Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
Next interview kondwa uzamusiyire wina and I wish Brian Banda atapanga interview this lady
Everything is a journey, we can NOT just have Brian Banda forever. Steve will learn and get better with time.
May God bless you mam adani anu awonekera ng'amba mulungu wakumenyerani nkhondo.
Yes she is a good women
Steve Kondwa Banda ngt mkotheka gawo lachiwiri udzasiyire wina osati iweyo.sutha kufusa mafuso
Palibe tamvapo Nanga kumangomva mayina azibale basi Kkkkkkkkkkkkkk host kom samapanga control mpaka akambe zonse zakunyumba kwao😅😅😅😅😅
😂😂😂
Good interview
Izi tinadusako kale ndipo Court linamula ndipo tinavota kale zisiyeni izi
I wish it was brian banda interviewing this lady.
Kwambiri uyuyu ananyika
@@MalawianCamerasamafusa mafuso oyenerela.
Chifukwq cha... know kuti aliyense Ali ndi ma technic yake yoyendetsera zinthu zake
@@KeithPMaliseroJr Do you think you have heard all that you wanted to hear from Jane Ansah?. Uyuyu at his level wayesesa koma he could’ve done better!
Absolutely 💯
Nanga what is mcp yopanga apoint nzungu kukhala ambassador nziko lake lomwe
Interview yake yaziii kumawuzana zogula nsomba zowona
Panga yako zoba
Mbamva iwe usatchule mulungu
Loss of my bundle, this interview uhhh
Yamugaya interview
Paja a DPP akawina amaiwala adani awo. Komanso amaiwala momwe adutsa. Ulendo uno muphunzire.
Thus interview ndi tea weniweni, panja 😂
Mai ulemu wanu. Chowonadi sichiposa pamenepa, kungoti Malawi nsanje. Mtolankhani ntchito yabwino mwagwira. Onyoza mulekeni ndimomwe anabadwira.
Mayi wabodza uyu
Chnyengo sichidali pa tip-ex pokha komaso ma figure ena Ena sama gwirizana
Interview yoipa ngati iyii sinayivelepo ndithu 😂😂😂
Aah DDP in this country again
Chilombo cha mai ichi kulankhula bodza ngt sadziwa mau a Mulungu
Poor host,poor questioning n failing to control of program
Interview yopanda pake iyi kungotayitsana nthawi ndi bundle
Koma ndiye
Mai mulungu akusamalileni kwambiri chisankho munayendesa bwino ndithu Koma anthu amafu kuika satana pampando Tonse amene tinanyoza maiwa mulungu atikhululukire ndithu
Guys what is DDP?
DPP is a winning party please tell your children right now kuti asadzakhaleso makape ngati iweyo.
😂😂😂😂😂Koma ndiye kuyankha
I don't think this interviewer guy watolapo kanthu pa zonse zayankhulidwazi Mmayizi mbwelela zakezo angomphwanya phwanya
Munthu olimba mtima mwa umfiti uyu.
Tililonse
Wabweraso mukazi wapitala mbava we
Kodi guys mumafuna kuti munthu afunse bwanji ?inuyo mukuganiza kuti Steve akanaziwa bwanji mafunso amene muli nawo inuyo mmutu mwanu mmmmm chilichonse kungolowesa ndale basi inuyo ngati munthu akufunsidwayo simunagwilizanenaye bwanji osangokhala chete, inuyo munthu ngati ameneyi kukumananaye kuti achedze naye mukuwona ngati pamakhala masewera kuti akupase mpata mmmm ayi guys
Mayi wabwino Inu mumalikonda dziko lino
it's not easy to kubela chisankho, ma monitors aja sangalore mpang'ono pomwe
Galimoto yomwe imakathilidwa mafutayo mmesa ndi yanu yomwe nde simmadziwa kuti mafuta mwathila ochepa
Aaaaa nde sunamvetuu ananena kuti akukathila mafuta as a way to escape from pipo kuti asawapange notice ndimomwe amakachosa ma number plates
mau a akulu akoma akagonela😂
Khani inakula ndi politics
She is really a good woman
In a true sense this lady did a good job. If you compare 2019 and 2021 figures, the results were the same. I think DPP won
God bless you mama
Amalawi tinangoyenera mayiyu kumpasa ulemu coz adanena kt amalawi mwanditukwana ,kundinyoza ,kusabwaza banja langa km one day mzakumbuka mau anga by Billy kaunda lero ndi izi sugar tikugula 5300
Exactly 💯
Mai amalikonda ziko uyu
What a poor interview. A waste of my time and data
Mai odekha
This is worst interview ever
Omwe ankapita kumakanena kuti nkhati siziyenda bwino pakhesedwa mwadzi anali chakwera.
Akungodzikolaso polankhulaNawoso ofusa ndiye panja penipeni.
