BON KALINDO LERO PA 24 AUGUST WAULURA A NDALE A SATANIC AKUTI NDIOMWE AKUPANGITSA NGOZI DAILY

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 28 окт 2024

Комментарии • 103

  • @potphermacheso6486
    @potphermacheso6486 2 месяца назад +14

    For all qhat is happening in Malawi if you are a true believer you can't blame anyone but the spirits behind any human being, komaso Malawi is no longer the same before Malawi was a God fearing nation but look now how wicked has Malawi became, social media youths wow!! ,God raised Powerful Man and women of God but gues what Malawi does ,is to criticize them that are all evil koma kwa asing'anga nde kwabwino kokaombeza nobody will talk ,Malawi my Nation remember where we are coming from and how God has been faithful years back nthaka yachonde yobala zipatso chakudya everywhere but now we are facing the anger of God ,let's go back to God for is only the solution ,remember we are also in the last days and do not forget what the bible says about the last days but the bible also says in 2 chronicles 7:14 if my people who called by my name shall humble themselves and pray,and seek my face and turn from their wicked ways then i will hear from heaven and I will forgive their sins and i will heal their land .Malawi come back to God .

  • @georgezaya1071
    @georgezaya1071 2 месяца назад +2

    Grace tchinga ananena kale asanamwalile amalawi mwaiwala kale

  • @DL2004-x9q
    @DL2004-x9q 2 месяца назад +2

    Exactly. Ndipo nde sikunati muyembekezele zoopsa zenizeni starting around October to 2025

  • @MaryChimowa-f8u
    @MaryChimowa-f8u 2 месяца назад +3

    Eksodo 22 vs18 musamulore wanyanga kunkhala ndimoyo Bon Kalindo mukunena zowonadi ofunika PEPHERO la oyela mtima osati mapephero Afitiwa ayi ineso ndimodzi ndikuima pogumuka kupepherela anthu aziko langa la Malawi.Bon Kalindo Ambuye akudze malire anu 🌺

  • @Walu-b9v
    @Walu-b9v 2 месяца назад +2

    ❤ i love bon kalindo poyamba anthu amakutengani ngati mkudya ndalama za anthu km fundo zazeru

  • @phillkaunda5623
    @phillkaunda5623 2 месяца назад +7

    Dziko Lili mmanja asatana. Malawi needs God 😢

  • @arthurprincenkhoma355
    @arthurprincenkhoma355 2 месяца назад +1

    It's a bloodshed time! Evil doers are at work....this isn't normal indeed smbdy is behind all this.Wat hurting 😭💔 moments are these! Accidents one after another.? Those that were seem to be Good pipo osadziwa kanthu but now into wicked practices.....Mulungu adzakuimbani mlandu for shedding the blood of innocent Pipo.

  • @violetpotani
    @violetpotani 2 месяца назад +8

    Zochititsa matha ndipo zosowetsa Chonena mm tathodwa ife ambuye imvani mapemphero athu

  • @BILLIATWESTON
    @BILLIATWESTON 2 месяца назад +1

    No we hardly ever see this before let God be God

  • @JamesGeosterMalikebuPhiri
    @JamesGeosterMalikebuPhiri 2 месяца назад +1

    Kalindo Mulungu amudalise bcz mawu amenewa anafunika kuyankhula azibusa or ma prophets, koma ali duu anthu a Mulungu.

  • @CorneliusSande
    @CorneliusSande 2 месяца назад +4

    Zoona tanse osauka tisale kudya masiku seven mayankho apezeka Mulungu wathu ngwa moyo.

  • @InnocentBanda-ze8de
    @InnocentBanda-ze8de 2 месяца назад

    Thank you Mr Bon kalindo ❤

  • @FlorenceSchorah
    @FlorenceSchorah 2 месяца назад

    May God hear our cry and prayer coz this things are not normal 😭🙏🙏

  • @CharityChikomo-hl1gz
    @CharityChikomo-hl1gz 2 месяца назад +9

    It's obvious dzikoli laipaa ngozizi siza normal and if we dnt stand together in prayer I dnt knw what is goin to deliver malawi

  • @RyleChole
    @RyleChole 2 месяца назад

    🎉zoona zimenezo a Bon koma nkupempheni kuti khalani mukudziwa chomwe mukuchita chifukwa akanganya amenewa si abwino

  • @ChifundohMitulo-bg2lv
    @ChifundohMitulo-bg2lv 2 месяца назад

    Lord of Mercy please hear our prayers 🙏

  • @ChrissieMakombe
    @ChrissieMakombe 2 месяца назад

    God help us

  • @lyiemanganjira9708
    @lyiemanganjira9708 2 месяца назад +1

    OH Lord,, hear our prayer. Malawi is crying

  • @WarriorKB-u3k
    @WarriorKB-u3k 2 месяца назад

    Dats tru mr chikangawa ndi wa satanic , ngozi zonsezi MCP ikudziwapo kanthu ndichifukwa ndimanena kuti nonse mudavotele MCP ndinu dzisilu mukuphetsa anthu

