ZOMWE ZAKAMBIDWA KU NSOKHANO WA AKULU AKULU AZIPEMBEZO 😱😱_26 December 2024

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 17 янв 2025

Комментарии • 201

  • @ObettoKamanga
    @ObettoKamanga 22 дня назад +5

    Nosense. Bishop Msusa amaopa Mulungu osati munthu. Kagwereni uko. Choonadi chimamasula. God sees mind you

  • @echitemaemmanuel3370
    @echitemaemmanuel3370 22 дня назад

    Bravo Arch Bishop Msusa...
    May Almighty YAHWEH bless and protect you..

  • @rabisonpias5131
    @rabisonpias5131 22 дня назад

    Dzidzukuru za Guru lija Lidapereka YESU kuti akapachikidwe nazuzidwa, Lidasamukira KU NYASALAND MALAWI 🇲🇼. Ena mwa iwo ndi awaa.
    VIVA Bishop MSUSA.

  • @ChristopherKadawati
    @ChristopherKadawati 22 дня назад +3

    Zayamba liti kuti ulaliki wa Mbusa adzichongedwa ndi gulu la azibusa amipinging yina?
    Mwalowerera za ndale ndi inuyo Atsogoleri.
    A Bishop amalalikira mu mpingo mwawo sanapangitse misonkhano wa Antolankhani.

  • @John-o5q1l
    @John-o5q1l 22 дня назад +2

    Useless faith leaders if at all muli atsogoleri . Bwanji simunangopita komweko nkukakamba naye . Why are you afraid of him ? Corrupt people will always talk nonsense like this. We believe and stand by what the Archbishop has said. Period.

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 22 дня назад +1

    May gud Lord almighty bless Msusa for ever

  • @Mervic-vm8eo
    @Mervic-vm8eo 22 дня назад +6

    Asatana Inu fotseki 😢😢😢😢 chikangawa party

  • @McdonaldChimwala-w9z
    @McdonaldChimwala-w9z 22 дня назад +2

    Tilikumbiyo kwa Bishop Msusa ifeyo.

  • @mathewssimbi3052
    @mathewssimbi3052 22 дня назад +3

    Ndipemphero Langa Kuti ndalama mwadyazo muwone nazo zowopsya pa mayo Wani IFA ija ikutiwawa mpaka pano

  • @PaulChibakuwa
    @PaulChibakuwa 22 дня назад +2

    Chilungamo sichiopa gulu, viva Malawi

  • @JoiceBwanali
    @JoiceBwanali 22 дня назад

    Azitumiki opepera osaganizira anthu awo,kuteroku akupatsani chibanzi,Mulungu akukanthen nonse,azibusa adyera.Viva bishop Thomas Msusa.

  • @JudithSikelo
    @JudithSikelo 22 дня назад +1

    Nanga sheheyu chibwibwichi bwanji?....komatu kunja kuno kuli mulungu......bravo bishop Msusa

  • @RexJeremiah-c9i
    @RexJeremiah-c9i 22 дня назад +2

    Akuru akuru ngati simukudziwa zomwe anthu akumvera kuwawa za imfayi aanthu akunyozani mukatha kulankhula zanu zachibwanachi pepani mulungu akukhululukireni nonse mukatha mukamverengazo . Bwanji mukaitane anthu omwe sadaitanidwe ku komishoni ija makamaka akumabanja kwa omwe adamwalira aja mukapeze zomwe akumva kuwawa

  • @RaphaelWinford-t7u
    @RaphaelWinford-t7u 22 дня назад

    Mumusiye Bishop msusa , zitsilu inu, mbuzi za atsogoreli, 😊😊

  • @SammyKalebe
    @SammyKalebe 22 дня назад +1

    Pangatalike maka one day is one day God is watching u.

  • @ThokoChimwala
    @ThokoChimwala 22 дня назад +1

    When David killed Uriah he thought it was done but God was on the scene he revealed every through Nathan one the truth will prevail money will fail.

  • @evansjohn7766
    @evansjohn7766 22 дня назад +1

    Abale ziwani izi,Yesu mwiniwake anane kwa atumiki kuti:muzawaziwa kuzera ntchito zawo,lelo musadabwe ndi azibusa amene adali mu Committe yofufuza za imfa ya VP,winaliense aona yekha mbali imene azibusa aja ali.

