Kudali Jumani kunja kuno amene amananso kuti adali mwana wa Kamuzu Zina ndi izi ati ndi mbale wake wa Mutharika. Aliponso wina amati ndi mwana wa Bakili koma amakanidwa.
Kaye kusemphana awa amachendewa ndizimene akuyakhulazo mmmmm inu tangopemphani musanamize amalawi Peter ndi bingu pamene amapita ku Tanzania history is best teacher waboza ameneyo wojiya wa mcp kmbe mukunama inuyo a mcp
Iwe tachoka apa zakuti akut zabozazo koditu inu mbczikuvutani iwe alinafe mulamba wojiyawo a mcp Peter ndi bingu ndi chemwali wake amenewo si akwamuthalika pa zaka 20 analikutiko Kodi iwe azinyemba alinafe azibale ake andaniyo ndi wojiya ameneyo akhawula ndiposo machende akeso ndi iweso ukufusa mafuso opepelaweso beans yako yofumbwayo
Pa banja si onse mumaphunzila same class same university or same secondary same primary musamususe inu inu mbuzi chifukwa cha chipani cha DPP Nonse osusa mumasusa ndi manyi omwe. Chipani ndi china chibale ndi china
January yu njala yavuta abale sangachitire mwina koma kupeza njira yoti upezeke ufa nyumba, komanso umphawi wako USA blame munthu wina ndivuto lako limenelo ndi uchitsiru wako galu iwe
Wakuba uyu watumidwa nd a mcp akamuthilile APM poison Koma game yawo yapheduka nanu a mbc yetsetsani ma program anu akhale womveka kwa amalawi chifukwa apa palibe chazelu.
Koma njalayi kuvumbukuka amisala ambiri. 😂😂😂
I admire SABC.Inu ma K1 anali okukwanirani
Kodi mwati iyiii ndi exclusive interview or comedy chifukwa panalibe opangaza serious apa kuphatikiza ofunsayoso sanali serious
Kudali Jumani kunja kuno amene amananso kuti adali mwana wa Kamuzu Zina ndi izi ati ndi mbale wake wa Mutharika. Aliponso wina amati ndi mwana wa Bakili koma amakanidwa.
Cholinga APM akhare Oipa ...Mukhauraa APM my vote
Aaah mchopenga ichii chadya zingat
Munthuyutu ndiwaboza chifukwa zomwe akufotokoza sizikugwilizana ndizomwe akufusidwa😊
Uyu ndigalu
Ndikumuziwa amakonda kuwabera anthu kumawanamiza kuti ndi mbarewake wa Bingu anayamba Bingu asanamwalire inu a MCP mwalandira munthu wopenga
sakuziwa alekeni komanso iyiyi siphura kanthu
Kaye kusemphana awa amachendewa ndizimene akuyakhulazo mmmmm inu tangopemphani musanamize amalawi Peter ndi bingu pamene amapita ku Tanzania history is best teacher waboza ameneyo wojiya wa mcp kmbe mukunama inuyo a mcp
Kodi mbudzi imeneyi ikuti chani kapena mwina uyu ndi yes matiki😂
Ifetu chomwe tikufuna ndi Black Box izizi sizitithandiza
Fundo zimene akunena pamenepo,ndizokambirana kutundu wawo not in paburic
Koma ine guys interview iyi ikundiwaza kwambiri ndaimvera ka 5 times mkuluyu aaaaaaaa
Nkhope imeneyo siyakwa munthalika
Chokuba si mchimwene wake wamutharika kuchikamwa😮
He is a frustrated man. Umphawi ndiye vuto apa. Where was he when Bingu and APM were making their own future.
Uyu ndi wakut? Uyu alibe nzeru
Ken zikhale ng'oma akuziwa coz anamupasa 100k pin
zikhare palibe chomwe angafotokozepo za izi nkhani ndiza ndale kufuna kuipisilana mbiri komanso kufuna kutenga mavoti mophweka koma nzolephereka izi
Kusuta fodya ndi njala eee😂😂😂
Komano zipindulanji izi kwa ife amalawi?
Iwe tachoka apa zakuti akut zabozazo koditu inu mbczikuvutani iwe alinafe mulamba wojiyawo a mcp Peter ndi bingu ndi chemwali wake amenewo si akwamuthalika pa zaka 20 analikutiko
Kodi iwe azinyemba alinafe azibale ake andaniyo ndi wojiya ameneyo akhawula ndiposo machende akeso ndi iweso ukufusa mafuso opepelaweso beans yako yofumbwayo
Ndamvetsetsa sopan ndiuphawi umene wamutuma gogoyu
Wadyela uyu
Chakwera akhale wa nzeru dziko likanamukanika? Bambo ingopemphani muzipita
Apite kwa uncle ake Apeter akafufuze zaubalezo osati pa television
Okuba ameneyo
Uyu ndi Onama. Angofuna kudyera anthu. Mmene wanna kuti Ambassador anauzidwa kuti azimpatsa galimoto ndi flag - wazigwilitsa. Mpaka akuti amalondera casket ya malemu Bingu - zonama zeni zeni....
Tv yombwambwana dziko lonse lapansi
Kodi zimemenezi nza ntchito yanji Ku dziko lino??? Fuel apezeka ? Fertilizer akhala 4,500 ? Passport ikhala 14,000 sugar 500 ?
