APM - NDIANYENYA-NYENGA MONGOKUMBUTSANA NYIMBO YAKALE YA DAN WADURA LUFANI

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 11 ноя 2024

Комментарии • 21

  • @MaxwellChiwaya-i8q
    @MaxwellChiwaya-i8q Месяц назад +5

    Eeeeeee nyimbo iyiyi apart from kut ndi ya ndale koma imandisangalatsa the dianamics rythem komanso well composed koma poti ndi yandale aaaaa bas nyc music

  • @Alexkalonga-t9s
    @Alexkalonga-t9s Месяц назад +3

    Ndipo chakwera akuziwa kut wamuimbira nyimbo yonyasa😂😂😂😂Iyi mesa ndinyimbo kaaa

  • @MaggieBanda-ft5tu
    @MaggieBanda-ft5tu Месяц назад

    Ine duuuu kuvetsela uku ndikumwetulila,Chiyimbo chopangila campain chomwechi😂😂💃

  • @dysonfysonchifundo2284
    @dysonfysonchifundo2284 Месяц назад

    Umu muli uthenga 🔥🔥🔥❤️

  • @chifundochiwaula998
    @chifundochiwaula998 Месяц назад

    Apm fire

  • @Langtonmilazi
    @Langtonmilazi Месяц назад

    Tizaimvera nthawi ya campaign. Dan lu angofuna kumusangalatsa chakwera koma ndi wa DPP akuwopa ndalama zamagazi zingamuphe

  • @StevenDastan-b9u
    @StevenDastan-b9u Месяц назад +1

    Nyimbo koma iz

  • @FunnyKatchenga
    @FunnyKatchenga Месяц назад +1

    Kale kumeneko, dziko likadali mphonje, sanapite Ku ng'ona party 😅😅😅

  • @patrickMakhumba-yc7rb
    @patrickMakhumba-yc7rb Месяц назад

    Kape uyu ngatitizivera nyimbo zikhara zomwezo basi zinazo takutaya kape iwe

  • @GraceLimani-zw7dx
    @GraceLimani-zw7dx Месяц назад

    Dan lu akavala nsale ya mcp a kuoneka ngati sanasambe akukhala ngati wamisala

  • @FrancisNyayi
    @FrancisNyayi Месяц назад +1

    Izi zinali ngat bakili ndi bingu

  • @HurmlysLangwan
    @HurmlysLangwan Месяц назад +2

    Fire

  • @MillicaBanda
    @MillicaBanda Месяц назад

    Zimabeba

  • @FeliamMakhoza-x7k
    @FeliamMakhoza-x7k Месяц назад

    Dan lu akutha kuyimba Nthawi imeneyo 🥱

  • @MusaMajudu
    @MusaMajudu Месяц назад +1

    Asananthe nthaw imeneyo nyimbo yokoma iyi koma pano alikudamu lang'onalo

  • @GraceLimani-zw7dx
    @GraceLimani-zw7dx Месяц назад

    Tiye nazo iwe tu uzitipangilatube campaign ukunama ndipo ukavala za dpp ukuoneka kusambatu

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm Месяц назад +2

    Ndpo anatiimbira nyimbo yabwno kusiyana ndi ya mcp ija akagwere kuchikangawa

  • @josephinemisomali6840
    @josephinemisomali6840 Месяц назад

    Nyimbo iyi a DPP adzikaika ku msokhano kt mwini wake yo idzimuwawa akamaona Paja sendela sisters ilipo ku Mcp ndiye Palibe chomvuta 😂😂😂

  • @FrancisNyayi
    @FrancisNyayi Месяц назад +1

    Share nyimboyo