@@MacxwellStuarts-h9r ndipo sindikanziwa Kuti ndi samvakunkhu wa adzibusa. Koma azibusa onse mitima yawo ili choncho?????? Titaya chikhulupiliro mwa Iwo ndithu.
Which is the best way 1 sit down and talk about the interest of our peaple 2 kukwela pa mwala ndi kumakhadzulana? Where there is a mistake you correct it we may choose to shout the mistake oky, but which is which?
Mau amulungu sadzapita pa chabe za masiku otsiriza adzankhala odzikonda onkha odzikujikila okonda ndalama osavela oobala nthawi yake ndi imeneyo achakwela sadzavaso mtaaaa
Bamboo,aaa chonde nthw sili kumbali yathu,amache ndi ababache plus Inu mukudziwa anali ndi mulungu pafupi mulungu wamoyo ku assemblies of God anamugalukila mwadala,nkukaleledwa ndi chirima alibe olo lamba mchiuno atazitolera ndi kutibera,nkukamupha chirima ndi anthu ena 8 nde mukuti titaye nthw ina amalawi tikufa pano tizimupempherera? Ayi pokhapo ine pokhapo khakhale mizimu yonse yamoyo ndi yakufa ineyo ndikuti mukutilakwira,bola mumemeze mmbindikilo wapadziko lonse Kwa okhuzika amabungwe,alendo amaiko ife eni nsanje to chitipa,nkhotakota to mchinji,udzachitike pa usiku wa pakati pa date 10 ndi 15 September kudikila pa 16 kukavota ndinjira yokhayo yokhaulitsira Satan,coz ndokanika kale ameneyo
Osaiwala kupanga subscribe, like and comment 🙏🙏
Powerful message Amen father 🙏🙏🙏🙏
Amen 🙏🙏🙏 and amen thanks you God 🙏🙏. Tiyeni tipephere kolimba Tisalekudya ndikumvala ziiguduli Kut Mulungu Atikhulukire amen🙏🙏🙏
woo my priest. great! preach us/them
Amen 🙏
Lord Jesus Christ help us choose the right leader who can fix our Malawi
Free us from the works Satan
Have mercy on us Lord 🙏🙏🙏
Palibe kumpempherera uyu ayi bola tipempherere APM ndi atsogeli onse a DPP basi uyu kwake ndi kuba kupha ndi kuononga
So inspiring msg
Mwayima pa chilungamo father, uyu sanali m'busa koma anali satan,
Chakwera kuli iweko mtendere ulibe serious kkk tangozimangilila basi uthane nazo, olo ma sausage sakukukomera ataaaa
Anangobisalirako ku assemblies of God mbiri zake nzokupha,ndikuba ameneyo muzimuona nkhopeyo,ine sanandiyerepo mu mtima mwanga
@@StandwellNjoka ndipo kuona kwanu ndendende mmene ndikuonera so ine. Uyu akhonza kuphadi. Nkhope yikuchita kuooopsya iyi eeeeh!!!
Great message
Ndayamba kuzindikila chifukwa Cha ulaliki uwu, chakwera Satan akumugwisa ntchito mulemekezeke ambuye mulungu .
Amenii Powerful preaching
❤❤tiyenayeni chikangawa
Mmmmm very powerful touching!!
Amen, Amen Powerful 🙏
Amen 🙏 🙏
Indeed,and powerful message
Tithandizeni athu amulungu,timedzedwa ndithu mukatitsiya
Powerful prayer.Amen.
Powerful
AMEN 🙏
Ambuye mulowelere nyengo zomwe tikudutsa a Malawi 🇲🇼
Koma chakwela walephela kuposa onse
Powerful message amen and amen Man of God
Very powerful prayer
Koma yaaaaa uku ndiye kulalikila uthenga wabwino wa Yesu Kristu ndipo Mulungu ndiye watiyankhula mdziko lino la Malawi ndipo wakumva amve ndipo osamva akhalebe osamva..... Uku ndiye kulalikila uthenga wabwino....ndadalitsika kwambiri ndi uthengawu .Ambuye akudalitseni Father Alizeo Ntalika
Go deeper Bishop, huuuuum kodi azibusa alalike bwanji kuti ziveke bwino amen and amen 🙏❤️ mere fire 🔥🔥
Mawu abusa
God is talking, go deeper
Ambuye ndinu nokha amene munalenga dziko lakumwamba ndi pansi tikupempha lnu atate kuti mutibweletsele mtendele mudziko mwathu mutisowetsele atsogoleli amene sakulabada za dziko lathu atate ameneo asalazeni kuti dziko lipitilile kuyenda ndi mtendele tipaseni nsogoleli oti aombole dziko lathu Amen
Satana wagwiritsa ntchito m, busa kuzunza ana a Mulungu kufuna kuwononga ma plan a Mulungu❤❤❤❤
❤Amen
Kunena zoona chakwera wachitisa azibusa manyazi ndipo samva ngakhale kuzuzulidwa
@@MacxwellStuarts-h9r ndipo sindikanziwa Kuti ndi samvakunkhu wa adzibusa. Koma azibusa onse mitima yawo ili choncho?????? Titaya chikhulupiliro mwa Iwo ndithu.
