Ndipo Zoonadi akuyenera kukonza ndende zanthu coz next year akukalowa ndi Iwo afune asafune kungosintha Boma chakwera pamodzi ndi Nduna Zake Ulendo wa ku Zomba prison.
Kabambe iweyo kalindo bakili muluzi tv peter nose ndamodzi nose alomwe munganene za bwino new MCP kumphatikizaposo namiwa nose ndinu omwe mukuvutika kt mulande boma km mukunama alomwe zelu palibe
I like this boldness speaking of the DC
Listening from Capetown ndi ulemu umene ndimapeleka kwa iwe Kalindo
The DC .The DC..Umakwana pitilizani ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Ndipo Zoonadi akuyenera kukonza ndende zanthu coz next year akukalowa ndi Iwo afune asafune kungosintha Boma chakwera pamodzi ndi Nduna Zake Ulendo wa ku Zomba prison.
Kd DPP inaba ndalama zambili nthawi yomwe mumachoka boma
The last Man standing 🔥🔥💪💪
Kalindo put more fire ✊💪
T/A Njolomole mfumu yaying,ono malinjani chikhamwaz lake same zomwe zikuchutika madela enawo, kod tikhale bwanji dziko lochepa kaleli
Thanks Mr president kalindo thanks
Aboni kalindo simukutopa koma,vuto ife anthu kusava zija mukanena nthawi yamumbuyo ineyo ndikamatsatira maodions anu ndizimene nzikuchitika lelo koma, chachikulu namalenga alowelere chifukwa vuto ndilarikulu.
Kkkk DC ukunena zoona nae manganya wanyanya angoyenda paliponse colinga ceniceni palibe komatu mwala oyenda yenda suyanga zoyanga yanga.DC mwacita bwino kumuzuzula manganya timakunyadilani mumatiyimilira.THE DC MWANA OWOPYA KWAMBIRI.
Bon kalindo amalankhula chilungamo ndipo posachedwapa andale ena akukalowa Kundende
🔥🔥🔥🔥 THE DC
God bless Kalindo
😂😂😂kuotcha zibwethe😂😂😂 my words❤
Zoona zake bwana kalindo🎉🎉
Kalindo the Dc ndinu abwana mphawi wa anthu osauka
Apa phiri lamulanje lija linyasa basi....DC ulemu wako🔥🔥🔥
Ndizoonadi zikuchitikadi ana akumabweza mwina osalembaso mayeso
The Dc mwana owopsaaa kwambr munthu ongoima pachilungamo mulungu azikusunga nd moyo wangwiro
The DC mwaiwala Rumphi.
The DC❤
Kod fertilizer agawa kwaa2 angati paaa2 20m/plus nzelu alibe zanuyo muuzeni choonadi chimumasule
Ndizoonad ngat ife talembedwa mayina anthu tonse a munsika wa bereu chinkhwawa ndimayidi number athu ndipo sindikudziwa kut akufuna akapange nawo chiyan ndiye the DC akunena zoona
Koma chakwera ambuye akuone😢😢😢
Former president, Dr bakili muluzi zazimenezi adalankhurapo kale ,chipani Cha MCP ,mchakupha mtundu onse,ndipo mchankhaza mtundu onse ,mchakuba mtundu onse ,pano kukhalangatinso ndife anthu okudza/ obwela kut chilichonse chomwe angati pange ,tilibe kopita , ,. Malawi dzuka, Malawi dzuka ,dzikoli ndilathu ,
Koma kabambe akhalenso osamala mcp ndicigawenga imagwiritsa ntchito poison kudZera moni wapanja
Zotsekula mmaso kwambiri
Zoona zandramazo ife kwathu ambili ana sakupita kusukulu nkhani yake imeneyo kumangochi ,Lilimbe sukulu.
