2025 SEPTEMBER MWATI SITITHAMANGA?!

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 20 янв 2025

Комментарии • 207

  • @Mirriumkamwendo
    @Mirriumkamwendo 8 дней назад +1

    Chakwera akukakamila pa mpando akuopa mlandu opha chilima

  • @HopePangani
    @HopePangani 8 дней назад

    Ife si zitsiru akuyenela kudziwa zmenezo😮 ndpo ndpo mkumano umenewo unali wa ztsru kwambri chifukwa munthu wabwnobwno sangamakamblane zopusazo ndipo ndkubwela kwa iwe Anabello kaya ndiwe chumba kapena kt osabeleka koma dzwa tsku nd limodz Mulungu Wanga wamoyo azakukantha chifukwa chakusankha kwako kochtra nkhanza dzko la Malawi.Tithana inuyo smungapose Mulungu wathu ndpo szkutheka zmenezo in Jesus Christ.

  • @JohnPaul-r4u
    @JohnPaul-r4u 16 дней назад +2

    Ndagula kale zanga ziwili ndizafela ntundu wanga wa malawi koma nditachita kumbali yanga akunama motoo ku malawiiiiii chaka chino 😢😢😢😢😢😢

    • @BreakMtambalika
      @BreakMtambalika 9 дней назад

      Akuba amenewo zomwe akambilanazo sizidzatheka. Akulimbikitsana zosatheka amenewo. Asirikali komanso apolisi ndi anthu anzeru kwambiri ndipo sangamvere zimenezo chifukwa akudziwa kuti ali ndi abale ambiri kumudziko. Choncho sangalole kuti abale awo adzabvutike chifukwa zitsiru zochepa.

  • @JoelTchuma-g3s
    @JoelTchuma-g3s 16 дней назад +2

    Mulungu wombolani Malawi akuonongeka Jehovah nissi(wotimenyera nkhondo).

  • @LuluKansonde-e6c
    @LuluKansonde-e6c 16 дней назад +3

    Akunama commanda ameneyo ndithu ndipo sitikulora zimenezo tikuzagawana malire ntcheu ife kumwera tizatenga wathu president ndipo tikuzaika border basi

  • @JOSEPHCHiMA-h1z
    @JOSEPHCHiMA-h1z 16 дней назад +2

    2025 dpp boma Apm my vote

  • @JonathanMakuta-ie1tk
    @JonathanMakuta-ie1tk 9 дней назад

    This gvt will be punished by the living God.

  • @HenryNanthuwa
    @HenryNanthuwa День назад

    Amenewo ndimaloto chabe

  • @BensonJere-i9k
    @BensonJere-i9k 6 дней назад

    Sizidzatheka,, si asilikali onse angalore zimenezo

  • @LucyMasamba-ll5cj
    @LucyMasamba-ll5cj 16 дней назад +4

    Sangawine olo atatani Mulungu akuona

  • @SamsonElason
    @SamsonElason 10 дней назад

    So pitiful for the elderly, children and the disable only God knows.

  • @JamesDismael-b4z
    @JamesDismael-b4z 8 дней назад

    Ndipo otumidwayo naye azasankhe mbali yake kufa kapena ayi.

  • @AlbertMatola-u9r
    @AlbertMatola-u9r 16 дней назад +2

    Mozambique. Next.... Malawi!

  • @aminajuma-x9t
    @aminajuma-x9t 8 дней назад

    Koma anzawo ajatu anangozisiya,iwowa bwanji nanga?
    Izakhala Mozambique 2?🙄

  • @zaidakarim1891
    @zaidakarim1891 6 дней назад

    1

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc 16 дней назад +2

    Olo,akhale ndi kumano sidziwapindulila,ngati sanaonepo, munthu ma boldgadi,akupululuka chakwela yo,kusala yekha.tiona,pa September popo.sitingalole,anabelayo,ndi silikaliyo,asazike.