Amen and amen powerful
Uyu nde munthu wa mulungud uyu guys 🙏🙏
Powerful massage
Waphadi dziko Chakwera koma trust me Mulungu azalanga yense opanga zoipa ndikupondeleza ena,,,,, all in all Chakwera hs failed
Power full message
Yona akuthawa utumiki nyengo zinavuta panyanja anthu ambili akanafa chimodzimodzi achakwera ana thawa utumiki wamulungu muchurch kukapanga zadziko leio ndizi anthu akuvutika ndi nthenda zamitundumitundu mvula ndiyi yukanika kwazaka.mchitidwe wamathanyula ndiumene una wononga asodomu ndi gomola.ambuye atichitile chifundo tinachita choipa pamasopake
Achakwera kulibe kupuma, uthenga ndiye ndiumenewo
Kkkkkk
Amen ❤
Amen amen ❤
Powerful
Mmmm Achakwra ingoziphani ndithu apa chabwino palibe
Very true
Komadi awa ndamene aja amatiudza kuti atitengera ku kanani awa. Mulungu chitani naye chikangawayu. Watitopetsa ife.
Koma ndikuti Amen Amen
Which is the best way 1 sit down and talk about the interest of our peaple 2 kukwela pa mwala ndi kumakhadzulana? Where there is a mistake you correct it we may choose to shout the mistake oky, but which is which?
Wokonza kulakwa kwa wina iwe ukudziwa kuti akulakwa nkumuikira kumbuyo umadzapweteka nawo limodzi olakwawo,ngati samva muleke dzamva nkhwangwa ili mmutu mwake.
Amen!!!!
Apa mutitenganso ngati adani?
Ifetu tizikupemphrelani , ngakhale inuyo mukutibveka ma unyolo.
Ehh uyu ndioipa muzimuona kukamwaku ngat bwalolandege muzimuyang'anisisa puleyu pakamwapake ngat polowa njoka shatap
Mayi ake amalimbikila kwambiri kumumenya pakamwapo chifukwa chosakhala ndi manyazi poyankhula 15:31
Amen and Amen
Amen amen amen
Chibekete komanso chisilu cha munthu ichi ....amafuna u president usakuziwa kuti boma limayendesedwa bwanji mbuzi iyi ndiye yandikwana
Amen nice player
Mau amulungu sadzapita pa chabe za masiku otsiriza adzankhala odzikonda onkha odzikujikila okonda ndalama osavela oobala nthawi yake ndi imeneyo achakwela sadzavaso mtaaaa
YONAH ABWERERE
Uzivere chisoni zanga
Akusambwadza iwe,awatu waputadala suwatha enanu tamvani.Mulungu waika wakewake kuti awononge dziko lake lomwe.
Amen
Mbusa osankhidwa ndi satana
Zoona BBO MUTHARIKA MURUNGU AKUTSOGORERENI PAKUMATIRARIKIRA .MAU AMBUYE TITHOKONE MURUNGU.
Mmmmm😢😢🙏
amen
Powerful
Ndipo popemphelapo pakufunikadi kwambiri , vula kulibe , njala igonelanso koma atsogoleli anthu aliduuuu ali busy kumangana ndikusaka ngati akusaka mbawala 🙌🙌🙌
😂😂 koma anzanu apumila kuti ai ndithu ukulu wa Ambuye ukuonekera
Chikangawa no chance watiputa dala a malawi, wadziyambitsa yekha mbuzi ya ma mbuzi nde chikangawa amenei tili nae nae chifukwa palibe chichita iye.
Koma chakwerayu ndi manyi ndithu mapwala ake dairy anthu azingokamba zaiye basi tchende lake
God have mercy on your people
Bola pempheroli likamatha apenge misala,kodinu akatolika mesa muli ndikabuku koti munthu akamapanga zosemphana mmamulowera mkameneko? Osangokatuluxa bwanji?
