I can see a leader in Kabambe, koma chofunika akuyenera kupanga ziganizo za kuya pa polical act yawo since next year ndizovuta chipani kuwina chokha atamemeza zipani zina zing'onozing'ono ndi zazikulu zomwe kuti ziwatsatile ndikuyenda nawo ngati mtsogoleri ozakhala pa ballot zizayenda ndithu. Learn and grow from the mistakes of the Tonse alliance regime komaso find a way to discipline the vice President, Ussi. Bring him to justice and show him nobody is above the party constitutional laws be it the president or any other leader otherwise wishing you nothing but the best. All we want is a better Malawi for us and those after us❤
Kabambe to be crystal honest with you sir, just make an alliance with dpp to push this MCP regime out,I'm mean if you do your politics for the sake of welfare of poor Malawian s over your personal interests.
United we stand sir, divided we all fall sir.

Amene Ali ndi nzelu akudziwa kuti munthu amene angawombole Malawi ndi DR Dalitso Kabambe
Fact❤
DK my vote mesaaaaa
UTM my vote ❤❤❤❤❤
Viva utm🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Pa utm palibe kusuthika ine my vote 🤝🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥 kabambe
Chipani ndi chomwechi ndipo sitikusintha
Kabambe boma atenga kumene maboma enawo tawaesapo koma manyaka alipanowo ndi 0,2025 achoka basi anthu oipa
Akufuna kuimila u Mp osati u president
Muchila akulu
@@ElizabethMulindeakumwa panado mutu odwal ena
DK my vote
Muchine a utm kabambe is a nice guy
Anthu akukunda manganya
❤❤❤❤❤❤❤ vote
Munthu amene anayambika mavutowa Ndi kabambe
Ndwe kape satana wakoyo osawathesa bwanji Engonga
More fire bwana
Utm ndiimeneyo kodi
Palije zelu apo mwasowa kumalawi uko ndinu apenga kwambiri chilima yane anaero boma ndi dpp basi
Mmmmmm nanu zopanda tsogolo izi iyaaa,tazionani dzipani zokwera kkkkkkk
Democracy
Tayambani pa mp osat u president mufuna mutiike madxuwa?
Kagwere UTM my vote ❤❤❤❤
Dk my vote
Mcp my vote
Kabambe to be crystal honest with you sir, just make an alliance with dpp to push this MCP regime out,I'm mean if you do your politics for the sake of welfare of poor Malawian s over your personal interests.
Kabambe is waisting his time. Akanakhala Ku dpp konkuja
Zako izo usova ku adpp kuli chani???
Moti inu mukupindula ku dpp ko😂😂😂koti zipani zonsezi zikupanga westing time kom dpp😂😂😂
Kabambe ndiwa dpp kumene
Democracy
@LinlyMateti eti inu simantha awa
Think twice sir ,why I'm I calling you to form an alliance. It will also save the cost of rerun elections.
Don't rush zimenezo can't you see za alliance angotigwilitsantchito
Akabanbe asavutke sangatenge boma olo zitavuta
Ovota ndiwe wekha???
Akuona Ngati ndiyekha uyu
Ovota tili chete
Mcp 2025
Do you not go alone as UTM no,form a strong coalition with DPP,Aford,if you think better for poor Malawian s.