Yankhulani Komaliza - Rachel Bandah Ft Favoured Martha (Our National Lyrics) +265992788289

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 18 июл 2023

Комментарии • 272

  • @user-ce6bk9co8k
    @user-ce6bk9co8k 4 месяца назад +9

    Nyimbo iyiyi nsaname ikusitha miyoyo ya anthu ochuluka kwambiri omwe amakhulupilira Mulungu. .

  • @user-zy6sc4nr4m
    @user-zy6sc4nr4m 5 месяцев назад +8

    Mmmm nyimbo iyi ikusuntha nyengo zanga ndipo ili pa repeat ❤❤❤❤

  • @lovekapito6311
    @lovekapito6311 25 дней назад +3

    Amen nyimbo muli uthenga

  • @elidajuma5207
    @elidajuma5207 8 месяцев назад +6

    ndine nsilamu koma uthenga uwu aaa ineyo ndikungoyimvela koma ndikulila ndi nyengo zanga

  • @MercyGondwe-w7s
    @MercyGondwe-w7s 5 дней назад

    Anthufe timakumana ndi ziphinjo zimenezi koma mulungu ndinu final destination no one can paint black if he put white❤❤❤❤

  • @estherbanda6429
    @estherbanda6429 6 месяцев назад +5

    Indeed muli ndi mau omaliza ndinu yawe.only God has the final say ❤❤❤

  • @AgnessMwenyekonde
    @AgnessMwenyekonde 16 дней назад

    Jesus has final say uplifting song ndipo ndadalisika Ambuye ayakhure komalizadi

  • @florencematemba119
    @florencematemba119 10 месяцев назад +11

    First day kuimvera nyimboi was on play me a song program koma nde ndinalira, this song is powerful

  • @BerthaMkonjo
    @BerthaMkonjo Месяц назад +2

    I Like this song❤❤

  • @leahchikhawo9396
    @leahchikhawo9396 16 часов назад

    Eeeeehhh nyimbo yolimbikitsa iyii mmmm ili pa repeat

  • @obvioussimwayi9940
    @obvioussimwayi9940 10 месяцев назад +4

    Ndikudikila mau omaliza yawee chitonzo kuwawa eeeee😢😢😢😢

  • @user-bw1pi2my5j
    @user-bw1pi2my5j 28 дней назад

    Ndinu muli ndimau omalizadi yaweh ❤❤❤ I love this song

  • @rejoicemagulumanya1240
    @rejoicemagulumanya1240 Месяц назад

    Muyankhula liti komalidza Yhawe panyengo zanga😭😭😭😭😭

  • @lawrencemakina2882
    @lawrencemakina2882 Месяц назад

    This is the last days indeed, Glory be to our God

  • @janejere8613
    @janejere8613 3 месяца назад +2

    Nyimbo iri bwino kwambiri. Ambuye alemekezeke kopambana

  • @LouisKashati
    @LouisKashati Месяц назад

    Koma muyakhure komaliza, tatopa mkunenedwa ifeee yaweh

  • @LawrenceMathias-yx8zk
    @LawrenceMathias-yx8zk 3 месяца назад +2

    This is what we call gospel with great messages

  • @GladysJohn-fq6wv
    @GladysJohn-fq6wv 2 месяца назад

    God am waiting for u,kuti muyankhule komaliza nyengo zanga

  • @MadaloNasimba
    @MadaloNasimba 28 дней назад

    powerful message ,God has the last say upon my situation🙏

  • @LINNLYMBETA
    @LINNLYMBETA Месяц назад

    FINAL SAY ILI NDINUYO YEHOVA MUIMILILE PA NYENGO ZANGA KOMANSO PA NYENGO ZATHU HALLELUJAH

  • @mercylipikwa2407
    @mercylipikwa2407 14 дней назад

    Nyimbo iyiyi anayiphika bwino, sanaphule yosapsya

  • @user-su2dq5lr1h
    @user-su2dq5lr1h 2 дня назад

    amen mau omaliza nd ateta kumwamba bas

  • @stellafebbychitimbe8673
    @stellafebbychitimbe8673 3 месяца назад +2

    God is always faithful to his people

  • @harrietchingapa-hj1ev
    @harrietchingapa-hj1ev 2 месяца назад

    yankhulani komaliza ndinu Ambuye 🙏🙏🙏

  • @user-jv4dg2ze4x
    @user-jv4dg2ze4x 4 месяца назад +9

    Thanks to the studio and both of you best singers! Yamenyedwa bwino ! God bless you! My inspirers

