A KUNKUYU ANAMIZIDWA NKHANI YA NYANJA NDI TANZANIA ATAWAPATSA MAP KOMA OSADZIWA INALI NYAMBO

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 6 янв 2025

Комментарии • 65

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani 6 дней назад +1

    Malawi Trends watiuza mzambri Mchakachi mawa thobwa lilipo INSHA A ALLAH

  • @BerthaKasambala-y5k
    @BerthaKasambala-y5k 4 дня назад +1

    Km kunkuyu ndi chakwera kenako tingonva kt anthu tonse atigurisa sure 🙆🥱

  • @michaelkallyz2425
    @michaelkallyz2425 6 дней назад +1

    Musaname ankol. Nkuluyi ndiboma akudziwa chomwe akupanga. Angokupusitsani chabe.

  • @kennedybanda
    @kennedybanda 7 дней назад +1

    Gwiraniko ankolo mbali yinayo tijambulise pano kwinako atamubisira za map,
    haye! haye! showooo!!!!

  • @AustinNangwale
    @AustinNangwale 7 дней назад +2

    Amaona Ngati kuyendetsa Boma ndikopweka kwasalaku muyamba kugulitsa anthu Kuti mukonze zithu 😊 I see more problems than what we are facing now

    • @MaryZgambo-p5m
      @MaryZgambo-p5m 7 дней назад

      Eeeee mesa anayamba kale kugulitsa amalawi ku Isirael

    • @ShamimuBisani
      @ShamimuBisani 6 дней назад +1

      I agree with u

  • @BashiruPendapenda
    @BashiruPendapenda 7 дней назад

    Wow!

  • @enocktebulo2965
    @enocktebulo2965 5 дней назад

    achisiru awa😂😂😂😂

  • @jameskachulu8141
    @jameskachulu8141 7 дней назад

    😂😂😂😂😂 Zisilu dza anthu

  • @ShabbaKunjira
    @ShabbaKunjira 3 дня назад

    🙆🙆🙆😭😭

  • @LilianKachala-yz2xf
    @LilianKachala-yz2xf 7 дней назад +1

    Zinthu Sizilibwino abwezetu ndalamazo

  • @TakalaniGlenda
    @TakalaniGlenda 7 дней назад +1

    Next time azagulitsa mpoto yonse serious mcp kudana nawo amalawi😂😂😂

  • @EDGARMPIKAMEZO
    @EDGARMPIKAMEZO 2 дня назад

    Anyani awa samalemekeza nyumba ya malamulo amapanga ziganizo zawo ngati mnyumba mwa azikazi awo. Amayiwala kuti lino ndi dziko muli anthu over 20,000,000. A MCP asamatenge dzikoli ngati ya mawo. Adzifunsa mzika maganizo awo.

  • @YolofaniUledi
    @YolofaniUledi 5 дней назад

    Chilungamo akuchidziwa

  • @ThomsonNyirenda-df9io
    @ThomsonNyirenda-df9io 7 дней назад

    😮😮😮😢😢 mmmmm

  • @LynesBanda-r1p
    @LynesBanda-r1p 7 дней назад

    Payipa pano malawi 🇲🇼 kaya akupita kuti😢😢

  • @MallioKulinji
    @MallioKulinji 7 дней назад

    Aaa ai Kumkuyuyo asatinamize kuti samadziwayi ndi zokonza izi inu aaa

  • @augustinechibbalazi8897
    @augustinechibbalazi8897 7 дней назад

    As of now leave Information Minister blameless until full scrutiny of rumour mongering.

  • @MadaloMachedwetsa
    @MadaloMachedwetsa 4 дня назад

    Boma la MCP mwadzadza mbutuma zenizeni

  • @PatrickMawerengabanda
    @PatrickMawerengabanda 2 дня назад

    Tizikadya kuti chambo Koma kulephera kwachekoso Ndiye mwatiwonjeza Moses utitukwanisa kwasala

  • @MasterMwela
    @MasterMwela 6 дней назад

    Maganizo ndi akuti Whatever it takes Moses Kunkuyu adzayankha mafunso pa Court. Dzilo it's not easy to sell. JUST LIKE THAT? Very disappointed.....Chikangawa ndigulu lake tsiku lina adzatankha mafunso, Mzimu wa Dr. H. Kamula Banda, mtsogoleri wathu woyamba, uwutse mumtendere..

  • @MarkKaliati
    @MarkKaliati 6 дней назад

    Malawi ndiulendo waku manda

  • @ExcitedBreakingWaves-oh3zb
    @ExcitedBreakingWaves-oh3zb 7 дней назад

    Iyeyo siduna ya foreign affairs analandila bwanji mapuwo.

  • @JaydeeAchalume
    @JaydeeAchalume 2 дня назад

    Kd mukuganiza kt achina Moses kukuyuwo sakuzindikila. kapena akutipusisa amalawi?

  • @EVERSONBANDA-j8h
    @EVERSONBANDA-j8h 7 дней назад

    Mnzosatheka a Nduna okha okha popanda UN kapenanso AU

  • @ExcitedBreakingWaves-oh3zb
    @ExcitedBreakingWaves-oh3zb 7 дней назад

    Kunkuyu si mmalawi weni weni.

  • @RedsonMakaka
    @RedsonMakaka 7 дней назад

    Show us the old map Tanzania,,, we are stupid indeed

  • @GeorgeWalasi-m5j
    @GeorgeWalasi-m5j 7 дней назад

    Koma ma press briefing olimbana ndi ma bishop

  • @GodfreyGondwe-b9r
    @GodfreyGondwe-b9r 7 дней назад +1

    Ndichifukwa vula siyikubwela mapili akwiya nyanjaso yakwiya

  • @SolomonMkandambili
    @SolomonMkandambili 7 дней назад

    How old is he?

