Ukazaziwa kut andale ambili amangofuna kukhutisa mimba zao mpamene uzasiye kuika moyo onse pa ndale usakupezapo kalikose nanga chonchi awa amayankhula tu kwambili before izizi koma lero ndi awa at akwiya chifukwa aluza chonchi dziko silingasinthe mpaka kale tizingosintha azitsogoleri koma ma team awo ali omwewo
The problem is you Guys simunagwirizane chimodzi. As much as there is Democracy komabe opikisana munachuluka pa udindo umodzi. You are killing the Party now
Khalidwe mchuma,komanso leadership ija imaoneka even polankhula,kaliat sangakhadzakhale pa ballot paper mkumayembekezela kut chipanicho chiwina,if akutuluka atuluke ife tilipambuyo kwa omwe Ambuye wawasankhawo
Kkkkkkkkkkkkk ka dziko kakang'ono koma anafeliya yokha yokha
Am supporting her wapanga chisankho chabwino, apite ku DPP bas mlomweyu
Okay...... ndale zachimidzi zaku Malawi
UTM is UTM even without kaliat, kabambe, Usi, kamala,
UTM is a movement not a person
Evelefini anafeliya😂😂😂😂 delegate wakwiyitsa anthu akulu akulu
Michael Usi anena kale kt anthuwa apwetekana okha asiyeni lero ndi izi
Usi ankanena koma anthu simnamvere😂😂
Aaaah UTM ikhala ikupitilirabe
Aaaaa 😅 desperation ija osazaiphwekesa😅..
Kmanso it was obvious sanakawina
Eeeeeeee this is something else.... Honestly now you know how a human being can use you.
Everything anafeliya anafeliya politics💔
🫵🫵🫵🫵🫵🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Ma fras kkkkk akadaimabe pa SG
Zaziiii aaaa koma andalewa eeee
Manganya anakuuzani izi
Ati bwezi mwina tuchita manyaz😂
Kwaola anthu aphana💔
Eeeh koma zambiri zikuchitika mdziko muno mhuu🙌
Welcome
mkharidwe onyanyara ndi week readership
Ndale pa Malawi Eeeish🙌
Ndipo ndizodwalitsa mutu iziii iiii 🙌🙌
Ukazaziwa kut andale ambili amangofuna kukhutisa mimba zao mpamene uzasiye kuika moyo onse pa ndale usakupezapo kalikose nanga chonchi awa amayankhula tu kwambili before izizi koma lero ndi awa at akwiya chifukwa aluza chonchi dziko silingasinthe mpaka kale tizingosintha azitsogoleri koma ma team awo ali omwewo
🤣🤣🤣🤣🤣🤣 malawian politics zopusa
😂😂 Ndie angavoteke Kaliat kukhala President ndindani abale 🤣😂🤣 Mzimayi uyuoso
🤣🤣🤣 apa nde alowela kutino
Kupanga decision utakwiya zotsatila zake ndi izi
1 akaliat anatengana ndanzawo ndauzana kuti tiyeni tituluke mu tonse alliance cholinga chawo chinali chofuna kutenga chipani koma maso mphenya awo analepheleka anali ngat angel osadziwa sankafunila zabwino SKC
2 anayambitsa maudani ndi manganya kumupekela nkhani zambili zoti sanapange mulungu amangoti dikila ndachititse manyazi adani ako anatutana nkagulu kawo ose anagwa ku convention mamillions anapita
3 chifukwa cha phuma ndi kulankhulitsa kudzitenga wanzeru kwambili alanditsa chipani ma apapa ndiizo ndi munthu wamba nchipani
Chomw3 angapange a kaliat ndiko kufunafuna mtsogoleli wawo wakale manganya komaso kabambe ndikuti akhale pansi akambilan3
She came to destroy UTM ....
Usi uja amaganiza bhooo
Ndale za pa Malawi😄
Ndale pa Malawi
😂😂😂😂😂😂Nkhan yake kumufuna kumazadya misokho anthu andale mmakwana 🤣
Vuto lakumalawi aliyense akufuna udindo ,komanso kuli anthu awa ndine chilunga anthu opoilaa ofuna kumuputsisa munthu
Eweeee zathapo
Ife timadziwa tu evelefinyi anafelira anafelira🤣🤣🤣
🎉seee the translation 😅😅and 😅
She should not stay in tht party move kaliat you good 🇲🇼🙄👋
Welcome to the world
Welcome to Dpp
😂😂😂 koma ku Malawi kuli ntchito
Ife izi timadziwa anthu anabela.....Usi uja ndi dolo....
Chipani ichi chikupita ku diphiphi eeeehh
Kaliat bwanjinso nanga?🤣
Wathawa ngongole uyu ku utm ya 4 billion
Achinyamata tiyeni ndale tisamazitengele kwambiri, nditha kutukula dziko munjira ina yosadzelaso mundale. Nanga ndizinthu izi?😃
Kkkkkkk km kaliat
Malawi
Akunva kuwawa eeeeee
Akunva kuning'ina
Mukamalimbana naye Kabambeyoooooo
Mumunva kuwawaaaaa
Ndikukaika ngati ndi Kaliat
Mai Kaliat ndi achisilu. Wadyera uyu galu wamunthu. Kulankhula kwa bwanjii uku. Ngwamisala uyu
The fall of mwenemutapa kingdom
Nkan madeligate anamponda mutu,,eve. SKC sanampase u running mate Ali mzeru zachabe ameneyi, ndkape,,zvaya UTM sya munthu ,we lost SKC ,iwe or uchoke ulibe phindu
My country people😂😂😂😂💔
Kaliati was and is a traitor😅😅
Politics sungayikwanise
Kaliati can't be a president no way.
Everything anafeliya anafeliya
Ndale ndi dirty game sure
Uyu atha kukhala anadya kale zake
Ndale ndale
Tamvanawo
Vuto loganiza Ngat ndale zingathese mavuto kunyumba kwao
I'm so disappointed 🙁
Zanu kumeneko ine
Ku Malawi mkokoma
Koma awaso aaaa
Uyu anazlodza kuchoka ku DPP
Rest in peace RSK
Who is RSK
Lol
What happened to let’s support the one who wins? Lero asintha thabwa?
Amalawi kumwamba tikakhale pampdzi
The problem is you Guys simunagwirizane chimodzi. As much as there is Democracy komabe opikisana munachuluka pa udindo umodzi.
You are killing the Party now
welcome To DPP mama
Kmatu anthufe musamatitenge ngat opusa
Unafoila wekha iwe
Koma yae
Apita kutiko
Are you sure that this is Kaliati???
No it's you 😂
Apapa nde palibe za editing, sunganame kuti this audio Ndi ya edit
Kaliati is traitor
Welcome to DPP
Malawi's politics
Andale anthu oputsa
Palibe ndamvapo madafakaz gimme my data
😂😂😂😂💔😂😂😂
Kwayipilatu
Zovuzedi2
Tikulandilani ku 🐓🤝
Tidzakapuma tikadzafika kumwamba
Zauchitsiru basi
Chonch malawi will still suffer mot apange chimodz as a party kma they are fighting 🙄this gonna boast Mcp for next year's election
Kaliati sakuzwa chot achite
Komatu kaliati