  • @LameckJohn-k2p
    @LameckJohn-k2p 10 дней назад

    Ambuye tiomboleni dziko la malawi

  • @JerieWytonTengani-h9q
    @JerieWytonTengani-h9q 9 дней назад

    Kodi inu a ASSEMBLES OF GOD ,Chakwerayi ndi mbusa wanudi? .

  • @JudithSadi
    @JudithSadi 16 дней назад +2

    There is God in heaven...he will never rule this country again

  • @RaladyeTambala
    @RaladyeTambala 9 дней назад

    Kodi inuyo mulungu munamuika pati koma mmapempela inu ine chonena kundisowa

  • @MarkBannda
    @MarkBannda 8 дней назад

    Kkkkk unaboza nkhuluzu iwe

  • @MusaLion-os1lx
    @MusaLion-os1lx 16 дней назад +2

    Ambuye atimenyere nkhondo komaso kuzasitha boma please anthu awa azakakhale kupolice moyo wawo onse ndithu

  • @MwaleNoxious
    @MwaleNoxious 16 дней назад

    🎉That's an indication that Chakwera is aware that whichever plan he'll take he can't win. MALAWIANS ARE NOT FOOLS.

  • @PatrickZinenanie
    @PatrickZinenanie 10 дней назад

    Chikangawa mafupa ako chithuphya chako

  • @MwaleNoxious
    @MwaleNoxious 16 дней назад +1

    Noxious Mwale. September is too far from now. Chakwera will see what he never expected. He is just fooled by those who surround him__ATIDYENAWO.
    Nanunso ATIDYENAWO__ AKAMAJEKETE CHENJERANI

  • @WaysoLufas
    @WaysoLufas 12 дней назад

    Amwene akunama ameneo isha!! Tkudziwa kt amaphaanthu chakwera koma salamula

  • @EversonGeorge
    @EversonGeorge 9 дней назад

    Malawi sali ngat maiko enawatu, akunamizanatu ameneyu, kuli Mulungu ku dziko lomwe alidodali

  • @mozesjackson6328
    @mozesjackson6328 9 дней назад

    Easy azawine tizaphana pansonkhano easy

  • @FrankElius-k7o
    @FrankElius-k7o 15 дней назад

    Mabatire Ake chakelayo mwanambwa uona kwiyo was Malawi

  • @miraclejohnphiri7687
    @miraclejohnphiri7687 10 дней назад

    Mai Ntalimanja muzangofela zaeni chonde ngat mumakonda moyo wanu muganize bwino

  • @YonaPearson
    @YonaPearson 16 дней назад

    Mwauze asilikari poti ndi a mcp koma ndikuona malawi mutayaka moto ovuta kuzimisa tayelwkeza kubela 😮😮

  • @RaladyeTambala
    @RaladyeTambala 9 дней назад

    Kodi achakwela mukufuna miyoyo yamalawi ose mwaziika ngati mulungu koma muzapha tose ichi ndiye mudziwe usatana wako waposa aliyese wolengedwa ndimulungu kodi kukula kwako kunali kotani iwe koma anabeleka iwe ndimuthudi koma ayi ine ndimakana

  • @JerieWytonTengani-h9q
    @JerieWytonTengani-h9q 9 дней назад

    Ife kuli bwino tifere dziko lathu ndipo muyese mudzaona

  • @JerieWytonTengani-h9q
    @JerieWytonTengani-h9q 9 дней назад

    Zitsiru izi ndi agalu onse

  • @NickUpoche
    @NickUpoche 16 дней назад +1

    Moti akudziwa zoti alephela kale😂😂😂
    Iyeyo olengedzao tidzakumana

    • @harrymicah6140
      @harrymicah6140 11 дней назад

      😂😂😂 ameneo akunamatu tizawonana siku lomwero

  • @JamesChiphazi
    @JamesChiphazi 9 дней назад

    Manken chigawa anali 1 pamalawi

  • @AndrewDeebastola-kd4mq
    @AndrewDeebastola-kd4mq 14 дней назад

    Kuzayaka moto kuphana kuphana Mozambique Mozambique

  • @g2foods
    @g2foods 16 дней назад

    Kkkkkkkk remember koika maliro ku nsipe, ntcheu........

