ZOMWE WAYANKHULA MARY CHILIMA CHIMWALILIRENI SAULOS CHILIMA KU MWAMBO YA MISA YOKUMBUKIRA A CHILIMA

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 11 сен 2024

Комментарии • 112

  • @TriciaMalikebu
    @TriciaMalikebu 24 дня назад +8

    Thank you Mrs Dr Mary Chilima for your courage, speaking with love & dignity. In our prayers. We are grateful to the Lord for you & family. We are blessed to have had such a son of the church & a servant of the Lord, may Our Lady intercede for his soul to her Son our Lord Jesus amen 🙏🏽

  • @beatsbymcstevens
    @beatsbymcstevens 24 дня назад +29

    Kaliati is a true servant of the SKC family ❤

  • @RaphaelKweve-u5s
    @RaphaelKweve-u5s 25 дней назад +24

    Skc ,,,nthawi zonse sindidutsa pamene ndaona post yokhudza inu ngakhale Chipani cha UTM,,,,Ndimakhulupilira kuti mumandiyankhulabe kudzera mwa anthu osiyanasiyana omwe amakhulupilira , ndikukonda utsogoleri wanu Mzimu wanu upitilize kutsogolera chipani cha UTM mpaka tsiku lina zolinga zanu zidzakwanilitsidwe,,May your Saul continue Rest in eternal Peace

    • @user-sb3jr1jy2b
      @user-sb3jr1jy2b 24 дня назад +1

      Yes poor recording the message is hardly heard

  • @SusanPilingu
    @SusanPilingu 25 дней назад +14

    Mai Chilima zikomo kwambili chifukwa mwayankhula mawu amphamvu komanso Mai Patrisha kaliyati mumawkondadi achilima tilipambuyo panu mama

  • @MalizeniOliviaBridan
    @MalizeniOliviaBridan 25 дней назад +26

    Koma patirisha ndinu mtsogolelidi okhulupilika pitilizani ndipo saulosi chilima munkankonda kuchokera pansi pantimawanu mwazoona

  • @isaacmikondo
    @isaacmikondo 25 дней назад +49

    Ka voice mumaika koyambililako ndisaname kamandibowaaa😂😂😂

    • @kennedychinguwo1640
      @kennedychinguwo1640 25 дней назад +1

      Ndipo ndi kobowa

    • @isaacmikondo
      @isaacmikondo 25 дней назад +1

      @@kennedychinguwo1640 mayesa ndilipo ndekhatu😆😆😆

    • @lucianogeoffrey4275
      @lucianogeoffrey4275 25 дней назад

      Akulu awa samava nafe tadandaulapo koma amava zake zokha😢

    • @mosysi324
      @mosysi324 25 дней назад +1

      Tiripo ambiri ine ndiye ndimaboweka koposa tayeaani akulu kugula mic abwino chonde

    • @cassimyusuf6683
      @cassimyusuf6683 25 дней назад +2

      Inetu mpaka ndimangopanga fast forward 😂

  • @augustMag
    @augustMag 25 дней назад +10

    Kwa akhristu eni Ake akatolika sitikudabwa pochulidwa kuti ndi odala Dr Chilima mtima wao osamila Kwa Mulungu nthawi zonse pamene anali moyo pansi pano osalafe utimphunzise kuzichepesa koma kukonda Mulungu koposa zonse pamoyo wanthu Dr Chilima indeed rest in internal legend 🙏🙏🙏🙏

  • @gracemaluwa4674
    @gracemaluwa4674 24 дня назад +6

    Mai Kaliati inuyo mumankondadi Chilima ,AMBUYE AKUDALITSENI

  • @jtm7233
    @jtm7233 24 дня назад

    JOYCE 🇲🇼 May God continue to be your strength madam Mary Chilima as you take over the service Your Husband was doing to God. He set us all a very good example of serving God always.
    Indeed may the beautiful Soul of Saulos Chilima rest in Eternal Peace.
    Tisaope, tisatope, tisafooke Ambuye alinafe

  • @spargomw
    @spargomw 25 дней назад +3

    Forever in our hearts. Timkaoda ngat mudachokapo😭😭😭😭 tikukhulupilira tidzaonana nanu mu ulemelero pakut Bible limatitsimikizira kut imfa simathero azonse koma Chiyambi cha moyo wina watsopano😢😢

  • @GeshoMwakitwile
    @GeshoMwakitwile 24 дня назад +8

    Sindikunva kaya ndi foni yanga I don't know

  • @chimwemwemuwalo2426
    @chimwemwemuwalo2426 22 дня назад

    We still pray for the entire family of our beloved dear leader SKC. May God continue taking care as well as protecting the bereaved family

