Kangaude: a Malawi ambiri akulemela kamba ka malonda ozembetsa anthu kulowa mdziko muno

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 30 ноя 2024

Комментарии • 104

  • @SliviaJosephy
    @SliviaJosephy 3 дня назад +12

    Apolisi akudziwapo kathu bcz thawi yomwe anagwidwa anthuwa onse akanamangidwa koma izi apolisi akudyera pomwepo

  • @Margaret-t7m
    @Margaret-t7m 3 дня назад +9

    Abel zulanga mulungu apitilile kukulisa malile ako, umayesesa ndithu, am very happy wafika kwathu, a police akuziwana chifukwa anthu ali ndi mulandu angawasiye bwanji okha kuti aziyendetsa galimoto

  • @TriciaMalikebu
    @TriciaMalikebu 21 час назад

    We need akuluakulu ngati awa, God bless & protect you our dear chiefs

  • @CliffordMwale-x4x
    @CliffordMwale-x4x День назад

    Thanks was immigration you are giving good answers.

  • @lastonmasoatenganji-bs5gf
    @lastonmasoatenganji-bs5gf 2 дня назад +1

    Mafumu, Mlungu akusungeni ndikukupatsani madalitso ochuluka. Mumalikonda dziko lathu. Dziko likulira kukhala ndi anthu ngati Inu. 🙏

  • @DamianoMakala
    @DamianoMakala 3 дня назад +2

    Big up to
    The senior chief ,ndi wa nzeru

  • @CliffordMwale-x4x
    @CliffordMwale-x4x День назад +1

    Atola nkhani mukusiya mafunso oyenera monga: " Ndichifukwa chiyani sanawamange zigawenga ndi unyolo, koma anangowasiya onse aziyenda mgalimoto pa okha opanda wapolisi?

  • @gracem-y8p
    @gracem-y8p 2 дня назад +1

    Trafficking is a very complex and dangerous operation. The name and identity of the informer should never have been revealed on national tv, that's putting his life at risk.
    Translation requires line by line osati asking munthu to trandlate the whole story separately, infirmation would be left out
    Serious and urgent Training on Trafficking is required for those working on these Trafficking areas and routes. Authorities are usually involved in facilitating the process and protective of them.
    Its strange that no-one took a video of all this, but this could be because they are protected.

  • @elias.m.chunga
    @elias.m.chunga 22 часа назад

    Mneneli wa apolisi wa bodza ngati uyo🤗🤗🤗🤗🤗

  • @SamNanyenjele
    @SamNanyenjele 3 дня назад +2

    Mafumu opepera

  • @DavidFyson
    @DavidFyson 5 часов назад

    Apolice akudziwapo kanthu chifukwa sakumasuka komaso anthuwa sanamangidwe olo ku sell kwao kulibeko

  • @GeorgeJere-u6o
    @GeorgeJere-u6o 17 часов назад

    Kkkkkk mu police wake uyu kukakhara mngelo😅😅

  • @preciousmlimbika9632
    @preciousmlimbika9632 2 дня назад +1

    wa police yo sakuyankha mafuso mopereka chilimbikitso kwa a Malawi. I dont know how eligible was he kut amupatse udindo ngati umenewo, kuthawa kuyankha mafuso. mmalo moyankha mafuso kumangolankhula chizungu then nkutanthauzira as if kuti anamufusa kuti apange translate

  • @kenamlibanga6517
    @kenamlibanga6517 3 дня назад +1

    The way he is responding bwana a polisiwa akudziwa kanthu amalawi sife ana ......

    • @grayjames904
      @grayjames904 3 дня назад

      That’s my point ndi wakuba

    • @MarthaChizi-h1u
      @MarthaChizi-h1u 3 дня назад

      And akulephera even kuyankha mafunso a simple kwambiri

  • @DavidFyson
    @DavidFyson 5 часов назад

    Eeesh koma guys , nanga anthu okatenga anthuwa kuwabweletsa kunowo basi amangowasiya?