  • @MakheyiChabwera
    @MakheyiChabwera 16 дней назад

    Mmmmm. Iwo simulungu

  • @GraceMasiye
    @GraceMasiye 16 дней назад

    Inu apposition,Kaya ndi ufiti wogula Kaya ndi mapoison amenewa ,Anabel mtalimanja akuyenera achunidwe ndponsoo osati Pano muzamukonze mu sept momo b4ve date, kuphatu Nyani ndikumutu ,agaluwa asatipwetekese mitu

  • @JohnPaul-r4u
    @JohnPaul-r4u 16 дней назад

    Ohooooo

  • @PulayaKalaka
    @PulayaKalaka 13 дней назад

    Ukunama iwe ndiwe wa dpp Galu wamuthu

  • @abgi.doctor.august
    @abgi.doctor.august 15 дней назад

    Nonsense meeting ationesa ife azipita uko akuwafunanso ndani

  • @RoseNjaidi
    @RoseNjaidi 14 дней назад

    Iliiiii ndi bodza zakamba zawathuuuu nzose akuziwa ndi chautaaa kumene tilowele

  • @JerieWytonTengani-h9q
    @JerieWytonTengani-h9q 9 дней назад

    Simwayamba kuvulaza anthu panokuombela ali mu ufulu wao? Apolice ndinu ana athu makolo anu ndife osati Chakwera ayi .Zitsiru izi.

  • @JerieWytonTengani-h9q
    @JerieWytonTengani-h9q 9 дней назад

    Chakwera ngati pali munthu opemphelera nyawu ndiwe ,Musinthe malo okasewelera chifukwa nyawu imakasewera kumanda kumene kuli mizimu ya wanthu omwalira.Choncho sinthani malo chifukwa mutu wanu wafika pa misala ndithu.

  • @haneefrazzack6672
    @haneefrazzack6672 15 дней назад

    Ifetu sitikumufuna bas ,bwanji akutikakamila

  • @AndrewDeebastola-kd4mq
    @AndrewDeebastola-kd4mq 14 дней назад

    Tili ready kuphana comment achakwera ayiwone

  • @DiversonMotah
    @DiversonMotah 16 дней назад +1

    Asiyeni tiwaonele mwina sanawone bodyguard akupha bwana wake

  • @ErickCPatrick
    @ErickCPatrick 16 дней назад +1

    ife,ku,mcp,takozeka,kale,kukavotela,,chakwela,nanga,inuyo,mukavotela,ndani

  • @ebinazielkandomo7803
    @ebinazielkandomo7803 13 дней назад

    Izi mukulankhula ndinu. Ponyani zomwe amakambirana kuti anthu amve zomwe amakambirana (audio yazokambirana) kuti dziko likhulupilire.

  • @RodneySupply-tx3ul
    @RodneySupply-tx3ul 16 дней назад +1

    Ngati ndizoona mwakaba zi Kuti agwirizana zoterezi ndimati musaope asilikali a police ndi army choyamba magulu awiri wa alimo angati Malawi muno poyerekeza ndi ife amalawi? Osaopa nafe tigwirizane chimozi Kuti a police ambition timakhala nawo limodzi tizangogawana kuthananawo asilikali army wo ndiochepa kuyerekeza ndi amalawi tonse muyala inapha goliyati mauta zinonga zikwanje tiyeni tiyambe kutolera kumasunga Kuti usiru uwu ngati utazachitika osachita mantha ku Syria wathawa president ndi moto zikwanje

  • @chekiamaabdul5083
    @chekiamaabdul5083 16 дней назад

    Mulungu si Chakwela

  • @GabrielMuziDlamini
    @GabrielMuziDlamini 11 дней назад

    Zandare izi basi

  • @NolityKondowe
    @NolityKondowe 15 дней назад

    Uyu ñdiwokoneza.Sitikufuna zonamiza anthu.watumidwa eti.Kaya akupasa zingati a opposition?