  • @user-eb4pt8wu7p
    @user-eb4pt8wu7p 25 дней назад +3

    We love you skc and UTM

  • @RoseKalamba-nr4dn
    @RoseKalamba-nr4dn 22 дня назад

    May God bless kaliati
    She stood by DPP after demise of bingu
    Now she's by UTM
    This lady is needs support

  • @FrancisNyayi
    @FrancisNyayi 25 дней назад +4

    Rest well our chilima 😢

  • @cecilia-jh3nh
    @cecilia-jh3nh 24 дня назад

    We miss you Dr. SKC! Pray for our beloved country from paradise…❤🎉Thank you Mary Chilima for your love for your husband in life and in death! ❤❤❤

  • @reginamsokera8704
    @reginamsokera8704 24 дня назад +1

    May the father of the fatherless and husband to the widows Jesus Christ continue to comfort you and your children

  • @honestakamata474
    @honestakamata474 24 дня назад +1

    Very powerful speech ❤

  • @corretabanda7685
    @corretabanda7685 25 дней назад +1

    Forever in our hearts Dr SKC

  • @MercyKachenje
    @MercyKachenje 24 дня назад +2

    Mai wachikhulupiriro, Mulungu apitilize kukulimbitsani mama,

  • @AleksaWilliams-qc6cn
    @AleksaWilliams-qc6cn 24 дня назад +2

    Pepani mama zosakhala bwino zomwe zinachitika,koma Mulungu yekha ndie akudziwa zonse

  • @macphallenclement6701
    @macphallenclement6701 9 дней назад

    Rest well SKC you will be remembered forever

  • @MariaBanda-s5k
    @MariaBanda-s5k 20 дней назад

    Mai Patricia Kaliati amamkondadi President wathu Dr SK Chilima,,,, Mulungu akudalitseni mayi

  • @PrincessVifaloma
    @PrincessVifaloma 24 дня назад

    Continue Resting in eternal peace 🕊️ SKC. Forever in our hearts 🥰 and your legacy will forever be our guider

  • @ThokoLungu-tq6pw
    @ThokoLungu-tq6pw 24 дня назад +1

    Forever in our hearts ❤😭

  • @joycembedza-t1i
    @joycembedza-t1i 22 дня назад

    Always in our hearts SKC😢

  • @MacDonaldkachala-cm5gc
    @MacDonaldkachala-cm5gc 25 дней назад +1

    Forever in my heart❤❤❤🙏🙏🙏

  • @Peacechafuwa-bs9xj
    @Peacechafuwa-bs9xj 25 дней назад +1

    May his soul continue rest in peace 🕊️

  • @user-sc7ih4op3l
    @user-sc7ih4op3l 25 дней назад +4

    Koma munthuyu akudutsa mu Nyengo zowawa tisanamepo 😭😭😭😭 anyway mulungu ndiwamkulu mu zose

  • @milliambandah1939
    @milliambandah1939 25 дней назад +2

    Imfa yosaiwalika kwa Malawi RIP

  • @emmanuelchavula7144
    @emmanuelchavula7144 24 дня назад +2

    Kaliyati loved SKC and entire utm party

  • @getrudemsemwe8346
    @getrudemsemwe8346 20 дней назад

    My president forever

  • @MathaNamanja
    @MathaNamanja 24 дня назад

    Mulungu adzikudalitsani Mai Kaliyati nsaname,You are the Pillar,zoonadi Munthu ndi Umunthu nzosiyanadi

  • @lyiemanganjira9708
    @lyiemanganjira9708 25 дней назад +2

    SKC continue to rest in peace 😢

  • @ruthchikhoswe6028
    @ruthchikhoswe6028 25 дней назад +2

    Continue resting in peace SKC🙏

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h 25 дней назад +2

    Skc rest well

  • @JosphineJoshua-gq1rp
    @JosphineJoshua-gq1rp 4 дня назад

    Yes the recording wasn't good as you can hear the sound.but we still stand still with u Mary

  • @user-bi3mt8vs7x
    @user-bi3mt8vs7x 12 дней назад

    Mary chilima amandisangatsa

  • @JosophineKaonga
    @JosophineKaonga 25 дней назад +1

    Wow he was such a dedicated man to his God❤

  • @Lunnah-b1t
    @Lunnah-b1t 24 дня назад

    Be strong mary and ur family

  • @feranjifeza6802
    @feranjifeza6802 24 дня назад +1

    Mpaka lero sindkhulupilira kuti kulibe nthawi zonse ndikaona picture yano mtima wanga umathuthumira ine sindimamvetsa mpaka lero SCK res in external peace

