A UDF M'Dani Wathu Number One Ndi Chipani Cha DPP - Mr Adbull

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 12 сен 2024
  • As the DPP prepares for its elective convention, it has sent out invitations to other political parties, including the UDF. Mr. Abdull, a supporter of the UDF, believes the UDF should decline the invitation because the DPP has never had the UDF's interests at heart.
    Pamene chipani cha DPP chikukonzekera msonkhano wawo wachisankho, chatumiza zoitanira zipani zina za ndale, kuphatikizapo chipani cha UDF. Bambo Abdull, omwe amatsatira chipani cha UDF, akukhulupirira kuti chipani cha UDF chiyenera kukana kuitanidwako chifukwa DPP sichinakhalepo ndi zofuna za chipani cha UDF.
    #malawi

Комментарии • 56

  • @MosesTangwe
    @MosesTangwe 29 дней назад +6

    Momwe zafikira dzikoli stikuyenera kuyang'ana zambuyo ai.ngati mbuyomu panali zolakwika ndibwino kuziunikirana than kufukulana,fukwa zimenezo sizithandiza

  • @SlindiryLoveness
    @SlindiryLoveness 29 дней назад +1

    Good point my brother awawa achipongwe kwabasi bakili kumupanga theki ndiposo kumumanga muluzi zaziii mupakana mulando watha panopa kamba ka chakwera

  • @WilliamBanda-o5r
    @WilliamBanda-o5r 29 дней назад +3

    Inuyotu mwachidziwikire ndinu wa mcp mwangobisalira ku udf

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 29 дней назад +4

    Koma Awa mwalandira ndarama chani pitani wuko

  • @UseniMailosi
    @UseniMailosi 29 дней назад +3

    UDF DPP Palibe udani sakale simeso❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @yassinn5634
    @yassinn5634 28 дней назад +1

    Munthuyu akunena zoona kwamunthu ozindikira chifukwa ambiri akunena zonyoza mkuluyu ndi a DPP. Panopa UDF poti inatha ilibe zimene ingachite ilibe mphamvu paja azungu anati `IF YOU CANNOT FIGHT THEM JUST JOIN THEM` UDF ikuyendera zimenezo.

  • @user-zj1xx1ic2m
    @user-zj1xx1ic2m 29 дней назад +1

    M'dani wanu kunyumba kwanu nde mudziti M'dani wanu not wathu 😢😢😢

  • @chifundocharles2348
    @chifundocharles2348 29 дней назад +1

    DPP it's best aise❤❤❤ and iwina 2025

  • @BwanaGD
    @BwanaGD 29 дней назад +1

    Kkkkkk iiii baba pepani ndinthu tatiyeni tigokoza pemwe tikufookapo ku UDF ko ndiposo musapiteko sanayitane inu tatiyeni tizigodya nawo ndalama tikulandirazi palibe zeru apa

  • @DavieChiyepa-e5v
    @DavieChiyepa-e5v 29 дней назад +1

    Wamisala iwe sumatha Chichewa

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of 29 дней назад

    Mmmmmmm koma kodi kumangochi kuli anthu azelu chotchi et chilungamo chimawawa

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 29 дней назад +1

    Chipani cha mcp ndichipani cha anthu oyipa kuteleko akufuna zioani zidane komatu izi sizitheka
    ....amalawi chilungamo achiziwa

  • @MauriceMukona
    @MauriceMukona 29 дней назад

    Iwe Abdull,mbolo yako,mawere akawilirana amayanjananso .Quaran & Bible zonsezo zimatiphunzitsa kukhululukirana.

  • @alickkachepa3801
    @alickkachepa3801 29 дней назад

    Ngati ubale awubwezeletsa a MCP ndi mozambique 🇲🇿 pali chani DPP and UDF

  • @Spaw-BTheGogoBoy
    @Spaw-BTheGogoBoy 29 дней назад +1

    Awa lero ayankhula zaziii sakundiwaza

  • @EstherBonga
    @EstherBonga 29 дней назад

    😅😅😅😅 Amagonanso kukamwa kuli yasa kodi sadzamiza ntchetche may chakwela 😂😂😂😂

  • @MjombaMjuba
    @MjombaMjuba 29 дней назад

    Chipani cha UDF chithe kumene, sitikuchifuna. Ine ndine m'chawa koma UDF sindikuyifuna chifukwa Bakili Muluzi ndiamene adapha chipanichi chifukwa cha nsanje. Ndipo uyuyu akunena zowonadi koma chifukwa choti a Chawa ndi mbuzi, zonsezi sakuwona. Dzitsiru a Chawa.

