NAYO DPP ISAZITENGE NGATI NDI ANGELO LERO ..Hot current 19/05/2024 a TTV's CONTENT.

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 1 окт 2024

Комментарии • 72

  • @JustinPhiri-kq2bb
    @JustinPhiri-kq2bb 4 месяца назад +6

    choti muziwe Chakwera sangazawine ampungu ndi amene azachuluke ngati sazapanga alliance

    • @ElesonChalemera
      @ElesonChalemera 4 месяца назад +2

      😂😂Chilungamo chimawa pepani pepani

  • @TarPoor-ye9jx
    @TarPoor-ye9jx 4 месяца назад +3

    And we know kut zodiak, mbc and times media all zili pansi pa mcp does why you scared please try to tell people the Truth not just blaming dpp only what's about mcp

    • @JamesMalango
      @JamesMalango 4 месяца назад +1

      Awanso ndi amantha asaname kuti samanyengerera mukuona ngati anzeru ndinu nokha

  • @SheenahMwalabu-iz3pr
    @SheenahMwalabu-iz3pr 4 месяца назад +3

    Olo mutayankhula bwanji, kulangiza bwanji, Chakwera sangasinthe ndi president wamwano ndioipa sinnaoneko eee. Ndinamukhulupilira koma ndinabetsa, bolanso tikanaika Chilima chifukwa amaoneka kuti zopusa safuna bwenzi zomamenyanazi anthu achipani cholamula kulibe 😢 ndezonse ndinthawi 2025 tiona chifukwa olo mulungu sakukondwa ndazo and l believe kuti malemu Sidik Mia bwenzi akusekelera izi

  • @LastoneBottomane
    @LastoneBottomane 4 месяца назад +2

    Pagulupa wa mcp ndi wonder enawa amangosatila but no wonder this is kandodos TV but zoona chakwera ndiolephera ndipo whether you like it or not mcp ikupita thank you

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn 4 месяца назад +5

    Mwadya banzitu iiiii koma ndalama anakonza

    • @ziyamporoma377
      @ziyamporoma377 4 месяца назад

      Kodi anthu akanena zosakukomelani ndekuti adya banzi? Do you think 20 million tonsefe tingakhale ndi maganizo amodzi?

    • @AleksaWilliams-qc6cn
      @AleksaWilliams-qc6cn 4 месяца назад

      @@ziyamporoma377 mwadya

  • @JusticeKawilira
    @JusticeKawilira 4 месяца назад +1

    Musavutike ndikuyankhula a Malawi akudziwa chabwino ndi choipa ndipo chomwe agwiracho ndi chomwecho DPP woyeeeeee

  • @Abdul-xk8dq
    @Abdul-xk8dq 4 месяца назад +2

    Koma inu simungathe kusiyanisa pa thawi ya dpp ndi ino tili ino?

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 4 месяца назад +1

    Ine mutanena bwanji za zoipa za DPP Koma ine ndikuwona Kuti DPP yinali bwino chifukwa fertilize wunali wosika , makhwara muzipatara analimo chimanga chinali palipose mapassport timawapeza kwina kulikose mosavuta Koma kubwera Kwa MCP moyo wolimba okhaokha angomba ndarama mopanda chisoni ndipo I like DPP

  • @PatrickLucius-bl3te
    @PatrickLucius-bl3te 4 месяца назад +3

    Mufune musafune kaya ndinu a times kaya zodiac koma CHOTI muziwe ndichakuti nkhondo imeneyi Mulung aimenya ndiponso aimaliza yekha.kukanakhala kt peter anakakamila nthawi imene ija bwezi kuli nkhondo yoopsya .koma mulungu anamunong'oneza peter kt zisiye kaye lero anthu azindikila kt chakwela ndi chilima anatinamiza anthu ayambanso kumufuna peter Muthalika .Nkhondo iyi Mulungu aimaliza yekha

  • @JamesMalango
    @JamesMalango 4 месяца назад +3

    Mumaziona ngati anzeru ndinu nokha m'Malawi muno mukamati kut simmanyengerera popeza ndinu amanthanso

    • @AndrewSimakweli
      @AndrewSimakweli 4 месяца назад

      🎉

    • @Allan-bk1
      @Allan-bk1 4 месяца назад

      Mmmm awatu kubwera pa tv ndikusonyeza kulimba mtima

  • @AhmadumkomaTambala-lr9gp
    @AhmadumkomaTambala-lr9gp 4 месяца назад +1

    Inuyo azibambo atatunu mukudya ka 20 zidyan mudziwe kunjakuno kulimulungu komanso mulindiana muzaziona

  • @WhiteRichard-cw2fo
    @WhiteRichard-cw2fo 4 месяца назад +1

    Inu mwayamba kudya ndalama zachakwela iti

  • @JIMMYWATHONJE
    @JIMMYWATHONJE 4 месяца назад +1

    Anyamata a mcp ntchito mukuigwila

  • @YoungScott-p7e
    @YoungScott-p7e 4 месяца назад +5

    Kodi mumalimbana ndi dpp chifukwa chani,Kodi mwaiwala kuti mcp inapha anthu ambiri mu ulamuliro wao motsogozedwa ndi kamuzu Banda,timadziwatu kuti times ndi yakubanja kwa akamuzu,komaso timadziwa kuti ndinu anthu adyera komaso muli mkhwapa mwa mcp.