  • @user-uw6kf9vn4k
    @user-uw6kf9vn4k 4 месяца назад +2

    Nyimbo ikuyakhula ndi nyengo zanga yakhulani komaliza Yahweh

  • @mailesibanda5812
    @mailesibanda5812 Месяц назад +1

    Powerful song God bless listening in from Zambia

  • @MonicaKudowa
    @MonicaKudowa 27 дней назад

    Yankhulani komaliza pa moyo wanga yahweh

  • @user-yn4pp4sz5p
    @user-yn4pp4sz5p 9 месяцев назад +4

    Only God has the final say

  • @user-cu2fu7vk5i
    @user-cu2fu7vk5i 3 месяца назад

    Yakhurani komaliza ndi inu Yahweh

  • @violetnhlema
    @violetnhlema 2 месяца назад

    Nyimbo imandisutha, very powerful massage.

  • @user-sm8gx4vf1v
    @user-sm8gx4vf1v 10 дней назад

    Lero lino ayankhule komaliza pa nyengo yanga

  • @ConwellSaidi
    @ConwellSaidi 23 дня назад

    Indeed Jesus has the final say
    Uplifting song

  • @Livinessbanda
    @Livinessbanda Месяц назад

    Nyimbo imnei eee imandtengela pena pake ambuye alemekezeke

  • @Elube-ij2rd
    @Elube-ij2rd Месяц назад +1

    Yankhulan komaliza ndinu yaweh eshhhhh ikundisuntha hvy

  • @vutolongwe7108
    @vutolongwe7108 10 месяцев назад +3

    Amen chikhulupirilo changa chili pamawu amaliza so touching 😢

  • @FloraChibambo
    @FloraChibambo 21 день назад

    Amen yankhulani kommaliza yahwew

  • @LindaTebulo-k4w
    @LindaTebulo-k4w 6 дней назад

    Limelo ndie dziko lapansi amakukhazika muzomwe iwe suli muchimenecho

  • @user-im4bs7fk9o
    @user-im4bs7fk9o 3 месяца назад +2

    This indeed touched my heart. Encouraging song.

  • @MasausoPhiri-o4g
    @MasausoPhiri-o4g 23 дня назад

    It is very good song, keep up

  • @WilliamMaduka
    @WilliamMaduka 3 месяца назад +1

    Yankhulani komaliza za Ana anga yaweh

  • @user-yq4qk6pc8w
    @user-yq4qk6pc8w 6 месяцев назад +2

    Very powerful song! Speaking to me

  • @SandraIssa-lo8il
    @SandraIssa-lo8il 9 месяцев назад +2

    Nyimbo yabwino kwambiri. Dziko lapansi limalankhura potengeradi nzeru zake zokha koma inu nokha ndiye mumadziwa munthu chiyambi ndimapeto ake.

  • @user-fx3bw8el5d
    @user-fx3bw8el5d 2 месяца назад

    Only God has a final say indeed!

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 10 месяцев назад +3

    Amen🙏🙏yankhulani koma Liza ndinu yahwe taweruzidwa kwakwana ndinu amene mmadziwa za moyo wanga🙌🙌🙌🔥🔥🔥

  • @Davie-zl1pq
    @Davie-zl1pq 2 месяца назад

    Thank you our artist for more things you sing to me nyengo zanga ndamusiyira yahwe