  • @giftstima2613
    @giftstima2613 2 часа назад

    Palibe akufunsa kuti aja anawapeza koyambilirako akunyengana zinatha bwanji?😢

  • @FaniletMasa
    @FaniletMasa 3 дня назад +1

    Muwawuze achapolawo ndimodzi amene akupanga nawo zolowetsa athu abwela muno chifukwa fundo zawo sizikuveka bwino koma amafuso ambiri akuwazemba chifukwa chan

  • @H-nyree
    @H-nyree День назад

    Uyu wapolice sari straight

  • @ExcitedBreakingWaves-oh3zb
    @ExcitedBreakingWaves-oh3zb 21 час назад

    Apolicewo ndiwopusa.nkhaniyo ndiyonvesa chisoni.

  • @CliffordMwale-x4x
    @CliffordMwale-x4x День назад

    Inspector Morris muyambe kuyankha zinthu zomwe zikuchitika osati maganizo anu. Inu ndi public officer (a Malawi anakulembani ntchito). Ntola nkhaniyo amaimilira a Malawi kuti adziwe zoona,; adziwe chomwe chinachitika; osati maganizo anu, kapena momwe inu apolisi mumagwirira ntchito ai. Inu simupiteko komwe mafumu ndi anthu awo anagwira anthu ochokera ku Somalia, pamodzi ndi zimbalangondo zinalowetsa anthuwo. Please learn to inform the Citizens.

  • @atupelemposa4786
    @atupelemposa4786 День назад

    Aliyese aku hustler

  • @PiliraniChalamanda65
    @PiliraniChalamanda65 3 дня назад +2

    Athu amenewo awatulusa nanga bwanji sakuyakha kt athuwo Ali kuti akungoyakha zosephana

  • @MariaSoza-e1m
    @MariaSoza-e1m 3 дня назад +2

    Abel zulanga umaigwila ntchito yotidziwitsa zili kunjaku zikomo ambuye azikutsogolela muchilichomse chako

  • @CliffordMwale-x4x
    @CliffordMwale-x4x День назад

    Mukanafunsa kuti kodi galimoto inathawa ija ndi zigawenga, kodi inagwidwa?

  • @MathewKalinkhu
    @MathewKalinkhu 2 дня назад +4

    Iwe Zulanga, a police aliko abwino koma ambirinso salibwino, mesa timaona a police kuthandizana ndi azikwanje ku Lilongwe kutema anthu amademo.

  • @ProdoBunday
    @ProdoBunday День назад

    Wa police mngelo kkkkkk aaaaa koma
    Uyu mulungu amulange iya

  • @NazeemCarelse
    @NazeemCarelse 2 дня назад +1

    Kodi achakwela, can you call this is a propaganda again? Dzikoli mwaligulitsa koma dziwani chimpdzi sir,siyanitsani pakati pa malawi wakale ndi malawi wapano, mafumu apano ndi akale ndizosiyana ndithu dziwani pangatalike pangafupike mudzachoka m'boma kudalitu anzanu

  • @JaneKadzuwa
    @JaneKadzuwa 3 дня назад +2

    Ndalama ndiyoopsa ndithu

  • @grayjames904
    @grayjames904 3 дня назад +1

    The police Statement can tell kut ndi khuluku mbamva yen yen

  • @WilsonChirwa-t9x
    @WilsonChirwa-t9x День назад

    Wa police akupsyesa mtima kwambili even now I'm regret kuti why I'm behind tv .

  • @ThokoChipinga
    @ThokoChipinga День назад

    Kuchoma sikwazibwana chitetezo chilipo kwambiri mafumu ndi anthu amudzi amamvana kwambiri.achapola akuzemba kwambiri kuyankha ndipo zikuoneka kuti nayeso ndikhalidwe lake.wapolisi mpaka kuphonya kuombera galimoto😂chonde nkhani imeneyi isathere pompa chilungamo chioneke

  • @LongmansLandscaping5
    @LongmansLandscaping5 2 дня назад +1

    Mfumuyi simtumbuka

  • @BlessingsMasakala
    @BlessingsMasakala 3 дня назад +1

    Wapolice uyu ndiochenjela funso limod amachuluka zoyankha zambl komanso kupha nthawi ya abell zulanga kt asafunse mafunso ambl komanso ndiwodziwa kuthawa ndimau 😂1 question amayankhula 400 words eeeish

