congratulations to the young talented Aidfest And Kineo, mumatha "Big thanks for to Jaakev mukukwaniritsa basi support yonse pa industry". I'm from Mozambique
Iweyo kuphwekesa nyimbo iyiyi nde umafuna nyimbo iyimbidwe bwino motani?🎉 🔥 hit .....am not a fan of Malawi Music that much but this is the music you call play whole night........Big up flames 🔥 zuwa salozerana aliyese amaliona ....hit fire 🔥 🎶 🎵
Reading through the comments, Regardless, the tune is well cooked and pure talent in story telling. Not every would be like that in those negative comments. Anyway, happy Friday
Everytime someone likes my comment ndilipano to watch it again 🔥
Bwela mphwanga uzawoneleso🤣
Eyo💥
Come again 😂
😊😊
Musatinyengepo apa aaaah😂😂😂
Don't tel they actually write nyimbo zao these guys...😅 motley crew 🚶🏾🙌🏾
Amuperekeza ndi Ena koma akamafika amafika yekha osati mpaka kubwera yekha eeeeee kunaipatu 😅😅😅😅😅henewe sounds pretty gud
Guys inuyo muli bho heavy osazatayana mukugwilizana heavy munyimbo
Wow that's great Song kept up mumatha inuyo guys 🔥
Ndipo ndimayidikira kuti ndirowele pa ukwati
To those who are not understanding because we do know chichewa, tikumane pano, nyimbo apha iyi eeeeh
Ilibho 🔥
Opanga beat ndidolo hvy
Khaaaa 🔥🙌
Kwakoma ndikuno
Ndipo live
Ndipoo amabweradi yekha😂
Ndikamadya plain amabwera yekha😂
NYC ❤
Hit iyi🔥🔥🔥
Mudyera
I will do 1 push up for every like that this comment gets ❤ this is hit
😂
You must be a bouncer now 😂
@@mayakadango3195 😄
😂😂😂😂😂
I will do 20 push-ups for every like
😂😂
Kwathu amabwera yekha ndi matenda ake pheee💃💃💥💥
🤣🤣🤣🤣 kumulandila ndi nkokomo
@@innocentchikapa9404 zinthu zake amwene😂😂
Kkkkkk
Kuwagawana
😂😂
I will not get tired to watch it again once you hit 🎯 a Like to me... Let's make it 100K first
Amene tayenda chothamanga from mikoz page like my comment 🤩🤩
jerous down nyimbo zanu zimamveka bho ndipo am one of your fans🎉🎉🎉🎉🎉
Ndipo live
True 🎉🎉
nyimbo ndi Hit iyiyi ... Kaya muti mkaziyi ndiwagulu koma kwathu amabwera yekha
Eeee weekend yuchedwa tivine ma bar mu
@@cloy28eyemark😂😂😂😂😂😂Km ndiye
Iwe umati
4@@ChimwemweIdanaMasiye
Thank you guys, I'm from Mozambique
U are welcome
Zolaulatu a kineo mwaiyamba verse and mwaika hook Track is lit
Ndipoooo
Chi heat
I think ambilinu Kineo samatsata alind solo songs pomwe Aidfest sinamvepo olo imoz
Mmmm man mostly amaoneka ko kut akupanga zambili ndi aidfirst yo..... Koma iyiyi kineo wapha
@@SophaiTadeyo komadi
Amene titha pa repeat let's gather here 🔥🔥🔥🔥
Koma nyimboyi mwati ndiyaku Malawi kuno. Too good to be true. 🎉
Itiyo
Kineo, I'm impressed now that umatha. I'm ur big fan. Yekha 🎵 🎶 tachezera nayo dzulo
Much love from here 🇿🇼 these guys they're representing Malawi
This is good music ❤team on repeat/ibwerezenso let's gather here🎉
Guys please share the video ,,, let’s make this sound blow up 🙏🙏
Amabwera yekha ...day ina adzabwera ndi HIV 🤣🤣...... Hit 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Nyimbo yolimbikitsa uhule. The vibe is just too fire koma
Anthu ndipo akulimbikiratu kuposa kugwira nthchito kkkkkk
Ok Malawi gut vibes. Zambia 🇿🇲 and Malawi means kuchalo. I gut our support from Zambia 🇿🇲
Our very own Blaq diamonds ❤😂 nyc one iyiyi ili pa repeat tuu ati uyuyu ndiwanga wanga basii eeeh pamenepo
😂😂 literally what I thought
For sure like blaq diamond ❤️❤️🥳🥳🥳
Hoooo God, this song is amazing ❤❤❤❤ from Mozambique
U are right ,but u should search vula Malaya,zeze kingston
Nde uike ma headsets olo ulumikize kuzima speaker mmene ikumaswela sound imeneyi
Guys lyi yokha yifike 1million view jealous down anawa akuyimba bwino ❤❤❤ love u kineo and aidfest 😊
You can say that again 🎉
koma nyimbo za ng'oma mkati ine nde zimandifikapo eish 😂❤zimakusintha mood osat masewera 💥👊🔥🔥
BadBoy Aid 🔥🔥🔥🔥🔥
Seanyfilms 🔥🔥
Yoba 🔥
Aidfest + Kineo🔥🔥🔥🔥
Kaya muziti mamunay nd wagulu amabwera yekha ❤🎉🎉
yes
