One of the benefits of the cross of christ jesus is the exchange that took place between jesus and his believers. With his stripes youw were healed. Be healed in the name of jesus right now
Koma ndimati tipepheko ,Kodi sizingatheke kutenga account number ya sir Paul Banda kuti mwina anthu ambiri tilikutali mwina kungatheke kumatumiza kangachepe through bank account.
Kale lathu God bless you Sir Paul
Quick recovery Sir Paul Banda may the good Lord be with you all the time
the best old Man very humble
One of the benefits of the cross of christ jesus is the exchange that took place between jesus and his believers. With his stripes youw were healed. Be healed in the name of jesus right now
I respect you sir poul
Sir Paul banda god be with you
God please touch your son Paul
Respect sir good bless you ❤❤❤❤
God be with you Paul banda
Quick recovery sir Paul Banda mulungu Ali mbali yanu
Ambuye akhuzeni a Paul ndizanja lamachilitso palibe chokulakani Ambuye
Ambuye akukhudzeni ndi dzanja lake la machilitso
Respect
♥️♥️♥️✊✊🙏🙏🇲🇼🇲🇼🇲🇼 LEGEND
Dzanja laMULUNGU wamphanvu likukhudzeni ndikukuchilitsani.
Inu bwana paul Banda ndinu akamuna munachokelanazo Pataki kumalawi Kuno palibenso ndinu akatundu
Koma ndimati tipepheko ,Kodi sizingatheke kutenga account number ya sir Paul Banda kuti mwina anthu ambiri tilikutali mwina kungatheke kumatumiza kangachepe through bank account.
Number it's there pa screen check properly boss....
Ngakhale number Yao tizitumizako ka 1000
Ndiwokoma mtima atithandiza father wathuyu akhala bwino
Muito simples sir Banda
Nthawi imeneo ife sitinabadwa
Ambuye apitilize kukupasani moyo wathanzi
Good suggestion...
Koma mulungu acitepo kanthu
Boma limalephela kuthandiza munthu wokoma mtima ndiwopanda nsanje ngati uyu.koma kumangoba ndalama basi.
Dzanja laMULUNGU likukhudzeni ndikukuchilitsani.