Это видео недоступно.
Сожалеем об этом.

Lulu - Tinkanena (Audio)

Поделиться
HTML-код
  • Опубликовано: 13 май 2022
  • Off his fourth album Ndakudziwa released in 2013, Tinkanena is one of Lulu's lesser known but powerful song.
    Full lyrics ----------
    Ndinkanena mwanawe momveka
    kunjaku kuli zilombo
    Unkayesa kukuda mwanawe
    kunjaku kuli zilombo
    unkayesa nkhanza mwanawe
    Taona kuli zilombo
    (ndikanena zinkauluka)
    Ine kumalira mwananga usiku ngogona kuli zilombo
    Sunandimvere iwe sunandimvere
    Unkati ife ndiachimidzi
    Unkati fashion sitiyidziwa
    Bwanji sunandimvere iwe sunandimvere
    Ungachepe mwendo nnabala iwe mwananga
    Sunandimvere iwe sunandimvere
    Unkati ife ndiachimidzi
    Unkati fashion sitiyidziwa
    Wadwala nayo fashion
    Zovala zodwalitsa nzotani
    Ungachepe mwendo nnabala iwe mwananga
    Unkayankha motumbwa mwananga
    Umveke ndakula ndatha ine
    Kukula kwaiwe wayamba kunjoya ndi ine
    ndakuvutikirane
    Ndinkalinda mwananga leroli tidziti
    Umange woyera iwe
    Anzako anapindulira
    Ali ndi ma degree
    Iwe degree yako ndi mphasayi
    Taona ooh
    Sunandimvere iwe sunandimvere
    Unkati ife ndiachimidzi
    Unkati fashion sitiyidziwa
    Bwanji sunandimvere iwe sunandimvere
    Ungachepe mwendo nnabala iwe mwananga
    Sunandimvere iwe sunandimvere
    Unkati ife ndiachimidzi
    Unkati fashion sitiyidziwa
    Wadwala nayo fashion
    Zovala zodwalitsa nzotani
    Ungachepe mwendo nnabala iwe mwananga

Комментарии • 12