Kupita koba chigayo, mmalo moyatsa bulb ndikulidza Chigayo...mcp kkkkkkkk
Ku Neno ana akulipira k8000 kwacha Maka Maka pa mchenga primary school
Ndimakunyadilani bro
aziiku songorera murungu iwe bonikarindo
The DC 🔥
Mbambande the DC😂😂
Paja ndi mulowe nzako
Tiliwonkonzeka tinthanawo MCP akunama kwambili,timakunyadilani man kalindo
DC pamakheta primary school ana akupeleka ma 5pin aliyense akuwakakamizanso kuti azipeleka ya phala
Nde mukayankhulayankhula, what's next?
Kunoso ku salima zikuchitika tipelekeleni lipotiro
Koma za chivomerezi chokha A Malawi tiyeni tikhaledi tcheru !!!! B ware of this revelation
Kusowa chochita
Mzimba south
Mapemphero ndiye akufunikadi koopsya mudziko lino
Mlungu wanyankhula?
Nde pamenepo mwalemba kuti Kabambe koma sinanvemo dzina la DK mu audio imeneyi
ku Lilongwe kunoso akukakamiza ndalama imeneyi
MCP ikhumudwa next year, kumene akuona ngati kuli maviti awoko anthu adzavota mosemphana ndizimene akuganiza iwowo, believe me😂😂😂😂😂
Ngati sazabelatu amenewo azakhumudwa sure😂
Vuto ndikusamva kwa anthuwa
❤❤❤❤😂😂😂
Koma abale mulungu akuona zimene akuchita chakwera ndiponso ndikanakhala ineyo kumalawiko sindikana bota
❤❤❤
Hahaha
Akalowe ndiiwowo mwati?
Kabambe iweyo kalindo bakili muluzi tv peter nose ndamodzi nose alomwe munganene za bwino new MCP kumphatikizaposo namiwa nose ndinu omwe mukuvutika kt mulande boma km mukunama alomwe zelu palibe
Hehehe ana anjoka inu mu kulimbana ndi alomwe for why??? Umbuli ndi matenda eti?? Musova Dr Kabambe 2025 boma UTM my vote ❤❤❤❤❤
Kunoso ana akubwezedwa kusukulu akuti ma 3500 koma makola akuyesesa kungwira manganyu kuti alipilile ana ma akulu mmmmmm
Mzuzu city zanyanya
Ndipo amvadi kuwawa ndipo sanati
Nde kalindo mpaka malomvu akunthela chifkwa ulankhula mpaka 2030
Indeee mpaka 2030 tikulamulidwa ndi munthu opanda mnzeru yo zoonadi
T/A mabuka
Chakwera kuja kuno kuli mulungu ndithu
Ase zakumulanjezo ubwino wake ndi kwanu konko uthana nazo wekha ife zisatikhuze tili kutali 😂😂😂🙌🙌onesa kumenyera ufulu kumeneko
The D C
Drama kwambili usi alindchbwana
The thing is this president Mr chakwera he's full of nonsense so next year we will show him the nyenkhwelias
We don't have president in malawi
Ndipo zoona zeni zeni a usi zikoli alilowetsa drama mkulu woputsa uyu
Alomwe dzelu alibe akamanyoza amawona ali nzelu ayi ife sitifuna kunyozako komamfundo
Indeee koma nyau nde zanzeru ana anjoka inu Dr Kabambe 2025 boma UTM my vote ❤❤❤❤❤
Chakwera ndimavuto
Osati ku nyau konko😂😂😂😂
Mmavetsera kuti ndimverako zomwe mwalemba za kabambe koma aaaaii ndithu
Kod bodza limene kufuna ma views
Indee zanzeru ndizija zayankhulidwa ndi nyau dzana zija nde za mnzeru 😂😂😂😂
Mulanjes
Kulomwe belt konko zimenezo,
Uyuyu panopa ndikuona kut akupenga saziwa zomwe akukanba
Bon kalindo number please
❤❤❤❤❤