😮😮😮😮😮😮
Mutembeleleswa agalu inu
Emen emen
Chakwela walephela
Chikangawa akut bwanji kumene aliko
Walephelelatu
Tchito ya Mulungu ndi kulanga ndi kuphuzitsana
Mulungu akukhululukireni, dzana lija you fought APM left and right, lero chachitika ndi chani, this is the government you supported
Go deeper a Bishop anthu 🎉🎉🎉🎉🎉
Zina laubusalo mukulakwisa mukamanena chonde ngakhale mulungu kumwambako sakukondwela ndidzinalimeneli mukuononga mbiri yazibusa opephela muchonadi osati zongovala dzinazi ngati malaya
Ame
Komatu uyu sakusoweka pephero loteloyi, Koma kumupepha ambuye kuti amutenge are uyu
Bamboo,aaa chonde nthw sili kumbali yathu,amache ndi ababache plus Inu mukudziwa anali ndi mulungu pafupi mulungu wamoyo ku assemblies of God anamugalukila mwadala,nkukaleledwa ndi chirima alibe olo lamba mchiuno atazitolera ndi kutibera,nkukamupha chirima ndi anthu ena 8 nde mukuti titaye nthw ina amalawi tikufa pano tizimupempherera? Ayi pokhapo ine pokhapo khakhale mizimu yonse yamoyo ndi yakufa ineyo ndikuti mukutilakwira,bola mumemeze mmbindikilo wapadziko lonse Kwa okhuzika amabungwe,alendo amaiko ife eni nsanje to chitipa,nkhotakota to mchinji,udzachitike pa usiku wa pakati pa date 10 ndi 15 September kudikila pa 16 kukavota ndinjira yokhayo yokhaulitsira Satan,coz ndokanika kale ameneyo
Kkkkkk koma ulaliki umenewu munthu wina adzivere chisoni a chakwera
Kodi mkuluyu anali M’busa? Koma zomwe akuchitatu nde zkusiyanatu
Apa pokha mwaiphonya obusa....Satana waponya joka kusankha m'busa kuti achititse Mulungu manyazi!??🤔🤔🤔🤔 Not Mulungu achititse manyazi Satana? Mulungu alibe vuto,ochita manyazi ndiifeyo...Apa sipanandimvekele bwino,mukumva kwanga....
Mulungu achititsa bwanji manyazi satana pamene mbusa wa Mulungu ndi amene wayamba kutumikila maganizo a satana? Apa satana ndi amene ali okondwa kwambiri chifukwa wakwanitsa kumutenga mbusa ndikuyamba kumugwilitsa ntchito zoyipa.
Asatana muli inu nomwe iyaaa
APulesident amva basi
Wena chakwela inhliziyo yakho imbi inzaba
Zona eeeeeeeee tiyeseko ena
Mot tizit sakudziwa koma tidzipephera kut atpatse tsongoreli wabwino. Nga t solom anapepha nzeru wosati chuma aiiii. chakwera akupepha chuma pano wosat nzeru zothandiza athu ayyyyiiiii
Amen Father
Moti muzigwira ntchito yomwe mulungu anakutumani dziko lapansi pano koma mukulowerera za padziko ambuye atithandizire o ma Prophet iz sangapange
Ukutanthauza chani nawe apa ngati fundo ulibe osangokhala bwanji
ndimene akugwilayi kutizindikilitsa momwe Satan amagwiritsila anthu pa dziko lapansi
ndimene akugwilayi kutizindikilitsa momwe Satan amagwiritsila anthu pa dziko lapansi
Remember kut iwoso ndiamalawi ndipo nawoso akuvutika nao ngati uli waganya ukhaula
Abusa acatholi amaphuzila chilichonse chikangawa uli mmadzi
Satana wapinya joka 😅😅😅😅
😂😂😂😂😂😂 zoona koma
Pepani pepani amalawi ine m'malo mwa Akristu onse pali mau makolo athu ankaweta mbuzi ndiye mbuzi zikadya mmunda mwa eni uyenera kukapepesa ndiye ine ndikupepesa kwambiri chifukwa cha mbuzi źimenezi m'malo molalikira uthenga waMulungu ndipo uthenga umeneu mulibemo Mulungu tichenjere tili m'masiku otsiliza mabishop chonde chonde chonde bwererani kwa Mulungu.
Upemphele kuti mudziwe choona
god help the people
Amen father
Chibekete komanso chisilu cha munthu ichi ....amafuna u president usakuziwa kuti boma limayendesedwa bwanji mbuzi iyi ndiye yandikwana
Indeeeeee Mulungu akulankhula yekha apa
Amen
Powerful
Amen Father
Amen
Amen
Amen
Amen