Kwamene mwamaliza kuonera video yi, tifotokozereni kt adhawo anakana ndalama chifukwa chani😅
kwatonse amene titenge matenda chifukwa cha nyimbo iyiyi,..lets gather here 🙃
Lol boss be serious😂
Kodi mukuti chani 😅
😂😂
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣 komatu 🙌🏾
congratulations to the young talented Aidfest And Kineo, mumatha "Big thanks for to Jaakev mukukwaniritsa basi support yonse pa industry". I'm from Mozambique
inuyo ndimadolo guys mumatha🔥
Please like my comment kuti ndibwereso
Mafanawa ndi madolo eee 🔥🔥
Akumabwera atavala mask ati tisaone milome
Patiently waiting😌♥️🔥
Iweyo kuphwekesa nyimbo iyiyi nde umafuna nyimbo iyimbidwe bwino motani?🎉 🔥 hit .....am not a fan of Malawi Music that much but this is the music you call play whole night........Big up flames 🔥 zuwa salozerana aliyese amaliona ....hit fire 🔥 🎶 🎵
It's the wagulu and chimulu part❤️🔥
💃💃💃ndpo
Cee pee acious alipano ku oonera yekha
Nice music 🎵
nyimbo ili Shap quality mwala mwala pati but if possible next time camera movement izachulukeko zimatibebera koma Yosemite boh I love it😍🔥🔥🔥
Ma kids inuyo mwatiyakhulira "Amabwera Yekha" YUNECO imveso apa
track iyi ili bhoo.. a Kineo abweraTUUU big up my niggah😅😅 tvela imenei popita ku Vekeshooni
I like the idea of getting tima model ta size yanu😅, baddest tune big up
Ndikuona ngt ma lyrics bwez kulemba chizungu kut anthu amene samava chichewa azitha kuva zomwe zikuimbidwa mu nyimbo mu
Searching for a soul mate Kuma comments ku kaya ndogwidwa paden azifika yekha 😄 🤣
Anapha ichi
Nyimbo ya sharp heavy. Just an observation. I think mukanayamba ndi verse instead of the hook
Kodi Nkhani ndiyakuti u still wanna be or sound like amapiano basi cause nde apapa nyimbo iliyose izivekatu ngati imodzi
Kwa tonse omwe nyimboi tatenga nayo zidzonono let's meet outside the mortuary kkkkkk
Reading through the comments, Regardless, the tune is well cooked and pure talent in story telling. Not every would be like that in those negative comments. Anyway, happy Friday
Bola mukanapanda kuponya link mwa fast ndikudikilila nthawi yakeyo koma apa mwatipanga chipongwe mwamva!!
Nde nyimboyi ndiyosangalala kuti munthu umagwira hule?
😂😂😂
comment tu t'appelle je m'appelle DRIPAVELLI
Munva je m'appelle osati m'bebeso
What asong
the song is a hit as usual, mumatha ma guy but you can do better on the models, ngati akudwala edzi atsikanawo
Kodi kuhopera nonse pali vuto? ☺️🏃♀️🏃♀️
nyimbo iyi ikumakhala on repeat ngat ndilindi chibwenzi😂😂😂💔🙌🏻
Who have watched more than 4 times lets gather here❤❤❤❤❤
I've jxt watched it once
Another Hit 1 mwatipanikizat oimba aku MW More! Fire works!!!! 💥💥💥💥💥💥💥
Kineo amatha guys eeeeeeeee 🔥🔥
Mkaziyo sangalephere kukhala wa gulu but nyimbo ili bho
Ukali okhaokha
Ana a kwathu
I have to agree, the presentation is superb... But for the concept of the track, I will leave that to the folks for their opinions
Nyimboyi ndyokoma hook yokha other wise it ain't worthy listening
Amabwera yekha kudzandiontse zachabe😂😂😂😂
Or akanangoyimba yekha kinyoo yo
Put some respect on his name 📛
who's watching with me right now
Bwanji kodi😂
who is here in 2024 for ❤loving this hit maker
Guyz tipangeni link dollar mkagulile ufa🙄🙄🙄🙄
Ma beat ofanana basi producer wanuyo ma plan amuthera eti?
Vacation is still on Number one. Koma yanuyi iliso bwino guys
Anthu Akaduka inu Chaka chino Mumva m'bebe😂😅
Why you don't like my comment guys is it because I'm from ntchisi?😂
😂😂😂😂 Iii kaya ndikuona udyo koma kineo yaipha wamudya mzakeyo zikomo
Kwanthu amabwera yekha zinazo muzikambira konko🤣🤣
This duo🔥🔥🔥🫵🏽
Malawi woyee
-Odi da w
simunakule ana inu muzaziona
H
I
V
siyamasewera
Killed🎉🎉🎉🎉🎉🎉
Awesome 👍😎
Wow just come across this beat. Don't know the artist lemme enjoy the beat
Nyimbo iyi ndi yolimbikitsa uhule 😂 komabe tivina
Yekha yekha opanda transport ati akandilipilila konko🙌💀
😂😂😂 zokakwezanaso bp izi
Kungokhala pa low bas