  • @RaphaelWinford-t7u
    @RaphaelWinford-t7u 22 дня назад

    Yakubayani. Zitsilu ifa sinakukhudzeni manyazi bwaaaa akapro😊

  • @RaphaelWinford-t7u
    @RaphaelWinford-t7u 22 дня назад

    Naye ndi munthu wayakhula ku mbali yake, Bishop God be with you take care.....

  • @stevenmwamadi3035
    @stevenmwamadi3035 22 дня назад

    Akupasani ndlama inu agaru inu mbuzi zawathu inu agaru wakutumani ndi chakwera akupwetekesani ndi crocodile wanuyo nonse ndi mbuzi ma carward nonse Allah amuteteza

  • @IsmailAhmed-i4l
    @IsmailAhmed-i4l 22 дня назад +4

    mwadya ndalama inu nonse Allah akupundani muwona wallah

    • @Titokachoka
      @Titokachoka 22 дня назад

      pathako panu anthu osaopa mulungu inu samalani ndmalilime anu anthu oipa inu

    • @LukaBenard-b4h
      @LukaBenard-b4h 22 дня назад

      Panyelo panu nonse anthu oyipa osangosiya ma udindo anu a uzimuwu a Nsusa palibe alakwisa ngati mwadya ndalama Mulungu akukuntheni ana anjoka owoneka opembeza

  • @DominicNantowa-t4d
    @DominicNantowa-t4d 22 дня назад +1

    Kwinaku nditukwana😮😮😮😮

  • @RaphaelWinford-t7u
    @RaphaelWinford-t7u 22 дня назад

    Afarisi ayuda inu zitsilu za atsogoreli mwadya ndalama mbuzi za wanthu , mumachitiranji zithu mobisa galu inu😢😢😢😢

  • @Dalsonchimlomo
    @Dalsonchimlomo 22 дня назад

    Amenewo ndi azibusa achinyengo ,kupha ndi dzisembwere. ndipo muno mulibe PAC kma agurukunyinda ,akhakhakha agalu mukuona ngat anthu adaphedwa kuchikangawa aja moyo sankaufuna bas ndisiye ndiyamba kutukwana

  • @RaphaelWinford-t7u
    @RaphaelWinford-t7u 22 дня назад

    Zitsilu za atsogoreli adyela mbuzi kwambili , kudana ndi chilungamo afarisi😊😊😊😊

  • @YusufChikweo
    @YusufChikweo 22 дня назад

    Asheikh ndinu azoba mwamva

  • @innocentwilfred-b5s
    @innocentwilfred-b5s 22 дня назад +1

    Welawela aneneye azibusa komanso mashe nizimuyanu kukuzuzulani kuti mukuchita zolakwika

  • @hastingskayange
    @hastingskayange 22 дня назад

    Azitsongoleri amane akulimbana ndi Bishop Msusa ndi amene akuchititsa dzikoli lidziwopedwa ngati ndi la kagulu kamodzi ndiposo amipingo inuyo mukutsutsana ndi Bishop Msusa ndine aziphuphu chifukwa nkhani ya mapemu Chilima mudakankhala kuti mumaopadi Mulungu bwezi mutalimbikitsa chilungamo pa nkhani gozi ya ndege ija.Ndiye pasakhaleso wina otsutea pa nkhani imeneyi chifukwa ndifeyo amalawi tikulira za ifa ya Chilima,ndipo ndinu zitsilu azitsongoleri okonda nyela...musiyeni Bishop Msusa apange zake zomwe akudziwa ....osamangodya ndalamazo bwanji

  • @RaphaelWinford-t7u
    @RaphaelWinford-t7u 22 дня назад

    Ayudasi....

  • @BrightMajor-h8l
    @BrightMajor-h8l 22 дня назад

    Mwadya ndalama ndiye muziti ndinu anthu amulungu?

  • @charlesmasauko4651
    @charlesmasauko4651 22 дня назад +1

    Ndi aGanyu awa isawamvera

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu 22 дня назад

    Za ziiiiiii! Makape inu mwatumidwa ndi Chakwera inu.