  • @GiftJulius-ro9ev
    @GiftJulius-ro9ev 29 дней назад

    Zowona fada alomwe ndi a manyi.....

  • @sungananigondwe2807
    @sungananigondwe2807 29 дней назад

    Zoona zake ndizimenezo sunaname ase

  • @Hamzamabvuto
    @Hamzamabvuto 29 дней назад +1

    Kuteleko watumidwa wapasidwa ndalama

  • @SlindiryLoveness
    @SlindiryLoveness 29 дней назад

    Koma kukuvala kokhako mwalakwisa ngati inuyo mumavaka zothina siouti winaso azatenga zovala zanu ayi ndiye kumeneko ndikulakwa smile yimene inuyo mulinayo ziyonse alinayo tangonenani zazipnizo koma ukuku mwalowa kwina chilungamo.chiwoneke ngati mazi

  • @NosiphoMazibuko-e9z
    @NosiphoMazibuko-e9z 29 дней назад

    Komadi ndizoona udf udatha chifukwa cha bingu kuyambila nthawi imenyo udf kulibe mpaka lero chulungamo koma Abdul maganizo abwino kwatu kwachuluka anthu obwela ozigulila malo kd kumulanje kulibe malo ife akumangochi timapita kumulanje ai bwanji zimalo abwino choke kumangochi abwelere kwawo kumulanje basi chewa abwele kulelongwe akumatitela ntchito kumangochi apolisi onse achigawo chapakati azipita kwawo akumatitela ntchito kumangochi mupite ku immigration kumangochi achewa okawoka ai abwelele kwawo ntchitoyo ndiyatu atisiyile ife anuwake kusukulu tidapitako ife

  • @ConfusedCheetah-ok9ui
    @ConfusedCheetah-ok9ui 29 дней назад

    Kkkkkk kkkkk ooh koma azibambo anatopa 😂😂😂😂😂😂😂

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of 29 дней назад

    UDF inatha chifukwa cha dpp

  • @DavieKumbanga
    @DavieKumbanga 29 дней назад

    Pita uno iwe

  • @MosesDzonzi-em5px
    @MosesDzonzi-em5px 29 дней назад

    Tayaambapotu kutukwanana tokhatokha Mmmm apa ndiye MCP kuyipatsa mpata kuti idzadutse mosavuta central region ikakunganaa tidzalimba? Tayiganizirani mmene imavotera lilongwe, dowa, dedza, kasungu and etc tilimba? Ulendo uno lilongwe Ndithuditu ifika 1 million plus idzabweza mavoti onse amaboma 11 akumwera enawo kudzangokwaniritsa 50%+1 voter DPP out

  • @MarkGonda-qr4vm
    @MarkGonda-qr4vm 29 дней назад

    Kodi uli ndi udindi wanji kuchipani sukudziwaso kulankhula

  • @AbudulJohn
    @AbudulJohn 29 дней назад

    Abudul za mbuyozo zisiyeni chomwe tikufuna ife ndi umodzi pano pa Malawi ndi mtendele UDF ipiteko bs

  • @AfredMbeta-pk1cn
    @AfredMbeta-pk1cn 29 дней назад

    Good voice for ever

  • @user-kp7le2pu7h
    @user-kp7le2pu7h 29 дней назад

    😂😂😂pa UDF ndi DPP apo ndye wanama ndipo wanamilatu DPP ndi UDF ndi amodzi ndipo amagwirizanaso kwambiri, iweyo wekha ndyemwe uli ndi mvuto ndi zipani ziwirizi

  • @MarkGonda-qr4vm
    @MarkGonda-qr4vm 29 дней назад

    Koma awa nzeru 2014 kunalibe zili panozi

  • @EdwardMathuwa
    @EdwardMathuwa 29 дней назад

    Usadane ndi dpp udf inatha mkale mkale nena za zeru apa what we need is coalition to boot out mcp osamasungila mangawa u can't achieve anything mvuto umbuli siwabwino