    • @mosespemba8822
      @mosespemba8822 4 месяца назад

      Umbuli uli ndiinunso 😂😂. You will hate MCP up to when? Mbuzi ya munthu,,

    • @YoungScott-p7e
      @YoungScott-p7e 4 месяца назад

      @@mosespemba8822 you have proven yourself of who you are,the nasty words always represent the real person.

  • @KassimmwStevenetc
    @KassimmwStevenetc 4 месяца назад +1

    Koma athu tiziganiza Chocho maka athu Ali aut Malawi

  • @SamukLungu-zg7fl
    @SamukLungu-zg7fl 4 месяца назад +1

    Vuto ndarama anapanga chakwela amaziwakuti uku ndikayikako chuma asatira ineyo wose amene akuyankhurapa nawoso anadwakare zake

  • @paulkachulu
    @paulkachulu 4 месяца назад

    Everyone knows that DPP has proven their worth, they are not perfect, yes..But they always deliver. You had been in Malawi, you have seen it yourself

  • @TarPoor-ye9jx
    @TarPoor-ye9jx 4 месяца назад +1

    Yes Malawi izi sizingapitise chisogolo dzkoli chkufunika Inu maguys pakanemapa musamaope mukuona kwanga Inuyo madolo mukuopa mcp kut munene chilungamo mukubweza mau kwambiri and mcp ikusaka bakili muluzi tv chifukwa chachlungamo chimene iyeuja amalankhula Malawi yonse kuli Bakili muluzi tv and Bon kalindo saopa munthu and Inu zoona Malo mot boma likhale likuona mavto amalawi akulimbana ndkusaka bakili muluzi tv pali dzeru tonse yalepera pazonse bas we need new leadership chakwela ,chilima ,mutharika sakufunika boma and nankhumwa too we don't want them you should tell them please

  • @RamseyGuveya
    @RamseyGuveya 4 месяца назад +1

    Dpp my vote olo mutanena bwanji

  • @MathewsSande
    @MathewsSande 4 месяца назад

    Mukamatero za dpp zimandinyasa kwambiri sindimafuna kumamva Zina limeneli Peter olo bingu amandinyasanso ndi zimbava zowononga dziko chonde musamatchule zinthu zimenezi

  • @mphatsojuliostandy4918
    @mphatsojuliostandy4918 4 месяца назад +3

    Mvuto la Malawi ndilimenelo saziwa chomwe akufuna ,DPP umakhala chete mukuti iyayi ikuyenera izuke MCP yatayirira chifukwa otsusa akhala chete ikati iyankhule mukuti inalikut isakhale angero lero

  • @cosmaspeter3123
    @cosmaspeter3123 4 месяца назад +1

    Dpp ndi moto

  • @MisheckChinjala
    @MisheckChinjala 4 месяца назад +1

    DPP 2025❤ from Cape Town South Africa Stellenbosch University

  • @DavidPhiri-o6w
    @DavidPhiri-o6w 4 месяца назад

    Achakwera sogolo alibe, peter muthalika sogolo walibe ... Let find someone to lead us these two mubusa ndi professor tiwataye uko atinamiza chani Poti both of them akhala pa mpando wa upresident for 5yrs but nothing did for the nation
    Wonse Kuba, nepotism very excellent... Palibe wina wowapotsa

  • @uchizJoelMumba
    @uchizJoelMumba 4 месяца назад

    Dpp sizabwelanso tiwaleko amene aja amapha anthu achialubino anthu oipa kwabasi

  • @llewellynkhungwa4712
    @llewellynkhungwa4712 4 месяца назад

    Bwana ndevu zamwayi Diso laku right likuoneka lotupatu

  • @chifundocharles2348
    @chifundocharles2348 4 месяца назад

    Title yanu ikusephana ndizomwe akuluakuluwa amakambilana🤣🤣

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 4 месяца назад

    Olo mudye baziii mulungu akuona mmene akuvutikila anthu ake ku malawi azaweluza

  • @SymonPaul-s8h
    @SymonPaul-s8h 4 месяца назад

    Munya muona bolan Dpp ili nd ma pictures abho ku mtundu wa amalawi

  • @BiquitoniNsandamila
    @BiquitoniNsandamila 4 месяца назад +2

    Sindikukaika kuti Nanunso mukudya nawo za chakwera

  • @AllanMafelo
    @AllanMafelo 4 месяца назад +1

    Aaa awasotu amakondela

  • @Patgregorymanyumba
    @Patgregorymanyumba 4 месяца назад

    Zipumi zanu mbuzi za anthu mukuzitenga ngati ndinu opambana

  • @DavidPhiri-o6w
    @DavidPhiri-o6w 4 месяца назад

    Guys mwalunkhula chilungamo, we must never say DPP but Peter muthalika munalipo pamupanfo zinthu zinakukanikani ,,, MCP yilibe vuto, problem ndi Chakwera walephera kukoza dziko.
    These two people please Malawian don't worst our time to vote for them at least they must handover to another person to represent their parties

  • @CyprianoSandalamu
    @CyprianoSandalamu 4 месяца назад +3

    Mcp my vote, during the time of DPP party,we have been killed by DPP party mainly the cost of dry maize,their cost was k60 per kg,but now we are going to admarc to sell dry maize at K650 per kg.But those they are not farming,they cry.Don't cry ,go to field and do farming you will not regret.