  • @FrankChanza-l3g
    @FrankChanza-l3g 4 часа назад

    😅😅😅😅km wa police ameneyu kathali wen wen

  • @NazeemCarelse
    @NazeemCarelse 2 дня назад

    That chapola is one of the 1 percent %%

  • @TriciaMalikebu
    @TriciaMalikebu 21 час назад

    The police guy is avoiding answering the questions, not giving facts of what happened or the way thru lost the car, how can they allow zigawenga to drive themselves & worse still at the back of the convoy😀😀😀

  • @ProdoBunday
    @ProdoBunday День назад

    Mneneli wa police yu akukanika kuyankha mafunso akudziwapo kanthu body language ikuchita kunena yokha

  • @MenacePaul-nk1jo
    @MenacePaul-nk1jo День назад

    Asiyeni ifeso timayenda choncho😅😅😅😅😅😅

  • @taombeedward5026
    @taombeedward5026 3 дня назад +1

    Wa police uyu ndi wa zweee ayakha bwanji zosemphana

  • @FunnyKatchenga
    @FunnyKatchenga День назад

    Kodi IG ameneyo kwao ndi kuti? Galu wachabechabe.

  • @FunnyKatchenga
    @FunnyKatchenga День назад

    Ngakhale a IG mayankhulidweo mmmm akudyela momwemo.

  • @kenamlibanga6517
    @kenamlibanga6517 3 дня назад +1

    Bwana apolisiwa chilungamo ngat wankulu wapolisi alibe ........ kulankhula kwavuta ........

  • @PrinceFoster-x9x
    @PrinceFoster-x9x День назад

    A police akudyanawo nawoso sangakambe zoona amenewa akuziwapo kathu muone zikuuakhaiwozo zosephana ndi mafuso

  • @AhamaduhSaidih
    @AhamaduhSaidih 2 дня назад

    😂😂uyu wa police akuziwapo kathu sakufotokoza statement yonveka

  • @cathykabvina3216
    @cathykabvina3216 3 дня назад +1

    Wa police wake ndiyemweyu amamunenayo ma statement ake akunveka mwa katangale

  • @ExcitedBreakingWaves-oh3zb
    @ExcitedBreakingWaves-oh3zb 21 час назад

    Sachita chilichonse.

  • @BlessingShaba-fn2bz
    @BlessingShaba-fn2bz 2 дня назад

    Kkkkkwapolice uyu mmmmm tambwali wenweni

  • @gladyschisomo4324
    @gladyschisomo4324 2 дня назад

    Akudziwana ndi apolice anthu amenewo that's why anawalola kuti mamafiya akwele yawo ayendetseso okha ndekuti ndimmene amapangila akagwidwa kuti athawe bwino then akawatenga ma somalia wo amakawatulutsa kupolice ko nkudzawatenga anthu aja

  • @francismillion1808
    @francismillion1808 День назад

    Zoonadi mmene wa police 😅😅😅😅

  • @WiltonSingini
    @WiltonSingini 2 дня назад

    Wapolice wopusa uyu palibe Cha zelu wanena

  • @jameschiziwa
    @jameschiziwa 3 дня назад

    😂😂😂 Kutetedza malawi eti..
    Munthu akagwidwa amaroredwatso kuyendetsa garimoto?? 😂😂😂😂

  • @ElizabethKazambwe
    @ElizabethKazambwe 2 дня назад

    A police wotu akukhala ngati a zenizeni chosecho ndiomwei ali mgiru lazachinyengo zaziii

  • @chippakaribafox2865
    @chippakaribafox2865 3 дня назад +1

    Chimwenndo bussiness

  • @HawaMamo-q2v
    @HawaMamo-q2v 2 дня назад

    Chimodzi modzi mene amayendela anthu akamabwela ku SA ,alibe mapassport koma eshi zomvuta

  • @HerbartKaphamthengo
    @HerbartKaphamthengo 3 дня назад

    Wapolice uyuyu sakuyankha ngati wapolice akuzembazemba bwanji.ameneyu ndiwachinyengo

