Это видео недоступно.
Сожалеем об этом.

BON KALINDO LERO PA 14 JULY 2024 NDIPITILIRA KUNG'ALURA |

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 12 июл 2024

Комментарии • 55

  • @user-yk5qd6sk8e
    @user-yk5qd6sk8e Месяц назад

    the dc pangoolni🎉🎉🎉🎉

  • @harisonvinthenga3554
    @harisonvinthenga3554 Месяц назад +1

    Background sizikukoma mukusokoneza kuti timvere bwino bwino

  • @OwamiSimeon
    @OwamiSimeon Месяц назад

    Born kalindo osawopa osafooka osatopa

  • @JafaliChiwimbi
    @JafaliChiwimbi Месяц назад +2

    Boooon kalindo ndiwe munthu wakulu kwambili umakwana ❤❤❤💪💪💪💪💪💪💪💪💪💪💪

  • @OliveaMapanga
    @OliveaMapanga Месяц назад

    Powerful massage

  • @StevenMangani
    @StevenMangani Месяц назад +2

    Mr admin, mwapanga zofooira, tikumvera mix audios nde sizikubeba. Improve

  • @user-sk3ld2ss7s
    @user-sk3ld2ss7s Месяц назад +1

    A Malawi mumafuna, presidente Otani, piter mutharika ali m'boma munkati ngoyipa pano kuli chakwera mukuti ngoyipa, mumafuna boma Lotani? Mumafuna zaulere zomwe ndi zosatheka chifukwa pa dziko lapansi kulibe president amene angakwanise kugawa zaulere, musamaganize mopusa nkhati Boni kalindo amangosokosela nkhati chibebe chopanda kanthu, anthu Aulesi amatangwanika ndikunhoza president ndi chipani cholamula m'malo molimbikira kugwira ntchito...

    • @user-xo8ms5wh2s
      @user-xo8ms5wh2s Месяц назад

      Choka nawe chitsiru amalawi amazirimbikira okha amadya okha koma ufulu tilibe mbuzi iwe galu

  • @user-sm4vo2uo7g
    @user-sm4vo2uo7g Месяц назад +2

    Kod iwe dziwe tv pakuveka ma sound awiri pamenepo sixikuveka bwino

  • @EusébioLázaro-k4p
    @EusébioLázaro-k4p Месяц назад +1

    Dr Boni kalindo wosawopa Kuno Ju Maputo

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs Месяц назад

    Ati poti abweresa mayendedwe a pa njanji nde akuti apanga chitukuko mmmm koma boma limeneli
    ... Mphuno salota

  • @YusufAjiruh-c5q
    @YusufAjiruh-c5q Месяц назад

    Munyengo yong'alura the DC

  • @Shaibmpondan
    @Shaibmpondan Месяц назад

    Munch ❤ the DC

  • @ShekelengDavid
    @ShekelengDavid Месяц назад +2

    The DC plis kip it up...... MULUNGU alinanu ndicholinga.....

  • @AsimenyeMweneungu
    @AsimenyeMweneungu Месяц назад

    Mumakwana Dc

  • @TalazanGamah
    @TalazanGamah Месяц назад

    Power spech

  • @Shelifibraheem
    @Shelifibraheem Месяц назад

    Kung'alula ndiku ng'alula basi

  • @faithmagombo3666
    @faithmagombo3666 Месяц назад

    ❤❤

  • @macksonwaiti6762
    @macksonwaiti6762 Месяц назад

    Alimi akulandidwa fodya Ku limbe ati chifukwa fodya wawo siwabwino, malo mowabwezera

  • @winniendafooka4216
    @winniendafooka4216 Месяц назад

    Voice izikhala imodzi please. Tizimva bwinobwino

  • @EmmanuelGasiten-fo5dr
    @EmmanuelGasiten-fo5dr Месяц назад

    A DC, TAMUNG'ALULENI OWONDAYI. (NDANSO) AKUFUNA TIMUTUKANE APEZE POFERA.

  • @Its_Desire05
    @Its_Desire05 Месяц назад

    Tapangani mute background sound yo

  • @NedMoses-nc7ev
    @NedMoses-nc7ev Месяц назад

    Kodi ku mpoto ndi kumwela ma ID SADAYAMBE?