  • @LawrenceMathias-yx8zk
    @LawrenceMathias-yx8zk 3 месяца назад +1

    This is what we call gospel

  • @user-bc7ct6gp7g
    @user-bc7ct6gp7g 5 месяцев назад +1

    Yankhulani komaliza Yahmweh😭😭🙏🙏🙏

  • @denishonde4090
    @denishonde4090 4 месяца назад +1

    Yankhulan komaliza Yahweh nd moyo wanga

  • @Amina-uc1vq
    @Amina-uc1vq Месяц назад

    Mmmmmmmm ndilibe chonena panyimbo iyiii

  • @user-qh5ow9qf3k
    @user-qh5ow9qf3k 23 дня назад

    Ooh yes Lord final word from you❤

  • @brendapatel3956
    @brendapatel3956 3 месяца назад +1

    The final word, voice of Yahweh

  • @RobertChipala
    @RobertChipala 17 дней назад

    Mmmmmm ndipo sizandikwana nyimbo iyi

  • @user-wr1ef4tp8l
    @user-wr1ef4tp8l 6 месяцев назад

    Ndipo nyimbo imeneyi ikundisutha moyo mwanga

  • @user-fk6cl1rq9z
    @user-fk6cl1rq9z 11 месяцев назад +2

    This song leaves my heart at peace, muli ndi mau omaliza ndinu YAHWE

  • @kingslyshawa9514
    @kingslyshawa9514 4 месяца назад +1

    This is complete, may the good lord continue blessing u and give the desire of your heart ❤️ 💙 💜 💖

  • @LalaNkhoma
    @LalaNkhoma 28 дней назад

    😢😢😢😢😢yakhulani komaliza yahweh

  • @AggieMoyo
    @AggieMoyo Месяц назад

    😭😭😭yankhulani komaliza Yahwe

  • @user-im4bs7fk9o
    @user-im4bs7fk9o 3 месяца назад

    Zoonna Di. Powerful song

  • @Evewachancy
    @Evewachancy 5 дней назад

    Love this song ❤❤❤

  • @chimwemwechimwala3635
    @chimwemwechimwala3635 День назад

    Nyimbo iyiyi ❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @NatashaBema
    @NatashaBema 6 месяцев назад +1

    Muli ndi omaliza ndinu Yahwe pamwana wanga anthu ayankhula ndipo nyimbo iyi imandilimbikitsa panyengo zanga zonse

  • @NatashaBema
    @NatashaBema 21 день назад

    Muli ndi Mau omaliza ndinu Yahwe

  • @user-hj2nt8el2c
    @user-hj2nt8el2c 3 месяца назад +1

    Groly to God having last word to my life

  • @jaqnazombe339
    @jaqnazombe339 3 месяца назад +1

    Yankhulani komaliza ambuye n yakhani mapemphero anga😢😢

  • @EnessKapumaManda
    @EnessKapumaManda Месяц назад

    Zooonadi mulidi ndimau omaliza ndinuyo yawe

  • @LalaNkhoma
    @LalaNkhoma 28 дней назад

    Yakhulani komaliza ndinu y esu

  • @user-uy4dr4ui3z
    @user-uy4dr4ui3z 9 месяцев назад +2

    my national anthem
    my prayer everyday

  • @violabotomani2524
    @violabotomani2524 11 месяцев назад +1

    Yankhulani komaliza Yahweh... Muli ndi mawu omaliza ndinu Yahweh 👏👏👏👏

  • @user-in9sl7nu1i
    @user-in9sl7nu1i 10 месяцев назад +3

    Only God has a final say❤❤

  • @catherinethewe3521
    @catherinethewe3521 6 месяцев назад +1

    Powerful message Rachel, i like the song

  • @AnnieChinkono
    @AnnieChinkono 28 дней назад

    Osintha nyengo ndinu nokha Yahweh
    Mau omaliza ndinundi Yahweh
    Amen.

  • @user-zf9mj4jj9w
    @user-zf9mj4jj9w 3 месяца назад

    Powerful song 🔥🔥🔥

  • @trycekondowe6126
    @trycekondowe6126 9 месяцев назад +2

    Powerful song ❤

  • @Ramseygrahnt99
    @Ramseygrahnt99 4 месяца назад

    Yankhulani komaliza yehova pa moyo wanga, pa mwana wanga ku banja langa komaso zatsogolo langa yahwe🙏🙏

