Bomboclat..... inu tumamva achina WizKid akuimba za state yaku Nigeria konko but we enjoy the song.... talk of nyimbo ina yake ya via Orlando from South Africa.... when rating nyimbo kumakhala ndi reference..... bomboclat
Komatu komwe mukunenako ndikunja if u know what I mean make your research about malawian audience & komwe anthu watchulawa audience yawo it's not the same we can't compare
Ka Mkazi ka ndi mwana mu music amaoneka kuti wayamba kumvera nyimbo kemene I dnt trust her Judgment I've seen in many instance asakuziwa nyimbo Zama artist from way back but anyway akuphunzila soon akhala good analyst
Mista Gray inu mukhala Adani Otani akakhala bridget ndi Adani ama Dimples 😂😂😂😂😂
On point Gray... Pa Chizmo beat iyoyo inali fast and yeyo amalowabe ka slow
Bomboclat..... inu tumamva achina WizKid akuimba za state yaku Nigeria konko but we enjoy the song.... talk of nyimbo ina yake ya via Orlando from South Africa.... when rating nyimbo kumakhala ndi reference..... bomboclat
Komatu komwe mukunenako ndikunja if u know what I mean make your research about malawian audience & komwe anthu watchulawa audience yawo it's not the same we can't compare
Anamva is a Flawless Song From Sean Morgan
Anamva is a good n simple hit for Sean Morgan 🔥🔥🔥
Komaso nyimbo ya charisma ft achina Gutter anse and gwamba
Apala angokumana apali 😅😅😅😅
Ndipo live
If possible bring possible on one of your episodes pilizi
I did not get y Bridget was smiling after mentioning nyimbo ya joe kellz then nduzaona kut it was directed by Leon 😂😂 now I get y
I'm glad you got it 😂😂
43:04 depression is real
Ka Mkazi ka ndi mwana mu music amaoneka kuti wayamba kumvera nyimbo kemene I dnt trust her Judgment I've seen in many instance asakuziwa nyimbo Zama artist from way back but anyway akuphunzila soon akhala good analyst
Yakwanatu 3:00pm ma guys
Mista gray mon kwa camera man
Chizmo anthu nyimbo zina mmamuverera chison tu
Koma maguyz inuyo mumatha
ndikufuna T-Shirt yo
Joe kellz🥳🥰
fire 🔥
Bring back blage
Dekhani abwera
Adani oKuda
Ife tikugodikira inuyo kut tiyendele limodzi
Kodi ndi Hamigo akumveka pansipo?
Yankho & Kay Leon
You must have heard one of those
Aah Hate 🚮😂
😂😂😂😂