  • @Aqiec09
    @Aqiec09 2 месяца назад

    Khani ndi mapephero basi Inu akalindo musatinamize ununso mukudziwapo kathu mfiti imadziwana ndi mfiti izake izi azituza ndi athu amulungu kuti awunje nda mfiti osati Inu oti mulanali limodzi kundale khani ndidyela chabe kagwereni uko

  • @ElizaMichongwe
    @ElizaMichongwe 2 месяца назад +3

    ambuye atithandizile izizisizowona ai zikupasa mantha kuyenda

    • @DzenzaSoliya
      @DzenzaSoliya 2 месяца назад

      Absolutely right and amen TODAY IS SUNDAY GO TO CHURCH 👇
      👇👇👇m.malawi-music.com/download/index.php?song=23635&t=9db9ce0d632cbd00957cf3ba289ff2df66cade4d3b381

  • @MchachaGoodson
    @MchachaGoodson 2 месяца назад +3

    Bon Kalindo bwanji mwana woopsa.audzeni awa amithenga ya satana nyansi ku Malawi.

  • @ChrisEdoh-i7i
    @ChrisEdoh-i7i 2 месяца назад

    Kumalawi kukufunika kusamusa athu ena sakuyenera kukhala malawi akasake kokhala in Jesus name

  • @EmmanuelPande-k5q
    @EmmanuelPande-k5q 2 месяца назад +3

    Nkhondo iyi siyolimbani ndi mwazi kapena thupi,koma tikulimbana ndi mphamvu ndi maulamuliro akumidima. Mulungu atichitire chifundo osati kuloza kapena kupanga mademo.Pephero ndi la mphamvu

    • @asamzymw571
      @asamzymw571 2 месяца назад

      Ndichifukwa tili osauka kaganizidwe akaka

  • @Geraldmkwewu
    @Geraldmkwewu 2 месяца назад +5

    Chikangawa ndi yudasi manganya atangopha chilima zose zinayambika pompaja ngt sitisamara titha amalawi bushiri pano sakugawa kamba ndichakwera ambuye tithandizeni ana anu tachepa lfe ndi bushili ndi chikangawa Lazaro fiti lzi asatanic😢😢😢

  • @babranzima8120
    @babranzima8120 2 месяца назад +2

    Thanks us true

  • @DeenesNurudMeke
    @DeenesNurudMeke 2 месяца назад

    Ndipo tisapusisike ndi anthu amene akuzitenga Opempherawa ndithutu

  • @ThomasBlessings-j8k
    @ThomasBlessings-j8k 2 месяца назад

    Ma prisons onse atuluke akalowemo anthu 6 chakwela ndi anthu ake munthu woyipa chikangawa

  • @SamuelMakonokaya-h8p
    @SamuelMakonokaya-h8p 2 месяца назад

    Akalindo mutulutseso report la alubino ankaphedwa nthawi ya DPP ija

  • @PeteriMangani
    @PeteriMangani 2 месяца назад

    We need to do fasting prayers

  • @NatashaBema
    @NatashaBema 2 месяца назад +3

    Masiku omaliza ili koma Chakwera wationetsa nyekhweeeee

  • @WarriorKB-u3k
    @WarriorKB-u3k 2 месяца назад

    Kalindo akunena zoona this is not normal presdent mr chikangawa ndi wa satanic nde amene akupangitsa ngozi zonsezi akubweza ngongole ya bushiri dziko lili mmanja mwa satana let's vote him out wationongela dziko

  • @ehinsupport3217
    @ehinsupport3217 2 месяца назад +1

    Akalindo ndinu mbuzi kwabasi. Inu umunthu mulibemo. Iweyo Kalindo ndiwe satana wotherathu

    • @ShabaniKuswere
      @ShabaniKuswere 2 месяца назад +1

      Koma iwe ndi mbuzi ndithu ndipo Mulungu akukhululukire kwambiri.

    • @edsongeorge8032
      @edsongeorge8032 2 месяца назад

      mbuzi ndiweyo aise wekha sungakhake ndichisoni ndimene zinthu zikuchitikira panopa uzikati bon kalindo ndichisiru God forgive you.

  • @DL2004-x9q
    @DL2004-x9q 2 месяца назад

    Nkani anthu ena akumalota akumawasainitsa ma contract a satanic these days 🙌🙌

  • @lungsTug
    @lungsTug 2 месяца назад

    Mapemphero akufunika ndithu nkhani ndiyowona koma izizi zawonjeza .

