Lucky Medo Wamu ft Edo G official audio
HTML-код
- Опубликовано: 8 фев 2025
- Iyi ndi nyimbo ya nzimayi yemwe akuvutika pa banja koma powona kuti kwawo sangakamulandile malingana ndi momwe zinalili nthawi yomwe ankalowa m'banja, makolo sanavomeleze kut alowe m'banja. Wakumana nawo mavuto akwawo kwa mamuna am amvela chisoni malingana ndikusamva kwa mwana wawo........
My friend 🎉
Umatha 🔥
Thank you bweziii