    • @AbdulsharifulKalipinde-m6u
      @AbdulsharifulKalipinde-m6u 15 дней назад

      2025 usamavele za boza
      Chifukwa program iyiyi ndi ya Amalawi osati ya Chikangawa ngati iwe
      Ife tikufuna anthu angati amenewa osati mbuzi zanu za MCP ayi

  • @RosinaWakuthera
    @RosinaWakuthera 16 дней назад

    Izizi zitha kukhala zoona ineyo masana wa lero nnagona ndadabwa ntalota tonse a Malawi tikukakamizidwa kutamanda chakwera ngati mmene ankapangila kamuzu muja that's so strange ndipo maloto amenewa ndadabwa nawo😢😢

  • @MartinKapasule
    @MartinKapasule 8 дней назад

    tizaphana basi ukamuziwa mdani wako umakhala okonzeka

  • @AnishaMoosa-ej7yr
    @AnishaMoosa-ej7yr 16 дней назад +2

    mulungu atithandiza musadandaule

  • @WillianBanda-p7d
    @WillianBanda-p7d 12 дней назад

    Ife tikamafa tizakhala anthu ambiri. Mfuti zathu nafeso zizakhwasule.

  • @ChimwemweSauka
    @ChimwemweSauka 12 дней назад

    Zoonadi brother simukunama anthu awa aonjedza

  • @IshmaelNesta-rb8dx
    @IshmaelNesta-rb8dx 16 дней назад

    Abwere azatipeza pa ground....azaona zosaona amenewo ndithudi

  • @HardsonSichali
    @HardsonSichali 16 дней назад

    OK awo nd maganizo awo koma chomwe wankoza mulungu sitikuziwa

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 15 дней назад

    Zimenezo sizizatheka Kodi achakwera amaganiza bwanji komatu achakwera ganizilani komwe mwachikera .....musabwelese nkhondo mmalawi muno

  • @McfallenKayuni
    @McfallenKayuni 16 дней назад +1

    Boma ndilomweri

  • @AbdulsharifulKalipinde-m6u
    @AbdulsharifulKalipinde-m6u 15 дней назад

    2 pin udya mpaka 2030 iweyo

  • @ChrispineMuzungu-l8h
    @ChrispineMuzungu-l8h 16 дней назад

    Akapanga zibwana afa osadwala makape amenewo

  • @GraceLimani-zw7dx
    @GraceLimani-zw7dx 15 дней назад

    Mulungu atimenyera nkhondo tili chete kwathu ndi kugwada pansi atiyankha si opus a ngatichakwera

  • @Lhanow
    @Lhanow 16 дней назад +1

    Ubwino wake apolicewo nyumba zawo tikuziziwa tizaocha ana awo pamodzi ndi akadzi awo tizapha

  • @LutenganohBandah
    @LutenganohBandah 16 дней назад

    Mmm mabodza awa aaa at adzawine ndiye ndan?

  • @MaryChavula-jz3di
    @MaryChavula-jz3di 16 дней назад +1

    Ndipo ndi zowona ine ndawona zimenezo ku ha kwa lelo dzikolino litadzadza ndi asilikali okha okha ndipo ndizoipa

  • @SibusisoMadube
    @SibusisoMadube 16 дней назад

    Ndikulumbila mbambadi Ngati apolisi akazangoti akutichitila nkhaza , mabanja awo azaotchedwa Moto. Nyumba zawo tikuziZiwa. Asamare kwambiri

  • @ucheopt
    @ucheopt 12 дней назад

    Agalu abodza inu...propaganda yosakupindulirani iyi..😅

  • @ThybaMtenje
    @ThybaMtenje 16 дней назад

    Kd mulungu angachoke kumwamba kudxatithandiza nkhan ndiyoti tikuenela kungopanga mgwilizano pochotsa chakwela pampando pakazachitika Force kulibwino kungodulilana malile kt adzilamulila mudzu wakwawo

