Kodi braz Deen kujambula movie mumapanga ndalama zingati coz ndili ndi ma movies more than 430 but zimandichulukira xochita koma ndiyamba kuzitulusa 2024 mashaallah koma ndikusakabe Sportsmanship
Broz ine mongokulimbikisani movie isamaoneke zachimizi ayi movie ili ndi fundo zedi kma poyakhula zizioneka za serious kwambiri please please ndangoyakhulapo
Mmakwanira guys🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Nice story kp it up guys
Nice One
Thanks bro
Kodi braz Deen kujambula movie mumapanga ndalama zingati coz ndili ndi ma movies more than 430 but zimandichulukira xochita koma ndiyamba kuzitulusa 2024 mashaallah koma ndikusakabe
Sportsmanship
Lets support our girls.
There is lesson we have to learn from it.good move bro
Keep up the good work guys🔥🔥🔥❤❤
Thanks
Broz ine mongokulimbikisani movie isamaoneke zachimizi ayi movie ili ndi fundo zedi kma poyakhula zizioneka za serious kwambiri please please ndangoyakhulapo
See you bro zilibwino
Koma ndiye ndikakafupitu
Ndi short story bro..
Mwaifupikitsa kwambili koma muli malangizo abwino
Next time will make it longer