  • @TameeraInglis
    @TameeraInglis 7 дней назад

    Inu anagulitsa awa asaname. Kuti samadziwa

  • @Enock-gu5ff
    @Enock-gu5ff 7 дней назад

    Yooh

  • @GodfreyGondwe-b9r
    @GodfreyGondwe-b9r 7 дней назад

    Sanawapusise amaziwa bwino bwino

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 7 дней назад

    Nde agulitsa zambiritu angoliwona kuti boma la Malawi likuyendetsedwa ndi anthu opepera mwapusatu apa kuchenjera konse kurha

  • @EliyasMtotela-o8p
    @EliyasMtotela-o8p 7 дней назад

    Timaziwa ife awawa kayaso gulitsan thetsan zikolo

  • @chirwaellace1093
    @chirwaellace1093 6 дней назад

    Too bad

  • @JamesChiphwanya-m4v
    @JamesChiphwanya-m4v 7 дней назад

    Koma guys mukamamuona kukuyu mutu mwake muli kuganiza kwa umuthu kapena nyani uyutu mutu mwake mulibe kathu lero anena zina mawa akuuzanitso zina mamina okha okha ndithu

  • @WillianBanda-p7d
    @WillianBanda-p7d 7 дней назад

    Angotenga yonse

  • @ThoccoChimbali-h6g
    @ThoccoChimbali-h6g 7 дней назад

    Malawi crocodile 🐊 party (mcp)boma la mbuzi zokha zokha including chakwela

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 7 дней назад

    Amangopanga zinthu mwina mwaphuma,mwinanso ankangoyankhapo za black asakuyidziwa kwenikweni zomwe black box imapanga

  • @OburyInock
    @OburyInock 7 дней назад

    Ichi chimozesi ndichisilu kwambili

  • @WallyMsiska
    @WallyMsiska 7 дней назад

    Zanyanjazo asayesele

  • @NikolasNanawe
    @NikolasNanawe 7 дней назад

    simukuziwa inu kd mwayamba liti kusata nkhani yanyanja inayamba kalekale mwakamuzu president wina aliyese zimachitika pro sanangulise ai

  • @GiftBello-v1i
    @GiftBello-v1i 7 дней назад

    Kenako agulitsa amayi awo , zitsilu za anthu , olo agulitsa Nyanja mavuto adziko ndiye atha , mafuta atengawo adzakhala amalawi adzakhala akugwilitsa ntchito for ever?

    • @zimmekapachika6784
      @zimmekapachika6784 7 дней назад

      😅😅😅😅😂😂😂ndipo agulitsano akazake😅😅😅😅yomweyo Chikangawa party

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 7 дней назад

    Akumkuyu amadziwa chimene akudziwa asatinamizepo apa

  • @RosinaPatel
    @RosinaPatel 7 дней назад

    MCP imaliza Malawi yonse

  • @IsaacMusa-py2jm
    @IsaacMusa-py2jm 7 дней назад

    Nduna yopusa imeneyi

  • @EVERSONBANDA-j8h
    @EVERSONBANDA-j8h 7 дней назад

    Nkhani iyi ya MALIRE a NDUNA okha okha mnzosatheka popanda UN kapenanso AU .

    • @ChavuksFrancois
      @ChavuksFrancois 7 дней назад

      Tsopano ku UN ukoko kuli lamulo limenelo akugwilitsa ntchito a Tanzania. Kodi committee ya azitsogoleri opuma anamumaiko anasankhiddwa kuti aluzanitse maiko awiriwa mu nthawi ya Bingu zinathera pati

  • @HendresonNambazo-u4i
    @HendresonNambazo-u4i 7 дней назад

    Koma Boma ili mmmmmm kaya

  • @JafaliAkimu-ll1bf
    @JafaliAkimu-ll1bf 7 дней назад

    boma la zitsiru ili zokha zokha

  • @YunusuMaulidi
    @YunusuMaulidi 7 дней назад

    A kunkuyu sangaganize chifukwa ali busy nkhani ya report la ndege

  • @vinceynyone6693
    @vinceynyone6693 7 дней назад

    The year to come you will sale even the hole Malawi land, and then wat where we r going to stay Mozambique or Tanzania????

  • @MagieJames
    @MagieJames 7 дней назад

    Kupusa kwa utsogoleri ndye mkumati boma ndlomweli sumukuchita manyanzi mukava kt nyanja yapita

  • @AbdulJohn-t7l
    @AbdulJohn-t7l 7 дней назад

    Koditu azisogoli amcp onse ndi opanda dzelu iwowa ndale samayiziwa? Koma kunkuyu iye sangafutse kuti chimenechi chikuthandawuza chani asanajambulise?chifukwa chake tiku kagulu aka ndi ka mbudzi za asogoleli mwazaza anthu oyendela mamina not brain

  • @kennedybanda
    @kennedybanda 7 дней назад

    The guy doesn't know map reading.

  • @d.chemixjiya5406
    @d.chemixjiya5406 7 дней назад

    Apapa nyanja yapita basi umboni ndi omweu. Kunkuyu the goat

  • @Nelsonmatenda
    @Nelsonmatenda 6 дней назад

    Koma azikwanje osawamanga, kumangowanena ma Bishop

  • @MsondaBanda
    @MsondaBanda 4 дня назад

    No mutu