Baibulo Bard BB-14_ Mulungu Ndi Wokhulupirika

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 9 фев 2025
  • Baibulo limaphunzitsa zinthu zachilendo kwambiri zokhudza Mulungu. Inde, ali wamphamvu yonse, wodziŵa zonse, ndipo alipo paliponse panthaŵi imodzi; koma nayenso amakhudzidwa mtima. Mu podcast iyi tikuwona umunthu wa Mulungu wa kukhulupirika. Nazi mfundo zingapo zosavuta za m'Baibulo zokhudza Mulungu ndi kukhulupirika.

Комментарии •