  • @simphiwenyirenda2392
    @simphiwenyirenda2392 23 дня назад

    Rest well skc...munatipweteka😢

  • @CarolineCarlos-dw5bn
    @CarolineCarlos-dw5bn 20 дней назад

    For ever in our hearts

  • @louisbonongwe8537
    @louisbonongwe8537 10 дней назад

    Mai kaliat amankondad SKC

  • @GoodluckVithumbiko
    @GoodluckVithumbiko 25 дней назад +1

    ambuye akhare nase pamene tikukumbukira abare wathu skc mzimu wake uwuse mtendere

  • @nathannbanda3345
    @nathannbanda3345 25 дней назад +1

    Powerful and Consoling speech ever to Malawians

  • @MaggieMaganizo
    @MaggieMaganizo 24 дня назад

    Continue to rest in peace Dr SkC

  • @RuthMasamba-ms2di
    @RuthMasamba-ms2di 24 дня назад

    Continue rest in peace DR SKC mitima yathu idakali yosweka, kma mulungu ekha nde odzwa zoxe

  • @KestonNGUBO
    @KestonNGUBO 24 дня назад

    Ine mupak nizamwalire sizaiwar mupak ines nizanfe kom inusa mukhare president ku chipan chanu mama please please naweya

  • @MariamJohn-dg4em
    @MariamJohn-dg4em 23 дня назад

    Skc rest in peace always 😢😢😢😢

  • @MercyAlfred-c1b
    @MercyAlfred-c1b 20 дней назад

    Speech sikuveka bwino bwino

  • @isabelmartin7567
    @isabelmartin7567 22 дня назад

    Mai kaliati ❤

  • @BrendaMaluwa
    @BrendaMaluwa 22 дня назад

    Koma sizimamveka loud and clear

  • @phillkaunda5623
    @phillkaunda5623 25 дней назад +3

    The recording is nor really good

  • @CharityMkandawire-t8u
    @CharityMkandawire-t8u 25 дней назад

    Continue resting in peace skc❤

  • @harrietmkusangombe
    @harrietmkusangombe 24 дня назад +1

    Continue resting in peace My president SKC

  • @jogechawa6192
    @jogechawa6192 22 дня назад

    Patricia kaliati atha kukhala president

  • @JosephyMhone
    @JosephyMhone 11 дней назад

    Mayi kaliyat amakonda chilima not usi

  • @pauljosephmakaula6835
    @pauljosephmakaula6835 24 дня назад +1

    Plz try to filter this most historical speech

  • @bosheenhakhomba
    @bosheenhakhomba 16 дней назад

    Kumvera kupiliratu

  • @Vincent-k4y
    @Vincent-k4y 25 дней назад +4

    zoon

  • @KateMunthali
    @KateMunthali 25 дней назад

    Mulungu apitilize kukulimbitsa mtima mama

  • @user-jn7bt1uy5s
    @user-jn7bt1uy5s 24 дня назад

    Continue rest in peace skc

  • @benjaminmvuma-rk6mu
    @benjaminmvuma-rk6mu 24 дня назад

    Mmmmm kaliati want the party that's all

  • @GraceGonani
    @GraceGonani 25 дней назад

    Rest in peace skc😭😭

  • @marthamusukwa7935
    @marthamusukwa7935 24 дня назад

    Rest in peace Dr Saulos Chilima

  • @kondwanichiwanda
    @kondwanichiwanda 25 дней назад

    Rest in peace 🕊️ biyeni

  • @DalitsoFrackson-j5u
    @DalitsoFrackson-j5u 15 дней назад

    Poor recording

  • @JoiceMasanjala
    @JoiceMasanjala 24 дня назад

    Rest in peace Mr chilima

  • @DevisonHala
    @DevisonHala 24 дня назад

    Onse ali okhudzidwa payifa imeneyo mulungu awakanthe

  • @user-hh4wn4vf9e
    @user-hh4wn4vf9e 25 дней назад

    ❤❤❤❤

  • @BashirSalanje-qs8ft
    @BashirSalanje-qs8ft 24 дня назад

    Sizikumveka bwino soundyo

  • @cossaphyxo
    @cossaphyxo 25 дней назад +1

    Rest in peace SKC 😢

  • @cmsanyama200
    @cmsanyama200 25 дней назад +2

    Iwe mtsogoleri wa chipani cha Mnthiko wadzuka bwanji?

  • @WeziKamanga
    @WeziKamanga 21 день назад

    Very poor recording

  • @AndrewjemesJemes
    @AndrewjemesJemes 25 дней назад +1

    Manganya alipo koma