  • @IbrahimMatick
    @IbrahimMatick 3 дня назад

    Anthu akamabwera ku jozi kuno opanda passport amapanga chocho bwanji athu mkupanga chocho asiyeni akungodusa sakuba ayi

  • @EstherZintambira-sq3yy
    @EstherZintambira-sq3yy 3 дня назад

    Angelo aaah apolice ake ati kumalawi haha

  • @KondwaniSomanje
    @KondwaniSomanje 3 дня назад

    Aaaa koma wapoluce uyu ndiwochenjeletsa akuthawa mafuso mwina adziwapo kathu

  • @AhamaduhSaidih
    @AhamaduhSaidih 2 дня назад

    😂😂😂😂😂😂😂😂😂wa police uyu nditambwali kwabasi akusephana ndimafuso km gyz

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm 3 дня назад

    Abel zulanga mulungu akuze malire amoyo wako pantchito ukugwira, police ya kumalawi ndie imeneyo

  • @user-gp10.10
    @user-gp10.10 2 дня назад

    Wa police uyuyu ndi mmene akuyankhira,mbambadi akudziwapo kanthu

  • @JamesKondwan
    @JamesKondwan 18 часов назад

    Anthuwo ndi amodzi sangawululane

  • @MisasaRomano
    @MisasaRomano 2 дня назад

    Mafumu athu ndi a community police mulungu adzikudalitsani. Mneneri wapolisi uyu mbuzi ya munthu zikuoneka kuti akudziwapo kanthu. A kulephera kuyankha mafunso omveka bwino. Kuyankha konyoza mafumu omwe agwira ntchito yotamandika kuti mafumu akunama. Shame

  • @lastonmasoatenganji-bs5gf
    @lastonmasoatenganji-bs5gf 2 дня назад

    Police ?????????

  • @FunnyKatchenga
    @FunnyKatchenga День назад

    Apololisi a boma la chakwera ukathyali okhaokha, sakusinthanso zoti akudya ndalama za ma Somalia,kathupi kali gwa. Shame on you.

  • @djmakedzana9917
    @djmakedzana9917 3 дня назад

    Guys mulibe wireless microphones, nthengomu ma cable mbweeeee

  • @dicksonmachilika
    @dicksonmachilika 2 дня назад

    Wapolice zimene wayankhulazo mmmmm.... sizinandigwile mtima.👎👎👎

  • @elizabethziba1652
    @elizabethziba1652 3 дня назад

    Wapolice ameneyi sali bwino ka investigation kakufunika pa ameneyi

  • @SamNanyenjele
    @SamNanyenjele 3 дня назад +1

    Opepera inu osangolandira ndalamazo bwanji muzafa mphawi zisilu inu khosi lalitaliro

    • @EstherZintambira-sq3yy
      @EstherZintambira-sq3yy 3 дня назад

      Kk eti umphawi thoo kumalawi

    • @elizabethziba1652
      @elizabethziba1652 3 дня назад +1

      Aaaaaaa nde uchitsirutu ukaononge Malawi chifukwa Cha 100thousand?

    • @HakeemJossam
      @HakeemJossam 3 дня назад

      Aaaah mk20,000 iwe mkapolodi ndrama imeneyo angatani nao?

    • @EstherZintambira-sq3yy
      @EstherZintambira-sq3yy 3 дня назад

      @HakeemJossam inetu ndimayesa apasa mwina mita mita aah 20 pin yandio per day

    • @gladyschisomo4324
      @gladyschisomo4324 2 дня назад

      Ndalama yake 130 yo? Olo kuli kugawanako agawana zingati naweso wangokhala mphawi wachabechabe

  • @MercyPhiri-u7r
    @MercyPhiri-u7r 3 дня назад

    Anthu akupanga zinyengo mma station mu kapokola iwe

  • @TrizaDzimbiri
    @TrizaDzimbiri 3 дня назад

    Wapolice uyu chirungamo akuchidziwa komano sanganene ai komano ife timangofuna tidziwe nawo kuti anthuwa amapita nawo kuti ??ngati anafika pa point yomawabisa kutchire,komaso ndimawatchula kuti katundu?

