Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
Guys give us were we can put little bit money for all you guys
WhatsApp 0991467764
Exactly
ndifundo yabwino
Mbambande tonde wadura. Kmano muyesese muziyambira pamene inathera ngat momwe amachitira azanu kma sewero iyi ndi#1❤
mumatha kuceza kkkkk
Amapanga kale mu intro
Komad Gaga mwamucedwetsa kamumangiren den kwao ya self hahahaahah😂😂😂😂
Jazila and Gaga daily kukangana, koma kabanja kameneka kazachezako khani zoseketsa
nane ndimadabwatu Kodi naweso umaziwona
Mai Phiri muphunzitseni Nagumbo aidziwe Bangwe asiye kunyazitsa mwamuna wake. Ndipo muipeperere akwatirane amenewo 😂😂😂😂
❤❤❤❤❤ yakoma pamenepo mukubwera bho sizochedwesazija
Koma anagumbo aaaah achibiliti ake ati😂😂😂😂😂😂😂
Chonde jazila kammangilen nyumba gaga mwamtayisa nthawi 😂😂😂😂
😂😂😂 Gaga sazatheka serious😂😂😂
Mwini mimba ya chisomo wapezeka ndi muthinda 😅😅😅😅
Mayi mphili mumakwana, anakhumbo zawawa😅😅😅
Kkkkk mai phiri kavuwevuwe2 kkkkkk
Gaga saundila afuna nyumba 😂😂😂😊
Big up guys mumaitha and ndinu number one
Munthu amatha kuswedwa pakhomo pake pomwe...😂😂
Mole amatha acting 🔥
Asernal pa kwao kukwapulidwa 😂😂😂😂
Muthinda mpakana ankolo anu anthu kumawakawira fertilizer mu munda kkkkkkk
Kkkkkk koma nagumbo kkkk ati ndikhoza kukupondani kkkk
Achiswa mundisamale fetereza kukawidwa ah ayi😅😅😅😂😂😂😂
Kkkkk koma chiswanthaka mmmm mpaka kukawidwa fertilizer mmmm bodza linali
Present from Mozambique 🖐️
Big up
Here we go with episode 102. Am second viewer today
Hello Malawi
Kkkkk akwatile mai Phiri chibiliti
Komatu Gaga anayamba kale kumuthamangitsa koma olo tsiku limodzi sanachokepo...😂😂😂
Mai phiri muwakomola anagumbo kkkkkk
Gaga oyeeee kkkkk Wakumana ndi che yusufu
Feteleza amakawidwa amangosiyako pang,on bc🤣🤣🤣🤣
i just love the mai phiri vs nagumbo part...... well articulated ................... serious acting
Gaga safuna kusiya katundu wake, mlesi gaga wachabechabe
Mumatha magaye ❤❤
Koma Achibiliti siizinthu aarh🤣😅 nkhani ija mpaka akaing'alula kwa madam 😂😂
KOMA MUTHINDA KKKKKKKKKKKKKK
mwini mimba ya chisomo wapezeka ndi muthinda 😅
Mumasangalatsa pa nyumba pathu,eeh timachita kudandaula nthawi kuchepa,kuno Ku Zomba
Mayi phiri mwayankhura chilungamo ❤❤❤ anagumbo matama kkk mwamuna sitimaseweretsa 😂
Ngati inamenyedwa arsenal pakwao ndiye bas 🤣🤣🤣🤣
Gaga uziphitha 🤣🤣🤣🤣🤣
Achibelitu mayi phiri akukufunani 😂😂😂😂😂
Gaga km,, akufuna nyumba kwawo akt 😂😂😂😂,,,
We love you guys ❤
Chibiliti woyeeee 😅😅😅
Gaga talented man
Mayi phiri mabodza 😂
Anagumbo amandisangalatsa😂
Gaga ulesi koma kudya ndiku chipinda
You're the best guys
Kkkkkk mai phiri sazatheka
Ai gaga zikomo umakwana kkk
Umakwana 🔥🔥🔥🔥
Arsenal pakwawo kkkkkkkkkkkkkkk
Watching from TETE moçambique
Timafina tionele ndeu aaaa
mayi phiri amasuleni anagumbo achibiliti ali mu chibiliti cha macheso koma sakudziwa kkkkkkk more fire 🔥 guys watching from Capetown
Tonde amandiwaza kwambiri mu clip yake
Mumatiwaza ngati zizibwera dele
Chiswa pa mankhwaala😂
Gaga ndi machine akufuna den 😂😂😂😂
Ukandimangila nyumba
Achimwene a Jazila mwadza inuyo
😂😂😂mwabebesa
Mole he know acting keep it up tikupempherera kut isakhale life in prison cos ndi mada kesitu😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Kuzangotulukila mjomba sopano
Komatu Mai phiri mzanuyo mumupangisa alowetu muthengo 😂😂😂😂
❤
Achibilit kumuthawa katundu 😂😂😂😂
Ndye mwati feteleza amak qa widwa?😮😮😮😮😅😅😅😅😅😅
Katundu wabwino😂
mutinda ankolo akubela
Achiswa bumbu😂
Yomweyo Gaga akakumangire nyumbayo basi akuchedwesa kkkkkkkkkk❤
Akuti kaya amati mdeya
Kodi Mr Ziveka ndi Mbiri akumana liti?
Mole Akita mbambande
Vuto mukumaphatikiza ndi zakele
Mamuna kufuna kumangilidwa nyumba😂😂😂😂😂koma Gaga ndi pumbwa kwabasi
Tonde wadula , best
Mai phiri ndi one
Mayi phili
Mbambande
😂😂😂😂😂
Kkkkkkkkkkk a Nagumbo sopano
Kod mumde ndi waxy K, mukut palibepo ubale iyayi?
thanks mabwana
Koma nganga eeeeee❤❤❤ amatha
Kkkkk 😂 kma yaaaaa akut wandichedwetsat
Che Yusuf wafika iweo kkkmmmmmm😂😂 kaya amukutcha kuti deya kaya gaga
Mole zamuvuta
Deya yemweyo 😂😂😂😂😂😂
Koma mayi phiri😂😂
keep going guyz
Gaga 💥😂😂
😂😂😂 akut deya
Tafika tiseke 😂😂
Gaga 😂😂😂😂😂
Banja la gaga 😂😂😂
Akolowa amakhulupirila za ufiti kwambiri akubela malumeyo
Koma gaga
Yusuf,,, akt Kaya amakutchula kt deya Kaya gaga km 😂😂😂😂😂.
Yalakwa basi akuti kaya kwanu amakuti deya

Ndye mwati feteleza amak qa widwa?😮😮😮😮
😅😅😅😅😅😅