Mbiri ya Charles Nsaku part 2 Pa mibawa Tv

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 27 ноя 2024

Комментарии • 18

  • @WillyPhiri-dg9bu
    @WillyPhiri-dg9bu 3 месяца назад +1

    Ndale teyeni tiasile andale let's mind Our own business Malawian musician, thanks Charles yapendekeka . willy chikuta phiri following from LUSAKA Zambia

  • @JohnmarkNazombe-hi9xd
    @JohnmarkNazombe-hi9xd 19 дней назад +1

    Very educative interview ❤❤❤

  • @sumanmedson6068
    @sumanmedson6068 Месяц назад

    Charles Nsaku ndi oyimba wabwino kwambiri vuto ndi zandalezo zinamusokoneza like phungu Joseph Nkasa

  • @JawaduShafie
    @JawaduShafie 15 дней назад

    Billy Kaunda ananena kuti album yake anajambula ndi ndalama zothandizidwa ndi azibale ake.I think mgwirizano wake ndi Lucius simukudziwadi,coz ananena izi Lucius ali moyo koma sanatsutse

  • @ancientnkhata1137
    @ancientnkhata1137 14 дней назад

    Charles Nsaku is honest

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 Месяц назад

    But uchitsiru wake ukuyimbanso za ndale abambo a Thomas 😊😊😊

  • @YusufJamesYusuf
    @YusufJamesYusuf 24 дня назад

    Nanga iwe wa factory 265 umapeza zingati aaaaaa nanga sitiziwe

  • @humphreychisanu2435
    @humphreychisanu2435 29 дней назад

    Charles ndimkamukonda kwambiri atangoyamba ndale ife tidamutuluka

  • @RashidWyson-i9j
    @RashidWyson-i9j 17 дней назад

    Tipaseni nambala ya msako

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 22 дня назад

    Pajaso uyu NDI wasatanic

  • @NikolasNanawe
    @NikolasNanawe Месяц назад

    ❤❤❤

  • @PartsonMdeza
    @PartsonMdeza 2 месяца назад +1

    nanga bwanj mwaimbaso ina ya ndale ku MCP

    • @ancientnkhata1137
      @ancientnkhata1137 14 дней назад

      Tamupatseni ndalama azisamalira banja lake asiye kuyimbira andale

  • @NelsonNyenga-r5x
    @NelsonNyenga-r5x Месяц назад

    Mumakwana nsaku tkudkra yapendekekayo

  • @RafickMbwana-l6f
    @RafickMbwana-l6f 4 месяца назад

    Ndiwachulingamo

  • @MarkMponda-do3ky
    @MarkMponda-do3ky 4 месяца назад +1

    Machine