  • @RaphaelMabuka
    @RaphaelMabuka 22 дня назад +2

    Akulu akulu adyera ambuye akukatheni nonsense achikangawa party

  • @JrAlfeoLungu
    @JrAlfeoLungu 22 дня назад

    They are all captured

  • @ThomasSambani-h1k
    @ThomasSambani-h1k 22 дня назад

    Ndalama zomwe akupasanizo muzazivbweza ngati yudasi anakabweza kumanso anazipha yekha kwasala pang'ono ku ha muyaluka nonse

  • @DaudiAwali
    @DaudiAwali 22 дня назад

    Masheh kmad ndinu mashehd ndalamazo muayankha kwa mululngu

  • @EvinessBisalomu
    @EvinessBisalomu 22 дня назад +2

    Chikangawa party iyi

  • @GloriaChinkanda
    @GloriaChinkanda 22 дня назад

    Anthu oipa inu adakakhala mwana wanu. A Bishop ali pachilungamo. Mukufuna nkhani ithe posanena chilungamo.

  • @MphatsoChilangiza
    @MphatsoChilangiza 22 дня назад

    Agalu nosenu mulibedi nzeru ukuwelengawe chifukwa chake unagwidwa chigoloro

  • @RemsyChipani
    @RemsyChipani 22 дня назад

    Mbambande bishop msusa osafooka osaopa osatopa

  • @WillamLawson-gk1lw
    @WillamLawson-gk1lw 22 дня назад

    Awa ndi adyera

  • @EdwinJumbe-u5m
    @EdwinJumbe-u5m 22 дня назад

    Alfred mphote zinthu zinakuvutani,inu kodi ndi mtumikibe?azimayi aja mwasiya kuwavura

  • @luwizaoffley6848
    @luwizaoffley6848 22 дня назад

    Bishop wanena zoonadi koma enanu ndi oopa Satan osati Mulungu

  • @KestherMkandawire
    @KestherMkandawire 22 дня назад +1

    Bishop akanangonena kuti ndikufuna kudzakhala vp wa utm osati akulankhula zopusazo iyeyo ngati amadziwa kuti zoona akudziwa anatani kupereka umboni ngati akutsutsa zomwe anzake ananenazo ndalama wampatsa kabambe zakubazo ndizomwe zamuoangitsa wataya uzimu

    • @PasquaMapemba-my9mw
      @PasquaMapemba-my9mw 22 дня назад +1

      Usamale kumwamba kungakuyankhe uli pansi pompano aise, kunali gulu la mai manjamkhosi ndi amzawo adachita chimodzimozi 1992/93 ukulimbana ndikumwamba please say SORRY TO GOD. That's my advice you my dear friend.

    • @TamikaKaponya
      @TamikaKaponya 22 дня назад

      ​@@PasquaMapemba-my9mwati kufuna kutchuka kuti amatha kupanga comment...Mulungu amuone mwapadera ndithu

    • @JonesChingaya-yf4gg
      @JonesChingaya-yf4gg 22 дня назад

      Ngati ineyo zimandiwawa mpaka lero koma panalibepo m'bale wanga ndie kuli bwanji mabanja a onse ofedwa. Umuziwe Yesu wamva. Zimatiwawatu ndie ena azibweranso ndi mbwerera???

    • @PasquaMapemba-my9mw
      @PasquaMapemba-my9mw 21 день назад

      @@KestherMkandawire satana iwe usatiphepo mutu.