    • @husseinsangala3374
      @husseinsangala3374 4 месяца назад

      You are selling that price bcoz of the devaluation your MCP brought but you can't see

  • @MuhireDominic-rw4vf
    @MuhireDominic-rw4vf 4 месяца назад

    Hot current 😂😂🔥🔥🔥❤❤❤

  • @WitnessMpakula-cs1so
    @WitnessMpakula-cs1so 4 месяца назад

    Hot current idatha ndi Brian banda

  • @BrightZionga
    @BrightZionga 4 месяца назад

    Mulungu akudalitseni nonse chifukwa chowaunikira amalawi I love guys inudi simutenga mbali mumangonena chilungamo chokha basi

  • @ziyamporoma377
    @ziyamporoma377 4 месяца назад

    Koma abale look at Wonder & Jona kumasoko ndi mmasayamo kodi anthuwa amenyedwa or I’m I just drunk?

  • @ziyamporoma377
    @ziyamporoma377 4 месяца назад

    Kodi andebvu zamwayi disolo akubulashani kapena Sakhalin bwanji?

  • @DavidPhiri-o6w
    @DavidPhiri-o6w 4 месяца назад

    Peter is musogolele wapha ma albinos ambiri, kuba ndi chisale, nepotism racist Peter galu. DPP yilibe vuto, problem ndi Peter muthalika ndi mudala woipa mutima kwambiri

    • @alexgweje8610
      @alexgweje8610 4 месяца назад +2

      Inu muli ndi umboni Kuti Peter amapha ma komanso Kuba???bwinotu musamatamike ndi kuyankhula nanga anthu akuphedwawa ndi munthalikanso

  • @NoahGodfrey-c5o
    @NoahGodfrey-c5o 4 месяца назад

    Andevu zamwayi mumaseka monyodora mumativetsa kukoma kwambiri kkkk

  • @JafaliAkimu-ll1bf
    @JafaliAkimu-ll1bf 4 месяца назад

    vuto ku mcp kwachuluka mbutuma za anthu anyawu ndi mbuzi zosapita ku xool

  • @AishaChibwana-b8o
    @AishaChibwana-b8o 4 месяца назад

    Ndipo ngati kuli chipani cha manyi nde ndi DPP anyamata inu

  • @geraldtuwaga-iz6ll
    @geraldtuwaga-iz6ll 4 месяца назад

    Bravo to you brilliant and breve gentlemen, you stand for us

  • @JafaliAkimu-ll1bf
    @JafaliAkimu-ll1bf 4 месяца назад

    chakwera ndi mbuzi ya munthu democras samaiwa kuti ndi chani vuto lili pamenepo or kungoti mcp ndi anthu ankhaza ndizitsiru

    • @ElesonChalemera
      @ElesonChalemera 4 месяца назад

      Izitu sizigwila ukamalemba utakwia umadumpha mau Ena 😂😂😂

  • @DennisDonework
    @DennisDonework 4 месяца назад

    Charge mpaka 45,000. Ngati ndi thini la chimanga kapena izicharger. Or magesi kulibe

  • @ChiyembekezoPhiri-sv8nw
    @ChiyembekezoPhiri-sv8nw 4 месяца назад

    Pankuku wayakhula bwino

  • @AlickLayson
    @AlickLayson 4 месяца назад

    47:05

  • @BlessingsLuclus-x2j
    @BlessingsLuclus-x2j 4 месяца назад +2

    Zikulipana ndi dpp chifukwa mbuzi izi zikudya kwachakwela buli ndichakwela

  • @NoahGodfrey-c5o
    @NoahGodfrey-c5o 4 месяца назад

    Wel done ndevu zamwayi

  • @AdenaGuest
    @AdenaGuest 4 месяца назад

    Anthioipamcp

  • @AlickLayson
    @AlickLayson 4 месяца назад

    Zooona xzake

  • @DavidPhiri-o6w
    @DavidPhiri-o6w 4 месяца назад

    Keep up ❤❤❤guys

  • @AdenaGuest
    @AdenaGuest 4 месяца назад

    Achabe

  • @tisuhmakhwah7085
    @tisuhmakhwah7085 4 месяца назад

    mcp

  • @alexmkolongo3089
    @alexmkolongo3089 4 месяца назад

    Mau amphamvu

  • @jemasmasimbi8109
    @jemasmasimbi8109 4 месяца назад

    mmm kupusa bas,,, ngat mulinshunga makwanu