  • @MphatsoMaguba
    @MphatsoMaguba 2 дня назад

    Sakuyankha mafunso uyu wapolisiyu aaaaaaaaa

  • @JailosPhiri-sk5ji
    @JailosPhiri-sk5ji 3 дня назад

    Wa police angozikolakola apa😮😮

  • @AustenMasonda-ze4qn
    @AustenMasonda-ze4qn 3 дня назад

    Kkkkk Angelo

  • @FaziluKenneth
    @FaziluKenneth 3 дня назад

    Lp😊😊

  • @GiftHarawa
    @GiftHarawa 3 дня назад

    Sakuankha zomveka ameneo

  • @CardoJustin-l7m
    @CardoJustin-l7m 3 дня назад

    Abel mpaka ku police koma ndiye mukulondolozatu

  • @NickUpoche
    @NickUpoche 3 дня назад +2

    😂😂😂 ifeso ulendo wakuno timayenda choncho asiyeni apitilize ulendo wawo abale.mwatani Kodi?

    • @IbrahimMatick
      @IbrahimMatick 3 дня назад

      Nkhani iyi ndiyoona km alakwanji ngati ampha muthu bwanji aaaaaa a malawi nawo

    • @SliviaJosephy
      @SliviaJosephy 3 дня назад

      Sanadyesele bwino bcz olo Mozambique amatelo zikatsephana 😂😂😅

  • @CardoJustin-l7m
    @CardoJustin-l7m 2 дня назад

    Nneneri uyu ndi galu kwabasi.

  • @mcsellahntv6896
    @mcsellahntv6896 3 дня назад

    Apatu ndiye apolice mwayaluka.

  • @TraverMbewe
    @TraverMbewe 2 дня назад

    Km wa emigration yo ndiwochenjelesa ntambwali

  • @VictorKamanga-v5e
    @VictorKamanga-v5e 3 дня назад

    Wa police uyu muntu wake

  • @preciouskapanga6733
    @preciouskapanga6733 3 дня назад

    Mukuthawa mafunsotu bwana🚮🚮 rubbish

  • @HarrisonNkunika
    @HarrisonNkunika 3 дня назад

    wapolisi opusa uyu galu

  • @omarlux3434
    @omarlux3434 3 дня назад

    Khani mukuyakha ndi iyi siungwilizana

    • @SliviaJosephy
      @SliviaJosephy 3 дня назад

      Ndipo abale inu aaa akuyakha zausilu bwanji

  • @KellyKephas
    @KellyKephas 3 дня назад

    ameneyi akuziwapo khathu koma akumuzimbela koma ❤❤❤

  • @HakeemJossam
    @HakeemJossam 3 дня назад

    Zikhale ati chani?

  • @nkhwaziaeros1845
    @nkhwaziaeros1845 3 дня назад +1

    A polisi awa ndi obhowa. I won’t be surprised if he is involved personally

  • @PiliraniChalamanda65
    @PiliraniChalamanda65 3 дня назад +1

    Wa police uyu ndimmodzi mwawathu amene akuthandizila nchitidwe umenewu ndipo chlichonse wayakhula chaziwikilatu kt Ali gulu lomwelo

  • @EllenChisani
    @EllenChisani 3 дня назад

    Komatu asilikali analiphera kung'ana ndege achilima ndi kumati ndikowilira . Koma anthu akumudzi kukayang'ana masomalia ai zikomo

    • @HerbartKaphamthengo
      @HerbartKaphamthengo 3 дня назад

      Kodi chilima yo mumaona Ngati sadzafa padziko pano palibepo wambewu aliyense adzafa.ndipo kufa kwamunthu kulikosiyanasiyana amene Aja nthawi yawo inakwana kunanakhala Kuti Mulungu anakana Kuti anthu amene Aja safe zikanatheka Koma ndiye Kuti nthawi yawo inakwana

    • @SliviaJosephy
      @SliviaJosephy 3 дня назад

      ​@@HerbartKaphamthengondipo anachita bwino kufa,, kusava

  • @FresherShaba-zc6we
    @FresherShaba-zc6we 3 дня назад

    Koma police. Arephera kuyankha pamenepo