Размер видео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показать панель управления
Автовоспроизведение
Автоповтор
I like the confidence of zinveka eeeeesh amaoneka osatekeseka kkkk.komanso atakhala contractor akhoza kukhala tambwali kkkkk
Banjadi ndi anthu awili,ndaonela LA gaga kkkkk APA pali chikondi cha nyoooooo
Amfumu awa NDE safuna chabwalo eti kkkkk
abale tonde yu kuchedwesa chochi bwanji pakana mwezi mwasiya
❤😂😂😂😂😅 we love you
Gaga apa banja walipeza kungositha bas makhalidwe
😂😂😂😂 musamuchite nkhanza emmah achamila 😂😂😂
Musamuchite nkhanza emmah achamila 😂😂
Next please
Emma kuyela anatenga bambo ake 😂😂😂
Wachiyawo akundiwaza kwambili 😂😂😂😂😂😂😂
Ndipo kuchedwetsa kwake atondewa mmmmm kulephela kudikila
Gaga akuti alindima cotation atutu😂😂
Jazillah wapeza mamuna😂😅😊
Kodi muli pa ntchuthi mpaka ma sabata awiri tizingobweleza za kale abale mmmmmmmm
🔥🔥🔥
I like this drama all the way from south Africa guys keep it up ziveka ndi Dolo basi
ka ntchito ka muthindakotu kalibwino
Kodi episode ina nde tadikila koma kuli ziiiih
Komatu Emma
29:04 Gaga vs jazila
My born again 😂😅
i like love play proceed doing so
Koma Mwana Wa Muthidwa Emmah😂😂😂😂😂Anabwera kudzakhala keep it up🎉
ZIMVEKA UMAKWANA KKKKKKKK
Gaga maboza too much 😂😅
Mulamu Mulamu 😂😅😅😂
Zavuta kwa Gaga uku
Mnyamata wa nagumbo 😂😅
Emma akuti akumandipangira nkhanza kusamba kawili pa tsiku ngati chamadzi 😂😂😂
Wamakhwala heavy 😅
Even the tone would make u feel comfortable
Amalezera ameneyo 😂😅😅
Sakuziwa gaga 😂😅😊
Madeya /Gaga 😂😂😂
Tonde mpaka 1week 1 day without new episode, zatani Ku likulu??
Kkkkkk Jazira nomber 1 kutetedza mamuna alowera kuti munthu wasiye shehe musiyeni ndi mulamu wanu ameneyo
Akuti ku police amawopako😅
More 🔥🔥🔥🔥 guys keep it up 💪💪💪💪💪
Best is *Tonde* followed by mdyangu😂😂😂😂
Akunama ameneyo palibe ganyu yake
Hahaha gaga❤❤❤
Next plz 😊😊😊😊😊
Anthu inu kuchedwa chonchi bwanji?
Gaga akuti anadya chisoso
Kkkkkk
Dzina la Gaga linachoka ku Mzuzu kkkkk gaga kadzikwedze bas
Mr Zimveka mumasuleni Gaga
Jezillah Ali muchikondi sangave china chilichose ameneyo wadyesedwa bazi
Tonde alikuti😅
0:25 koma part ya 105 ituluka?
Gaga ndi Zimveka mmm akupatsidwa nthawi yochuluka pa zinthu zimodzimodzi, why? Interest ikumachokatu choncho
Ndipo zooona zosabebaso
I support
Gaga odzingoimba Kwathu sipadziko
Gaga 😂😂😂😂
😂😂😂😂😂Emma kuyeradi ngati bambo ake
Gaga born again
Jazira achiwene anu akukundani Gaga achoke bs
Yayambika kkkk
anakupatsa dzina la Gaga nindani 😂😂😂
Kod Muthinda umagwra ntchito yanji ubwana umnewu
EMA anasowa bwanji 🎉😅😂😮
Ma dolla asowatu
More fire guys
Kkkkkkkk
Waiting ndione kut gaga zamuthera bwanji kkk nanga silent killer okupha chifuniro zimuthera bwanji kkkkk
Zaveka kuti zinveka ndioveka Ali bhoo amandivesa kukoma
Gaga mwana wa masiye 😩😩😩😩😩😩😩
Hello
Nkhanza kwa Emma
Waiting guys
Asaa
Gaga akufuna ganyu 😂😂😂
Mfumu iyi ndimaikonda
Gaga tsopano mh 😂😂😂
team yosakhumudwitsa
Tafika ife basi
Mwana aliku town kwa bambo ake😅
bwanji ma guys tikudikila siikuoneka plz guys
Dora ndizakwatira
tiyambanapotu😂
Kkkkkk ndinagwira kaletu
tangopitilizan ndi Chiso yemweyo maniii, mesa mwampatsa kale pathupi mundisiyile ka Dora kangako😂😂😂
Tapangani tichape nawo mmeso
Gaga wapeza nkazi wabwino usinthe olo ulibe ndi mpando womwe Aljazira wakukonda.
❤❤❤❤ guyz
Dora umakwanila pa business Yako ya mowa
Muthinda wagwa nchikondi kkkk
honestlly kkkk
Kudikilila mwachete
Kamtima dyokoduokotu apa kkk
Tikudikilira ife
Tayambani guy's
Mwayamba kachibwana moti data izingota zazi zilekeke
Mmmm kuyankhula kwabwanji uku
Kakolope nyanja Kato zikukuipira
Ndiposo😮
@@MayamikoNsabwe-v1xkuyankhula ngti kulibe mawa
🙄tafikatu
Gaga 😂😂😂😂😂😂