  • @GremLekani
    @GremLekani 15 дней назад

    Tionetseni nkumanowo osamangotinamiza

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 13 дней назад

    UKUNAMA VALANTINO ANABEL CHAKWERA NOSE MUKUNAMA MUDZAPHEDWA NDI ANTHU DZAYEREKEZENI

  • @bornface4786
    @bornface4786 16 дней назад

    Nde kuti MCP ikudziwa kuti pa ground ndi 0 pa 10

  • @MIRRIAMMAKATA
    @MIRRIAMMAKATA 13 дней назад

    Kufa kufa kkkkkk

  • @McfallenKayuni
    @McfallenKayuni 16 дней назад

    Ukunama akutuma ndani

  • @JohnMhlanga-e3n
    @JohnMhlanga-e3n 16 дней назад

    Mmmm

  • @Lizzie-h1k
    @Lizzie-h1k 16 дней назад

    Aaaaa...chakwera wachani??? Angapambane kuti wachita chani???

  • @franciskampandira7698
    @franciskampandira7698 16 дней назад +1

    Apite akateteze nyanja uko ngati ali asilikari enieni osati kulimbana ndi anthu wamba

  • @StevenKupheka
    @StevenKupheka 9 дней назад

    Tidzamenyanapo chaka chaka mchino

  • @FrankPatrick-p1t
    @FrankPatrick-p1t 16 дней назад +1

    Mbuzi za anthu zimenezi,oyamba kufa azakhala iwowo

  • @MIRRIAMMAKATA
    @MIRRIAMMAKATA 13 дней назад

    Azatiphe tonse basi azatsare

  • @JumaEriya
    @JumaEriya 9 дней назад

    May mtari manja uri mumadzi ukufa iwe yaka chino

  • @BeatŕiceMfundenji
    @BeatŕiceMfundenji 15 дней назад

    Amcp enanu mumabowa ndi ma comment anu autsiru kodi mulipo nokha Mulungu simunthu mcp sinalenge Malawi

  • @VeroMaster-lo1mu
    @VeroMaster-lo1mu 15 дней назад

    Mulungu wa malawi ndi wokhulupilika kodi busa wa ntundu wanji uyu

  • @JamesChimera-x8c
    @JamesChimera-x8c 16 дней назад

    Arozaliyio muli ndibodza meeting yo osayisumila bwanji poti mulindi umboni ndipo zikuoneka mwangopekaizizi

  • @EvasonThupilifana
    @EvasonThupilifana 16 дней назад

    Kod anabero mtalimanja anthu analephela kumuchotsa PA mpando

  • @JustinMakoka
    @JustinMakoka 16 дней назад

    Ifenso tikhonzeka osadandaula Mozambique 2

  • @EdwardBanda-j7e
    @EdwardBanda-j7e 16 дней назад +1

    Cadet iwe choka yamba zako

  • @AngeloGerman-p3c
    @AngeloGerman-p3c 16 дней назад

    Malawi tiyeni chakwera asayimile MCP.kapena ndinene Kuti chipani cha MCP chisayimile pachisankho azapikisane ndi ma opposition onkha. Tiyiyambe ndeu before voting time

  • @ehinsupport3217
    @ehinsupport3217 15 дней назад

    Ndinu abodza kwambiri man, mukhale ndi manyazi kwambiri. Msamanamidze anthu inu mwatani Kodi?

  • @WilliamTausi-y5v
    @WilliamTausi-y5v 13 дней назад

    Uthamange ndiwe

  • @YoxyJay
    @YoxyJay 16 дней назад +1

    😭😭😭

  • @willytengani1193
    @willytengani1193 15 дней назад

    Akunamizana amenewa azavota siiwowo Mcp ikuchoka bas

  • @Mtchujuku
    @Mtchujuku 16 дней назад

    mmmh koma social media abale

  • @ChipasireMhesha-fz4dv
    @ChipasireMhesha-fz4dv 16 дней назад

    Pa ground ndipamene pazayankha

  • @ehinsupport3217
    @ehinsupport3217 15 дней назад

    Chakwera ndi Boma kale iwe . Ndiwe galu kwabasi, uchoke mmalawi muno stupit iwe, usamatinanidzepo apa mbuzi iwe

  • @DoreenLivata
    @DoreenLivata 10 дней назад

    Mukunamatu