Next interview kondwa uzamusiyire wina and I wish Brian Banda atapanga interview this lady
Everything is a journey, we can NOT just have Brian Banda forever. Steve will learn and get better with time.
May God bless you mam adani anu awonekera ng'amba mulungu wakumenyerani nkhondo.
Yes she is a good women
Steve Kondwa Banda ngt mkotheka gawo lachiwiri udzasiyire wina osati iweyo.sutha kufusa mafuso
Palibe tamvapo
Nanga kumangomva mayina azibale basi
Kkkkkkkkkkkkkk host kom samapanga control mpaka akambe zonse zakunyumba kwao😅😅😅😅😅
😂😂😂
Good interview
Izi tinadusako kale ndipo Court linamula ndipo tinavota kale zisiyeni izi
I wish it was brian banda interviewing this lady.
Kwambiri uyuyu ananyika
@@MalawianCamerasamafusa mafuso oyenerela.
Chifukwq cha... know kuti aliyense Ali ndi ma technic yake yoyendetsera zinthu zake
@@KeithPMaliseroJr Do you think you have heard all that you wanted to hear from Jane Ansah?. Uyuyu at his level wayesesa koma he could’ve done better!
Absolutely 💯
Nanga what is mcp yopanga apoint nzungu kukhala ambassador nziko lake lomwe
Interview yake yaziii kumawuzana zogula nsomba zowona
Panga yako zoba
Mbamva iwe usatchule mulungu
Loss of my bundle, this interview uhhh
Yamugaya interview
Paja a DPP akawina amaiwala adani awo. Komanso amaiwala momwe adutsa.
Ulendo uno muphunzire.
Thus interview ndi tea weniweni, panja 😂
Mai ulemu wanu. Chowonadi sichiposa pamenepa, kungoti Malawi nsanje. Mtolankhani ntchito yabwino mwagwira. Onyoza mulekeni ndimomwe anabadwira.
Mayi wabodza uyu
Chnyengo sichidali pa tip-ex pokha komaso ma figure ena Ena sama gwirizana
Interview yoipa ngati iyii sinayivelepo ndithu 😂😂😂
Aah DDP in this country again
Chilombo cha mai ichi kulankhula bodza ngt sadziwa mau a Mulungu
Poor host,poor questioning n failing to control of program
Interview yopanda pake iyi kungotayitsana nthawi ndi bundle
Koma ndiye
Mai mulungu akusamalileni kwambiri chisankho munayendesa bwino ndithu
Koma anthu amafu kuika satana pampando
Tonse amene tinanyoza maiwa mulungu atikhululukire ndithu
Guys what is DDP?
DPP is a winning party please tell your children right now kuti asadzakhaleso makape ngati iweyo.
😂😂😂😂😂Koma ndiye kuyankha
I don't think this interviewer guy watolapo kanthu pa zonse zayankhulidwazi Mmayizi mbwelela zakezo angomphwanya phwanya
Munthu olimba mtima mwa umfiti uyu.
Tililonse
Wabweraso mukazi wapitala mbava we
Kodi guys mumafuna kuti munthu afunse bwanji ?inuyo mukuganiza kuti Steve akanaziwa bwanji mafunso amene muli nawo inuyo mmutu mwanu mmmmm chilichonse kungolowesa ndale basi inuyo ngati munthu akufunsidwayo simunagwilizanenaye bwanji osangokhala chete, inuyo munthu ngati ameneyi kukumananaye kuti achedze naye mukuwona ngati pamakhala masewera kuti akupase mpata mmmm ayi guys
Mayi wabwino Inu mumalikonda dziko lino
it's not easy to kubela chisankho, ma monitors aja sangalore mpang'ono pomwe
Galimoto yomwe imakathilidwa mafutayo mmesa ndi yanu yomwe nde simmadziwa kuti mafuta mwathila ochepa
Aaaaa nde sunamvetuu ananena kuti akukathila mafuta as a way to escape from pipo kuti asawapange notice ndimomwe amakachosa ma number plates
mau a akulu akoma akagonela😂
Khani inakula ndi politics
She is really a good woman
In a true sense this lady did a good job. If you compare 2019 and 2021 figures, the results were the same. I think DPP won
God bless you mama
Amalawi tinangoyenera mayiyu kumpasa ulemu coz adanena kt amalawi mwanditukwana ,kundinyoza ,kusabwaza banja langa km one day mzakumbuka mau anga by Billy kaunda lero ndi izi sugar tikugula 5300
Exactly 💯
Mai amalikonda ziko uyu
What a poor interview. A waste of my time and data
Mai odekha
This is worst interview ever
Omwe ankapita kumakanena kuti nkhati siziyenda bwino pakhesedwa mwadzi anali chakwera.
Akungodzikolaso polankhula
Nawoso ofusa ndiye panja penipeni.