  • @IanAllstal
    @IanAllstal 2 месяца назад

    The D C Booooooon kalindo 🔥💪

  • @harrispheleni2205
    @harrispheleni2205 2 месяца назад

    Birds of the same feather flock together

  • @MangulenjeTwangu
    @MangulenjeTwangu 2 месяца назад

    Only God know's about

  • @VictorJaphet-z5l
    @VictorJaphet-z5l 2 месяца назад

    Bon kalindo saimira athu osauka Bon kalindo amaimira athu a Dpp asakunamizeni

  • @MonicaJohn-cx3el
    @MonicaJohn-cx3el 2 месяца назад

    Khaniyi ndiyona

  • @ehinsupport3217
    @ehinsupport3217 2 месяца назад

    Kalindo ulibe mfundo, ndipo takudziwa kuti umangotumidwa ndi azipani dzotsutsa

  • @MercyHassan-p4e
    @MercyHassan-p4e 2 месяца назад +1

    Zufunikira ma pemphero amphamvu komaso ma demo our president Bon karindo timakunyadirani kwambiri mukharise komaso ambuye azikudaritsani mkukupasani moyo wautari ❤🎉

  • @TembaniMwasanyira
    @TembaniMwasanyira 2 месяца назад

    Amen

  • @ClydeNyasulu-tk6fj
    @ClydeNyasulu-tk6fj 2 месяца назад

    😢😢😢komatu sakupanga bwino bwanji angofa okha😊

  • @TembaniMwasanyira
    @TembaniMwasanyira 2 месяца назад

    Amen amen

  • @AllanChabwela
    @AllanChabwela 2 месяца назад

    President wathu

  • @PeterPhiri-di1ux
    @PeterPhiri-di1ux 2 месяца назад +6

    tiyeni tika matche kunyumba ya bomayo osachokako mpakana chakwera atachoka pampando

    • @MasaMasina
      @MasaMasina 2 месяца назад

      Masewela eti.

    • @asamzymw571
      @asamzymw571 2 месяца назад

      Ndiouma mtima ameneuja atha kulamula a police atiombere

  • @babranzima8120
    @babranzima8120 2 месяца назад +1

    Zoona zake zamasatanic sotinazionepo zotero mmmm zovesa chisoni kwambiri

  • @JuliusKamoto
    @JuliusKamoto 2 месяца назад +1

    😭😭😭😭😭😭

  • @MaryBanda-n3h
    @MaryBanda-n3h 2 месяца назад

    Kwambri osakhulupira abusa ai koma timutulire namalenga

  • @ChomboNgosi
    @ChomboNgosi 2 месяца назад

    My dc❤❤❤❤

  • @yotamumahomed1313
    @yotamumahomed1313 2 месяца назад

    Koma ngat chakwera angadzawinenso iyoyo ndi nkhondo bas

  • @MercyChirwa-uj4ib
    @MercyChirwa-uj4ib 2 месяца назад

    Chakwera watiika pamavuto,sure. Mmmmmm

  • @lukechikondwa
    @lukechikondwa 2 месяца назад

    Koma amalawi tuyenela kuyima za serious in prayers

  • @PiliraniDanielDaniel
    @PiliraniDanielDaniel 2 месяца назад

    ichi chidatha supu ndithu, kupanga ndale ndingozi! Kodi sumadziwa kuti amalawi timadziwa kuti zonse umachitazi ndichifukwa choti Chakwera samakupatsa udindo m'boma

  • @RobertNyaude
    @RobertNyaude 2 месяца назад

    Mapangano aku dziko la mdima.

  • @DeenesNurudMeke
    @DeenesNurudMeke 2 месяца назад

    Esh ngozi zanji zochitika Daily esh

  • @GodfreyWhayo-hh1dm
    @GodfreyWhayo-hh1dm 2 месяца назад

    Ma prison athu ndi awanthu osaukafe . Anthu andarama akangogula bail kumakhala kutha kwa milandu yao . Amphawi tiribe kolowera .

  • @Yungjoe786
    @Yungjoe786 2 месяца назад

    That’s too bad eish

  • @EthelOsman
    @EthelOsman 2 месяца назад

    Inuso nde comment yopanda yesu inu nokha iweyo pakamwa pako posanukha mudziwe yesu amayi

  • @mwaisulaimana
    @mwaisulaimana 2 месяца назад +2

    Kumapeto kwa dziko..

