
Chakwela naye aphedweso. Pamodzi ndiwonse anatenga. gawo. Pa ifa ya abale wanthu. Ndipo. Dziko kuyambila lero achotse. Paudindo. Wolamula
Ka boma aka next year kakuturuka basi
Amen and amen powerful massage timtama ambuye i like this song ❤
Ndilindimantha kuti m,busa wakuphayu akutumizirani zigawenga zotchedwa nduna zimu wa saulos chilima amene anapangitsa kuti mnyamata ngati ine kuvotera mcp use mumtendere🎉🎉🎉
Who can pursue criminal case..for this tragedy??
Zoona anachitidwa chipongwe chilima
Udalikuti iweyo chimutu chako iwe siwe busa galu iwe wanena zowe udakoza kozase abusa adamwalila sabale wanu mwanenad zowona zomwe udakoza.
Mulungu athandize dziko lathu
Chakwera kwake ndi kuba ,kupha ndi kuononga
Mazibusa akusaka ndalama tsopano
Azibusa achinyengo kadikirani chilango cha MULUNGU mmalo zomalalikira kuti akhale obadwa mwatsopano opusa inu
Lipoti koma limeneli osati amatinamiza zija
Bodzatu kkk😢😢😢😢 Satana iwe kutseka airport 😂😂😂😂
Ndikhalidwe lawo
No secret under pa ma chikangawa
ambuye😢😢😢😢
Anthu kuipa chonchi ngati zinyama mmmm
Ameneyo mmati saulosi chilima ndi ngozi chabe kwanu kulibe manda? Mwina ananena kuti sazamwalira mwina zimenezo big zilibe phindu
Kodi mukuti bwanji akulu inu? Sizikuvekatu
SKC still resting in peace 😢😢😢
A shumba nde inu mupindurapo Chan???