  • @praisemachokocha-dp1yc
    @praisemachokocha-dp1yc 22 дня назад

    But living God he knows everything, and Holy spirit never lie

  • @YusufChikweo
    @YusufChikweo 22 дня назад

    Iwe sheikh usamale tikupangila kabnet tikuthothola uzitenge bwino

  • @abdul-rasheedsalika
    @abdul-rasheedsalika 22 дня назад

    😂😂 Akt iyyyākum wal dhwanna, mmqso mwako iwe😂

  • @stevenmwamadi3035
    @stevenmwamadi3035 22 дня назад

    Tiri kumbuyo kwa bishop ndipo Allah adalise bishop nsusa

  • @FortunateChimwaza-j4r
    @FortunateChimwaza-j4r 22 дня назад

    Musamachite kuwelenga chonde,mwadyetsedwa banzi

  • @Kenmoney-xp7tz
    @Kenmoney-xp7tz 22 дня назад

    Anthu onsewa ndi a MCP ndichifukwa sizinachedwe kubwera pa press briefing... Malawi musadandaule ndi ntchito za ndale izi

  • @ArnoldSefasi
    @ArnoldSefasi 22 дня назад

    Eya ,abishop adanena zowina ndipo tili ku mbuyo kwa bishop,ndipo mukuwabakira ndi anthu akupha ndi chipani choti mbiri yake idayipa kale,mwachidure ndinu akanyimbi

  • @JohnAlisa-f4v
    @JohnAlisa-f4v 22 дня назад

    Wanena wanena basi sipabwelera ai zikuyenera kutipweteka anali nkatolika mzathu🎉🎉

  • @MuhammadNtauchila
    @MuhammadNtauchila 22 дня назад

    Eeeeshii Buddle yanga ine

  • @AustinNangwale
    @AustinNangwale 22 дня назад

    Komatu no matter how long it takes one day Fitiyo idzaziwika ndithu 😢

  • @Eric-gb9ms
    @Eric-gb9ms 21 день назад

    Anthu woyipa inu mukutsutsana ndi mulungu Msusa nd yekhayo wa mulungu

  • @RonaldGama-gz9ug
    @RonaldGama-gz9ug 22 дня назад

    Zauchitsiru ine ndi amene ndinali nawo kotumiza mitembo anthu aja iweyo ngati ndani mwapatsidwa ndalama kuti mufute chilungamo ofunika kuyamba kunderani makomo mwanu tsopano mwatitora agalu inu..

  • @TecnoPop3-k2c
    @TecnoPop3-k2c 22 дня назад

    Mukurimbana ndi mbusa osasusana ndi nthanyiwanwanji simukuyankhapo afitiinu chakwela manyazi amugwira

  • @BeatriceZimphango-iy7ee
    @BeatriceZimphango-iy7ee 22 дня назад

    Osapita Kwao mukauze bwa?

  • @Enock-gu5ff
    @Enock-gu5ff 22 дня назад

    Ine ndiririmodzi ndi ansusa komaso ndine ntumiki kuyankhura cirungamo ndi bwino zedi ngati cirungamo cakwiriridwa zimabweresa cisokonezo not cirungamo. Cirungamo cimango thandiza adindo kudziwa kuti sangapusise amarawi onse ai

  • @SimonBanda-b1f
    @SimonBanda-b1f 22 дня назад

    Andale akugwiritsa ntchito Abusa adyera
    Pangani zachilungamo ngati a Christu or ngati ma Muslim wowopa Mulungu.
    Azibusa adyera komanso Afiti

  • @MolesBrown
    @MolesBrown 22 дня назад

    Asusa alandila ndalama kwa munthalika ndipwake kabambe ana anjoka susa ndi satana

  • @ArnoldSefasi
    @ArnoldSefasi 22 дня назад

    Akupatsani zingati? Ndinu atsiru nonse amene munakumana ku mkumaniwu

  • @wisdomnkhoma-zl3qm
    @wisdomnkhoma-zl3qm 22 дня назад

    Inu ndinu asatana. Osadandaula ndi mizimu ya anthu adafa afa, Inu ambuye akuoneni

  • @ChristopherKadawati
    @ChristopherKadawati 22 дня назад

    Ngati Mulungu ali ndi inu mphamvu mwayitenga kuti?