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon 2 месяца назад

    Panopa simumganene za azibusa mziko la malawi WINAWE olo ukunenakuti osalozachala munthu ukunama of cause masiku otsiriza ndiye ananenakuti zizichitikira ku malawi kokha? AZIBUSA ambiri ku malawi anasiya kutumikira Mulungu akutumikira satana onse ndi ASATANIC kulibe mbusa oopa Mulungu ayi bon kalindo wayankhula bwino kuti tikadalira mapemphero azibusa tothapo tonse chifukwa iwo azipemphera kuziwanda zaozo mavuto sangathe koma ife tiime kutsutsana nacho choipacho

  • @chiletsokazembe-ri4ic
    @chiletsokazembe-ri4ic 2 месяца назад

    ziwanda zikuyenda dziko muno ndizaiweyo born kalindo chifukwa dziko lino iweyo sulifunila zabwino umafunitsitsa kut anthu tidzimenyana apa ukufuna udzilankhula ngati kut ndiwe wachifundo koma ndiwe munthu oipa kwambiri amene sukufuna kut anthu tidzikhala mwamtendele ndiwe munthu oipa iwe

  • @YvonneFombe
    @YvonneFombe 2 месяца назад +1

    Iweyonso uli momwemo

  • @JuniorSaine-d6r
    @JuniorSaine-d6r 2 месяца назад

    Some agreements are bad

  • @chiletsokazembe-ri4ic
    @chiletsokazembe-ri4ic 2 месяца назад

    inu aborn kod inu si asatanic? ngati sindinu asatanic nanga bwanji mumamemeza anthu kut ayambe kuyende pa nseu; kod zija mumatiuza kut tikamanche kod sinkhondo amenei? mukusiyana bwanji inuyo ndi wasatanic

  • @MaikNkhoma
    @MaikNkhoma 2 месяца назад

    😂😂iweniwopenga ndipo amene angakuvele niwopenga mzako

  • @AlinafeBockshen
    @AlinafeBockshen 2 месяца назад

    Zovuta kwabasi

  • @GraceLimani-zw7dx
    @GraceLimani-zw7dx 2 месяца назад

    A chakwera anazolowera kupempha Ali ku Church ndiye a kupempha za Nthumba mwawo shame on him

  • @EmmanuelMkata
    @EmmanuelMkata 2 месяца назад

    Sompano mwana wa Munthu awoneka

  • @JohnYoweli
    @JohnYoweli 2 месяца назад

    Dzilile wekha

  • @MaxwellDzaone-ym1vg
    @MaxwellDzaone-ym1vg 2 месяца назад

    Pakufunika m'bindikiro Wa mapemphero

  • @TakondwaSulani
    @TakondwaSulani 2 месяца назад

    Ndipo zoona tizililire tokha ndi ana athu

  • @StalloneButao
    @StalloneButao 2 месяца назад +1

    Kkkkkkkkk njinga kuipempha wachikulire

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs 2 месяца назад +1

    Eeeee zoopsatu kwabas

    • @OnnicahBanda
      @OnnicahBanda 2 месяца назад

      Ndipo zomvetsa chisoni ❤❤❤ chuma azidyera magaz anthu osalakwa

  • @MaryMalemia
    @MaryMalemia 2 месяца назад +1

    Tseka pakamwa ponunkhapo

  • @MosesMsiska-x2n
    @MosesMsiska-x2n 2 месяца назад +1

    Kodi Ngozi zayambira ku Malawi? Kodi Ngozi yayamba chifukwa cha boma la MCP? Chitsiru iwe otsatimenyetsa Mutu your hatelate will leading you to hell.

    • @listonnantapo1670
      @listonnantapo1670 2 месяца назад +2

      Ndege kuchikangawa inamenya mwala koma osayaka. Lero ikukayaka minibus chifukwa choomba galimoto imzake. Zoopsa.

    • @DL2004-x9q
      @DL2004-x9q 2 месяца назад

      Ndiyetu sunati azaziona aise. Vuto lake uchitsiru wa anthu ngt inu ndi omwe uzapangitse kuti mwazi wambili upite

    • @OnnicahBanda
      @OnnicahBanda 2 месяца назад

      Ulibe uzimu iwe sukuona km tiziti iwe

    • @OnnicahBanda
      @OnnicahBanda 2 месяца назад

      ​@@DL2004-x9qndipo zoona iye Ati kuva kukoma coz gweroli silinafikile nyumba mwake.....

  • @WarriorKB-u3k
    @WarriorKB-u3k 2 месяца назад

    Dats tru mr chikangawa ndi wa satanic , ngozi zonsezi MCP ikudziwapo kanthu ndichifukwa ndimanena kuti nonse mudavotele MCP ndinu dzisilu mukuphetsa anthu

  • @KondwaniMapota
    @KondwaniMapota 2 месяца назад

    God help us

  • @WarriorKB-u3k
    @WarriorKB-u3k 2 месяца назад

    Dats tru mr chikangawa ndi wa satanic , ngozi zonsezi MCP ikudziwapo kanthu ndichifukwa ndimanena kuti nonse mudavotele MCP ndinu dzisilu mukuphetsa anthu