Ena Kuti Police Ifunse Mafuso Pazimene Mumanena Pa Social Media Mudziti Akutisaka - Moses Kumkuyu

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 30 сен 2024
  • On Nyasa VoiceBox, Minister of Information Moses Kumkuyu laments how some Malawians use social media to spread lies about events happening in the country. He also took the time to thank Malawians for their patience and their desire to hear from official government sources and credible media houses regarding the death and funeral arrangements of the late Vice President Right Honourable Saulos Chilima and eight other Malawians who died in a plane crash.
    Pa Nyasa VoiceBox nduna yowona zofalitsa nkhani Moses Kumkuyu wadandaula ndi momwe Amalawi ena amagwilitsila nchito malo ochezera a pa Intaneti kufalitsa mabodza pa zochitika m’dziko muno. Anaperekanso nthawi yothokoza Amalawi chifukwa cha kudekha kwawo komanso kufuna kumva kuchokera ku boma komanso nyumba zofalitsa nkhani zodalirika pa nkhani ya imfa ndi mwambo wa maliro a wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Saulos Chilima ndi a Malawi ena asanu ndi atatu amene adafa pa ngozi ya ndege.
    #malawi

Комментарии • 28

  • @AdoptedNaijaBoy
    @AdoptedNaijaBoy 3 месяца назад +3

    My favourite chanel intro well out spoken

  • @ShabaniKuswere
    @ShabaniKuswere 3 месяца назад +1

    Amalawi ake ati akuthokozedwawo? Mmalawi wake ine ai ndakana kuthokozedwa kwanuko sir,zanuzo mudzipanga komko ndakukanirani

  • @Extratremendouszeus
    @Extratremendouszeus 3 месяца назад +1

    Amve kuchokera boma lake
    Pali boma ap@???

  • @MustafaLikaomba
    @MustafaLikaomba 3 месяца назад +1

    Palibe yemwe akuopa kukuyu akunama ede tatopa ndimaboooza

  • @SandraBanda-hd1li
    @SandraBanda-hd1li 3 месяца назад

    Galu.. kunkuyu... wa kupha... Usatiopseze.... mfiti. Machende. akonso

  • @LeendaDeborah2005
    @LeendaDeborah2005 3 месяца назад

    Ndiyetu social media yo idandithandiza kudziwa kuti Saulos Chilima adamwalira tsiku lija munkanama kuti ndege mudakayisakabe.
    Aboma and a media nonsenu kaya MBC, Times, Zodiak etc., nonsenu ndinu anthu opanda chilungamo. And sindikufuna kunva chilungamo ndichinve kwa anthu akuboma ndikufuna ndinve kwa independent detectives ochokelanso kunja kuti azafufuze bwino

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 3 месяца назад

    Tangozisiyani izi boma lake liti limene anthu Amati adikile musatibiwepo apa

  • @omarrasheed5568
    @omarrasheed5568 3 месяца назад

    Zoopyezana zinantha nthawi yakamuzu ino ndinthawi ya democracy

  • @johnmpatama1461
    @johnmpatama1461 3 месяца назад +1

    Witika

  • @Extratremendouszeus
    @Extratremendouszeus 3 месяца назад

    Iwenso channel chakochi uziona zoika..osat zilizonse

  • @McDonaldbeketeNkhata-n4l
    @McDonaldbeketeNkhata-n4l 3 месяца назад

    Tikopa kulankhu kopa kumangidwa tizanena pamavoti

  • @martinnyirongo2892
    @martinnyirongo2892 3 месяца назад

    Suka

  • @charlesbanda7594
    @charlesbanda7594 3 месяца назад

    Mmmmm we're still confused

  • @EvanceWame-v7v
    @EvanceWame-v7v 3 месяца назад

    Kuyankhula kokhuta ndalama zabomatu uku

  • @praisekadammanja9431
    @praisekadammanja9431 3 месяца назад

    😂😂nde chona chake chiti akunenacho nae uyu

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule 3 месяца назад

    Witika walikuti

  • @mustafanaminga
    @mustafanaminga 3 месяца назад

    4:33

  • @NdamvaScnp
    @NdamvaScnp 3 месяца назад

    Machende akunkuyu

  • @JohnAdam-uw3gv
    @JohnAdam-uw3gv 3 месяца назад

    Kunkuyu pakunya pako galu

  • @BrightZionga
    @BrightZionga 3 месяца назад

    Kkkkkk kaya tsoka ozidziwa

  • @MusaWilliam-t8n
    @MusaWilliam-t8n 3 месяца назад

    Mboloyawoyo akunkuyuwo

  • @DavidPeter-e2o
    @DavidPeter-e2o 3 месяца назад

    Chindele imwe mxm

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp 3 месяца назад

    Dziko laono ngeka

  • @MineMoyo
    @MineMoyo 3 месяца назад

    Mxm machende

  • @Robertmkango
    @Robertmkango 3 месяца назад

    Palibe boma pano

  • @HanifaTabia
    @HanifaTabia 3 месяца назад

    Akumkuyu akhuta

  • @WisdomBlack-uu7zt
    @WisdomBlack-uu7zt 3 месяца назад

    WitiKA

  • @mustafanaminga
    @mustafanaminga 3 месяца назад

    Wabozaaa