CHIPANI KA UTM KU ZATI BWANJI🙌🙌🙌🙌

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 12 сен 2024

Комментарии • 53

  • @paulmanyamba5437
    @paulmanyamba5437 3 месяца назад +2

    Ndipo sukunama amalawi pano anaonadi utm ndiye kwasala afitsi okhaokha opanda nzeru

  • @user-qp8kh2hj9o
    @user-qp8kh2hj9o 3 месяца назад +2

    SKC my vote ❤❤❤

  • @ShadrickTukura
    @ShadrickTukura 3 месяца назад +1

    Kunkuyu amanyadiratu kuti Koma ndalama ndiye tizidyatu 😅😅😅😅😅

  • @yusufsadic2930
    @yusufsadic2930 3 месяца назад +1

    Chim kamalizits maulendowo

  • @user-nj5vu8cd5l
    @user-nj5vu8cd5l 3 месяца назад +2

    Saulos chilima Moto

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu 3 месяца назад

    Tabwelelani mumbuyo ku udf , nakhumwa ndiwa mcp asakupusiseni, mai kalitati asakupusisei chilima yo nde mbamva yaikuku

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete 3 месяца назад +1

    Ndalamazo ndezikubwela komano zichitila ndikugula magalimoto awo udula basi bagamoyo

  • @LindiweMoloi-wn5qo
    @LindiweMoloi-wn5qo 3 месяца назад

    Kaliyatti ndi chilima zikalimani palibe akukufunani mungozitayisa nthawi ,inu ndi mbabva tatopa nanu

  • @YohanePatrick-lc2lq
    @YohanePatrick-lc2lq 3 месяца назад

    Bomalit lakuba utm mcp yakuba aononga dziko atipha pano mayiko akutithamangitsa akuti atopa nafe kodzani dziko lathu otsati kuli bela ayi

  • @EagerChicken-qj6xu
    @EagerChicken-qj6xu 3 месяца назад

    Zaziii

  • @user-le9su3mt7r
    @user-le9su3mt7r 3 месяца назад

    Chakwela mbava achokee

  • @user-nj5vu8cd5l
    @user-nj5vu8cd5l 3 месяца назад +2

    Utm moto

  • @ChawasoMlotha-ys6bf
    @ChawasoMlotha-ys6bf 3 месяца назад +4

    Kuzitaisa nthawi 🤣🤣🤣🤣

  • @RelaxCool-dp9jn
    @RelaxCool-dp9jn 3 месяца назад

    Mmmmm chipani chambava, simunganenedi zachipanidi lelo munazuzulidwa zanalija wudyo kkkl

  • @JafaliAkimu-ll1bf
    @JafaliAkimu-ll1bf 3 месяца назад +3

    zitsiru za anthu izi

  • @JimmyIsaac-xd4ef
    @JimmyIsaac-xd4ef 3 месяца назад +1

    Chipani cha PDP ,UTM ,MCPazitsogoleli ake onse odzikonda

  • @louisgolden
    @louisgolden 3 месяца назад

    Ndiye azidikila zimenezozo ndindani komaso anthu chomwe akusatila pa UTM ndichiyani

  • @ishmaeldama8906
    @ishmaeldama8906 3 месяца назад

    Akayimila kubanja kwako

  • @salimmkumakumakitombi-yc7pw
    @salimmkumakumakitombi-yc7pw 3 месяца назад

    awa akufuna kupadidwa tameki kuti amve kuti sakufunidwa.bwanji kungoti kakaka pomwe musalufunidwa

  • @RabsonMulumbe
    @RabsonMulumbe 3 месяца назад

    Zakolona bro nkhondo zatha wabweretsa factor Ina ya kugulitsidwa kwa ma factory, KOma Laza kkkkkkkkkkk

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 3 месяца назад

    Chinachilonse chomwe Chakwera wachigwira chimanunkha manyi

  • @YonahBanda-kp9rm
    @YonahBanda-kp9rm 3 месяца назад

    Chatha ichi basi🤣

  • @chrisschikozera7271
    @chrisschikozera7271 3 месяца назад

    😂😂😂😂😂......koma mcp stop complaining about kukwera kwakatudu athu timagula fertilizer pa mtengo was 22 000 and sugar too was good price osamagodadaula aaaa useless president

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole 3 месяца назад

    Achakwerawa cha umunthu chidachoka kalekale.😮

  • @yusufsadic2930
    @yusufsadic2930 3 месяца назад

    Adyeren nthawi yakendino

  • @EdwardMathuwa
    @EdwardMathuwa 3 месяца назад

    Chipani chopanda tsongolo ichi

  • @shaibuJames-c3w
    @shaibuJames-c3w 3 месяца назад

    lnu chilima anali kale anthu maso ndi Apm osati may try tatopa ife

  • @replacefruittreenursery
    @replacefruittreenursery 3 месяца назад

    Ndalama zomwe umamangira zipatala ndi police iwe kariati sidzinari zako zinari za amalawi noti zako .

  • @user-tl1jq2gc5b
    @user-tl1jq2gc5b 3 месяца назад

    Inu APM uja mmmm size alibe

  • @NgomaRaheem
    @NgomaRaheem 3 месяца назад

    Zopusa bas utm ndekut chan

  • @PatrickGonagona
    @PatrickGonagona 3 месяца назад

    What is UTM kapitani uko mukagwere anthu onama inuuu

  • @ishmaeldama8906
    @ishmaeldama8906 3 месяца назад

    Cha pa face book 😂😂

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x 3 месяца назад

    😂😂😂😂😂😂koma abale UTM mpakana??? 😂😂

  • @PatrickNamakhoma-zm6kq
    @PatrickNamakhoma-zm6kq 3 месяца назад

    ndie cholinga cha mtsokhano chinali chani? anthutu akungosowa intertainment mmidzimu. musapusisike ndi kukula kwa number ya anthu

  • @Henry-vw2cz
    @Henry-vw2cz 3 месяца назад

    😂😂😂😂😂😂😂😂aaaaaaaaaaaaaa

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x 3 месяца назад

    APM Palibe size yake ku Malawi kuno nkhani ndi Adad basi tikuwadikira ifeeee enanu mungozitaitsa nthawi😂😂😂

    • @user-eh1mg3ww6d
      @user-eh1mg3ww6d 3 месяца назад

      Adad oyeeee ❤❤

    • @user-uc1pd1tc2x
      @user-uc1pd1tc2x 3 месяца назад

      @@user-eh1mg3ww6d Woyeeeeeeee 🤸🏿🤸🏿🤸🏿🤸🏿

    • @spargomw
      @spargomw 3 месяца назад

      Peter yemweyo❤❤❤ Mbuzi izi zikupita 2025. Ndipo akadzangotuluka asadzayembekereso kut adzalowaso mpaka kutha kwa dziko😂😂😂

    • @user-eh1mg3ww6d
      @user-eh1mg3ww6d 3 месяца назад

      @@spargomw powerful

    • @patrickmandalawe745
      @patrickmandalawe745 3 месяца назад

      Mavuto ndithu

  • @GiftChitsulo
    @GiftChitsulo 3 месяца назад

    Koma m,Malawi wiwe unakhala bwanji pakana utm dpd MCP kkkkkk anthuni mukufuna akugwiliseni tchito kenako ndikukutayani anthu simumachedwa kuiwala kkkk

  • @user-du9qs4tb6u
    @user-du9qs4tb6u 3 месяца назад

    Fake party