  • @TecnoPop3-k2c
    @TecnoPop3-k2c 22 дня назад

    Aaaa inundemumaononga zikorino ndichifukwa chake aphesa anthu ambiri mazibusa opanda chirungamo satana

  • @NelsonSimenti
    @NelsonSimenti 22 дня назад

    Mbuzi zachabechabe, inuyo anthu olungama inu odzitcha asibusa okhudzidwa,akadakhala kuti ndi m'balewanu yemwe adafera kuchikangawa kuja, Kodi mphanvu zomayankhula motumbwa Chomcho mukadazipeza? Mulungu akukhululukireni

  • @PirlyzThom
    @PirlyzThom 22 дня назад

    Makhuta ndalama zamagazi agalu Inu wangongoyamba simunati akatolika simutikwanitsa muziona

  • @BrightMajor-h8l
    @BrightMajor-h8l 22 дня назад

    Nonse munasonkhana kumeneko ndinu zitsiru

  • @ObettoKamanga
    @ObettoKamanga 22 дня назад

    Si inu azipembedzo inu anzanu otumikira Mulungu wamoyo adatulukamo bwaa

  • @owenchikopa7266
    @owenchikopa7266 22 дня назад

    Kodi a Bishop Msusa ngati M'Malawi ndiye kuti alive ufulu olankhulapo maganizo awo. Iwo akuti sanakhutire ndi report lija. Uthenga ndi umenewu basi sitikusintha.

  • @JerasonBanda
    @JerasonBanda 22 дня назад

    Amalawi simungatipusitse pano MCP is evil watch their downfall God is cleaning them up anthu anafa ifa yochita kuwapangira , zimatiwawa u will face the music

  • @McdonaldChimwala-w9z
    @McdonaldChimwala-w9z 22 дня назад

    Anthu achinyengo awa kkkk

  • @GeraldChilundu-e3v
    @GeraldChilundu-e3v 22 дня назад

    Ambuye mulungu akuyendereni mwapadera inu mwadya ndalama kumapanga press conference iyi. Manyazi akupezeni koma simupita nazo patali

  • @PaulManyamba
    @PaulManyamba 22 дня назад

    Palibe chomwe mukukamba agwape inu ngati mwalandila ndalama ingopitani mukagule chimanga abale anu azidya musatiyankhuluse pambali plz

  • @VinGenerators
    @VinGenerators 22 дня назад

    Kodi blackbox lili kuti inuso azibusa mwakhuta ndalama zamagazi za chakwera kazikageyani ku state house komweko

  • @ChidaPhiri
    @ChidaPhiri 22 дня назад

    Walandila ndalama iwe ulibe chilungamo chitsiru simsilam iwe satana weni weni.

  • @AcctyhBuno
    @AcctyhBuno 22 дня назад

    Anthu amakhala akupempha kafukufuku kuti achitike monsemuja bwanji simumabwela poyela ngati mwabwelela apamu ndikuwauza apule nonsenu panyapanu sife ana adatana inu

  • @AlickDickison
    @AlickDickison 22 дня назад

    Zamisala basi mwatentheka nayetu nsusa zaziiii mwadya ma bunz uko

  • @TonyMhone
    @TonyMhone 22 дня назад

    Azibusa nonse mwakumana pa mtsokhano umeneu mwa inu Mulungu mulibemo. Ndikupemphera Kuti achite nanu moyenera machimo mukupangawo. Zitserekwete nonse

  • @Patgregorymanyumba
    @Patgregorymanyumba 22 дня назад

    Zopanda pake a MCP inu sinu amipingo

  • @TecnoPop3-k2c
    @TecnoPop3-k2c 22 дня назад

    Aaaa kupusa kuribwino kusapemphera chifukwa timakurupirira azibusa komaazibusao aphesa chirima

  • @StevieChilinde
    @StevieChilinde 22 дня назад

    Bolanso munakapanda kuyankhula Inu makape.kodi Malawi akupita kuti?musalimbane ndi nzanu inu.kodi tiziti akuluakulu Inu mitu yanu ndiyouma eti.sitizikukulupililani inunso.mwatitayila nthawi;mpakana kusonkhana konseko kumayankhula zopusa Ngati zimenezo?koma masiku osiliza tiona zinthu.