  • @user-yc5bt3vx8i
    @user-yc5bt3vx8i 24 дня назад

    Powerful message 🙌

  • @patricianyimbiri3522
    @patricianyimbiri3522 8 месяцев назад +1

    People can sing eeee, in love with the voice mmmm nyc song

  • @user-ge9xd8mj7g
    @user-ge9xd8mj7g 5 месяцев назад

    Ndavesala mokwanila zomwe ziko likuyakhula 😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢 yakhulani komaliza ndinu yehova osalemphela 😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢

  • @marynkhata9707
    @marynkhata9707 8 месяцев назад

    Nyimbo yabwino yankhulani komaliza Yahweh zikomo pa nyimbo yabwinoyi amen

  • @user-fl6qe4xq1f
    @user-fl6qe4xq1f 10 месяцев назад +1

    Nice song ndaikonda ayankhuledi komaliza yahwee zamoyo wanga😢

  • @BerthaChiyenda
    @BerthaChiyenda 9 месяцев назад +1

    Ndanvetsera mokwanira kuyakhula kwa dziko koma nthawi yakwana yakhulani komaliza baba

  • @user-le4ox7ly9z
    @user-le4ox7ly9z 6 месяцев назад

    He has a final say🙏

  • @patienceMbewe
    @patienceMbewe 10 дней назад

    God has my final say

  • @Davie-zl1pq
    @Davie-zl1pq 2 месяца назад

    The massage is enough.

  • @JaneGwedemu-ds1lp
    @JaneGwedemu-ds1lp 9 месяцев назад +1

    Eish this song eee mau ndilibe yandililitsa ine

  • @DavisKatema
    @DavisKatema 3 месяца назад

    Very powerful song

  • @user-tj7ed7tb6q
    @user-tj7ed7tb6q 7 месяцев назад +1

    Yankhulani komaliza YAHWEH 😢😢😢😢😢😢ohhhh God

  • @user-ok7oh6ck4j
    @user-ok7oh6ck4j 7 месяцев назад +1

    Amen nice song🙏🙏

  • @WilliamMaduka
    @WilliamMaduka 3 месяца назад

    Yankhulani komaliza baba😢😢😢

  • @user-im4bs7fk9o
    @user-im4bs7fk9o 3 месяца назад +1

    Kuthyapula nyimbo kawawa. Keep on moving

  • @LonelyNkosi
    @LonelyNkosi 2 месяца назад

    What a touching gospel song ,,❤,,ndipo this song it's very touching

  • @DorothyShora-kg1md
    @DorothyShora-kg1md 10 месяцев назад +1

    Only you load ndiyangure yehova pamoyo wanga 😭😭

  • @user-kr2qd2yi8p
    @user-kr2qd2yi8p 2 месяца назад

    Mmmmm koma zoonad my national anthem, every day prayer God has a final say 🙏 ❤❤❤

  • @user-wn2rx9pz1n
    @user-wn2rx9pz1n 9 месяцев назад

    Yakhulani komaliza yehovah pamimba yanga imasulidwe mudzina layesu ❤

  • @brendapatel3956
    @brendapatel3956 3 месяца назад

    Oh yes, may a Mulungu ndi mau okhawo a moyo ndi ochita Chita pa nyengo za omudalira iye. Mau enawa asatisunthe, koma a Yahweh.

  • @user-zx3vt6ql6h
    @user-zx3vt6ql6h 8 месяцев назад

    I lyk these song koopsa ndipo ndimainvera dairy olo la 20 pasiku ndipo myimbo imeneyii imangogwilizana ndi nyengo zomwe ndikudusamo

  • @user-xm1xe4fd5m
    @user-xm1xe4fd5m 7 месяцев назад

    Indeed God has the final say to me....musalole Adani anga andiseke...banja ndili nao mwana ai yakhulani komaliza baba😢😢😢

  • @jessiesakala8704
    @jessiesakala8704 3 месяца назад

    Powerful message❤❤❤

  • @user-vb2wf4mi6o
    @user-vb2wf4mi6o Месяц назад

    Nyimbo yabwino kwambiri ndipo nzoonadi Ambuye muli ndi liu lomaliza no matter what

  • @PempheroPhiri-ui9df
    @PempheroPhiri-ui9df 2 месяца назад

    Beautiful gospel ambuye ndinubnokha muli ndi mawu omaliza 🙏