Zopanda ntchito izi
Malume muyaluka nazo izi, iwe simulomwetu ukundimvekera kachiyawo yawo eeeee😂😂😂😂😂😂
Wapatsidwa ndalama ndi MCP uyu ndipo ndiopoira
Kkkk eshi kumalawi mkokoma kwabasi
Koma kwinaku nditukwana
MCP ili ndi ndalama zoseweletsa
Koma anthu mumadziwa kunama 😂😂😂
Sindikukhulupilra ndi mdoba mdoba wa mtawn😅😅😅😅
Pa banja si onse mumaphunzila same class same university or same secondary same primary musamususe inu inu mbuzi chifukwa cha chipani cha DPP Nonse osusa mumasusa ndi manyi omwe. Chipani ndi china chibale ndi china
Baba osapanga phuma, munthuyu naye wamikisa nkhani akuti walowa MCP kuchoka ku DPP.
Zikanakhala kuti anangobwelera nkhani za chibale bwezi palibe nkhani za zipani
Wangudwa
Momwe anzake amaphunzira iyeyu anali busy ndi nyanga ....nkokhwima aka nkani abale ake amakathawa....kakuoneka so koipa mtima...fwetseki
Kkkkkkkkkk km guyz mot ukaramba koseku km umuthu mulibe km ndalama ndisatanadi
This just shows how much you fear APM 😂
Uyu andilakwisa
January yu njala yavuta abale sangachitire mwina koma kupeza njira yoti upezeke ufa nyumba, komanso umphawi wako USA blame munthu wina ndivuto lako limenelo ndi uchitsiru wako galu iwe
Mulibe ma program ena ku MBC ko oti angathandize dziko?
Zaziiiiiiii!!!
Mcp zawavuta mpaka kugura athu gogo wabodza uyuuu
munthawi ya bingu anali kuti aaaa
kutumidwa Kwinaku muziona ponamizila
Koma abale umphawi sizinthu,ndipo ngati kuli munthu opya,ndiye ndimphawi,amalola kunena boza cholinga apeze thandizo
Wakuba uyu watumidwa nd a mcp akamuthilile APM poison Koma game yawo yapheduka nanu a mbc yetsetsani ma program anu akhale womveka kwa amalawi chifukwa apa palibe chazelu.
Mwabwera rit anganga inu zigawenga za mcp
Musatengeke naye ameneyu simunthu wabmwino
Wamisala uyu
MBC 😂😂😂 izizi kwa ife amalawi zitithandiza chan
Wabodza uyuuu
Kodi kufanana mayina ndiye chibale 😂😂😂😂 zavuta ameneyu
Awa mutu wawo sumagwila za udani wawo ndi muthalika zisatikhuze ife tikupanga zoti peter abwelele muboma athese njala akulu amenewa akuziwa ntengo wa thumba lachimanga pano ? Pasanapanu malume
Nde mwat Dr Lazarus mc cathy kachero 😂😂😂😂😂
Nkhani ndi ndalama 😅😅
Nthawi yonseyi anali kutiko m'dalayu ndi mbava
Nde mpaka kusapota khonglesi????
Uyuyu ndiwaboza chifukwa dzina ndimoto chifukwa ngakhale mayina amafana unalikuti nthawi yonseyi ikufuna kumupha munthu uziwe kuti yemwe akukutumayo akupweteketsa kodi ngati ukumudziwa Peter munthalika uphale wake anakavinidwa kuti?
AM NOT CONVINCED WITH THIS FOOL
Ubale wake wotani komanso kuli abingu iwowa anali kuti ? Komanso ngati palidi chibale awawa ndi anthu oipa awoneswratu kuipa mtima ndipo sianthu owathandiza.
Ndi Wabodza uyu
Aaaaa palibe zimenezo Anthu akuziwa bwino lomwe za banja la Muthalika mugulen nfiti uyu Anthu ntchito za DPP akuziwa bwino lomwe
Machende ako, kwa munthalika kulibeko mbuli galu iwe
Wakuba Uyu sichibale
Njala yavuta iyi
Mene enawo amaphudzira iwe.
Unali kut
Kkkkkk nfundo za M.C.P zakupha Anthu ku chikangawa kkkkkk Mutaye si M'bale wa Bingu uyu kkkkkk uyuyu apanga chan uyu kkkkk vote A.P.M
Kkkkkk kapolo uyu
Useless interview ever😢
Kkkk eeeh kwabvuta
wabodza uyu watumidwa kongofanana mayina basi
Wakuba
Kape ameneo alibe chikondi
Mbc zosabebatu.....
wosangonena kut mukupempetsa
Chakwera wamupasa ndalama madala opanda dzeru inu paliinupa mukufuna mukafa muzantchuke ndigulilidwa bokosi labwino mmmmmmm nthawi yatha iyi
Uphawi sizithu
Kulibe zimenezo
Wabodza uyu wanamizidwa ndi nyau
propaganda 😂😂😂😂😂😂😂
Mbc
sukulu simunalimbikile bwanji ???😂😂😂😂😂😂
Wabodza uyu
Mdala uyu ndiochenjela akufuna kudya nao waona kt zikudyeka zabooka ndpo aiphula kma asaname kt Pali ubale ndi akubaja kwaa Muthalika