  • @AlexKihiye
    @AlexKihiye 22 дня назад

    Palibe walakhula wakhula kya inu wanu ndi mulungudi kma

  • @PasquaMapemba-my9mw
    @PasquaMapemba-my9mw 22 дня назад

    Ndinu anthu omvetsa CHISONI nonse muli apa. Mukayankha kumwamba ndalama anyamata inu zili ndi malipiro ake. ATAKUPATSANI UMBONI MUDZAYANKHA??? TIPATSENSONI MAINA ANU BWANJI NDI MIPINGO YANU NONSE MULI PAMENEPA. NDE INUYO POTINSO MUKUWELUZA INUYO KUWERUZAKO NDE MWAKUTENGA KUTI? KKKKK KOMA MALAWI MULUNGU ATIMVERE CHISONI NDITHU. AKATOLIKA!!! OSAOPA, OSAFOOKA NDIPO OSATOPA. Chilungamo chikatifikitse ku mparadizo. Mdzina la atate ndilamwana ndi lamzimu oyera. Amen.

  • @JohnZingapeta
    @JohnZingapeta 22 дня назад

    Patalike pafupike...chilungamo tizachiziwe ndithu

  • @GraciousGIbbu
    @GraciousGIbbu 22 дня назад

    Mwambi wake ndi menya galu kuti uone mbuyake

  • @FelixLivison-mk2cf
    @FelixLivison-mk2cf 22 дня назад

    Inuyo zikukomelani poti munapasidwa mamillion kuti musamasusane ndi president wanuyo kapangani only god knows and time will come.muzabweza mwazi umene ukuyenda dziko lathulo.

  • @allanimindozo9937
    @allanimindozo9937 22 дня назад

    Amisara inu mukuinangat Malawi ndí opusa et 2025 agalu inu amp azaku njatani agalu inu tsek

  • @aaronbamusi9802
    @aaronbamusi9802 22 дня назад

    Money Can buy anything

  • @McdonaldChimwala-w9z
    @McdonaldChimwala-w9z 22 дня назад

    Zinalizakale zimenezo.

  • @WesleyKalimwayi
    @WesleyKalimwayi 22 дня назад

    Koma ku Malawi kulibe azibusa patumbo panu

  • @AgnessKalindo
    @AgnessKalindo 22 дня назад

    Kma ma sheh ndi mazibusa muziyakhura chilungamo , dzanuyo anayakhura zoona ndi chifukwa chani mukusutsana naye mwalandira ndilama ndikumayakhura ma ntuzu chocho mumazitenga ngati ndani inuyo? Chipani chamagazi mukuchiyikira kumbuyo nonse machende anu . Chisokonezo cha chani? Iwo wooso zimene anachita ngakhale inu mukuziwa even ndi mene akumachita anthu amenewa mu kuziwona nokha ? Km inu allah azakulengeni ndipo inu Jehovah azakulengeniso . Ndi inu nonse opusa ndithu.

  • @BrendaKaole
    @BrendaKaole 22 дня назад

    Tayani nthawi bola chilungamo mukuchiziwa

  • @CassimMbalaka
    @CassimMbalaka 22 дня назад

    Zaziiiiiiii mwadya ndarama agalu inu manyi anu nose muli pamenepo

  • @bandaBanda-d5v
    @bandaBanda-d5v 22 дня назад

    Kupatsani ndalama zitsulo kwambiri panyapano

  • @benjaminmanda3202
    @benjaminmanda3202 22 дня назад

    Awa simaganizo anu achipembezo zikuonetsa kut achita kukulembelan mkukanika ndikuwerenga nkomwe mkanthidwa ndithu ndalama imathatu

  • @madalitsoonale5338
    @madalitsoonale5338 22 дня назад

    Kkkkk by just lukn at these pipo u can automatically conclude that they are mcp gurus agalu achabechabe awa

  • @EdwinZiwa-x2g
    @EdwinZiwa-x2g 22 дня назад

    Mukuzesa chisokonezo ndinu iye Kodi zakuwawani chifukwa wanene maganizo ake mwasowa zokamba agalu inu kodi

  • @DynaWilson-d1b
    @DynaWilson-d1b 22 дня назад

    Kulimbana ndi munthu odzodzedwa kuziitanila matembelero

  • @TecnoPop3-k2c
    @TecnoPop3-k2c 22 дня назад

    Tikurupirira bwanji azibusa anarephera kunena chirungamo pazimene anagwirizana ku alaanse.chakwera.ndi chirima.zisiruinu