  • @MisheckAselo
    @MisheckAselo Месяц назад

    Umakwana bon kalindo MCP yaonjeza kwabasi 🎉🎉

  • @MervinAckim
    @MervinAckim Месяц назад

    Zikumveka ziwili2 apa

  • @user-un8yq1gg2i
    @user-un8yq1gg2i Месяц назад +2

    Boooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooooon kalindoooo heheeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeee

  • @GetrudeBanda-sd1yf
    @GetrudeBanda-sd1yf Месяц назад +1

    Zoonad asiyeni a UTM achite zomwe akufuna

  • @FatsaniMchenga
    @FatsaniMchenga Месяц назад

    Kkkkkkk koma uyu

  • @KyleWyngaard-kf4jg
    @KyleWyngaard-kf4jg Месяц назад

    Born kalindo mumatiimilira, keep it up

  • @EmmanuelJoseph-lj5eu
    @EmmanuelJoseph-lj5eu Месяц назад

    MCP zavuta basi, more fire Mr Kali do tilinanu limodzi

  • @user-iu8ow8jz6z
    @user-iu8ow8jz6z Месяц назад

    Zoona palibe kuvotela cha nzika
    More fire more fire

  • @MussaHassani-zg1hm
    @MussaHassani-zg1hm Месяц назад

    Thanks boss

  • @austinvincent773
    @austinvincent773 Месяц назад

    Tunva zinthu ziwilitu pakamodzi why dont u kuchotsa voice ya video mwaikayo

  • @morrisnyundo-ob5ev
    @morrisnyundo-ob5ev Месяц назад

    Keep fire burning mr

  • @jamessheki4293
    @jamessheki4293 Месяц назад

    Komatu Winiko penapake ngakhale umatibalalitsa koma umanena zoona, zambiri umalankhula zikumachitika😂,menyani nkhondo man

  • @JohnChipeta-wg9cf
    @JohnChipeta-wg9cf Месяц назад

    DC timakunyadirani pali anthu aku area 25 tikamaver inu ndi nbakili muluz TV akut azitimenya

  • @danmbuzi
    @danmbuzi Месяц назад

    The men men engineered

  • @TemwaKabisa
    @TemwaKabisa Месяц назад

    The DC ❤❤

  • @MphatsoSteven-r8n
    @MphatsoSteven-r8n Месяц назад

    The DC 😘😘😘

  • @MemorieMwasinga
    @MemorieMwasinga Месяц назад

    Followed

  • @user-vg3os8xx5t
    @user-vg3os8xx5t Месяц назад

    Why is it poor recording today there's sound waves that is confusing to listen

  • @MariamChipoka
    @MariamChipoka Месяц назад

    Zikuyenera ku ng'alulidwa

  • @AnaffSayamika-uh6vg
    @AnaffSayamika-uh6vg Месяц назад

    The DC 💥💥💥

  • @hillarytambulasi5914
    @hillarytambulasi5914 Месяц назад

    Poor standard video. Nanga what do you want us to here there?

  • @EusébioLázaro-k4p
    @EusébioLázaro-k4p Месяц назад

    Wosawopa

  • @user-ux9ik4zr5x
    @user-ux9ik4zr5x Месяц назад

    Can you please be serious with your editing coz tikumvera ma audio awiri nthawi imodzi,u better stop using that video clip coz is boring

  • @marcelolemos1484
    @marcelolemos1484 Месяц назад

    💪

  • @maderluda5501
    @maderluda5501 Месяц назад

    Editing yavutatuu apaa mix reactions Ya 2 videos

  • @YousufKadwala
    @YousufKadwala Месяц назад

    Ulemu wanu

  • @francissumbulero2291
    @francissumbulero2291 Месяц назад

    Za power

  • @samhussen708
    @samhussen708 Месяц назад

    Thee dccçcc

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y Месяц назад

    The Dc bon kalindo good Messnge ❤

  • @princedetbozsmallboy1749
    @princedetbozsmallboy1749 Месяц назад

    Why you use another voice from old video this is not professional my brother

  • @AssanOsman
    @AssanOsman Месяц назад

    Akatundu omanga ndimawaya