KODI NDE MWATI MALAWI AKUPITA KUTI? GULU LA AMAI AWALAUKILA CHAKWERA POSANKHA CABINET MOWANYOZA AMAI

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 21 янв 2025

Комментарии • 27

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 19 дней назад +7

    Ngakhale mutakhala azimai 90% ntchito yao ndikumvetsera ndi kuombera mmanja. Azimai a kumalawi anakaganizabe ngati ma house wife.

  • @dumisanijonazi8355
    @dumisanijonazi8355 19 дней назад +5

    Zauchitsiru olo a balance zimathandiza chani?

  • @BakhePaliso-h8h
    @BakhePaliso-h8h 19 дней назад +1

    APM my vote

  • @FosterNtonya
    @FosterNtonya 17 дней назад

    Akunenazona pitemuthalika Poti dimaumadana ndikunika

  • @PetersKondana
    @PetersKondana 19 дней назад +1

    Uyotu uyo si wa DPP koma ndi wa chikangawa

  • @JoelTchuma-g3s
    @JoelTchuma-g3s 16 дней назад

    Akupita ku Bagamoyo

  • @viennasamuel2976
    @viennasamuel2976 19 дней назад +1

    Mavuto aziphaso akumamveka kum'mwela kokha bwanji?

  • @AyasiWhite-l6s
    @AyasiWhite-l6s 19 дней назад +1

    President ofoira uyu mxelu kuchita kumuposa Joyce banda mzeru

  • @ChristopherManase-s1f
    @ChristopherManase-s1f 18 дней назад

    Ma cadet awa inu. Ndani sakuwadziwa awa

  • @FosterNtonya
    @FosterNtonya 17 дней назад

    Chakwerandiopa siwabwino agosiyaba

  • @AyasiWhite-l6s
    @AyasiWhite-l6s 19 дней назад +1

    Mcp chipani chokumpha chilima ndi kasambala plus 8 people

  • @SteveKamwendo-wi8to
    @SteveKamwendo-wi8to 18 дней назад

    Chakwera ndi president owononga

  • @viennasamuel2976
    @viennasamuel2976 19 дней назад

    Kwinako nditukwana mwakhala chete nthawi yonseyi kani mulipo? Olo atawaika m'mipando akupanga chani? Zaziii

  • @YohaneDossi
    @YohaneDossi 19 дней назад +1

    Zauchitsilu basi gender yakuti,ndi president UTI amene anasankhako ma minister 50 50 amai ndi abambo basi mwamuwonelera chakwera popeza samakutankhani agalu inu kwambiri

  • @miraclejohnphiri7687
    @miraclejohnphiri7687 19 дней назад

    Zimafika thawi yot olo mutayakhula sizingamveke ndalama zikachuka mutu umasiya kugwila

  • @BakhePaliso-h8h
    @BakhePaliso-h8h 19 дней назад

    NRB mutisamare musatikhomerere

  • @BisiyeleJanuary
    @BisiyeleJanuary 19 дней назад +1

    Mumakokomeza kwambili mukumasiyanitsa bwanji kod malankhulidwe anu

    • @EvansEgra
      @EvansEgra 19 дней назад

      Wokonderà awa,amangobweretsa za uchisiru za Dpp, ,Akufunabe kuti u hifwamba opha ma Alubino udźayambenso

    • @ElizabethMajiga
      @ElizabethMajiga 18 дней назад

      Inde bola wokupha ma vp wa alibwino😂😂😂😂omatigonetsa ndinjala

    • @MariaNkhata-i9q
      @MariaNkhata-i9q 18 дней назад

      ​@@EvansEgravuto ku chikangawa kuja sizocheza

  • @wadyazakealibemulandu
    @wadyazakealibemulandu 19 дней назад

    Mcp ndi manyi okhaokha ikununkha

  • @BIZIWECK
    @BIZIWECK 19 дней назад

    🤰🤱

  • @WisdomMoyo-j9t
    @WisdomMoyo-j9t 19 дней назад +2

    Anayamba ndi amuthalika kuononga dzikoli ndichifukwa chake tinawachotsa,nde atsanamidze anthu kt azawathandiza anthu

    • @ElizabethMajiga
      @ElizabethMajiga 18 дней назад

      Ngati anayamba ndi Peter iye bwanji osakoza ,,,,unali usana kule mwana timadyatu ife ndi Peter

    • @EvansEgra
      @EvansEgra 18 дней назад

      @@ElizabethMajiga Umadya nchiyani? Nanga munamuchotsera nchiyani

    • @MariaNkhata-i9q
      @MariaNkhata-i9q 18 дней назад +1

      Iwo anabwela kuzakonza koma apanga mess bolanso muthalika 😅😅😅😅😅😅

    • @FosterNtonya
      @FosterNtonya 17 дней назад

      Iweso ndi vi waboza was mcp ndiye to wanongakwambili chimene akuchita sakuziwa mumangofunakubabas mukuanamizila kutidpp inawononga zaboza anonga ndiamcp bomalakhaza gatimfiti gatimkazi mwalanda timayesa kutimsamala kuposa mamuna wakaleyo komamwalephela akukumbukila wakaleyo kusonyezakuti palibechomenemukuchita amcp 0/precent