  • @BENSONRANGWANI
    @BENSONRANGWANI 29 дней назад

    Chakwelawamupha chilima zasala zosatila Zach

  • @DigleDafter
    @DigleDafter 29 дней назад

    Komatu uyu sakuziwa chomwe akufuna akatero MCP yamudyesa sikono udani ulinawo ndiwe osati onse a UDF ayi

  • @Mpondapromise9
    @Mpondapromise9 29 дней назад

    Otumidwa awa

  • @Bensonmtupa-v8n
    @Bensonmtupa-v8n 29 дней назад

    Zaziii zangokuvutan

  • @DigleDafter
    @DigleDafter 29 дней назад

    Athu sangakuvele iwe mwana wa hule

  • @petertaulo8014
    @petertaulo8014 29 дней назад

    😂😂😂😂 koma ndiye wabandulatu MONICA!

  • @giftmwale8475
    @giftmwale8475 29 дней назад

    Kuvala nde chaninso abakha inu

  • @ZionekaMember
    @ZionekaMember 29 дней назад

    Mukatelo mwaninkhidwa yolankhulila

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 29 дней назад

    Mayi ameneyi kaya anakatengedwa kuti kayi .....amakhala ngati mbuli .....kuyang,ana masowo nkhwezule weniweni

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete 29 дней назад

    Abdullah mukulakhula zoonadi komano ziko mmene lafikiramu tisayang'aneso m'mbuyo khanindikuchosa manyaka amcp awa basi

    • @MjombaMjuba
      @MjombaMjuba 29 дней назад

      Amwene, ndizowonadi DPP ndimene idachotsa ife a UDF m'boma koma lero ife a Chawa, mijomba, tayiwala zimenezo. Achawa ndife atsankho kupambana aTumbuka. Chomwe a Chawa tikufuna nkuti tiwone kuti Atupele Muluzi ali pa mpando wa u president, koma tayiwala kuti president amachita kuvoteledwa ndi Wanthu. Ngati tilibe ma vote okwanila sitingalowe m'boma.

  • @DauglasBowa
    @DauglasBowa 29 дней назад

    So what's going on? what are you trying to say?

  • @SlindiryLoveness
    @SlindiryLoveness 29 дней назад

    Abdullah zinazo takumvani koma zonena zakuphazo mukunama palibo boma limene silinawonongo miyoyo ya anthu mu malawi kodi kuti tikufunseni matafale anafela muwulamuliro wanji achina billy kaunda kuwawasaka mupakana kuthawa mumalawi ndiye mukunena zimenezo musanamizepo anthu apa muzinena chabe za wubwino wachipani chanu osati zakuphazi panopa mcp tikukhala mwaufulu sitinamve kuti munthu wagwida ndiziwaro uko kuti muwone amene kale anali kupanga nkhaza mu mcp ndi amenewoso anapanga zipani zawo kuwukira mcp ndiye nenani zina osati zimene mukunenazo tikususani

  • @user-yh3dw6qu7z
    @user-yh3dw6qu7z 29 дней назад

    Open Openga iwe

  • @AishaChipande
    @AishaChipande 29 дней назад

    Nkhaza anthu inu eeeeee km amalawi 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @user-si7po9sd5i
    @user-si7po9sd5i 29 дней назад

    Galu

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn 29 дней назад

    Ndie udf ingawine payokha? Kunganiza kwabwanji uku

  • @YellowmanMalawi-qe8zh
    @YellowmanMalawi-qe8zh 29 дней назад

    Zakale zapita kaloweni ku mcp

  • @ListerMkandawire
    @ListerMkandawire 29 дней назад

    😂😂😂😂 sukunama aise monica iiishii

  • @MabvutoMichaelPanagona
    @MabvutoMichaelPanagona 29 дней назад

    Bwinotu

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile 29 дней назад

    Munthuyu akunena chilungamo ,mavuto onsewa ndi dpp kugawanisa mutundu no one zambiri zawonongeka mene dpp inafikila Malawi munomm

  • @NoorRasheed-re5vh
    @NoorRasheed-re5vh 29 дней назад

    Adati onongela chipani chathu cha UDF opusa ameneyi

  • @user-dw9zi6bo3o
    @user-dw9zi6bo3o 29 дней назад

    DPP is nasrt, you are very right